Video není dostupné.
Omlouváme se.

UDF, DPP AND UTM APANGA MGWIRIZANO ? |

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 15. 03. 2024

Komentáře • 163

  • @AlexManuelMisomali-sv1vn
    @AlexManuelMisomali-sv1vn Před měsícem +3

    It is very very difficult for the UTM to make an alliance again with the MCP and the reason it's not only that they've killed Saulosi Chilima but even before Chilima died the alliance was already broken and Chakwera openly said that he'll stand for the MCP as a presidential candidate in 2025

  • @Littlefair7
    @Littlefair7 Před 4 měsíci +4

    Umenewu ungakhale mgwirizano wabwino kwambiri.

  • @user-fh4pq9lu9d
    @user-fh4pq9lu9d Před 4 měsíci +1

    Yes in politics there is no permanent enemy,UDF ,DPP, UTM can upset the tables.

  • @Kamwachale
    @Kamwachale Před 4 měsíci +1

    APM is not alone for campaigns

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w Před 4 měsíci +6

    MCP ndi chakwera akuchoka kale, palibeso kuwina apa, a Malawi akuzunzika kunjaku.

    • @robsontyg3928
      @robsontyg3928 Před 4 měsíci

      Who cares, pathako pamako

    • @fanie6913
      @fanie6913 Před 4 měsíci

      ​@@robsontyg3928inunso ndia chitsiru bwanji...kulalata zomwezi

    • @robsontyg3928
      @robsontyg3928 Před 4 měsíci

      @@fanie6913 mahule, chomwe umadziwa nding'andula kumatako kwako kununkhako

  • @LovemoreSalima
    @LovemoreSalima Před 2 měsíci +2

    Ndizofunikira km chilima ndiye ai ndiokula mtima.
    Udf ,dpp, musalole chilima ai.

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y Před 4 měsíci

    Good Message

  • @abdulrafiquekalembo469
    @abdulrafiquekalembo469 Před 4 měsíci +3

    Chilima ndi okula mtima we he must stay there in Tonse Alliance!!!

  • @IsaacBands-ir7ii
    @IsaacBands-ir7ii Před 4 měsíci

    Yes

  • @user-ln5hw7dn9g
    @user-ln5hw7dn9g Před 4 měsíci +2

    Mukuti Chilima ndi mistake munampatsako mpata kuti alamule kapena ndi zomwe mumalota

    • @LovemoreSalima
      @LovemoreSalima Před 2 měsíci

      Akulu akuluti posankha msogoleri amayang'ana khalidwe,satenga aliyetse chifukwa ndi wandevu za waiti ayi, ndiye ziwani kt APM anamuona kt alibe zomuyenereza kukhala msogoleri. Ndiye vuto ndilokuti ziko lathu lazaza ndi anthu mbuli zophudzira.

