KU MCP KUSAMBWAZANA ZAMASEWERA AYI 🔥🔥🔥🔥

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 8. 09. 2024

Komentáře • 46

  • @Yusufu-Daudi
    @Yusufu-Daudi Před měsícem +7

    Koma anthu wa apwetekanatu uku😂😂

  • @GiftMakowa-k9f
    @GiftMakowa-k9f Před měsícem +1

    Anyani awa kapena Kuti bwaa

  • @user-eh1mg3ww6d
    @user-eh1mg3ww6d Před měsícem +6

    Ndipo apwetekane ndipo aphane okha okha athu oipa awa asatana

  • @juliochiwalo
    @juliochiwalo Před měsícem +1

    Mk14 billion ku mwaza mwazitenga kuti kuba basi ndi chifukwa chake anthu mmalawi muno sakukufunani mukhulupirira 2025

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h Před měsícem +1

    😂😂tikufuna aphane kumene anthu woyipa kwambili

  • @WilliamBandaWili
    @WilliamBandaWili Před měsícem +3

    Lazalo mumuchotsepo sakuyendetsa bwino dziko sankhani wina uyuyu akuonongera

  • @rexnyalugwe4910
    @rexnyalugwe4910 Před měsícem

    "Dzina langa lasowa mayoooo" San B

  • @RichmanIssah
    @RichmanIssah Před měsícem

    Amati UTM yagawanika APA MCP ndeyatani yankhani

  • @TasoMuyande
    @TasoMuyande Před měsícem +1

    Akuyankhuala mwamzerutu,,

  • @GiftMakowa-k9f
    @GiftMakowa-k9f Před měsícem

    Mbuzi izi zizigundana kumene

  • @BrunoChakukuma
    @BrunoChakukuma Před měsícem

    Kupusa eti mukukanga chifkwa chaife ndife ana anu

  • @EfeloYovita
    @EfeloYovita Před měsícem +2

    nde nose nfinu akatangsle or ndalama za misonkho ya amalawi m malo mogula mankhwala chakudya feterizer otchipa koma zaka 4 palibe chomwe mwapanga president ndi nduna zake zonse mbava zokha zokha , minister of finance kupezeka ndimatumba andalama ku airport kumusiya or kulengeza pawailes ayi achoke omenewa

  • @user-pl8kw3dc9d
    @user-pl8kw3dc9d Před měsícem +1

    Chikangawa inazorowera kumpha mapwara anu agaru

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole Před měsícem +3

    Chikangawa party km wangondisangallatsa mkuluyu kuyankhula modekha mwanzeru kuposa chakwera.

  • @user-jl6sq3ph1b
    @user-jl6sq3ph1b Před měsícem

    Muchoseni chakwera sakuyenelaso kusogolela ziko lino musakhe ena basi km chikangawa muchoseni akuonengelani mcp ofcz chikangawa ndi mbamva kmaso ndi okupha ndie muonengesa chipani chanucho cha mcp azikusogolela ubusa uja basi ziko walilephela iyeyo 😂😂😂😂

  • @lacksonsiyadi943
    @lacksonsiyadi943 Před měsícem

    Kuyankhul mwachilungamo zokhudza migwirizano eeeeee sizinaende bwinodi mayo ine ABIYENI aja

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy Před měsícem

    Bola pamenepo 😊

  • @MisheckAselo
    @MisheckAselo Před měsícem +1

    Koma ndiye simunati mukuona ngati magazi achina chilima ndi ena 8 aja, musowa mtendere muona 😢

    • @ChikupizgaKajawaMkandawire
      @ChikupizgaKajawaMkandawire Před měsícem

      Sizikugwilizana ndipo ndiwe waboza asee

    • @ChikupizgaKajawaMkandawire
      @ChikupizgaKajawaMkandawire Před měsícem

      Inu ma albino munadya aja mumasowa ntendele?

