KULONDOLOZA ZA IMFA YA AGNESS KATENGEZA...

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 8. 09. 2024

Komentáře • 49

  • @ChristianChimwaye-yg9ti
    @ChristianChimwaye-yg9ti Před 8 měsíci +1

    Koma MALAWI 🇲🇼 POLICE MWAYIGWIRA NTCHITO. ❤❤❤❤❤❤

  • @raytavares2256
    @raytavares2256 Před 8 měsíci +4

    Why Are police exposing the details now while the other group is not arrested? You are still investigating the matter and revealing updates just gives a chance to the other criminals Amos committed all the crimes with. You have given the chance for other robbers and nurderes to escape justice.

  • @ChisomoMsiska-oi2vg
    @ChisomoMsiska-oi2vg Před 8 měsíci +4

    Uyu nayeso aphedwe chimunthu chopanda nzeru zoona kupha mubale wako yemwe amakudyesa😢

  • @SinoliaEfelemu
    @SinoliaEfelemu Před 8 měsíci

    Good job keep it up

  • @mzeewandembonyirongo2972
    @mzeewandembonyirongo2972 Před 8 měsíci +7

    Police you have been fast to talk to the public before arresting the others...you have made them run now.

    • @grayjames904
      @grayjames904 Před 8 měsíci

      Zaboza inu ogwidwa agwidwabe though ayankhulapo and they’re not going in deep details zoyakhula zinalipo lkale how come they catch the dude? Mufuna Muzise ntchito a police 😅😅

    • @matheromichellenkhalamba
      @matheromichellenkhalamba Před 8 měsíci

      They know their job, if they have managed to find the lead they have already cracked the case.

    • @noshallsnesu9174
      @noshallsnesu9174 Před 8 měsíci

      4:36

  • @MercyMwale-wc4lr
    @MercyMwale-wc4lr Před 8 měsíci +1

    Mmmh koma abale...your own blood

  • @user-zr9uw5hd5f
    @user-zr9uw5hd5f Před 8 měsíci

    Good job

  • @user-hs5xv6bk2f
    @user-hs5xv6bk2f Před 8 měsíci +3

    Mapazianu apolisi mukulephela kumanga anthu amene akuphesa amalawi ambiri Pano zakubuchala zilipati zakufamase zilipati zawitika zilipati lelo mwabwela poyela chifukwa Choti ndimphawi uyu mukunena Kuti simumauzidwa inu apolisi zonse zakufamase kubuchala Moti simukuziwapo khanthu site ana tsiku likubwela muzanena nokha tisanakufunseni mafunso

  • @user-gk6bf7xe9g
    @user-gk6bf7xe9g Před 8 měsíci +1

    Uyuso aphedwe bas palibe kuchitila mwina ai ⚔️🗡️⚒️🧷🔪🐯🐆🐅🪱🦂

  • @user-vp5mg5qz9e
    @user-vp5mg5qz9e Před 8 měsíci

    Congratulation Lilongwe police

  • @ibrahimbamusi109
    @ibrahimbamusi109 Před 8 měsíci +1

    Allan witika ndiye zili pat

  • @user-uu3wy8vl1y
    @user-uu3wy8vl1y Před 8 měsíci +2

    Kodi za Njaunju zinathela pati?

    • @Martha1436
      @Martha1436 Před 8 měsíci

      Ndipo Inenso ndikadakonda nditadziwa.

  • @EdythGloryNamponya
    @EdythGloryNamponya Před 8 měsíci +1

    Kenako tidzamva zoti wafera mu cell

  • @user-fg5iw1qy1k
    @user-fg5iw1qy1k Před 8 měsíci +4

    Kuthamangatu kumuonesa koma akapezeka wagulu la apolice azanu mubisa agalu inu mmmm

  • @davidzgambo
    @davidzgambo Před 7 měsíci

    tikufuna detailed report ya Witika

  • @johnman4619
    @johnman4619 Před 8 měsíci +1

    Apolice athu simumachedwa kumpeza munthu aka thawa .koma mulibe chilungamo mumamtayanso after mutadya mabanzi

  • @VictoriaWilliam-ms2ft
    @VictoriaWilliam-ms2ft Před 8 měsíci

    Nkuthekanso kuti mwina waulura kale Amosiyo Koma mwina ndiodziwika Akulephera kumubweretsa poyera

  • @raytavares2256
    @raytavares2256 Před 8 měsíci +1

    This boy Amos Is dangerous, having a sister and living with his sister for free food and secured free

  • @user-tz5jo3dd9t
    @user-tz5jo3dd9t Před 5 měsíci

    Mmmm koma anaganiza bwanji uyu

  • @user-vh9uk1jy7w
    @user-vh9uk1jy7w Před 8 měsíci

    Mukamaliza mlandu umenewu mumtengenso Soulosi Chilima wa ku maulanso naye

  • @masulasanudi7286
    @masulasanudi7286 Před 8 měsíci +1

    Kod mulandu wa Witika uli pat? Pot uyo sali m'boma ndy kuthamangatu kumuyalutsa eee koma apolice mmmm chinyengo

  • @user-lg6ym4hz3w
    @user-lg6ym4hz3w Před 8 měsíci

    Ndipo tikudikila kuti timve watching from Lesotho

  • @azunguauskay4903
    @azunguauskay4903 Před 8 měsíci

    Mnyamata oyipa

  • @user-qh3nb4vx9j
    @user-qh3nb4vx9j Před 8 měsíci

    We need cctv

  • @user-mu2qw6br2f
    @user-mu2qw6br2f Před 8 měsíci

    Mtolakhani usamangoti "mlongo wawo" use also brother wa omwalirayo chichewa Cha mlongo wawo sichigwiritsidwa ntchito dziko lonse

  • @user-zy8uy3fw5x
    @user-zy8uy3fw5x Před 8 měsíci

    Inu anatumidwa ndi andale ameneyo

  • @user-to4or4jw9g
    @user-to4or4jw9g Před 8 měsíci +1

    Koma ngakhale amupeza Amos'yo amufunse bwino bwino chifukwa nkutheka alipo anamutuma

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 Před 8 měsíci +1

    Iiiii chimunthu chikulukulucho kumasungidwa mmmmm ndekutidi chinali chigawega kwao anachilemphera mchobvuta iiiiii koma mpaka kupha mlongo wake eeeeee

  • @ChristianChimwaye-yg9ti
    @ChristianChimwaye-yg9ti Před 8 měsíci

    Palibeso zoti uyuyu ndi mlongo wawo ayi afunika akaphedwe

  • @user-in3sh8ru7o
    @user-in3sh8ru7o Před 8 měsíci

    Sikusinja uyu amphedwe

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 Před 8 měsíci

    Eeeeeeee 🙆🙆🙆🙆

  • @BeautyKunje
    @BeautyKunje Před 8 měsíci

    Mu2 oipa kwambri olo umunthu osampeza

  • @user-qj7ze8vh4l
    @user-qj7ze8vh4l Před 8 měsíci

    Eeeee

  • @user-rv2sr2gr5f
    @user-rv2sr2gr5f Před 8 měsíci

    Km galu iwe kupha mulongo wako food for free

  • @austinvincent773
    @austinvincent773 Před 8 měsíci

    Anamuphelanji

  • @reziejamw4205
    @reziejamw4205 Před 8 měsíci

    sad news😡

  • @user-ic1xl1tu3m
    @user-ic1xl1tu3m Před 8 měsíci +1

    Khondo ndanasi amakupha ndi wako

  • @user-is9fk8uz9i
    @user-is9fk8uz9i Před 8 měsíci

    Good job