Am a DPP fan with my family koma izi ndi zoona ndipo ndagwirizana nazo. Akuluwa atipweteketsa akungofuna u present koma MP ndi ma khansala njeee. Apa mco izawinanso na nkhalidqe wake ukakhala uwuwu
Ulemu wanu ahead Chilungamo chimawawa kwambili mot pamenepo Ena azimva mosiyana Km kwa ine ukundi yankhulilla bwino kwambili m'bale wanga Mulungu akutsogoreleni paulunsi wanu 🇲🇼😍🙏 But my vote Dr Laz 90%✔️ Ndi president yekhayo akupanga zatsogolo yamawa Dr Laz ❤🇲🇼👏
Peter ndi Atupele mufana a Kayenda muwadye ngati bwana chilima, komaso mene ukuvekera mu speech yakoyi ndiwe WA mcp, langizo akulu Samalani zandale muvuralanazo.
Ndipo munthuyu akunena zoona kwambiri. Chilungamo chimawawa, mutharika has to step down and help in rebuilding the party. He's too old to make decisions that can drive the party forward
Akunenazo ndi zowona koma mcp sitikufuna Inu a dpp ndi APM konzani chikhalidwe amalawi akukuyembekezelani kuti muwapulumutsa koma simufuna kudzipeleka kwa amalawi mumadzikonda
Apa palibepo amene mungafanizile ndi muluzi apa.muluzi ankatha kulankhula komanso aproach adalinayo .muluzi ankadziwa chochita panthawi yake.muluzi he was so close kwa a maudindo onse kuyambila ku area .mukukumbuka inu kalindo adanena kuti adad ngakhale district governor sakumudziwa wa dpp .vuto atsogoleli athu a dpp ambiri amangotha mwano wooo!
Dpp ndalama zawo amapatsa achina bonikalindo mtanyiwa Limpompo fm yawo fm lomwe fm anamiwa asalo bakili tv ndi azizawo akuti azitukwana chakwela ndi boma lake daily koma zipindula chani palibe
Atupele anachenjera simudzamudyeranso You keep your vote He will keep his money Who are you to ask if ndalama za abakili zinatha? Ali ndi ana akuwasungila
Takhala tikukuuzanitu kuti, atsogoleri anuwo ndi odzikonda. Amangoyang'ana zawo zokha komanso akuba. Dpp mu nthawi ya Bingu chinali chipani cha dziko koma lero ndi family party. Same as udf ndi Aford. Sindidzazisatiranso
Ine ndiwaku mangochi koma ine sindingakhale wa MCP mwene
The leaders are sleeping too much yooooooo😂😂😂😂
Athu akumangochi ndiolakwa atupele kapena Peta siwovutika ayi amalawi ndamene akuvutika mudziganidzile nokha mumavotandinu bwanji simumavotela dpp kapena udf mukudziwakuti mcp ndiyakupha ndinu agalu achina mangochi mumadzitenga ngati madolo muli oputsa agalu
Very true. Opositions ,your attitude must change
Sikuti a mcp mukodwe sikuti akutama inu ayi, nanuso musachulukitse zolakhura kwina mutinyansa
Munthu onena kachilungamo ngati ku dpp sangamukonde ai. Muzingobva apm my vote munthu akuteloyo ali ku theba 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Am a DPP fan with my family koma izi ndi zoona ndipo ndagwirizana nazo. Akuluwa atipweteketsa akungofuna u present koma MP ndi ma khansala njeee. Apa mco izawinanso na nkhalidqe wake ukakhala uwuwu
Akunena zoona mnyamatayu
Ineyo ndikuona ngati dzikoli likufunika ti pephele kwambili mwinaso vuto si apostion koma chilipo chipani cha magazichi akupepelela kuti athuwa angokhala ngati sakufanana kuthandiza koma kumalawi sikuli bwino kuli m,dima wakulu kwambili koma ambuye atimenyela khondo ndithu mulungu alipo
Mmmm ai Mulungu amathandiza wolimbikila
UTM ndi afford alliance basi
Exactly Peter wakalamba atupele kunyada
Ulemu wanu mayankhulidwe anuwo
Ndipo munthu uyuyu akunena zoona ndithu ndipo kumangochiko mcp ikhazikika
MCP singawine kumangochi kokubako munali limozi mwene 😅😅😅😅
Zooooona azitiuza zoona osati azititayisa nthawi
Nkhaniyo ndiyowona
Ulemu wanu ahead
Chilungamo chimawawa kwambili mot pamenepo Ena azimva mosiyana
Km kwa ine ukundi yankhulilla bwino kwambili m'bale wanga
Mulungu akutsogoreleni paulunsi wanu 🇲🇼😍🙏
But my vote Dr Laz 90%✔️
Ndi president yekhayo akupanga zatsogolo yamawa
Dr Laz ❤🇲🇼👏
Vuto ndinu anthu akumangochi osati Apm kapena Atupele, dyera bas. Koma chokuti muziwe olo mutaipasa ma voti chotani MCP ilibe kuyamika kunjaku kunali anzanu omapereka support ku MCP pano inawameza. Muphunzire kukhala anthu anzeru popanga ziganizo zofunika ngat zimenezi.
