KWAGWANJI - KUSANTHULA ZOMWE ZACHITIKA KU UTM 12 July 2024

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 11. 07. 2024

Komentáře • 252

  • @cassimyusuf6683
    @cassimyusuf6683 Před 24 dny +40

    UTM have made a brilliant decision, simungakhale limodzi ndi anthu ankhaza, okhesa mwazi

  • @augustMag
    @augustMag Před 24 dny +11

    Kuganiza mwanzeru UTM palibe chokhalira mu gwirizano pamene mwini wake amene anasayinira kulibe ❤❤❤

    • @user-ty1vq9lq6w
      @user-ty1vq9lq6w Před 24 dny

      Achita bwino kutulukamo ngati ankaonetsa nkhanza chilima alipompo

    • @DinesiKafukiza
      @DinesiKafukiza Před 19 dny +1

      Mbambande zakhalabwinokwambili

  • @CathrineBizza
    @CathrineBizza Před 24 dny +14

    Zandikomela izi till pambuyo panu a utm osafooka

  • @user-im7sc2my4w
    @user-im7sc2my4w Před 24 dny +14

    Tingopempha kuti amene atenge mpando wa chilima akhale munthu wokhwima nzeru ,kuti ma members asabalalike. Mr Usi ,ndi munthu wanzeru ,mumuwone zomwe apange ,musiyeni amalize term yoyambaonga mwa Mr malemu Chilima Mr Usi akhalabe wa UTM ,mudzandikhulupilila

  • @mkhulukinyata5198
    @mkhulukinyata5198 Před 23 dny +1

    Well done UTM..You have made the good decision for being separate it yourself from the Killer's .. I'm from Zimbabwe but my fore-fathers are Malawian's.. So they've been telling us about how Harsh MCP was on that past years ago ..Mapanga bino kuchokha ku muwanthu wakuyipa yawa ..

  • @juliusnjerengo2610
    @juliusnjerengo2610 Před 23 dny +1

    The combination of Brian, Jona and Wonder it is same as Aki, Paw Paw and Sam Loko. Very Entertaining.

  • @user-tf7yi9fp2u
    @user-tf7yi9fp2u Před 24 dny +11

    UTM is intact and is more united after the death and infact many people have joined UTM but don't just see the NEC only. We are set with votes in 2025. Whatever will come out as UTM we will cling to the principles no matter what come may. Viva UTM. If agreement was respected there would have been cordial working relationship. Why out of the full support, campaigning for you and you choose to ill treat him the whole of four years mmmmm not true of being a true Malawian and a Christian. So what is your conscious telling you today? Remember there is always tmrw. Be good to people as you will soon need them. Viva UTM

    • @JohnTchirati
      @JohnTchirati Před 24 dny +1

      MCP imapha kuyamba kare historically, komabe Chakwela is not involved but people around him.

    • @JohnTchirati
      @JohnTchirati Před 24 dny

      Just the remarks oti ndizaimanso? Pa alliance??????

  • @StiveKantiki
    @StiveKantiki Před 24 dny +3

    Banja linali la amayi amagonesedwa nyumba yo dontha lelo amai amwalila mukagulile anawo nyumba adabwa anawo ndi ulemu ukubwelawo amai awo samaziona achitabwino kutuluka l ❤ utm more 🔥

  • @jacobstvn7995
    @jacobstvn7995 Před 24 dny +6

    Malawi lost a visionary leader because MCP greedy behavior....UTM has moved out, let them enjoy the seats!! As Malawi we have not benefited from this alliance....we have been hurt even more!! So disappointing!!

  • @user-fd6oh2vc1c
    @user-fd6oh2vc1c Před 22 dny

    You guys so massive.Wonder u r so wise dear brother….we are proud of you three Big boys.

  • @JohnChiwaya-ym5me
    @JohnChiwaya-ym5me Před 24 dny +3

    Ma guys , you have scrutinised the politics well. Ndakunyadilani zeedi

  • @ThaboMoffia-j7p
    @ThaboMoffia-j7p Před 23 dny +1

    Big up UTM ndipo zamanganyazo ndizosagwiladi mtima zatha zatha osabwelela mbuyo

  • @user-zh9kb2sj2i
    @user-zh9kb2sj2i Před 24 dny +4

    Akanatuluka kalekale chilima sanakamwalila 😢

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w Před 24 dny +4

    Jona pankuku ukunena zoon, Usi si wa UTM, bwanji amakaimila u mp as independent pamene ali mu UTM. Manganya ndi wa MCP basi.

