KOMA ZOMWE AYANKHULA A MICHAEL USI UKU 🤔🤔🤔

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 8. 09. 2024

Komentáře • 73

  • @matthewskatete4763
    @matthewskatete4763 Před měsícem +7

    Amalawi ndife omvetsa chisoni timasekerera zopusa

  • @AllanJentala-g6h
    @AllanJentala-g6h Před měsícem +6

    ❤❤❤Anthu samvetsa kut munthu nd munthu nthawi zina amafunako kusangalala Dr Usi used songs in his speech only to attract people's attention. Ena akuona ngat akulakwitsa eee koma a malawi mulibe pabwino

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh Před měsícem +2

    Peter sangawine agogo aja akunama

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh Před měsícem +2

    Peter anakanika kuthetsa mavuto ali minister of education apa agogo akukanika kuthetsa mavuto ali mu DPP machende ake peter

  • @KhumboVumu
    @KhumboVumu Před měsícem +1

    He doesn't even know that what will happen after 2025 election sazamuonaso uyu. He was not a real utm member uyu ndi yudasi weni weni

  • @ZionekaMember
    @ZionekaMember Před měsícem +2

    Ndionele Tikufelanji apa

  • @MemoryMbepula
    @MemoryMbepula Před měsícem

    Nothing impresse us the fact that the same chakwera didn't protect Chilima enough. He was abused in his hands. Antaaaa amawo

  • @zionekansinde2817
    @zionekansinde2817 Před měsícem +4

    Mr VP, at the level you are, you didn’t need to respond to this issue in public, go and discuss issues with your SG please. You are acting immature. Zikuchititsa manyazi izizi guys

    • @ChimmsRichardOrden
      @ChimmsRichardOrden Před měsícem

      Akuluwa samamva mupitilizabe kumawanamiza anthu kodi inu simuopa Mulungu? Nthawi yonsei ngongolezo sonali kuti? Musamale

  • @francogibsonkananji9975
    @francogibsonkananji9975 Před měsícem +5

    gyz awa atitayitsa nthawi

  • @ashimfack6423
    @ashimfack6423 Před měsícem

    Intellectual usi so much substance in you

  • @tamalangoma2765
    @tamalangoma2765 Před měsícem +3

    Kupwetekedwa mtima kumeneko koma a makandulo kutukwana ndi kudya kwanu shaaaaa

  • @user-mb8ye1ve5w
    @user-mb8ye1ve5w Před měsícem +2

    Mau omanga dziko, zikomo a Veep Right Honourable Usi

  • @chifundoKaluvi-ey5uw
    @chifundoKaluvi-ey5uw Před měsícem +1

    Nalowa Kut Peter 2025 akutenga boma mungozinamiza

  • @user-qp8kh2hj9o
    @user-qp8kh2hj9o Před měsícem +3

    Uyu ndi mfiti kale lonse samavala za utm chilima alipo bwanji koma satana ndi munthu ndadziwa sopano 😢

  • @Felixgogoda-ke8iy
    @Felixgogoda-ke8iy Před měsícem +1

    Izi ayi sizitithandiza

  • @gracemkandawire8769
    @gracemkandawire8769 Před měsícem +2

    Anthu akungofunako ngongole,,aziwonatu anthu,,,Albie manyazi

  • @GiftJulius-ro9ev
    @GiftJulius-ro9ev Před měsícem

    Dpp no more.....2025 yathela pomwepo...🙋🙋

  • @KennedyPhiri-c7g
    @KennedyPhiri-c7g Před měsícem

    Peter akatenge ngongore or mtukura pakhomo ndi Kaliyati 😂😂😂😂

  • @macksonkalasa9668
    @macksonkalasa9668 Před měsícem

    Exit Everton chimulirenji enters Michael Usi

  • @JafaliAkimu-ll1bf
    @JafaliAkimu-ll1bf Před měsícem +3

    chitsiru cha munthu chigawenga ichi

  • @masterchitabwino898
    @masterchitabwino898 Před měsícem

    Akuyankha anthu ngati akumuzuzula ndi anthu yet akuti akuluzanisa chipani iyeyo ndiyemwe akumwaza chipani. Mudyereni

