Malawi yagwira munthu olakwika ndi kumutumiza ku Rwanda; Vincent is not Theoneste

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 13. 06. 2023

Komentáře • 283

  • @markoviskyhernandez9706
    @markoviskyhernandez9706 Před rokem +5

    Some few people are saying kuti maburundi azipita kwawo chifukwa ku Rwanda ndi ku Burundi kulibe nkhondo. Mukudziwa kuti ku South Afrika kuli amalawi 6 miliyoni? Ndee kuno ku Malawi kuli nkhondo? Ku Zimbabwe, malawians are 5 millions. Kuno kuli nkhondo? Ku Botswana, kuli 1.5 millions of malawians who are working mostly in construction sector. Is there war in Malawi? Europe ndi USA, Canada, ....muli amalawi ambili, sakubwelera chifukwa cha nkhondo ili kuno!??? Mukudana ndi anthu omwe ali mu midzi ndi ma towns who are less than 10 thausands whereas Malawi has 6 millions citizens in South Africa?? Xenophobia is not good and kumbukilani kuti onse awa ndi ma black ngati ife. We are brothers. And you don't flee your country because of war only. Human Right violations and poverty make also people to flee their countries. Do you think munthu amathawa kwawo pa kufuna kwake without reasons? Jealousy!!

  • @greychizaka4088
    @greychizaka4088 Před rokem +3

    King you can be a good adviser even to a president. I respect you humble beast. Imagine your underground but doing a great job

  • @LUCKYM4787
    @LUCKYM4787 Před rokem +3

    Thanks very much bg mn respect ndawi zonse matisegura matso ndi ubongo nditu ndikutipatsa mphavu dziko lathu lamalawi srs

    • @BandaWotch-po2el
      @BandaWotch-po2el Před rokem +1

      Kagame was rebell in Uganda. My fellow Zambians am a historian ,

  • @mbaliehaward947
    @mbaliehaward947 Před rokem +1

    Munya manyi mulungu akukantheni pa zomwe mukuchita nonse even chakwelayo mulungu akutumizileni matenda ma banja mwanu mu dzina la yesu

  • @daviemafunga
    @daviemafunga Před rokem +10

    😢😢malawi ndalama anaimva kukoma heavy

  • @rashidstamburi2705
    @rashidstamburi2705 Před rokem +6

    Komatu a'malawi ngati ndidyela tiphetsa anthu osalakwa please 😭😭

  • @kabehorwanda8725
    @kabehorwanda8725 Před rokem +2

    Good job brother continue we really appreciate your information 👍 👏

  • @kubengovender6996
    @kubengovender6996 Před rokem +2

    Big man!! Mumayitha ndinu number one mumakwana!!

  • @webstermbewe8395
    @webstermbewe8395 Před rokem +6

    Thanks bosses for the extensive variety of information daily themed
    Provide other needed data

  • @luckyprosper3812
    @luckyprosper3812 Před rokem +1

    Thanks your Excellency Dr Bakili muluzi

  • @mariezorgen7735
    @mariezorgen7735 Před rokem

    Money killed Jesus,,,,aah malawi,,,,thanks brother ,,continue bible Suzanne was saved ,,lies lies Killes, and then ,,,! ,!?may God protect you wise speaker.. continue the wisdom to open malawi ,,,,if Only he could resign!, is respectful than to destroy poor innocent creatures and create disorders of no peace ,,Lord keep malawi land of peace, malawi pray pray,,God loves you,,

  • @abdulkatopola3612
    @abdulkatopola3612 Před rokem +2

    M'busa wanji wotengeka ndi zinthu za kumidima zokha zokha mkumanamiza anthu kut anali m'busa ...mbuzi za anthu

  • @soxdososola2937
    @soxdososola2937 Před rokem +2

    Only 4 years MALAWI yavunda kale nde kuli-bwanji akaWinaso CHAKWERA yiiih?

