Koma Zikhale with all that pomp calling himself "nyama zikuluzikulu" but only managing 93 votes basi? Koma ma delegates ndi anthu opusisa. For Mkaka it was obvious kuluza because he called himself "mwini wa chipani" he thought he was. Untouchable, he was living in his own world 🌎 he never cared
Apresident achakwera ndi munthu wabwino koma kuchipaniku kuli afisi odyazoola ndamene aluzawo moo respect to Mr he presidentmukanakhala kuti munayamba kale kuwalangiza anawa sibwezi congress party Ili yambiri zonyasa fire Ben
Mkaka amuyedzeka😅😅
😂😂😂😂😂 absolutely
Kudzimva Mkaka...amawona ngati iyeyo ndiye ngwazi ya MCP
Congratulations to all the winners,, Jessy kabwira welcome back the iron lady.
Mumba amayenela kuwina koma amukhomelela
Mumba anawina nchifukwa chake amamuopa
Mukumva bwanji akamajekete akunkuyu ndi achithyola tiyamba kukusakanino udindo uja umakubelekani panotu muli pa mbalambanda paja timakambatu ife nde pano mukuti bwanjiiiiiiiii
Musokoneza2 izi2 ndizachipani chane koma those people are still ministers
Catherine Gotani Hara just the right person. Jessy Kabwira the iron lady welcome back, well deserved position
Imeneyo we have edzekalised zavuta
Kubetsa ndarama zikhare wakumana nazotu🤣 rip kunkuyu and chinthyola muona zakudano
Viva zikhale,chithyola mkaka we're watching you
Mmmh Mkaka matama onse aja athela pano
Zikhale ng'oma kkk umakwana iweyo bro!! 😂😂😂😂😂
Nsonda uladi Musa 😂😂 dausi mwawaika pati mbuzi dza dziko la Malawi shame on u stupid old people 😢😢
Koma Zikhale with all that pomp calling himself "nyama zikuluzikulu" but only managing 93 votes basi? Koma ma delegates ndi anthu opusisa. For Mkaka it was obvious kuluza because he called himself "mwini wa chipani" he thought he was. Untouchable, he was living in his own world 🌎 he never cared
Malawi ndi dziko lomvesa chisoni,deal munapanga ndinu maguy atatu otchuka mwaluza inu koma awina ndi ena,njiru bas zikhale ,kumkuyu and mkaka
Apresident achakwera ndi munthu wabwino koma kuchipaniku kuli afisi odyazoola ndamene aluzawo moo respect to Mr he presidentmukanakhala kuti munayamba kale kuwalangiza anawa sibwezi congress party Ili yambiri zonyasa fire Ben
Kutsogolo kwa Dziko lathu likudetsa nkhawa .
Ndiye zikhala bwanji manganya uyo odziwa upempha pempha
😂😂😂😂😂😂 zikhale ng'oma 😂kunkuyu 😅mkaka chityola mukumva bwanji mu mtima
Kkkkkkk anthu oyipa mulungu sanalole.
Onse ayedzekedwa 😅😅😅😅😅😅
😂😂😂 sanawine hahaha
Anthu 4 amenewa ndi omwe awononga chipani cha mcp
Amenewa ayiwona yanyooooooh
Ukuphonyesa tikudzikuwa ife mkuluyi anati awina ndipo wawina
Awa ndimakapedi Aaaa nanga chiasankho cha dziko lonse mudzavutika bwanji
Mtima woyipa kuziwa kunyoza basi let love read not evil tongue always
Mtima woyipa kuziwa kunyoza basi let love read not evil tongue always
Zikhare uzivere chisonii😢
Nyama zikuluzikulu😂
Zikhare wanya nayo 😂😂😂😂😂
Akunkuyu sangawine mesa amalesa mapemphero ama candle ndiye awina bwanji munthu ndi satana wakhaulatu ameneyo kunkuyu wagwa nayo
Somebody has been edzakalized..
Tingoti amuyedzeka mchilomwe
Apita ma million a zikhale ,rip chithyola😂😂😂
Apa ndiye aba zeni zeni
Azikhale
Ambuye zikomo ukadzikweza Mulungu amakutsitsa langizo langa musaphane poti n, khalidwe lanu zosiyilana izi..
Keth nsukwa sadafune kuti mumba awine amadana naye
Mr Kamal bluesuit😂
MULIBWANJI A ULAD MUSSA NDI NDI A KEN NSOND? DZITSIRU INU ZAGANYU ZA MCP NZANU DAUS ALI PHEE! KOMA INU KUPUSA BASI MUNYATU MUSOWA KOLOWELA AGALUUU!
😂😂😂😂
😂😂😂😂esh
😂😂zikhale chaniyo
Ayiwala aManganya pa VP
For now we are waiting for utm convention 🥰🥰🥰
Dausi anaziwa kt azinjinjilika uku afa osadwala Mr chikangawa sakuchexa
Bungwe ili silitithandiza
Wanyanayo kamanjekete
Mutu ukulilenji mopanda nzeru. Abweza zake akagulitsa zimajekete zakezo.
Congratulations to the winners
Kuchipan mpaka ampongozi
😅😅😅😅 Kaka zamuvuta kwambili uku wadziwa kuti Anthu amadana zopusa
Sitikunvetsa, Ofuna Engineer Mumba tinalipo ambiri, zatheka Bwa?
Was the task to write subtitles for the speaker given to a kindergarten?
National asem
😂😂😂😂😂😂 kwachwma asaaa
Km kamajeket ulibwino kapena libwele phala namalila
Kod uku kunalibe 50 +1
Zikhale
Dzisankho dza anthu 1.500 mpata too days aaàa mbugwe Ili silitha kugwira ntchito
Maudindo asankhidwa koma mmene zinthu zilipano akuzimva bwanji
Ndipo aise aaaaa zausiru zenzen
Eti zoona m'pakana 2 days shaaaaa
docter mr chikangawa
Ken, nzonda akulila ndiulad mussa munya ndiye mulowela kuti
Change golo azapita ku convention ya DPP kkk