Video není dostupné.
Omlouváme se.

BON KALINDO LERO PA 15 JULY 2024 |

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 18. 08. 2024

Komentáře • 65

  • @dondamissonchdziwe3958
    @dondamissonchdziwe3958 Před měsícem +1

    Good spoken, BOM palavra, muito obrigado já deve abrir olhos, população de Malawi, Open your eyes people of Malawi, good Democracy don't be afraid

  • @RickMahangano
    @RickMahangano Před měsícem +1

    Wonderful speech, brain washing @educative, I stand to support you sir, kip the fire burning,,,,,,

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h Před měsícem

    God bless you Mr DC president wa mzelu

  • @PetrusTlhokwane
    @PetrusTlhokwane Před měsícem

    Ndipo ndizoonadi km anthu amene ali mayiko akunja ayenela kuvota apasike mupata ❤❤

  • @DoniexChisale
    @DoniexChisale Před měsícem +3

    Our DC...Timamva nanu kukoma.....you are our our mouth piece.....

  • @MatthewsJohn-kv8fj
    @MatthewsJohn-kv8fj Před měsícem

    Chakwera akufuna kuononga dziko lathu lamtendere achokepo Pampanga zamulemphrela chinsiru cha mumunthu impich😊

  • @GetrudeBanda-sd1yf
    @GetrudeBanda-sd1yf Před měsícem +5

    Nafetso amene tili kunja tipasidwe mwai ovota

  • @TemwaKabisa
    @TemwaKabisa Před měsícem +1

    Good message Mr bon kalindo the DC ❤❤❤

  • @DannyDaka-sn2fj
    @DannyDaka-sn2fj Před měsícem

    Bon kalindo umatipanga usaope muthu

  • @MussaHassani-zg1hm
    @MussaHassani-zg1hm Před měsícem +4

    Yes our president kalindo thanks so much for ur spish

  • @ExcitedBreakingWaves-oh3zb
    @ExcitedBreakingWaves-oh3zb Před měsícem

    Bwana president wa osauka.achenjezi atsikana omwe akunamizidwa kuti ntchito kumayiko a chi Arabia akafika uko aku akumakhala akapolo,kumawagona muwakakamiza komanso kugwira ntchito popanda nthawi yopuma.chonde achenjezeni anthu athu.

  • @MussahJames-po9cl
    @MussahJames-po9cl Před měsícem

    Yes bon kalindo ❤❤❤

  • @temwarachaelkhonje3733
    @temwarachaelkhonje3733 Před měsícem +1

    Booooooooooooooooooon Kalindo more firee

  • @AjibuTwalibu
    @AjibuTwalibu Před měsícem

    Bon kalindo
    Ndi munthu mmodzi
    Amene angapangise AMalawi ambili kukhala ozindikila
    Thanks DC MALAWI WAKE UP

  • @user-cg5ml7ym4v
    @user-cg5ml7ym4v Před měsícem

    Nafeso tili kunja tipatsidwe mwai kuti tivote tsogoleri tikumukonda chifukwa 50% amalawi tili kunja kwa dziko la Malawi 🇲🇼

  • @Mohammed-sk1fy
    @Mohammed-sk1fy Před měsícem +1

    Our poor president, salute 🫡

  • @HawaHussein-d4l
    @HawaHussein-d4l Před měsícem

    Thanks Mr d c for giving people your good message

  • @MemoryGiftKumfela
    @MemoryGiftKumfela Před měsícem

    Tidzayima pachilungamo guys kalindo mulungu azimupatsa moyo wautali

  • @Shelifibraheem
    @Shelifibraheem Před měsícem

    Our mbambande president pangolin the excellence Mr pangolin namanyonyole BORN KALINDO. U are fighter for real.

  • @TuribakomwamakolaTuribakomwama

    God bless kalindo

  • @Moses51
    @Moses51 Před měsícem +1

    Keep up update 💪💪💪🇲🇼 the Dc bon kalindo 🎉

  • @user-ez8zs1iq9k
    @user-ez8zs1iq9k Před měsícem +1

    Odana ndi chilungamo aziweluze yekha ife tikufuna ma audio azitulutsa katatu or ka four pa siku 😂😂😂😂😂

  • @user-ks3uw8gj8h
    @user-ks3uw8gj8h Před měsícem

    Koditu kugona Kumene a Malawi tinakali Ntuloku tidzangozindikila Tsiku linali ndife ma Lwandanise, or Israelites, Tulo taliwonjeza 😮😮😮

  • @giftdulamkalenga7344
    @giftdulamkalenga7344 Před měsícem +1

    Ambuye ATULUSE NDODO ija pleaz

  • @JohnTutu-l3b
    @JohnTutu-l3b Před měsícem

    Ndipo 😂😂😂😂😂😂 angosiya zikori iiiiiii

  • @GiftRashid
    @GiftRashid Před měsícem

    Ndizowonadi bon kalindo yipase moto

  • @peterchikwakwa8476
    @peterchikwakwa8476 Před měsícem

    Mmakwana moya

  • @augustMag
    @augustMag Před měsícem

    Mr Bon Kalindo you're our speech Malawi ❤❤

  • @GLABELMW
    @GLABELMW Před měsícem

    Osaopa bon kalindo tikuva kuwawa ife ambawi akumudzi tilibe ntchito zindu zikuka zikudulabe titani ife ambawi akumudzi boon osagona

