MUNTHU WAMULUNGU kuling'alura boma la CHAKWERA...lalephera

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 1. 07. 2024
  • Video from HONEST

Komentáře • 82

  • @harrisonkalimbakatha5339

    That's a very greatful speech we need such type of people who can't fear but they stand for the right thing keep it up pastor/bishop

  • @user-bu4wn5br5l
    @user-bu4wn5br5l Před dnem +3

    I LIKE YOU FATHER AWUZIDWE ZOONA NGAKHALE ALI OSAMVA KOMA TIDZAWONANA PA 2025

  • @AlexManuelMisomali-sv1vn

    You have spoken wisely and positively to all the audience that's true kuti this government of Chakwera and his tonse alliance have totally failed and destroyed Malawian economy and it will be difficult for the next government to restore it

  • @user-cy9zp4fb2m
    @user-cy9zp4fb2m Před dnem +2

    Muli nzeru umu this audio shud reach to the state 🏠

  • @user-ui4ux5kc8d
    @user-ui4ux5kc8d Před dnem +2

    Ndipo zimafunika kutii uthengawu uwafikire ndithu ukulu amenewa munthu osamva ngati ameneyi sindinamuonepo inee maulendo mbwee mbwee

  • @stanleymollen7273
    @stanleymollen7273 Před dnem +4

    A patriot.....kuphunzitsa economics momveka bwino...economics 101

  • @AbdulrazaaqLeyani-k2i
    @AbdulrazaaqLeyani-k2i Před 2 dny +5

    True and lovely words

  • @paulmanyamba5437
    @paulmanyamba5437 Před dnem +1

    Akulu mulungu adzikusogolelani mukuyankhula chilungamo ngati munthu wamulungu

  • @paulbanda9638
    @paulbanda9638 Před dnem

    Patakhala kuvota mau anu ndavotera kale,u r a good preacher

  • @patrickndojime1632
    @patrickndojime1632 Před dnem

    That's true i do respect your massage father keep it up i like the ward's you taling as

  • @user-cq2gd5hc4v
    @user-cq2gd5hc4v Před dnem

    Zikumveka bwino ndithu kuchokera pa mawu amenewa boma la abusa a Chakwera lalepheradi. Zikufunika kusankha moyenera.

  • @AndrewMukhwapa-qj4vo

    Thanks very much God bless you. Your talking the truth

  • @AndrewMukhwapa-qj4vo

    Your talking the truth God bless you thanks very muh

  • @RabeccaMkandawire-i9j
    @RabeccaMkandawire-i9j Před dnem +3

    A Malawi kususuka zithu zoti sizitithandiza kukopeke nditu k500

  • @kingsleymsampha2260
    @kingsleymsampha2260 Před dnem +1

    Chilungamo chilibe zoti wochimwa ali momwemo ayi. Truth will remain and the wise will choose the right way to go. The foolish will blame the advice.

  • @user-lu8px7td6p
    @user-lu8px7td6p Před dnem +1

    God bless you pastor don't fear for that you know is no clear but to talk people to know

  • @user-mj2te7vl6p
    @user-mj2te7vl6p Před dnem

    Thank you man of God

  • @TopoTopo-bm4vw
    @TopoTopo-bm4vw Před dnem

    Good advice thanks

  • @giftnyirongo-ey3qy
    @giftnyirongo-ey3qy Před dnem +1

    What an intelligent gentleman

  • @hamiltonsolomon3756

    Well said......👏👏👏👏👏👏👏👏

  • @JeanKambala-gm1zr
    @JeanKambala-gm1zr Před dnem +1

    Kodi abishop mawuwo basi antha siinu mikuyankhula ndimulungu wakutumani. Tikudikila titsegulenni maso ndi chilungamo

  • @WilliamBandaWili
    @WilliamBandaWili Před dnem +1

    Boma anachita kulilira ili that's y vamunyera chakwera pls anthu apa central region musamuvoterenso uyuyu atipha