  • @charlesnkhomah6751
    @charlesnkhomah6751 Před rokem +1

    our government is full of rubbish,,,,bigman you are doing very good job bakili muluzi tv salute

  • @markoviskyhernandez9706
    @markoviskyhernandez9706 Před rokem +2

    Thank you very much you the owner of this channel. You are widely opening my eyes. I was ignorant about the issues of Rwanda, Burundi and great lakes region in general.
    I had information that the current president of Rwanda is a good president, but on another hand, I had information that he is a monster, savage.
    Simply, the ones who make the publicities and whitewashing his image are westerners who put him on power and he is working for them by stealing in the Democratic Republic of Congo. But for an awake african, this is a bad leader, a traitor of Africa. The western media presents him as savior of Africa, but you know that if an African leader is loved by the ones who always steal from Africa, it means that this leader is working for them!! He is selling Africa to them. He is a traitor for africans!!

  • @thomasmwitiya1447
    @thomasmwitiya1447 Před rokem +3

    You're the best bro,,,keep it up

  • @amabhohlela.3492
    @amabhohlela.3492 Před rokem +2

    Mmmmmm....koma akuenela Ndalamayo ibwezedwe...komanso aNdunawo akuenela apite ku Rwanda akamutuluse Munthu osalakwa please!!!please!!!Very sad 😭😭😭😭😭

  • @professorsafuta3936
    @professorsafuta3936 Před rokem +1

    Thanks for updating us

  • @BenissoneErnesto-kn9bd
    @BenissoneErnesto-kn9bd Před rokem +1

    Watching from Mozambique kuvesera mwachidwi

  • @katalamajames4947
    @katalamajames4947 Před rokem +1

    Asogoleli alelo ndi mbuzi zaanthu kukonda ndalama munya muona

  • @princekabvina1718
    @princekabvina1718 Před rokem +1

    He is a puppet of NATO and Son of devil I like that one...keep the fire burning Boss much respect and salute

  • @luckyprosper3812
    @luckyprosper3812 Před rokem +2

    A bakiri chonde mudzawauzekonso anthu za ma prison a ku rwanda.sadziwa kalikonse anthuwa.

  • @sayidimisessa
    @sayidimisessa Před rokem +3

    Where we're going malawi??
    Amalawi tiri kumalawi amoto 😢😢😢😢😢

  • @phillimonzgambo1663
    @phillimonzgambo1663 Před rokem +1

    We need that man to come back to Malawi because have no problem to Rwanda that is business Man to Malawi gagame you can send back that man

  • @vickylupiya6909
    @vickylupiya6909 Před rokem +1

    I like your page very much broh....
    Do a favor by explaining the story of museveni and America on anti gay law😌

  • @EmmanuelThom2-xf6ij
    @EmmanuelThom2-xf6ij Před rokem +1

    Thanx for updates

  • @ahmedmsume1489
    @ahmedmsume1489 Před rokem +2

    Koma iweyo ase ur the best

  • @abisalomchunga6695
    @abisalomchunga6695 Před rokem +2

    Keep it up big man

  • @yamikanikhanga4527
    @yamikanikhanga4527 Před rokem +2

    Vuto lovotela nyawu

  • @iwellyobujudithphiri7819

    MALAWI LOVE OF MORNEY.CORRAPTION

  • @abe9104
    @abe9104 Před rokem +1

    i like you my brother man. am liseng you from Zambia

  • @alexgweje8610
    @alexgweje8610 Před rokem +2

    Eish Mulungu atithandize
    Chakwera Ndi unduna wake wonse Mulungu awakanthe sure
    Ndipo zikhale ng'oma usamale ndalama imeneyo ndi makape anzakowo ndithu God will punish you
    Paul Kagame ndi mfiti wachabe chabe

  • @AnordThomson-iw5ny
    @AnordThomson-iw5ny Před rokem +1

    A malawi nose amene munavotera chakwera pankholo panu, ngati kuponda bwelani tipondane pompano pantumbopo agalu chifukwa zosezi ndinuyo amene munavotera chakwera