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg Před 24 dny +3

    Achita bwino a UTM kusiyana nadzo dzigawenga dza MCP dzamagazi mmanja 😢😢

  • @ChimwemweBottomani-hc5ju
    @ChimwemweBottomani-hc5ju Před 24 dny +1

    This is brilliant Utm u made a right decision my advice is...dont let USI to join you hes evil like chakwera...congrats team

  • @Christophermalema-o8t
    @Christophermalema-o8t Před 24 dny

    Thanks for your constructive decision UTM.You have made a right channel which will attract some people even to join you & vote for you in 2025 elections.May the almighty God paveway for you.

  • @ahmedwyson4865
    @ahmedwyson4865 Před 24 dny +3

    Apapa nde ma team akumana
    Ndikamamvera nganizi chaaa ndimachita kumva kukhoma

  • @VincentKatimba
    @VincentKatimba Před 24 dny +1

    That's a good distion wamkulu akakhala kuyipa sachita kumuuza amaonera mphepo tiripambuyo panu utm oyeee am I ❤🎉tikulira chilima ife timamukonda kwambiri 😂😂😂😂

  • @user-lz4kc5ob1t
    @user-lz4kc5ob1t Před 24 dny +3

    Ndevu zamwayi munthu wanzeru kwambiri

  • @FrankKambwani
    @FrankKambwani Před 24 dny +2

    Mtsikana wamzeru amati akafunsilidwa ndi mamuna panjira asanalore amapita kukawafotokozera abale ndi makolo ake cholinga onse adziyendera limodzi ndi mtsikanayo mumaganizo...Apapa vuto ndidaliwona ine pa Usi atasankhidwa kuti akhale vp sadapite kwamakolo(utm)kukakhala nao pansi adangoti ndatola banja dzotsatila dzake makolo akudzamuzimudziwa mamuna uja kuti ndi chimbalangondo it's too late ana akwatilana kale.Usi adzikhweza ndithu.😅😅

  • @user-wi8xw9qh7n
    @user-wi8xw9qh7n Před 24 dny +4

    Sitikuwaopa sitifooka mcp must goooo

  • @stanleymatolabanda5460
    @stanleymatolabanda5460 Před 24 dny +4

    Ndangwirizana nazo zomwe chipani changa cha UTM chachita ndipo MCP iyiwale zotenga boma ndipo Chewa Muziwona kwanu kwatha akupha inu

    • @MayorMagombo
      @MayorMagombo Před 24 dny

      You are a liar , mcp is there to stay , you are just waste your time. DPP HAS MANIPULATED YOU SICK PEOPLE.

    • @lillynhlema9656
      @lillynhlema9656 Před 24 dny

      Ndipo achita bwino kwabasi

  • @batsong.chitseko5903
    @batsong.chitseko5903 Před 24 dny +3

    Usi ngwa MCP. kuchoka mu mgwilizano a UTM achita bwino.

  • @JohnConar-kq4hi
    @JohnConar-kq4hi Před 24 dny +1

    That's what I was waiting utm be strong 💪

  • @Lunnah-b1t
    @Lunnah-b1t Před 23 dny

    Mwayakhula bwino zedi ,wakumva wamva,mumatiyimilira guys love from cp,more fire

  • @YOMALO.
    @YOMALO. Před 24 dny +1

    😂guys, you're making the show enjoyable

  • @ChifundoNinje
    @ChifundoNinje Před 24 dny +4

    Mwaganiza mwa mzelu a utm km mubwerere kumeneko munachokela

  • @RobertGoliat-gt2qh
    @RobertGoliat-gt2qh Před 24 dny +1

    Usi ndi wamzeru zakuya and tsiku lina azalankhulanso zamzeru kma UTM yachita bwino kutuluka mumgwirizano

  • @BittonRashid
    @BittonRashid Před 23 dny

    Koma azibambo tikuyamikileni siyamika mukulowa mmanda mumatilankhulila odana nanu ndiodana ndichilungamo.ndakamba izi chifukwa mbalizonse mumagundako osanva asanve zikomo azibambo ❤

  • @SandforeKadzamira
    @SandforeKadzamira Před 24 dny +12

    Brian Banda,sitidzampezanso presenter ngati iwe

  • @user-oj2fy7vx1z
    @user-oj2fy7vx1z Před 22 dny

    Best analysis

  • @mphatsosadiki4983
    @mphatsosadiki4983 Před 24 dny

    Its not too late for UTM kubwelera Kwa make komwe anachokera.......🎉🎉🎉.I would love ma alliance akamachitika azinena zomwe agwilizana .