  • @carlossadimba595
    @carlossadimba595 Před 4 měsíci +1

    Ndye angakhale president ndani of coz there is no permanent udani in politics

  • @alomuddin8801
    @alomuddin8801 Před měsícem

    good news that's we want thank u

  • @user-hg8zy8pt5b
    @user-hg8zy8pt5b Před 4 měsíci +4

    APM ,UDF , UTM apange zomwezo( chakwera watinyasa matongo yake

  • @NgomaRaheem
    @NgomaRaheem Před 4 měsíci

    Awona nyenkhwe sanati akang'wing'wiwo

  • @johnkatapeh7182
    @johnkatapeh7182 Před 4 měsíci +1

    Joker waife tampanga kale withdraw❤ chilima

  • @Disiel-ez1ce
    @Disiel-ez1ce Před 4 měsíci

    Okay ziomo 🔥🔥🔥🔥👍👍

  • @user-uh3yu9nn9q
    @user-uh3yu9nn9q Před 4 měsíci +1

    Ndipo musazikonde kapena kuzengereza pangani zomwezo

  • @wangachindeya8577
    @wangachindeya8577 Před 4 měsíci +2

    Dpp iyende yokha ngt amalawi akufuna zinthu zisinthe

    • @user-jy4do9iy1j
      @user-jy4do9iy1j Před 4 měsíci

      Kuti anthu azizaba bwino pitala akugona. Pa mpando

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 Před 8 hodinami

    Kuno Dpp ndiye yapita apa mwawonaso waboma apa 2025 muwonaso

  • @KodindineNdani-yh1of
    @KodindineNdani-yh1of Před 4 měsíci +1

    😂mabodza ku Malawi 😅.. muzitorere

  • @user-qx1hk2pz1b
    @user-qx1hk2pz1b Před 4 měsíci

    More 🔥

  • @PaulChaleka-lb4vx
    @PaulChaleka-lb4vx Před 2 měsíci

    Chilima adzatsogolere adzawina coz chilima Ali ndi value pa ndale

  • @BrightKuyaka
    @BrightKuyaka Před 4 měsíci

    Nkhani ndiyomweyo, koma pa nkhani ya president sangakulilane mitima?

  • @RobertThungula
    @RobertThungula Před 10 hodinami

    Zipani zigwirizane kuyendera limodzi kuti mcp isaone mpata

  • @Kasawalah
    @Kasawalah Před 4 měsíci

    Yes ndizoona zizacitikadi mukunenazi

  • @JinoreKalemba
    @JinoreKalemba Před 4 měsíci

    Ndizoona zomwe akuyakhulazo Kuti MCP igonjele UTM zithu zikatelo zikhala bwino app AI awasiye apange zawo

  • @RaymondKaumba
    @RaymondKaumba Před 29 dny

    Migwirizano imeneyi are not for development

  • @user-qp8kh2hj9o
    @user-qp8kh2hj9o Před 4 měsíci

    Hehehe DPP president wake ndani? Pitala hu za 80+ana ake anayi😂😂😂😂😂

  • @user-zf4ij4vs3d
    @user-zf4ij4vs3d Před 4 měsíci +1

    Dpp ukulowa m,boma awa alephela basi ayenela kuvomeleza

  • @KenChitete-pg3ws
    @KenChitete-pg3ws Před 4 měsíci

    Mugwilidzano ukhodza kukhalapo,,,,,funso!!! Kodi pa athu atatuwa president a khala ndani??????

  • @user-xx5jj5bc3d
    @user-xx5jj5bc3d Před 4 měsíci +1

    Kod mwat gogo wathu apm pano ali ndizaka zingat 😂😂😂😂 koma azakwanisa kuyenda from Nsanje to Kalonga Nkhotakota to Mchinj

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl Před 4 měsíci +1

    Utm ikagwele pulesident wa utm ndi wosapanganika inuyo ngati mukujiya ya utm mwagwa nayo amalawi salola

  • @HamzaHaluna
    @HamzaHaluna Před 4 měsíci

    Olo DPP ithayima payokha izawina chifukwa chakut ndi mene ilili panopa Malawi 🇲🇼 Sali bwino Malawi 🇲🇼 wathu tikulila ndimene akutipangila Amene akulamulia Lero lino

  • @owenmasekokamadya6695
    @owenmasekokamadya6695 Před měsícem

    OK

  • @robertrichman9376
    @robertrichman9376 Před 4 měsíci

    I'll never trust any alliance , onsewa ndimbava zeni zeni ndipo alibeso phindu

  • @user-gx5ht9gm3z
    @user-gx5ht9gm3z Před 4 měsíci

    NO PAIN NO GAIN TIMANDIKIL ZIMENEZ VIVA UDF VIVA APM VIVA UTM

  • @user-iy8vi7nn8r
    @user-iy8vi7nn8r Před 4 měsíci

    Any Government involving chilima mistake

  • @user-cf9yz3ei5o
    @user-cf9yz3ei5o Před 4 měsíci

    But alliances have already failed

  • @BashielSalade
    @BashielSalade Před 20 dny

    Zikhala bwino zagwilizano

  • @MonicatimanyeShaba
    @MonicatimanyeShaba Před 4 měsíci

    Ndizoona mcp ikapanda kugonjerana ndi utm chawopalibe a mcp azamva nkhwangwa ili m'mutu😂