  • @calistabenson4880
    @calistabenson4880 Před rokem

    Koma pls Malawi wanga ndalama izi tikunzisa nawo anthu osalakwa mmhh Ambuye atichotsere mtima wamwala omwe wangobwera from no where mwa ife bro Ambuye Ali mbali akhala mboni yako osadanda ay pitiliza kulilira kwa Mulungu wako amamva ndpo akumenyera nkhondo Amen

  • @zeckbmalawi8017
    @zeckbmalawi8017 Před rokem

    Thanks boss inu mumanenena chilungamo osaopa munthu

  • @cassimyusuf6683
    @cassimyusuf6683 Před rokem +1

    Dziko lathu lalowa chibwana kwambiri, how dare iwowo kumalola kulamulidwa ndi Paul kagame 😢

  • @AliforceBiziman
    @AliforceBiziman Před rokem +2

    Zonadi

  • @fansciodancun6036
    @fansciodancun6036 Před rokem

    Best channel ever

  • @BizweckMbwindinga
    @BizweckMbwindinga Před rokem +3

    ❤❤❤ you my man mumatipasa ma update ya boh

  • @lastonekaponya7675
    @lastonekaponya7675 Před rokem +1

    Chonde MULUNGU mulangeni zikhala Ng OMA NDA chakwera taonani munthu uja mumati ndi busayu wayamba kuphetsa anthu kodi munthu wamulungu angapange zoipa chonchi

  • @user-xc1xt2qd7t
    @user-xc1xt2qd7t Před rokem +1

    Keep up bro

  • @elijahrambiki1149
    @elijahrambiki1149 Před rokem +1

    Anthu akuyenela kuchitapo kanthu, ndipo nduna imeneyi ikuyenela kutula pansi udindo

  • @AbuOsman-ts6ef
    @AbuOsman-ts6ef Před rokem +1

    Ambuye alowelelepo ndalama ziwapweteka anthu awa walakwa chiyani

  • @gracelimani1526
    @gracelimani1526 Před rokem +1

    Ambuye awakhululukire achakwera akufuna kuononga miyoyo ya anthu chifukwa cha ndalama

  • @shadreckpatrickmkisi8819

    Tell us more about the health life of yoweli kaguta museveni

  • @thomassimbaya197
    @thomassimbaya197 Před rokem +1

    Indeed you are a great man may God bless your days I hope you search the story of Adamson mushala in Zambia and The story of the mailing brothers in Zambia watching from Zambia muchinga province

    • @BandaWotch-po2el
      @BandaWotch-po2el Před rokem

      You don't know kagame, kagame is a silent killer it's only Mr Joe Biden and British Army can deal with him,

    • @BandaWotch-po2el
      @BandaWotch-po2el Před rokem

      I told you my fellow malawans ,. that USA and British Army can destroy entire world world if they want, so who's kagame? panyopake asabwere KU Malawi na KU Zambia cause we have beautiful girl s in Zambia and Malawi they can't manage to run, MR H h and Chakwera Mwaona? Careful plz,Stick to USA and British

  • @JamesJere-qu7lb
    @JamesJere-qu7lb Před rokem

    Nimavera che ma comment anowo ATI uli boo brother Komatsu anthu Akufa but muli nuu pa radio malawi chonde chonde chitaniponi kanthu from zambia 🇿🇲

  • @ziwani3682
    @ziwani3682 Před rokem +1

    BIG 👍

  • @merviselias6230
    @merviselias6230 Před rokem +3

    Chakwera Why 😭😭😭😭😭😭

  • @musambk
    @musambk Před rokem

    Ndakupendasana

  • @allanimindozo9937
    @allanimindozo9937 Před rokem

    May almighty God protecte the man who never deposite gvment

  • @austinharawa720
    @austinharawa720 Před rokem +1

    Tinakuzan MCP iribe umunthu lero ndi izi...