  • @TonnyDyton
    @TonnyDyton Před 24 dny +1

    Likamatha banja or palafini wamunyali amapopedwamo

  • @user-ml2vw1dc9c
    @user-ml2vw1dc9c Před 24 dny +1

    Lef nthawi coach adachoka 😢😢😢

  • @BlessigsChabzola
    @BlessigsChabzola Před 24 dny +2

    Achita bwino kutuluka chakwera angakhale oyamba kupereka kalata ya upulezidenti kuchipani chawo, osakumbukira zosawakhuza zomwe anasayinira ndi malemu.

  • @leonardgondwe1470
    @leonardgondwe1470 Před 24 dny

    Zoonadi kuti Mr usi wabalalika chifukwa chakuti masapota a utm sakufuna mgwirizano pomwe a usi ndi a vice a boma😊😊😊

  • @WilsonMagongwa
    @WilsonMagongwa Před 23 dny

    Ngati pali kugawikana ku utm koma ochokawo apanga chiganizo chabwino ndale za a Michael Usi zitipwetekesa akufuna iwo okha ziziwayendela bwino kusiya 20 million people omwe akuvutika.

  • @Aqiec09
    @Aqiec09 Před 18 dny +1

    Can you pliz build your own better Malawi than criticizing others , I mean all those with meaningless coments , because I see no one Will ever be perfect on this

  • @user-du9qs4tb6u
    @user-du9qs4tb6u Před 24 dny

    I'm coming to malawi I want to meet you guys well done

  • @user-zh9kb2sj2i
    @user-zh9kb2sj2i Před 24 dny +1

    Inu musapusisike mcp ndiyomweinanenakuti zagwilizano sakuzidziwa

  • @AndersonChiponola
    @AndersonChiponola Před 24 dny +1

    Koma to be honest utm Ikuyenera kukhala pasi kusankha munthu wa nzeru otherwise chipani chawo chitha kudzakhala chopanda tsogoro because to be honest wisdom ya Chilima simugafanizira Anthu amene angoyankhulawa chifukwa foundation ya utm akudziwa bwino ndi Chilima koma vuto anafa Anthu asanawauze zithu. UDF ngati inatha tsogoreri alipo kuli bwanji UTM leader anamwalira kwa ine is no future ku UTM

  • @user-oc8nj3or6y
    @user-oc8nj3or6y Před 24 dny

    We're not afraid anymore ndipo we're going to register with the aim of goin to vote ❤on a serious note,,,we cannot fail to survive that's because of Michel Utsi,,,nono let him do what he can

  • @Cathy-oc7vd
    @Cathy-oc7vd Před 23 dny

    Gwirizano sunathe pano ayi.. unatha 2 years ago, this is just formal panopo

  • @grantnantchito2919
    @grantnantchito2919 Před 24 dny

    To us🎉we had no questions on the Statement made 😢 Don't put us words in our mouths. Decision well made on our behalf

  • @LeviChakwira
    @LeviChakwira Před 24 dny

    This is a great move❤❤❤❤

  • @HappyKanyangala-oq1kk
    @HappyKanyangala-oq1kk Před 24 dny +1

    Amabodxa inu

  • @SlindileAyanda-sz4zw
    @SlindileAyanda-sz4zw Před 23 dny

    That's great idea utm

  • @RemaniBanda-u2n
    @RemaniBanda-u2n Před 24 dny +1

    achita bwino awonezina

  • @lillynhlema9656
    @lillynhlema9656 Před 24 dny +1

    Koma decision ndaikondq
    That's part of kumulemekezq chilima after all the torture he went through with mcp

  • @InnocentEdasi
    @InnocentEdasi Před 24 dny +4

    UTM osafooka🔥🔥🔥. , mzimu wa Chilima wuse mumtendele

  • @MadaKanene
    @MadaKanene Před 24 dny

    Komatu band yagawana zida vinyo atantha kale 😮,,, I think is too late 🕐,,,, when justice delays become injustice

  • @user-un6qv6sj3h
    @user-un6qv6sj3h Před 24 dny +6

    Achita bwino ndithu ❤❤❤

    • @ManninLongwe
      @ManninLongwe Před 24 dny

      Ngati mwatelemu mwathesa mugwilizano amene azayimila usogoleri kumbali yanu ya utm yomwe azakhala pa baluti ndindani?