  • @jahmanmakwinja-ef7zn
    @jahmanmakwinja-ef7zn Před 4 měsíci

    Zikumveka ndthu bro ndpo izi ndizotheka even a Malawi ambiri adzalikonda ganizo limeneri fog sure

  • @user-fs1ox7ou1b
    @user-fs1ox7ou1b Před 4 měsíci

    Maganizo abwino tipange zoti mcp isalamulirenso mmalawi muno

  • @JimmyMpinda
    @JimmyMpinda Před měsícem

    Nice alliance

  • @HarrisonMwanga-xy4sc
    @HarrisonMwanga-xy4sc Před 4 měsíci

    Atsitse katundu ngati satelo achoka ndipo Malawi tikati no is no.

  • @RaphealKwelani
    @RaphealKwelani Před 2 měsíci

    Wapenga matumbiyu akufunako ndalam😅😅😅

  • @AleksaWilliams-qc6cn
    @AleksaWilliams-qc6cn Před 4 měsíci +1

    Udf ndi Dpp zilibwino ,koma Utm aaaaa no idea sir

  • @KlokkieFielies
    @KlokkieFielies Před měsícem

    UDF AND DPP THAT'S WOLL WILL BE BETTER WE DON'T WANT MCP ANYMORE IN MALAWI .

  • @user-qv4ko6ps4j
    @user-qv4ko6ps4j Před 4 měsíci

    Mgwilizano wa DPP, UDF and UTM ukadzangiwina mu 2025 mkuyamba kulamulila mmmmmmmmmmmm Chakwela ndi nduna zake tidzambwandila ngati nkhuku wa ku prison because aononga misonkho ya a Malawi ndie tidzafinya banja lonse la Chakwela,,,,,,adzabweze zathu

  • @RaymondKaumba
    @RaymondKaumba Před 29 dny

    80yrs wakalamba mdalayu

  • @abdulrafiquekalembo469
    @abdulrafiquekalembo469 Před 4 měsíci

    UTM ikhale komko kwa a Satana aliko.Ife DPP+UDF+Aford we can agree.
    UTM not good guys

  • @usumanidaudi
    @usumanidaudi Před 4 měsíci

    Gwirizano ukharepo basi chakwera watikwana

  • @FelixMhango
    @FelixMhango Před 2 měsíci

    Tinned momveka pano popanda migwilizano palibe chipani chingapambabe 50+1 ilipoyi.
    Komaso iwalani kuti utm ingapange alayansi ndi dpp. Zinazi mukungoganiza

  • @user-kj2tc9nj5g
    @user-kj2tc9nj5g Před 4 měsíci

    Chilima adapangidwa addicted wa mgwilizano

  • @user-sf9vn7ml7s
    @user-sf9vn7ml7s Před 4 měsíci

    1:32 Mcp ndi UTM akuyenela Kuykendala be limozi asaiyane

  • @user-pj3rf4rn9w
    @user-pj3rf4rn9w Před 4 měsíci

    Koma zoona chilima mukumufunaso ine ayi

  • @SylecMdala
    @SylecMdala Před 4 měsíci

    Ndipo akapanga chibwana chilima alamulazikol

  • @user-ml2vw1dc9c
    @user-ml2vw1dc9c Před 4 měsíci

    Ndiye atapanga mgwilizano PPP UTM. UDF president adzakhala ndani poti chilima watopa kukhala wachiwili. Komaso Gogo muthalika akufunaso kukhala president. awo ndimaloto achumba sizingatheke