Kutitukwanitsa kwambiri aaaaa ulesi ndi kukuladi ndithu penanso mwano amangofuna anthu kuti awathandize basi kkkkkk
Atupele Muluzi is not a political figure. he is after position
Ndipotu za manyi zenizeni
Komad brother ukunenazo ndizoona akudzimva kwambiri akuyenera kudzuka
Anthu akumamgochi ndi osagwilizana guys
Peter ndi Atupele mufana a Kayenda muwadye ngati bwana chilima, komaso mene ukuvekera mu speech yakoyi ndiwe WA mcp, langizo akulu Samalani zandale muvuralanazo.
Mkamwa monukhamo mcp nde chan opusa iwe
Ndipo munthuyu akunena zoona kwambiri. Chilungamo chimawawa, mutharika has to step down and help in rebuilding the party. He's too old to make decisions that can drive the party forward
Zoozadi iziii
Atupele ndi member chabe wa UDF .koma apatero nkhani ndiyawo ndi APM
Zalakwikadi tavomeledwa
inu maganizo anu mukutipo bwanji nanga olakwisa ndan?? A mangochi mwina a tsogoleli osusa boma
Anthu akumangochi ndiokonda ndalam chabe anasiya udf kuthamangila dpp apa asiya dpp kuthamangila mcp
Azolowela ambelechile 😂
Ndipo anthu awa akutipwetekisa kwambiri iiii koma anthu awa
Kungowina mcp 2025 kumalawi kuzayenda mwazi
Peter ndi tupele amanyi awa serious mcp sitiifuna koma akanganya inu ayi ayi ndithu
Akunenazo ndi zowona koma mcp sitikufuna Inu a dpp ndi APM konzani chikhalidwe amalawi akukuyembekezelani kuti muwapulumutsa koma simufuna kudzipeleka kwa amalawi mumadzikonda
Apa palibepo amene mungafanizile ndi muluzi apa.muluzi ankatha kulankhula komanso aproach adalinayo .muluzi ankadziwa chochita panthawi yake.muluzi he was so close kwa a maudindo onse kuyambila ku area .mukukumbuka inu kalindo adanena kuti adad ngakhale district governor sakumudziwa wa dpp .vuto atsogoleli athu a dpp ambiri amangotha mwano wooo!
Chilipo chachikulu chomwe chikuchitika,sanawine wamcp ndioopsa a mcp
Paja timafuna kusintha utsogoleri wa dziko ndie don't blame opposition parties, tinachita kuwathamangitsa boma mpaka ku court ndie osamapsa nazo mtima, ndipo ndife tomwe timaombera mmanja kuti awa achoke atikwana ndie tiwavutisiranji kuti adzuke???????? leave them
Anthu awa analigulitsa dzikoli Kwa chakwera ndipo zawo anadya ndipo akuzidya
Ankaziwa ndani kuti MCP kumangochi itha kuwina
Pano alichete sakhunzidwanso
Boma lilipoli linachita kulanda dziko ndipo chikhala
Malemu Bingu wamuthalika analipo sakanalora kupeleka kuzinyawu zotukwana zikoli owina wina kukalokera kulipeleka dziko
amayi awa ndichitsilu komanso umbili ulimo APM ndi Atupele sizakhunze ndinuyo amene mumapanga mademo kut mcp ikhale pomwe ilipa panoso panga chimodzimodz
Mutavutike ndi inuyo atupele ndi wolemela peter olemela komanso iwenso ndi wa mcp machende ako
Chisiru iwe vuto rako ndi chani muzimayi iwe tose tipitiliza kuzuzika ndi ana Ako womwe azavutika ndi MCP
Khalani ku mcp zanu izo,,, mesa anthu munasakha nokha mcp ndiye mukufuna chani
Iwe akupatsa ndalama chitsiru chamunthu galu iwe ngat walandira ndalama ingodya
Sizachizolowezi anthu adapenya amafuna khalidwe osati chìpani chipanisamadya koma action to serve people
Watumidwa iwe ungofuna kuipisa APM ndi Atupele
Za ziiii zikuchitikazi sukuziona
Akunena zoona nfanayu UDF & DPP there useless party's kukanika kutsutsa
Sanatumidwe koma chilungamo opposition ukugona too much