  • @user-nj5vu8cd5l
    @user-nj5vu8cd5l Před 23 dny

    Usi is good guy, he is not far behavior like Chilima. UTM members don't destroy party because of losing Chilima. Once you will start pointing figure someone in a party you will realize tomorrow when party is going to an end

  • @user-tl9xg4fg9x
    @user-tl9xg4fg9x Před 23 dny

    Zachitabwino mubwelele kumene munachoka kuti tichose chigawengachi

  • @SamuelAntone-mz6nq
    @SamuelAntone-mz6nq Před 22 dny

    Zakhala bwino tidakalila ife malilo wanthu panopa

  • @user-vm7iz6oz6r
    @user-vm7iz6oz6r Před 24 dny

    Zilibwino kwambilili mmm sha,,,wakwiya ndi fit😂😂

  • @samalanimacdonald9373
    @samalanimacdonald9373 Před 23 dny

    Ndenvu zamwayi koma abanda akulakwila chiyan

  • @VanaKhama
    @VanaKhama Před 24 dny

    Amene anathawqpo a yufi ngati ine sangadabwe

  • @user-dg5pc6rz1b
    @user-dg5pc6rz1b Před 24 dny +1

    Mcp yatha koma vuto ndilakuti libela mavoti mfunso nkumati inu azipani mukukonzekela chani kuti nchitidwe obela mavoti usadzachitike?

  • @brainsmkumbwa6267
    @brainsmkumbwa6267 Před 24 dny

    Iam over the moon for the decision made by U.T.M,zaunetsa kuti Chilima wasiya anthu oganiza moyenelera

  • @HarrisMathew-ve5ib
    @HarrisMathew-ve5ib Před 24 dny

    Bravo 👍

  • @allahslave7177
    @allahslave7177 Před 24 dny

    Usi ali ngati munthu wa banja amene ali ndi chibwenzi panja ndipo nachipanga value chibwenzi pamaso pa banja ndiye ankhoswe abanjawo they come to know , thats alibe intereste mwa Usi a Utm

  • @omarmkwanda2184
    @omarmkwanda2184 Před 23 dny

    Micheal usi ndi njoka mu udzu, alibe mtsogolo

  • @user-co3wr3rn4h
    @user-co3wr3rn4h Před 23 dny

    Ife tilinganga pambuyo pa utm phee

  • @NosiphoMazwai
    @NosiphoMazwai Před 24 dny

    Live from capetown

  • @ziggympandakwaya3054
    @ziggympandakwaya3054 Před 24 dny

    Keep the fire burning UTM

  • @madalitsochiumia755
    @madalitsochiumia755 Před 23 dny

    That's great decision UTM

  • @FrancisDominic-w1s
    @FrancisDominic-w1s Před 24 dny +1

    Ausi ngati sasamara azafera kusata

  • @dondamissonchdziwe3958

    Achoka mochedwa atawaphera Kale Chilima,kuimba chiminingo Njobvu zaononga zapita Kale

  • @PatrickMulangala-os4by
    @PatrickMulangala-os4by Před 24 dny +1

    Ndevu za mwayi wadya mbali yake

  • @GeraldMandindi-ll1zq
    @GeraldMandindi-ll1zq Před 24 dny

    Mr usi akusamala ntchito, osati zachipani

  • @BlessingMkonda
    @BlessingMkonda Před 22 dny

    Sats true words

  • @user-vm7iz6oz6r
    @user-vm7iz6oz6r Před 24 dny

    Muziyagana kuno guys mukuopa?

  • @PeterDandaula-ci5un
    @PeterDandaula-ci5un Před 24 dny +1

    Komabe atuluka nkhwangwa ili mmutu kale

  • @fumumdolo7341
    @fumumdolo7341 Před 24 dny

    UTM has made the right political decision. Deputy President was supposed to lead to put the house in order. The guy lacks stamina to judge Malawians mind. USI can't afford to unite UTM it's lost opportunity, he could have demonstrated in presence of his boss. Very tricky situation to USI and MCP.