    • @MisheckAselo
      @MisheckAselo Před měsícem

      @@ChikupizgaKajawaMkandawire Tandiuza ndani alubino adafaela ku chikangawa, apa aise ndipa social media ndiye zoti uzindifunsa mafunso opoila wamva, panga zako

    • @MisheckAselo
      @MisheckAselo Před měsícem

      @@ChikupizgaKajawaMkandawire🤭🤭🤭🤭🤭

    • @MisheckAselo
      @MisheckAselo Před měsícem

      @@ChikupizgaKajawaMkandawire ngati kwanu mumadya anthu ndikwanuko, ine sindidya anthu wamva kunakukanika kungodusa comment yangai ndiwe upusa zedi

  • @owenkabango
    @owenkabango Před měsícem

    Bon kalindo

  • @FatimanickisJaffer
    @FatimanickisJaffer Před měsícem

    Agala chauya inu a mcp tinatop nanu ife mutuluk mu boma palibe tikuchiona chazelu ife iyaah shem on you 😒😒😒😒

  • @LongiMtimabii
    @LongiMtimabii Před měsícem +1

    Agalu anthu inu

  • @user-nc4vi1jt5g
    @user-nc4vi1jt5g Před měsícem

    Agaluinu mfiti anthu oipa demokarase mmaidziwa kumupha chilima ulendouno unali wachilima apamwasankha chakwera ndichipangano chimenecho mfiti inu amcp pitilizani

    • @ChikupizgaKajawaMkandawire
      @ChikupizgaKajawaMkandawire Před měsícem

      Ku dpp kuli democracy ?

    • @user-tj1ms3bg3x
      @user-tj1ms3bg3x Před měsícem

      Sitilukamba za DPP koma tilunena za inu Muli pampandonu .
      Mukutitsogoleranu.
      Mwatisaukitsa a Malawi fe.
      Zaka four kulamilira koma ataaa mavuto okha okha😂😂😂😂 Mayo Malawi uja kumvetsa chisoni.
      Zinthu kumangokwera chisawawa A Pule Ali chetee....
      Olo kulowererapo kuti munthu wakumudzi mwina nkuthandizika ayi tere kungoti duu
      Busy kumangopakula nkumawomola basi nde ndi ma cabinet onsetu kungoti cheete kumangomva kunong'a.
      Apa zasendera nde mwayambapo kuyimba nyimbo Malawi athandizikee mmm too late.
      Nkhanga zaona....

  • @ChristopherKabwazi
    @ChristopherKabwazi Před měsícem

    Ndizimenezotu

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 Před měsícem

    Ife tinanena kale kuti mcp ndi ufiti

  • @Musa1828-l5d
    @Musa1828-l5d Před měsícem

    Dzitsiru idzi dzabetsa boma anthu opusa kwambri kupha Chilima kuja anapanga mistek yaikulu kwambri nyini zamanu

    • @LongiMtimabii
      @LongiMtimabii Před měsícem

      😂😂😂😂 mwakwiilatu sir

    • @Musa1828-l5d
      @Musa1828-l5d Před měsícem

      @@LongiMtimabii dzitsiru amwene idzi and kupha chilima ndi mistek yaikulu heavy, ndipo ku Malawi sikuzakhalaso chipani chotchedwa Mcp ikutha basi

    • @ChikupizgaKajawaMkandawire
      @ChikupizgaKajawaMkandawire Před měsícem

      Kkkkkkkk chilima anaphedwa munjila yanji a mcp ankayendesa ndege ija

    • @isaacchiwaula731
      @isaacchiwaula731 Před měsícem

      ​@@Musa1828-l5dMCP siingathe aise, ndipo dziwa kut onsewa ndianthu oti anachokera ku MCP komweko

    • @user-dh8ho2qt4h
      @user-dh8ho2qt4h Před měsícem

      ​@@ChikupizgaKajawaMkandawiremzadya kholowa chaka chamawa Inu. Bwanji mitima yanu ndiyokwera? ngt sindinu akupha bwanji zimakuwawani. Iiiiii kma ana achikangawa , mwatumidwa ndi bambo Anu chikangawa? Kut mziziyanganira ma comment ya anthu?

  • @user-pl8kw3dc9d
    @user-pl8kw3dc9d Před měsícem

    Agaru inu mumpha mufe ndithu