  • @juliochiwalo
    @juliochiwalo Před měsícem +1

    A chakwera ndi boma lanu.la MCP ndalama za anthu omwe anapuma ntchito zikupita kuti zaka zitatu anthu akudikirabe ena mpaka akumwalira shame on Mcp govt

  • @gracemkandawire8769
    @gracemkandawire8769 Před měsícem

    Ngati kungatheke a Kalindo muwaitane a Njawala kumbali muwathandizile zoti apange ndi UTM

  • @Raph-kayRaph-kay-g5v
    @Raph-kayRaph-kay-g5v Před měsícem +1

    Tizingophanopo ndi miyala basi tieni kwa zikhale ng'oma konko miyala mmanja tiyenitiyeni tiyeni inu

  • @CharlesPhiri-ds1rk
    @CharlesPhiri-ds1rk Před měsícem

    Zonvetsa chisoni Malawi

  • @Alicia-ns5ho
    @Alicia-ns5ho Před měsícem

    More fire

  • @colleenMpaya
    @colleenMpaya Před měsícem

    Mmatiimilira Mr president ❤

  • @OwamiSimeon
    @OwamiSimeon Před měsícem

    Born kalindo the decee ur president

  • @ziwani3682
    @ziwani3682 Před měsícem

    Mr president pitrizan

  • @MemoryGiftKumfela
    @MemoryGiftKumfela Před měsícem

    Achoke chakwela ndi mbuzi

  • @stevejizaremu3396
    @stevejizaremu3396 Před měsícem

    The DC

  • @user-mv1wg2qd6i
    @user-mv1wg2qd6i Před měsícem

    Good message DC

  • @MaundalaKazembe
    @MaundalaKazembe Před měsícem

    D C MBAMBANDE

  • @ChrifordBiziel
    @ChrifordBiziel Před měsícem

    Zulo m'malo moti 42million iye akut mabilliin kkkkk amarawi!!!!!

  • @Shadreckdingiswayo
    @Shadreckdingiswayo Před měsícem

    Number ya Bon kalindo bwanji ndili ndi zoti ndimuyakhule

  • @chamiyuna.siraji
    @chamiyuna.siraji Před měsícem

    Wayangura bwino ❤ boni kalindo

  • @user-dp7bc7yy6s
    @user-dp7bc7yy6s Před měsícem

    Boma ilili ndimbola kwambiri akufuna kt tizapite ku Mocambique wapansi kuli kuthawa nkhondo

  • @HUMPHREYPAANA
    @HUMPHREYPAANA Před měsícem +1

    Pitilizan boss

  • @BambordKabambe
    @BambordKabambe Před měsícem

    AKULU MUDZIDUMPHITSAKO MASIKU MAPETO AKE ZIKUKHALA NGATI NKHANIZI MUMANGOPEKA AT LEAST PRODUCE AN AUDIO ONCE OR TWICE A WEEK NOT EVERYDAY KODI DAILY NKHANIZO ZIMAKHALADI AUTHENTIC😢😢😢😢😢

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y Před měsícem

    Good Messnge Mr bon kalindo ❤

  • @SteveNkhambule
    @SteveNkhambule Před měsícem

    Even bakili muluzi TV akhala akuyankhula for long time

  • @DanneilMguntha
    @DanneilMguntha Před měsícem

    Thanks Bon kalindo

  • @ChrifordBiziel
    @ChrifordBiziel Před měsícem

    Koma adzasiya boon karindo mudzakhara ndimakonda anji dziwe?

  • @shanlaljith5389
    @shanlaljith5389 Před měsícem

    Tiziyasa maudzu mmalo mwakandilo

  • @JunaKananji
    @JunaKananji Před měsícem

    Bon karido ❤❤❤❤❤❤you

  • @JanaMussa
    @JanaMussa Před měsícem +1

    Zilibwino

  • @AbdirashidMohamedIbrahim-ib9uy

    Mwauze ni achibwana 👊👊✊🦾

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 Před měsícem

    The DC DC kung'alula MCP

  • @GiftSaidimbewe
    @GiftSaidimbewe Před měsícem

    Zoona boma silitikuganizira

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole Před měsícem

    Tinayika munthu oyipa pampando 👿

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs Před měsícem

    Boma ili mmmm lodzikonda

  • @MilacleSankhani
    @MilacleSankhani Před měsícem

    Kalindo nd 1

  • @Moses51
    @Moses51 Před měsícem

    Odanandichulungamo ziwani kuti ndiyenawo zochita zawo zimozi

  • @peterchikwakwa8476
    @peterchikwakwa8476 Před měsícem

    Mmakwana moya