  • @user-co2cz2ht8j
    @user-co2cz2ht8j Před dnem

    This pastor should not get arrested 🔥🔥🔥💯

  • @user-vu4cz1mt4f
    @user-vu4cz1mt4f Před dnem

    Zochezatu mukauze
    Tatopa ndimbuz izi
    Mpaka anthu aMulungu kuyamba kuwayankhulisa zandale chifkwa chakuononga ndalama mopusa

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete Před dnem

    Good speech ❤❤❤❤

  • @WilliamBandaWili
    @WilliamBandaWili Před dnem

    Akanakhala wins chakwera akanangoimika manja chifukwa zinthu sizilibwino muno mu Malawi walephera yekha anthu chance anamupatsa

  • @clalesschisale3792
    @clalesschisale3792 Před dnem

    Our next Bishop of blantyre archdiocese

  • @KennethMchenga-j9c
    @KennethMchenga-j9c Před dnem

    Very true man of God

  • @user-dp7bc7yy6s
    @user-dp7bc7yy6s Před dnem

    Bg amenewo ndiye mau amphav zinthuzi zimafunika kuganiza mozama tisanasankhe otilamulira

  • @beakab2378
    @beakab2378 Před dnem

    Well said

  • @user-dy3iz1il1d
    @user-dy3iz1il1d Před dnem +1

    Oro muthalika a lowe mudzavutika chimodzimodzi musaone kuti akalowa Mutalika ndiye zinthu zisintha ayi mukuzinamiza kwambiri tiyeni tiziwelenga mau aMulungu atiuza zoona awatu ndi masiku otsiliza Buku lopatulika linanana kale kuti masikuotsiliza mudzaona nkhondo kukangana mu maiko osiyanasiya and munthu afzakonda ndalama not munthu nzake ndipo zinthu zambiri zidzakhala zokwera mtengo kwambiri ine ndakambako zokomo abale mwabuye

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 Před dnem

    That's true pastor we need to use the brain life now is expensive

  • @gabrielmulowe8481
    @gabrielmulowe8481 Před dnem

    Anthu Ngati awa ndi amene timawacuna

  • @HedgensChisale
    @HedgensChisale Před dnem

    Ine ndinauza koma sakuva

  • @user-lw9su5om5z
    @user-lw9su5om5z Před 2 dny +2

    It's true that they failed

  • @KENETHMAJASA-ud5ee
    @KENETHMAJASA-ud5ee Před dnem

    Strong man of God

  • @kingsleymsampha2260

    Samuel told Saul kuti umfumu wanu wakanidwa. Ndiye abusa azingoti zakumwamba?? Kulowa kumwamba ndi umphawi aaaaah

  • @BressingsMahele
    @BressingsMahele Před dnem

    Powerful

  • @JosephAMoses-ne8ji
    @JosephAMoses-ne8ji Před 2 dny

    It is very true that they have failed

  • @JamesMalango
    @JamesMalango Před 2 dny

    Ndiponso achepesanso mauwo

  • @user-gd7xm7xr9v
    @user-gd7xm7xr9v Před dnem +1

    Church silimakhala ndi anthu a opposition okha, mliso a m boma, ukulalika mosasamala utha kuyambanitsa anthu m MPINGO. Maka nthawi ya campaign tilimoyi.

    • @user-pn7cj9hb3t
      @user-pn7cj9hb3t Před dnem

      Kodi umafuna anene kuti zithu zilibwino zisali bwino? Taganizani kae bwinobwino amwene osathamanga poyakhula taonani kwa nthawi yoyamba anthu a Mulungu kuyankhulapo m'mene dziko likuyendera ndipo ndi ambiri zedi moti mukwanitsa kuwaletsa onsewo? Tadekhani inuyo ngati simukuona manvutowa khala phee muzingodyelera apa sakunena za campaign ayi koma kutsegula maso anthu amene akunvutika, ndipo idakakhala campaign in church bwezi pakunveka ena kumutsutsa pompo koma ngati akumuombera m'manja choncho ndekuti anthuwo akunvomerezana nazo zomwe munthu wa nzeruyu akuyankhula ku mpingo wa Mulungu. Dziwani kuti mudziko Mulungu adalenga anthu anzeru kuposa azitsogoleri anthuwa koma kuzichepetsa kokha kumapambanitsa so you better watch your mouth.

