This is what Malawians were waiting to hear from you. You made a right decision. Thumbs up to you all. We are fully supporting you, and we shall be behind you forever.
This is practical and very positive politics. Let's follow this path. I never new that in UTM there are some pipo who think like this. There is so much unnecessary noise which pipo think is politics but nope. God bless you.
Yes l gree with you Mai,koma ngati simungamve magnanimous a Maiyi ndiye kuti mulibe magnanimous ofuna kutumikila a Malawi koma kukhutisa mamba zanu osati kuombola aMalawi ku Bagamoyo,please paganism chtheka kugwilana manja kuombola Malawi ku mng"anjo ya moto,machine ngati achitila kuno ku south Africa kupanga boma la Malawi colution Government, osakonda anthu awo mwasiye choncho
Mwaganiza mokhwima maganizo abale athu a utm kupanga mgwilizano ndi DPP komanso tili ndichikhulupiliro kuti zipani mwanenazo mosogozedwa ndi Ambuye komanso anthu kulilira dziko lamalawi pamene lafikapa liphulidwe pa moto osatira azipanizo sionse angakondwere koma ambuye achite kufuna kwake pempho a DPP zichepeseninso pa anzanuwo kondanani samaliranani khululukirananipangani umodzi ochokera pansi pa mtima may God bless you
Mai mawu anu ndi amphamvu ambuye awadalitse
Zipani zonsenzi zili pansi pa DPP. so lingaliro labwino kubwerera Ku DPP
watching from Cape Town
Very true Madam, we need to have strong party for alliance
Very true mandam ,ndazikonda kwambili bwerelani kwa amai anu basi tingwetse MCP ,
You have proven to have big brains than other men in UTM, you have our support
Eishii koma apapa zikhala bwino bwanji ndipo zitero ndithu❤❤
This is what Malawians were waiting to hear from you. You made a right decision. Thumbs up to you all. We are fully supporting you, and we shall be behind you forever.
Mau amphamvu Mai atigwira mtima Bambo wanu APM akulandilani ndi manja awiri sangalore kuti ana Ake asowe kopita iye qlipo
Komatu amai awa alankhula zomanga Malawi wasopano God bless you mama
I totally agree with you
Powerful massage madam and am looking forward for the mgwirizano that is coming viva 🇲🇼 🇲🇼 🇲🇼 viva DPP,,,, watching 👀 from Lusaka
Mai mwayankhula za nzeru koopsya ndipo iiiiih sindikutha kukumvesesani kuti nzeru zinenezi bwanji inuyo
Mayi uyuyu amaganiza mwachungu ngati mwamuna 🎉❤❤❤❤❤❤❤
Mai inuyo very true watching from LESOTHO ndipo ndi Mulungu amene wakunong'onezani kuti muyankhule mau amenewo
Good decision sitikufuna njara ku Malawi
Mau ogwila mtima kwambili 💙💙💙🔥🔥🔥
Powerful message mama
Mau mau,udani wampaka muyaya mundale mulibe Tiyeni kwaADad bola Ng'onazi tizitulutse 🔥🔥
MCP ndidzaida mpaka muyaya.
Muli power speach inuyo mama🙏🙏💯💪
Zoonadi ma tigwirizane NDI DPP,ATM,AFORD+UDF ......moto buuuuu
Ikugwetsani MCP sizamwana😂😂😂😂😂😂😂 chakwera motoooo komaso chakwera kuwina DPP yonse tidzaponyanso Yamanja alomwe kwao sitikuyesa
Dpp, UTM,Alford, and UDF chonde phalani ziko pamoto tikudalira inu
@@ivychithyoka1551 chakwera akupha Goliath ndi mwala umodzi 2025 gwirani yesu Adani muwaponde bwino achakwera ndikuthandizani kuponda achepa
You is best futures ❤❤ 100% that's one plan A not B ❤❤❤❤❤❤❤🎉
Thanks madam for the advice
Patricia kaliat ndi makina paokha welcome back mom ur loved
Powerful mama mwaganiza kuposa mwamuna ndakukondani🎉
UTM ndi DPP palibe udani if anything UTM yabadwa kuchokera ku DPP. Peter is cool ndiyemwe anamukonda SKC kuti ayambe ndale.