  • @user-ul4pm3bq4c
    @user-ul4pm3bq4c Před rokem

    Yonse big man umatha

  • @alihibrahim
    @alihibrahim Před rokem

    I follow you bro very well

  • @samuwilliam7478
    @samuwilliam7478 Před rokem +1

    Komatu kamudzu Banda anasiyina kuti munthu yemwe walowa kumalawi sayenera kungwidwa ndikutumizidwa kwawo Malawi ndichani

  • @ishakatimbe7341
    @ishakatimbe7341 Před rokem

    Timakunyadirani Big man

  • @user-ix4yp5lp8m
    @user-ix4yp5lp8m Před rokem +1

    Koma m tima wanga wandigunda movetsa chisoni kwambili. Huuuuuuuu kulakwatu KUMENEKO.

  • @patricksinyala1345
    @patricksinyala1345 Před rokem +1

    Komanso Mr chakwela akumaganiza bwanji kwenikweni?

  • @yasinkamwendo-jf7sc
    @yasinkamwendo-jf7sc Před rokem +2

    My broda😂😂😂😂boma ili ndilibe nalo mawu

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 Před rokem

    Awasumile basi no two ways about it 😢😢akonda ndalama ngati hule

  • @chrisboyce229
    @chrisboyce229 Před rokem +1

    Malawi ndi Dziko lomvetsa cisoni ndithu😢

  • @quraishmusakatunga1754

    My big bro

  • @user-bg5sl3xk6n
    @user-bg5sl3xk6n Před rokem +6

    May almighty God continue protecting u brother

  • @susanmbite4425
    @susanmbite4425 Před rokem

    Chagwera ngt uli mdiumunthu siyani zimenezo kagame simunthu wapa enthu ambiri ndiponso amene amagwira chito yake,chake ndikupa nikuononga iweyo ndani thi ndalama timene agupatsani uziwona anzanu sanali wopusa ngt ukuo a ndunama kafuseni peter wa muthalika

  • @devlinebhema2729
    @devlinebhema2729 Před rokem +1

    mmbusa kumapanga izi zoona ayi mulungu amukanthe

  • @user-mn1vh7rh7n
    @user-mn1vh7rh7n Před rokem

    Eysh mchifukwa anamodwee akubwela ku Malawi chifukwa atsogokeleli akee ndi a dyela😂

  • @wilsonsawasawa3794
    @wilsonsawasawa3794 Před rokem +2

    Wonderful narration

  • @dellingsmunthali2669
    @dellingsmunthali2669 Před rokem

    Kodi amatipasa uthengau ndi ndani?amakwanira ndipo ndinaseguka mutu just because of this brother"

  • @molicieeosama8877
    @molicieeosama8877 Před rokem +1

    Boma likupanga zithu m'chimbulimbuli.

  • @MaxwellMustafa-ec8fc
    @MaxwellMustafa-ec8fc Před rokem

    Is corrupt God bless you my brother

  • @khalifacalvinajass9998
    @khalifacalvinajass9998 Před rokem +1

    Osamvotelas agalu amenewe

  • @wysonchinyangalala3505
    @wysonchinyangalala3505 Před rokem +1

    Kom Malawi 🇲🇼 mmmm kulibe chabwino

  • @user-zk5nu5fh6l
    @user-zk5nu5fh6l Před rokem

    Anduna atichitasa manyazi ndi dyela😂😂

  • @isaacmussa2942
    @isaacmussa2942 Před rokem

    Akatero akamupha Bambo ameneyo eee koma dziko lapasi laora

  • @androidgame7484
    @androidgame7484 Před rokem

    Osayiwala malawi imasunga zigawenga

  • @charliepoulaliecky1893

    Andunawa Mmene wakulira mutuwo koma opanda nzeru

  • @eunicemoyo6024
    @eunicemoyo6024 Před rokem +1

    Bolani agwe prezdent ameneyu mu 25 mu sitikufuna chabwerayu

    • @atupelephambala1233
      @atupelephambala1233 Před rokem

      Komano MCP mchani azawo a mu Tonse alliance kuwakhomelera dollar akudya okha plus za fertilizer