Auzeni zoona izii mkuthamangitsa anyamata kuchipani ndikutenga nkharamba kuti akhare president angapange kamupeni agogo awo mumene zakuvutirani apa zizakharatso chocho chaka chamawa ndipo or mutukwane mkungotaya nthawi yanu pachabe kutukwana kulibe yankho zaoneka apa bwaa 😂😂
Iwe...akutuma
ndi zoona
Anthu awa azatipwetekesa tisamale zawo zinayela kare
Dpp ndalama zawo amapatsa achina bonikalindo mtanyiwa Limpompo fm yawo fm lomwe fm anamiwa asalo bakili tv ndi azizawo akuti azitukwana chakwela ndi boma lake daily koma zipindula chani palibe
Chizungucho akut chani .. " No. Men ??' wachiyawo wangalusa brasa😂😂😂
Ayao akumangochi ndi mbuzi opusa kwambili
Mukunena zoona,apa kuwina kwa MCP sinkhani yabwino
No men yomweyo chifunga chikangawa iwee
Ine ndimadana kowopsa ndi mcp komadi apa mwaonjeza,komatu mwatha mawu😂
Zosagwira mutu izi kwa oyiziwa mcp sindinena zambiri
Wapasidwa zingati
anthutu pano amafuna thandizo osati chipani or mtundu ndiye musamale chifukwa chakwera akumwaza chitukuko pena palipose
Atupele anachenjera simudzamudyeranso
You keep your vote
He will keep his money
Who are you to ask if ndalama za abakili zinatha?
Ali ndi ana akuwasungila
Iwe galu wa chabe chabe....leave APM alone, Nkhalamba yo inaononga zinthu ngati mmbusa wako wa nyau yo?
Garu iwe
Takhala tikukuuzanitu kuti, atsogoleri anuwo ndi odzikonda. Amangoyang'ana zawo zokha komanso akuba. Dpp mu nthawi ya Bingu chinali chipani cha dziko koma lero ndi family party. Same as udf ndi Aford. Sindidzazisatiranso
Choka wa mcp chikangawa iwee
Nimakape tiwaonetsa 2025apatangoyamba
sanatumidwe akukanba chikubgami
Tell them,umbombo basi
Bwampini iwe watumidwa umati adzichita kugwilira pochonga?
Mutharika is poom poom
Watumidwa
😂😂😂😂😂 wadyiwire
Dziwani Kuti MCP NDi chipani machini chenicheni chakhazikika chá dzikolose lá malawi, atsogoleriwake alibe nthawi yopanga njomba pá golo, akumangogoletseratu, kumwaza dzitukuko...
Chifukwa ACP nakingalilo awo ndiokuti aliononge dziko lino ndipo kungowinaso athu amenewa azichita ku lowa m,manyumba ndikumatipha amoyo koma mulungu si Lazaro
Auzeni UDF has failed us
Nkhani ndi yoti anthu aku mangochi mwagulitsa vote yanu ndi mcp
Iiiiih iwe zitaye zama councillor zo, MCP ndichan 😂😂😂
Zazizii palibe chomwe ukunena ife tagwirizana kwathu kuno mcp ipakile 2025
Simunayambe kulila tsono, munyera
MCP simungaikwanitse inuu
Kkkkk koma yah utm fire
Awecheteje jomba 😂😂😂😂😂😂,akulepheladi.apo,mwanena jomba,wakuchosa chitsotso maso,ndi nasi.
Watunidwa asakudziwa ndani Kuti MCP yabela
Uuuuuuu chokani apa akutumani
Komatu dpp mmmm ai nayituluka kuluza pakhomo
Zoonadi manyaka awa okaoka
Auuiuze 🥰
Ndakukonda kuyankhula kwanu big!!!
Kutereko chete ameneyu adzakalowa mmboma adzatinyesa
Peter mutharika is too old he must leave the party for young people
tapita uko iwe
Akupatse support ndani uzitenge bwn chamba ukusutacho amalawife tinasutapo ungatiuze chani nkhwere iwe
UDF yagona
Usogoleli wapita ndi chilima awa sangakwanise akunama
Kkkkkk zoona auze
Mmm ndi wa MCP ameneya wapasa kenakake zoti alankhule za manyi zi
Aaaaaah , siudziwa choonadi iwe
Wadya basi uyu watumidwa
😂Mwadya zambili galu yiwe
Kkkkkk akut
Useless
opepela uyu
The leaders are sleeping too much yooooooo😂😂😂😂