NDI 50K MUTHA KUPEZA PASSPORT KU MALAWI MU UTSOGOLERI WA CHAKWERA |

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 11. 09. 2024

Komentáře • 35

  • @princekabvina1718
    @princekabvina1718 Před 6 měsíci +1

    Akuti sizinayambike munzimvesesa pilizi 😂😂😂kodi njala et ziyamba mtsogolo let's wait and see ndiChakweratu uyu ndiwabhooza osaiwala

  • @MathewsMANDUTU-lh6oo
    @MathewsMANDUTU-lh6oo Před 6 měsíci +1

    Kaya atasisa kufka pa 4,500mwk sangawine abisale mu passport wanama atsogoleri uyu ndi IDIAMIN wa kumalawi

  • @JafaliAjusa-zg2xi
    @JafaliAjusa-zg2xi Před 6 měsíci +1

    Akunama ine ndinali komko asakupusiseni ,amandiuza kut ngat ndikufuna ya 21 days ndipeleke 550000 thousands Ndipo ndabwerera

  • @neemahkapatamoyo9563
    @neemahkapatamoyo9563 Před 6 měsíci +1

    Campeny imeneyo olo atsitse mesa vote ili mumtima koditu nthawi ikubwerayi zinthu zikhala bwino cholinga mukamuvoteleso nde poti a Malawi pano anawona

  • @user-qq3ip1od6i
    @user-qq3ip1od6i Před 6 měsíci +1

    Campaign mood. This won't take us far,, can't we do things for the best interest of country

  • @VictoriaKumwenda-k6o
    @VictoriaKumwenda-k6o Před 6 měsíci +1

    Mmaziwa kutukwana adpp yatsika passport ku malawi

  • @user-mp9ed2gh6u
    @user-mp9ed2gh6u Před 6 měsíci +1

    Ayamba lit ,team ya beach soccer mapreyer 8 akanika kupeze ma passport waboza iwe😂😂😂😂

  • @HarrisonMwanga-xy4sc
    @HarrisonMwanga-xy4sc Před 6 měsíci +1

    Ndizoona zina zikachitika,kumayamikila.apa,zambili zisitha.

  • @TiyaMtete-o3h
    @TiyaMtete-o3h Před 6 měsíci +1

    Yadula yimeneyo 16 pages out of 60 and 5years expired out of 10 years

  • @abdulrafiquekalembo469
    @abdulrafiquekalembo469 Před 6 měsíci +1

    Umbuli inuuuu.passport akupanga aDzuka publishing company komanso ma page alipo 16 expires in 5yrs mmalo mwa 10.akudziwa kuti ambirinu ndi ambuli akinamizani mosavuta.
    Palibe progress.Campany imene inkapanga ma passport ija inatenga ma security features ena ndipo iyi akupanga agalu amanewayi ndiyosavuta kuyiba anthu kukasintha ma features. Fufuzani bwino misanayambe kunyadira izi aMalaei inuuuuuu Eish aMalawiiiii.Inu mchifukwa a ndale savutika kukunamizanitu. Ubulutu too much

  • @ElatonGwaza
    @ElatonGwaza Před 6 měsíci +1

    Koma abale mukati izankhala 15 lero mukuti 50 zasiya ndikale pamenepa

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 Před 5 měsíci

    M C P useless government mbamva zokhazokha kulibe ma passport angofuna kukuberani ma 50 pin anuwo

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 Před 5 měsíci

    Ndi waboza uyu kulibe ma passport akungonamiza anthu kungofuna kubera basi kulibe chazeru kumeneko 😢😢

  • @alfredbanda886
    @alfredbanda886 Před 6 měsíci

    Under Mbuziiiii Government Chi Bulutu Chakwela Nyawuuuu

  • @MaryTchapo-py4hh
    @MaryTchapo-py4hh Před 6 měsíci +1

    Yachoka pa 14000 kufika pa 50000

  • @KarimSydney-d6p
    @KarimSydney-d6p Před 6 měsíci +1

    Pokhapo chakwera wakhalako ngati munthu

  • @user-pj3qi7gb3s
    @user-pj3qi7gb3s Před 6 měsíci +1

    Ine ndabwelela komweko

  • @Abdul-xk8dq
    @Abdul-xk8dq Před 6 měsíci +1

    Ukutandauza chiyani poti amkati k14.000 lelo ukuti k50.000 😂

  • @user-po6ir6eh4z
    @user-po6ir6eh4z Před 6 měsíci

    Chakwera ndi boma lake ndi mbava zotheratu kubisalira mzina la Mulungu agalu amenewa sazawinabe

  • @patricgama4788
    @patricgama4788 Před 6 měsíci +2

    Ayamba liti wabodza iwe

  • @user-pj3qi7gb3s
    @user-pj3qi7gb3s Před 6 měsíci +1

    WA MCP iwe choka apa

  • @WakisaMwaulambo-wt7rn

    How can you check for your passport when it's ready ?

  • @chesuman7227
    @chesuman7227 Před 6 měsíci +1

    Bola zikhale zoona

  • @rashidlamos3403
    @rashidlamos3403 Před 6 měsíci +1

    Koma zoonad izi

  • @patricgama4788
    @patricgama4788 Před 6 měsíci +1

    Iwetu ndi chakwela wakoyo

  • @user-mh8ji1wd7f
    @user-mh8ji1wd7f Před 6 měsíci +1

    Mwayambapi kampeni

  • @user-xt2gu9yt9q
    @user-xt2gu9yt9q Před 6 měsíci

    Mapasipoti kale anali 14000 or atakhala 50,000 sitengo waukulu komaso thawi yose dzaka 5 zatha apa tikupita kukapeni zakutumbo galu wachabe chabe

    • @neemahkapatamoyo9563
      @neemahkapatamoyo9563 Před 6 měsíci +1

      Kkkkkk Koma guys eish ayi Zikomo komaso pa 50 afunaso kenakake kapamwamba izifikaso 120 Kuti ituluke

  • @BFWCPHIRI1978
    @BFWCPHIRI1978 Před 6 měsíci

    Boma loyendetsedwa ndi ma mafia obisala mdzina la Mulungu, koma ali ana anjoka.zoona angamati passport atsitsa yet achotsa 5yrs ku passport ndi ma peji 44 pa mtengo wa k50 pin cholinga chawo mchani kodi? Pa dziko lonse la pansi maiko onse ma passport amatha mu 10yrs tsano Chakwela waganiza bwanji kuti uchotse 5yrs?

  • @NgomaRaheem
    @NgomaRaheem Před 6 měsíci

    Passport yatsika yosayamba? Zopepera et

  • @MaryTchapo-py4hh
    @MaryTchapo-py4hh Před 6 měsíci +1

    Bodza iwe

  • @chriskamzy7083
    @chriskamzy7083 Před 6 měsíci

    Anati 4500 not 50pin apa siinasikebe potengera ndi deal yathu

  • @user-iy8vi7nn8r
    @user-iy8vi7nn8r Před 6 měsíci

    Useless if he was wise he was going to drop prices on feltrizer and other basic needs and then passport

  • @user-si7po9sd5i
    @user-si7po9sd5i Před 6 měsíci

    Campaign iyi tikudziwa