Chabwino ndakumvani nde tinene kuti UTM itsogole ngatidi Pali kumvanadi
That's good Idea madam
Chakwera sakupuma bwino. Madam mumaganiza mokuya I agree and let's vote dpp utm afford udf, tigwilane manja.
Tiyeni tigwilizane ndi DPP, UDF plus Aford kungotero tagwesa
@@masterchitabwino898 ndipo chomwe chizachitike ndi zija amati 'Landslide victory', m'gwilizano omwe ungachepetsenso za kugawana mitundu. Nkhani yomwe akamba Mai wo. Atsogoleri omwe akukhuzidwa asakulirane mitima, agwilizane, azichepetse atiphule a Malawi mu nyengo yowawa ngati imeneyi..eesh!!!
Kwambili UTM mulungu akudalisen Ife tikufuna Malawi wa rendere osati Opana UTM thenks
Thenks utm popangangwilizano ndi dpp atiphera saulosi achoke fayaa
Mai kaliyati libikisani anthu ife sitifuna mcp
Good advice ,join together to remove the devil.plz.
Thanks Mai anthu mwayankhula bwino kwambiri thanks so much for ur spish
zoona koma tipange zimodzi chakwera achoke udani pambuyo pangani zomwezoo moto kuti bhuu!j
Wake uppp UTM family, that's right decision madamm, let's forget about the past!!!
Very Bravest speech Sister I salute you
Omwe akusunga udaniwo tawafunsani kuti kodi wina watichosera chiyembekezo chathuyu ndi awa omwe tinasiyana nawo mwamtenderewa kwabwino kulowera nkuti? Coz pakakhala kugawanikana kwazipani MCP sichokadi u are right
This is practical and very positive politics.
Let's follow this path. I never new that in UTM there are some pipo who think like this. There is so much unnecessary noise which pipo think is politics but nope.
God bless you.
Well spoken madam boss 🙏🙏🙏
That's true Comrade there is no permanent political enemy in politics
If we want tizivutikabe let's VOTE for MCP
Eya mama joinani basi pangani zomwezobasi tibwerere ku dpp basi
Amai munabadwa mwakuya more 🔥
100% mai, UTM, DPP ndi AFORD gwirizanani mugwetse MCP ndi chakwera atitopetsa, mai wa nzeru kobasi.
Chakwera ndiye mmmmmmm mavutotu awa........utm inakuthandizani koma wokudya bwino kukhala inu nokha zooona?
Ndipo akapanda kutuluka tiwatulutse ndiifeyo UTM,DPP, AFORD combine with UDF mcp will be defeated mai iminoyo ndi amzeru kwambiri
Powerful tiyeni amalawi tidzuke tigwiranane manja Mcp paulendo anthu akupha inenso I wish kuti Mcp imwalire viva UTM viva DPP Rest well our hello
You r the great mama
Live from south Africa cape town
Mukunva koma amalawi? Osakakamila ku mcp ife a dpp timakukondani a utm 🎉🎉❤
Good watching from Joburg
Ichoke mcp please dpp my vote
That is point UTM ikuyenera kupanga mgwirizano DPP
I think Bon Kalindo ayamkhuleponso pamkhaniyi kuti a Malawi tilimbe mtima
@@anthonysawa2039 adanena kale kuti chokani ku chikangawa party pitani komwe munachokera kwa atate anu ku thyolo.
Ife tili DUU (DPP, UDF, UTM) kumastand
Well done mama nkhani.imeneo ndiyabwino tiyeni ku dpp. Amene akufuna ku mcp sianthu.amenewa
Mai MULUNGU azikudalisani chifukwa chamawu anu amphamvu ndachilimbikiso, tiyeni tigwirane manja kuti tichotse ng'onazi m"dziko muno
Ndipo amai inu mumadziwa kuyakhula ndipo mukunena zoona ofunika kuchosa MCP osainyengerera
Very amazing let's unit ❤ watching from Cape Town
Powerful ❤
We're with you madam
Mayi muli ndinzeru zakuya, and l will prefer mau anu anveke ku UTM.
