Fuji Mw - Anadziwa kale (official Music Video)

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 21. 06. 2024
  • #trending #malawi #zambia #africa #afrobeat #music #zimbabwe
    Verse 1
    Umandigwila zanja tikamayenda
    Umaimba phone ukandisowa
    Naneso khawa mtima zimandigwila
    Zinthu zanga zonse et wosayenda
    Makolo achoka ubwere pa den bwanji
    Makolo achokapoo nanga ukuopelaji
    Tandiuze nanga ubwela nthawi iti ndakupatsa plan plan
    Nanga tikumane chapati kwathu kuno samakudziwa ndani?
    Hook
    Anadziwa kale makolo anga
    Anadziwa kale makolo anga
    Kuti iweyo ndi chibwenzi changa
    Kuti iweyo ndi chibwenzi changa
    Anadziwa kale makolo anga
    Kuti iweyo ndi chibwenzi changa
    Kuti iweyo ndi chibwenzi changa
    Verse 2
    Umakhala nane tsiku lonse
    Umayenda nane pali ponse
    Ndikankhumudwa kunyumba kwathu amadziwa
    ikamatsika misozi amadziwa ndayambana nawe
    Or mukakumana, manyazi mumachitilana
    Mukakumanaaaaa mumangoyang'anana
    Tandiuze nanga ubwela nthawi iti ndakupatsa plan plan
    Nanga tikumane chapati kwathu kuno samakudziwa ndani
    Hook
    Anadziwa kale makolo anga
    Anadziwa kale makolo anga
    Kuti iweyo ndi chibwenzi changa
    Kuti iweyo ndi chibwenzi changa
    Anadziwa kale makolo anga
    Kuti iweyo ndi chibwenzi changa
    Kuti iweyo ndi chibwenzi changa

Komentáře • 9