  • @Patricia_Chisankha
    @Patricia_Chisankha Před dnem

    Unenesko uli papa

  • @user-sr6hc3pv8o
    @user-sr6hc3pv8o Před dnem

    🙏🙏🙏🙏

  • @user-sb6by9sq5n
    @user-sb6by9sq5n Před dnem

    🙏🙏🙏🙏🙏

  • @user-gd7xm7xr9v
    @user-gd7xm7xr9v Před dnem

    Osati zocheza

  • @EdsonKamwendo
    @EdsonKamwendo Před dnem

    Mbambande Father

  • @MarcosDjussa
    @MarcosDjussa Před dnem

    Mumakwanila fr 😂😂

  • @martinmoyo4211
    @martinmoyo4211 Před dnem

    Kudzudzula kulipamenepo koma inunso atsogoleri athu achikatolika mulindivuto. Timakonda kuloza chala anzathu koma ndichani timapangapo polithandiza bomalo.
    Tikati tiyang'anitsitse kumpingo kwathu inuyo atsogoleri a ntchito anunso simumawasala molongosoka mumalipiro. Mwachitsanzo a Gulupa samapatsidwa malipiro abwino komanso a ntchito ena. Ifenso tikonze gawo lanthu mpamene tidzizuzula enawa. You should also set good example in leadership. Zisakomere mbuzi kugunda galu.

  • @IsaacMusa-py2jm
    @IsaacMusa-py2jm Před dnem

    Zamphanvu 🙏

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz Před dnem

    Kukhala ngati kachilungamo

  • @MphatsoMvula-k6e
    @MphatsoMvula-k6e Před dnem

    Udatani umuwuza peter wakoyo mbuli ya mbusa iwelenge yohane 10 mbusa wakuba iwe

  • @LilianKachala-yz2xf

    Takumvani Abusa

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy Před dnem

    Zochezatu😂😂😂😂😂 chilungamo

  • @user-fd1tu6ku1r
    @user-fd1tu6ku1r Před dnem

    Chakwera ndi Tambala Wakuda anabwera kuzaononga Dziko lino

  • @RonicSouza-sk5ux
    @RonicSouza-sk5ux Před dnem

    Mau

  • @user-gd7xm7xr9v
    @user-gd7xm7xr9v Před dnem

    Sizocheza

  • @user-cy4pg1bo5o
    @user-cy4pg1bo5o Před dnem

    Ku bandura osaopa osafooka kkkk

  • @Doreen-vw9ws
    @Doreen-vw9ws Před dnem

    Palibe chomwe amaziwa chipani chosaziwa economy chipani chomvesa chisoni

  • @user-ti8ds7iq8z
    @user-ti8ds7iq8z Před dnem

    Akumanganitu

  • @user-dy3iz1il1d
    @user-dy3iz1il1d Před dnem

    Uyu ndi wabodza anthu malo poti awauze anthuwa mau achipulumutso akupanga kampeni yandani inu mungafanizile dziko lamalawi la Mozambique or zambiya zambia ndi dzikolimene limagulitsa miyala ya mtengo wapatali komanso muli Ma boulder ambili amatolera ndalama zochuluka komanso kumalawi timabalana kwambiri sizigwiliza ndikuchepa kwadzikolo Mozambique kuli ma madoko awili amene ama bweletsa ndalama plus mogodi anthu amulungu ngati awa ndi amene amapangitsa kuti dziko lisamayende bwino chifukwa amaiwala mau aMulungu amayamba kulalikira ndale mudziko simungakhale m'dalitso ayi toyeni tizipemphera kuti mulungu afalitse Malawi zikomo