❤❤❤❤ that's beautiful idea Mai kariat
Tilowele ku DPP komweko basi,aDadi munthu womvetsa akatilandila,adadi sadziwa kupha munthu chifukwa chophangila maudindo ndi ndalama
Very true mai
UTM, Aford, UDF and DPP maganizo abwino
That's live mama, ndipo simukulakwisa ai.... Bwererani komwe mudachoka ndithu
Yes l gree with you Mai,koma ngati simungamve magnanimous a Maiyi ndiye kuti mulibe magnanimous ofuna kutumikila a Malawi koma kukhutisa mamba zanu osati kuombola aMalawi ku Bagamoyo,please paganism chtheka kugwilana manja kuombola Malawi ku mng"anjo ya moto,machine ngati achitila kuno ku south Africa kupanga boma la Malawi colution Government, osakonda anthu awo mwasiye choncho
Koma2 voice yo ikundimvekera ngati mai mai awa anali a Opposition omwe adali miyezi yathayi
Mwaganiza bwino Utm ndipo ambuye azikudalisan nonse
Vutonso DPP kuli wanthu ozikonda ndiye kaya tilowerekuti🙆🏻♂️
Ubale umenewu ine ndikugwirizana nawo .apo ine nkakuvoterani mmamawa
Good idea
God bless u mama
Zoonadi omwe a kulankhura ndi a DPP kuti UTM ipange mgwirizano ndi DPP, ndipo akuterowoso kuwa vomereza kuwauza kuti otsogola akhale wa UTM
Eyaka titero mukayima pa nokhat simuwina ,inenso ndikuti MCP isowepo apa bas
Mwalakhula zoona Amayi ofunika gwilidzano ndi DPP mavuto awonjeza mmm.
Mayi mwalankhula bwino chilima was a child of apm there is no problem to go back to DPP
Iyi ndye n point
That's good idea Ma, l salute you 💪💪 power to the people.
Vuto lake limakhala limeneli, timakhala desperate kufuna kuchotsa chipani cholamula ndiye mapeto ake timangopanga ma plan osayang'ana kumbuyo kapena kuti kutsogoloku ziziyenda bwanji.
Kuyakhula kwabwino mama ambuye azikundalisani kwambili
UTM , DPP, AFORD and AFFORD make one thing with concrete agreement we were tired please with MCP regimes
Bravo!!! UTM welcome to DPP
We have to join together gentlemen and ladies indeed
I salute you mama , good decision more 🔥🔥🔥🔥🔥
Kwambili izodi ndizoona 1 to 1 inu nokha ndi mcp kt mungamuchose mm ayi simungathe pitan ku dpp and UDF komaso afodi basi anawa azinyera ndiiithuuu
Mau amenewo amphamvu pangani mgwilizano ndi Dpp ganizo la bwino limeneli Mai muli.ndi nzeru
Zilibwino musabweleso mbuyo go forward mayi iweyo ndiwed wazelu kwambiri
Ndili mbali yanu🌹boma ilo
God bless you mama good decision ❤
Zowona amayi takumvani ndipo mfundo yogwira ntima❤
Mau mau mau pachingelezi timazati so shall it be in Jesus name
Komazoonad utm or dpp payokha singachose mcp pakufunikadi mgwilizano
Osanena Kuti ine zinandi pweteka iyai,munene Kuti m'mene adamu phera, Chilima Aliyense M'malawi zamuwawa, ndiponso nkhani imeneyi MCP tizawona Ku sogoloku Chakwera tizawona basi
Ndizowona mai ndipofunika kwambiri kupanga mgwilizano ndi chipani cha DPP basi
Amayi anga mwanyangula bwino bwanji mut mwanga ndikusangalala ndi mawu anga zikomo mulungu akudalitsen pakana zongolo
Siyani ma udani , mangani chimodzi ngati a Malawi,
MCP ichoke ndipo isazapezekenso ku Malawi.
Watching from JOHANNESBURG
Utm patsogolo ndi Mai chilima.....
Mayi wadzeru kuposa amuna iweeeeeeewh!!!!!!!! Mulungu akudalitse......
Mawu abwino mama mulandile ulemu wanu ❤
Mwaganiza mokhwima maganizo abale athu a utm kupanga mgwilizano ndi DPP komanso tili ndichikhulupiliro kuti zipani mwanenazo mosogozedwa ndi Ambuye komanso anthu kulilira dziko lamalawi pamene lafikapa liphulidwe pa moto osatira azipanizo sionse angakondwere koma ambuye achite kufuna kwake pempho a DPP zichepeseninso pa anzanuwo kondanani samaliranani khululukirananipangani umodzi ochokera pansi pa mtima may God bless you
Mama mwayangura bwion wi love you ❤❤dpp moto 🔥
Maganizo abwino mom.