    • @susanmbite4425
      @susanmbite4425 Před rokem

      Chagwera ambuye akuyendere mwapadera wadxuza mizimu ya anthu ndipo ndalama zimene warandira kwa poul kagame sumuziwa zimene amapanga wapa anthu watsala ndiweyo

  • @user-ww1lu2ch6z
    @user-ww1lu2ch6z Před rokem

    One Africa

  • @GreenBadani
    @GreenBadani Před měsícem

    👍

  • @milajimussa4120
    @milajimussa4120 Před rokem +1

    Malawi dziko losava olopangitsa manyazi

  • @mordecaikachale2497
    @mordecaikachale2497 Před rokem

    Malawi government must support this man ...mumatha kwambiri man ndipo mumamveka chilungamo kwambiri

  • @rickiez
    @rickiez Před rokem

    A Malawi tisayawile nkulu uyu pamene anali chief of stuff wa malemu Bingu wa mutharika kuti nduna zimavutika kuti zikomane ndi President masiku apitawo.
    Hello Mr. Chakwera beware the Ades of march!

  • @Rafiki-pk7hw
    @Rafiki-pk7hw Před rokem

    Problem is that chakwera ndi Muthu agona kwambili.

  • @duwalikangaharryadams6832

    Please guy's Malawi stop this nonsense money is nothing than life and freedom

  • @mustaffahhemmad
    @mustaffahhemmad Před rokem +1

    Boma la a chakwera ndiye bola ma boma inatu

  • @InnocentNawasha-kc6ij

    Commander woyamba wapita asala foty chakuti

  • @user-mb6ts8vi8j
    @user-mb6ts8vi8j Před rokem +1

    Zomwe mwarankura zonse ndi Zona zokazoka

  • @user-ix4yp5lp8m
    @user-ix4yp5lp8m Před rokem

    Eshiiiiiiiii

  • @captainhigo8362
    @captainhigo8362 Před rokem

    Facts

  • @Agnessmwale-ng4by
    @Agnessmwale-ng4by Před rokem +1

    Zosakara bwino

  • @lewisbonongwe8518
    @lewisbonongwe8518 Před rokem

    Malawi eish

  • @anafieintuka8090
    @anafieintuka8090 Před rokem +1

    Nthawi zonse ndinu olandilidwa kucheza nanu

  • @user-yy4jt6ky9x
    @user-yy4jt6ky9x Před rokem

    ❤❤❤❤

  • @chrissygama8678
    @chrissygama8678 Před rokem

    Iweyo palbenso ku malawi kuno iwe nd mfumu ya history ku Africa 🌍even ku Europe 🇪🇺

  • @titomethiwa4213
    @titomethiwa4213 Před rokem +1

    Muthu woipa kwambiri

  • @jamesbeaufort8980
    @jamesbeaufort8980 Před rokem +2

    This is insern government

  • @hendresonsande5156
    @hendresonsande5156 Před rokem

    Koma ngati ali wa ku Ruwanda achita bwino kuntumiza kwawo

  • @ephertkutapira
    @ephertkutapira Před rokem

    Paul Kagame anabwera kuno ku Malawi nthawi Bingu Wa Muthalika mpaka nseu wa Chilambula anautchula dzina lake,sanayambe lero kugwirizana ndi boma la Malawi,ngati Zikhale walandila ndalama kamusumire

  • @lastonekaponya7675
    @lastonekaponya7675 Před rokem

    Ine ndipanga fasting kuti anthu amenewa angokhala masiku ochepa MULUNGU awachotsere masiku okhalira padzikopano

  • @jahiemmusa8796
    @jahiemmusa8796 Před rokem +1

    ndimbudzi sawanthu mulungu asilange