    • @user-un6qv6sj3h
      @user-un6qv6sj3h Před dnem

      Akunenatu chipulumutso kupulumutsa miyoyo ya anthu apulumuke kunjala kuumphawi kukukwera mitengo ya zinthu Kodi mau oti kupulumukawa amakamba zakumwamba kokha pepani ngati ndakulakwirani koma sitingamakambe zaulemelero ukudzawo pamene apapa anthu tikuvutika

  • @user-bd5kw8oq1r
    @user-bd5kw8oq1r Před dnem

    Popeza mwati ndi munthu wa Mulungu bola tamva koma sanafike kukhala mwana wa Mulungu popeza nayeso ndi wochimwa koma ndi wa bodza uyu Ngati kumpingo kwawo walephera ndiye alonze chala wina angoyesetsa nayeso kutukula dzikolino ndizofunika kugwilana manja koma mukalowetsa ndale ndi mu mpingo momwe ndiye Kuti tigwa tonse ndi nkhosa zomwe or iye sungayendetse dziko ife a DPP zinatikanika kale 😅😅😅

  • @user-pl2lj6mh1z
    @user-pl2lj6mh1z Před dnem

    Ameen Ameen tikuvutika abale mulungu atikhululukile achakwela chonde mwachose ndithu

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj Před dnem +1

    Alomwe awa tazilarikilani za ufumu wa Mulungu

  • @victormasambuka8366

    Mu church mumakhala anthu azipani zasiyasyana sibwino kukamba za ndale mufzagawanittsa church as a pastor keep your opinion to yourself

  • @johnkambala692
    @johnkambala692 Před dnem

    These are part of Malawi disaster

  • @MosesLeckson
    @MosesLeckson Před dnem

    Zoona zake

  • @user-dy3iz1il1d
    @user-dy3iz1il1d Před dnem

    Uyu ndiwabodza zambia nayo ili pamavuto azachuma munthu wa mulunguyu ndiwabodza kwambiri

  • @YOMALO.
    @YOMALO. Před 2 dny +1

    This is a proof that MCP will reign again

  • @user-kt5bq2wg6v
    @user-kt5bq2wg6v Před dnem

    Simudayankhule bwino bispo. Munthu wamulungu sanayenera kutero

  • @ChisomoNthukwa
    @ChisomoNthukwa Před dnem

    Opusa ameneyi zikugwilizana bwanji ndiulaliki

  • @user-gd7xm7xr9v
    @user-gd7xm7xr9v Před dnem +1

    Iweso ukulalika zopusa, economics yakuti unaphunzira iwe, you do not compare zinthu zosiyana,, Mozambique ukuchita compare ndi Malawi, kapena Tanzania .... Just chinthu chimodzi like DOOKO,LA PA NYANJA ..... what it earns cannot compare ndi Malawi.Ukawauzenso nawe omwe akutumawo.

    • @marryphili5419
      @marryphili5419 Před dnem

      Ngati ndiwe wa MCP wuzipase wulemu amalawi tilipa moto sitimasekesekerere ndi mbamva zimenezi

    • @user-pr4xk7wk6r
      @user-pr4xk7wk6r Před dnem

      Ndiwe opusa kwambiri ndi MCP yakoyo

    • @simeonbanda4240
      @simeonbanda4240 Před dnem

      Umva pheni wa MCP ulendo uno

    • @johnchrispine3949
      @johnchrispine3949 Před dnem

      Point ndiyonena kuti, zinthu zochepa zomwe tili nazo tizigwirisa ntchito bwino.

  • @HarryKandani
    @HarryKandani Před dnem

    Anthu oipa inu ndi inu nomwe munali pastogolo kulemba ma kalata kuuza anthu kuti avotele agule wa

  • @paulmanyamba5437
    @paulmanyamba5437 Před dnem +1

    Akulu mulungu adzikusogolelani mukuyankhula chilungamo ngati munthu wamulungu