  • @JamesSeven-ew4ix
    @JamesSeven-ew4ix Před měsícem

    Working hard pays

  • @masterchitabwino898
    @masterchitabwino898 Před měsícem

    Bambo a sikono pa program ya Tikuferanji

  • @MaikNkhoma
    @MaikNkhoma Před měsícem +2

    Bwana mumakwana

  • @EcksonMmanga
    @EcksonMmanga Před měsícem

    Manganya amakapanga sewelo

  • @petertaulo8014
    @petertaulo8014 Před měsícem +2

    Akunamiza ameneyu

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh Před měsícem

    DPP chilichose kunyoza basi musiya 2025 muluzabe

  • @Jaccob-t3t
    @Jaccob-t3t Před měsícem

    😂😂😂😂😂😂😂😂 siukukwana usi

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh Před měsícem

    Mumafuna azisekelera chinkhalamba chanu zopusa basi

  • @user-bs9ny7vl6o
    @user-bs9ny7vl6o Před měsícem

    Nkhan ndi convertion basi athana nawee garu yiweee

  • @jedoforsure2842
    @jedoforsure2842 Před měsícem +1

    Mumakwana big Mr VP

  • @user-je7qi9cr6e
    @user-je7qi9cr6e Před měsícem +1

    China chikuti "ine ayi" kkkk

  • @lacksonsiyadi943
    @lacksonsiyadi943 Před měsícem +2

    Koma anthu mulibe ntchito

  • @JimmyIsaac-xd4ef
    @JimmyIsaac-xd4ef Před měsícem

    Awa satithandiza Kahani ikhale yangongole basi, Koma osamapeleka

    • @PociahMack
      @PociahMack Před měsícem

      Inu nkhan yinkhale Yama candle

  • @GebengaGebenga
    @GebengaGebenga Před měsícem

    Achisiru awa akungoononga ndalama zaboma basi power anthu Akuvutika

  • @petertaulo8014
    @petertaulo8014 Před měsícem +3

    Manyi amuthu

  • @JonesChingaya-yf4gg
    @JonesChingaya-yf4gg Před měsícem

    Iwe Usi ukanene kut President wanena kut tisasankhane, are you serious?? Taonani Ku state house kwazaza achewa, maunduna achewa, kodi kumeneko sikusankhana mitundu.

  • @GeraldMandindi-ll1zq
    @GeraldMandindi-ll1zq Před měsícem

    Uyutu akufuna atipusise za UTM sakuyankhulapo ayi.

  • @christophermtonga8535
    @christophermtonga8535 Před měsícem

    Usi doesnt know true supporters of SKC.

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh Před měsícem

    MCP. Boma

  • @NelsonNyalugwe
    @NelsonNyalugwe Před měsícem

    Useless VP wasting money for nothing going here and there talking nosense while on ground there's empty, too much allowances for him, what a shame!!!

  • @user-cd4df3vg4y
    @user-cd4df3vg4y Před měsícem

    Yudasi uyu

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h Před měsícem

    Awa atitayisa nthawi gys palibe zomwe akukamba agalu awa

  • @Kenmoney-xp7tz
    @Kenmoney-xp7tz Před měsícem

    Chokapa galu iwe okondedwa wako amadya yenna osakugaila? Iwe mbuzi kwabasi

  • @INNOCENTMOFOLO-io8tg
    @INNOCENTMOFOLO-io8tg Před měsícem

    ndàlama ñdiyàchabe ndithu ànthuwà àñgofunà ndàlamazo

  • @user-bd5kw8oq1r
    @user-bd5kw8oq1r Před měsícem

    Anayamba ndi ndi gulu la akaliati ku chita zosayenera kukamba pagulu

  • @MayamikoPhiri-q7c
    @MayamikoPhiri-q7c Před měsícem

    Dr Usi sopano

  • @user-fy5lw8vk9k
    @user-fy5lw8vk9k Před měsícem

    Adangofupika NDI mzeru zomwe

  • @CharlesBanda-kv8bh
    @CharlesBanda-kv8bh Před měsícem

    Inuyo a sg anuyo sayankhula pa public..is she not mature herself?

  • @ChikondiChauma-ib9pg
    @ChikondiChauma-ib9pg Před měsícem

    Hot 265 tipasilen wathu anzeru osat a v p awawa akungonga muthu opepetulidwa

  • @EnerstMwachande-yt5sj
    @EnerstMwachande-yt5sj Před měsícem

    Akuwona ngati ali kundagala

  • @WanangwaMfune
    @WanangwaMfune Před měsícem

    Eeee koma kunari khwimbi mmmm

  • @Elen-n1p
    @Elen-n1p Před měsícem

    Matsiku otsiliza zoona Malawi mwasanduka azisunzo aaaaa n

  • @sadteam2513
    @sadteam2513 Před měsícem

    Kkkkkkk

  • @daviechannel8603
    @daviechannel8603 Před měsícem

    Osagoopeleka bwanji

  • @daviechannel8603
    @daviechannel8603 Před měsícem

    Mmmmmmmm mavuto

  • @jogechawa6192
    @jogechawa6192 Před měsícem

    Watikwana uyu yudasi

  • @Mahamudu-q6b
    @Mahamudu-q6b Před měsícem

    😮😢😢

  • @LuchiKapanga-zy9jh
    @LuchiKapanga-zy9jh Před měsícem

    Chomwe wakuyakhula sakuvhiziwa

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj Před měsícem

    Ndalama tiyeni tisegule maso

  • @MangapeChunga-n1k
    @MangapeChunga-n1k Před měsícem

    Mutukwana mutopa nokha

  • @AlinafeChibwana
    @AlinafeChibwana Před měsícem

    Koma vp mumatha

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y Před měsícem

    Mwapha chilima imwe

  • @SabinaNkhoma-sf7kz
    @SabinaNkhoma-sf7kz Před měsícem +1

    Daily tiziva zangomgole

  • @user-es4jt6ds8m
    @user-es4jt6ds8m Před měsícem

    Galu iwe

  • @chifundoKaluvi-ey5uw
    @chifundoKaluvi-ey5uw Před měsícem

    Akunamawa tikubwela kumamuyika Peter pampando