  • @user-du9qs4tb6u
    @user-du9qs4tb6u Před 24 dny

    A mcp ndi akupha
    Chakwela ndiwe munthu oipa machende ako

  • @gracemkandawire8769
    @gracemkandawire8769 Před 24 dny

    Usi ndi Tambwali,,nanji wakhalila Mpando wonona

  • @user-du9qs4tb6u
    @user-du9qs4tb6u Před 24 dny

    Ausi si wa utm ndi anthu usana

  • @GreyMtungama
    @GreyMtungama Před 24 dny

    Umakwana wonder kikikik ma usher omweo

  • @LawrentNyasulu
    @LawrentNyasulu Před 23 dny

    Koma apamkuku banja latsopabo anthu amagona 4pm akuti usiku umafupika

  • @user-cf9yz3ei5o
    @user-cf9yz3ei5o Před 24 dny

    Bravo Kalitta asiyeni

  • @LinlyNakombe
    @LinlyNakombe Před 23 dny

    Good decision

  • @GodfreyWhayo-hh1dm
    @GodfreyWhayo-hh1dm Před 23 dny

    A MCP adakwera pachulu ndikulengeza kuti wina afune Kaya asafune iwowo adzapambana chisankho ndi 70% . Kodi kapena anaconda kale mwala ?

  • @sylviamsonthe
    @sylviamsonthe Před 24 dny

    Good move❤UTM

  • @gracemkandawire8769
    @gracemkandawire8769 Před 24 dny

    It's too early for questions

  • @user-un6qv6sj3h
    @user-un6qv6sj3h Před 24 dny

    Usi sadakapange consult anzake a UTM kuti andisankha udindo ndiye titani? Koma adangoti mutu gwaaa kukalumbira uyu ngwa MCP basi

  • @user-zh9kb2sj2i
    @user-zh9kb2sj2i Před 24 dny

    Gyz mwayankhulamawu amphamvu kwambili kumapetoku mcp ikudzimva kuti inafikapo anthuose atulukawa anagwilantchitoqambili maka chilima

  • @user-xx4jb9se3z
    @user-xx4jb9se3z Před 23 dny

    Utm my vote

  • @lukepeter8290
    @lukepeter8290 Před 22 dny

    A banda mwati anatani 😅

  • @francisvisage2705
    @francisvisage2705 Před 24 dny

    Body language ya Ndevu Zamwayi can tell Kuti anadyako Chibanzi from MCP

  • @beinhardkausiwa7107
    @beinhardkausiwa7107 Před 23 dny

    Wonder amaonetsera kuti iyeyo ndiwa mcp

  • @princekaponda
    @princekaponda Před 24 dny

    Panja amati azayakhula zambiri pa 19 ... Nde mafutso tizafuse zimenezo , azatiyakhaa

  • @onester4946
    @onester4946 Před 24 dny

    It's so sad to hear that in 2024 mcp is doing what it did during kamuzu era

  • @user-uv5rf4zt5q
    @user-uv5rf4zt5q Před 24 dny

    It's a right decision if they moved out early chilima could be alive today.

  • @user-rp9wy6rd1q
    @user-rp9wy6rd1q Před 24 dny

    Achita bwino 🎉

  • @Aqiec09
    @Aqiec09 Před 18 dny +1

    Chilima was the only perfect leader to utm party enanu ndiye worse wat makes you better than the other political leaders, the problem is that you guys simukufuna usi kudzakhala acting president because of your stiggy minds trust God on this he might guide you better than akhungu okhaokha kutsongorerana njila , that's means your don't love Malawi but being proud to your self intrest

  • @AndersonNason
    @AndersonNason Před 24 dny

    Aiaiaia kodi et

  • @gracemkandawire8769
    @gracemkandawire8769 Před 24 dny

    Palibe chokanila ,,iwe wonder,,,chipanichi chikulondoledwa ndi anthu ,,anachita bwino kukana mafuso

  • @IssaJohn-cb8vn
    @IssaJohn-cb8vn Před 24 dny +1

    Amwene awa ali pakatiwa sindimawavesesa zokamba zawo serious

    • @SheenahMwalabu-iz3pr
      @SheenahMwalabu-iz3pr Před 24 dny

      Ndipo ngati ndinu nokha kkk amamuikilanji kaya. Apapa ikanabeba akanakhalapo a Chunga not Jonayo aaa. Amangodziwa kusokosa ndipo muli fundolesi 😂 mudzitimverako plz a times we love you but uyoyo wavala blueyo apume mu programyi. Ndinakupemphaninso to bring Mr Kapito John, Asowa and muli mutu mmenemuja 😂