    • @user-gx6ux9wi3u
      @user-gx6ux9wi3u Před 4 měsíci

      Kkkkkkkk azakhala chilima president Peter sakufunatu kuimila koma akumukakamiza

  • @user-ln3zx6wo4w
    @user-ln3zx6wo4w Před 4 měsíci

    Mcp kusamva akuonangat ndalama zingagule vote

  • @user-qp7nx9ri3y
    @user-qp7nx9ri3y Před 4 měsíci

    Yes,ziyenela kudzakhaladi choncho kuti mcp idzamve kupweteka

  • @alfredmongola900
    @alfredmongola900 Před 4 měsíci

    Ngati UTM , udf achite alliance ndi dpp ziribwino coz ndinthwi ya chilima ndi atupele kukhala atsogoleri chifukwa muthalika wakula ndiye kuti anyamata awiriwa azatenga upresident mmodzi mwa awiriwa

  • @user-og9hw8lg8u
    @user-og9hw8lg8u Před 4 měsíci

    Here we go ❤

  • @IssahAluba
    @IssahAluba Před měsícem

    MCP sitikuifuna lokoitatheratu

  • @SelisonChamba
    @SelisonChamba Před 4 měsíci

    Zosezi ndi udyera mwala oyendayenda suyanga ndere

  • @FrankKajipenjere
    @FrankKajipenjere Před 4 měsíci

    Pangani zomwezo basi mesa chilima anamukana awa nanuso pangani mugwirizano basi😂

  • @daviekamanga1417
    @daviekamanga1417 Před 4 měsíci

    MCP NDIYAMPHAMVU KOMASO NGATI UTM INGAPITESO KU DPP TIITCHULA KUTI NDIYOYENDAYENDA NGATI MPHEPO ILIBE KUKHAZIKIKA PAMOZI AKANAKHALA KAZI TIKANATI NDIHULE WAKULU KOMA ZONYOZA AZAWO AYI

  • @Milanzi-nb5fv
    @Milanzi-nb5fv Před 4 měsíci

    MCP sikuwinanso or mutasakanikilana ndi UTM

  • @user-zv3ul2md2m
    @user-zv3ul2md2m Před 4 měsíci

    What ever allayance bola chilima atsogole apo ayi zivuta

  • @CidrickMbengwa
    @CidrickMbengwa Před 4 měsíci

    Chilungamo chimawawa SKC ndikatundu ameneyu

  • @PaulChaleka-lb4vx
    @PaulChaleka-lb4vx Před 2 měsíci

    50+1adzapangitsa kt alliance ichitike chifukwa Pali be adzapeze 50+1% koma chakwera ndi khuluku

  • @christophergibson72
    @christophergibson72 Před 4 měsíci

    Phatikizanani tizakunyeyeni dziwani dziko Lamawi a landlord anatenga

  • @WisdomBlack-uu7zt
    @WisdomBlack-uu7zt Před 2 měsíci

    Chilima ndye ai sitikumufuna nd khuluku olo APM sangalole zmenezo

  • @user-qm1qb2jp4s
    @user-qm1qb2jp4s Před 4 měsíci

    Zitatelo DPP utm plus udf can help to rescue malawi

  • @user-wx1jt5fd2j
    @user-wx1jt5fd2j Před 4 měsíci

    Ndipake DPP ndi UDF kupanga ngwirizano zikhonza kuthandiza ziko lamalawi akazalowa m boma koma azaonese chisanzo cha bwino

  • @KassimmwSteven-og8ny
    @KassimmwSteven-og8ny Před 4 měsíci

    Apa zikuyendera KUt chilima abwerere zachitika manyazi kuziko izi

  • @jestonmapondela1339
    @jestonmapondela1339 Před 4 měsíci

    Aaaaa zimenezo tilibenazo ntchito aphatikizanebava zokhazokha mbuli zidzawavotela Koma ozindikira sangapange apa asowa kolowera asiye ndare azipanga zina

  • @gasperJEllias
    @gasperJEllias Před 4 měsíci

    Dpp woyeeeeeeeeee with UDF. + UTM. 2025 mcp inya manyi.

  • @SumanJames
    @SumanJames Před 28 dny

    Mwakhwana akalindo munthu wamkulu

  • @happymumba2261
    @happymumba2261 Před 4 měsíci +1

    Bola apange zomwezo

  • @ScaverManjedza
    @ScaverManjedza Před 4 měsíci

    Compaign ya ulendo unoo nde kuli zinthuuu🤣🤣🤣🤣

  • @EnerstNtchefu-nk9gf
    @EnerstNtchefu-nk9gf Před 3 měsíci

    Kkkkkkkk palibe chomwe mungapage

  • @OmmarKassim
    @OmmarKassim Před 4 měsíci

    Ndipo akapanda kumusalamala Chilima apita nao DPp

  • @AdamYas-ec9oc
    @AdamYas-ec9oc Před 2 měsíci

    Atrue news

  • @user-jn9tz3li3v
    @user-jn9tz3li3v Před 4 měsíci

    Not UTM chifukwa Chikima has no direction

  • @thomluciouss7360
    @thomluciouss7360 Před 4 měsíci

    Gwilizano wa UDF ndi DPP ndiwakalekale Musachite kukaikaso ali limodzi paka 2030 woo

  • @JohnJohn-og8rt
    @JohnJohn-og8rt Před měsícem

    Zoona bhola zisakare ntchotcho

  • @user-lj3jb6hf9f
    @user-lj3jb6hf9f Před 4 měsíci

    Chakwera aonesa ubusa wakedi kutidi anali woona,komanso apange mipingo kugomezeka kapena ayi kutengela iyeyo.

  • @NditajiMaxwell-cz8ir
    @NditajiMaxwell-cz8ir Před 4 měsíci

    Km chilima vuto ma joke amamuchulukila komaso mmene wapangila zinthu zake aaaaa kukhululupilira kukuvuta tsopano😊

  • @SmilingFishingRod-zc4wx
    @SmilingFishingRod-zc4wx Před 4 měsíci +1

    Chilima ndi chipani chale musyireni akhale nacho payekha
    Chilima ndiokanika ndipo ndiopsya mmaganizo
    Atha kupanga ubale koma DPP ikazalowa mmboma mumuona azagalukilanso mmutu mwa Chilima simumayenda bwino

    • @user-jf3kv3jl2h
      @user-jf3kv3jl2h Před 4 měsíci

      Ndip kwambiri ayiwala kale kt chilima ndioyipa mtima

  • @user-gz9iy7sd7j
    @user-gz9iy7sd7j Před 4 měsíci

    Utm ikhalebe komwe iliko Chllima not a trusted young guy.

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 Před 4 měsíci

    Pangani zomwezo guys ife chakwera watikwana sitikumufunaso talira mokwana koma mulungu ayakha popano pasara pang'ono chabe

  • @frankcassim
    @frankcassim Před měsícem

    MCP siyingawine

  • @SpancerChikopa
    @SpancerChikopa Před 2 měsíci

    That's gud

  • @user-xl1ly3op9u
    @user-xl1ly3op9u Před 2 měsíci

    Dpp udf komanso afford ine utm toto ndakana,

  • @webstermbewe8395
    @webstermbewe8395 Před 4 měsíci

    Thanks very much appreciate

  • @user-le3lr6jn7g
    @user-le3lr6jn7g Před 3 měsíci

    Ndipo tingompempha Chihana kuti nayenso azajoine mgwilizano umenewu enawa owone nyekhwe

  • @Alliechamolie
    @Alliechamolie Před měsícem

    Kodi guys mzungu ndiwosaloledwa kuyimila zikolathuli pazisakho

  • @WilliamBandaWili
    @WilliamBandaWili Před měsícem

    Apo niboma kale mcp ili mmadzi

  • @MosesStory
    @MosesStory Před 4 měsíci

    Zonse zomwe mukunezi mzanzelu koma kumadziwa Kati dpp inaluza ililimodzi apamukatengela kudzikonda malawi akhalabe pamavuto

  • @aliwillardkundaje1083
    @aliwillardkundaje1083 Před měsícem

    Add Aford and PDP

  • @user-sf9vn7ml7s
    @user-sf9vn7ml7s Před 4 měsíci

    Akuyenela Kuykendala limodzi kuti akwanilitse maso phenya awo 2063