Kamuzu Chibambo Kutsimikiza Kuti Tonse Alliance Sakudziwa chimene Akuchita|Amamangidwa Mmasamba

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 17. 03. 2024
  • We are reacting and commenting on what the former MCP publicity secretary is saying about Tonse Alliance Government failure to fulfill campaign promises.. Malawi is Worse off than it was 5 years ago...he admits!!

Komentáře • 11

  • @JamesMalango
    @JamesMalango Před 4 měsíci

    Mukutipsa nkhani zabwino komano zomaduladulazo ma discussion sizikuchita bwino ai

  • @dumisanimoyo3152
    @dumisanimoyo3152 Před 4 měsíci

    Mumene tayambira sizikuyenda sizikuyenda iye akukhuta osatenga action bwanji amalawi

  • @webstermbewe8395
    @webstermbewe8395 Před 4 měsíci

    Boss this si good BUT DONT INTERUOT THE DISCUSSION YOU ARE MAKING IT SO LOUSE, LOW, LOSE WAIT

  • @user-jn9tz3li3v
    @user-jn9tz3li3v Před 4 měsíci

    Brian Banda ndi Kasakula amamutukwana kwambiri APM. Koma panopa they are regretting chifukwa mbuzi yayo Chakwela akulephela kuyendesa dziko momvesa chisoni.

  • @AhmadumkomaTambala-lr9gp
    @AhmadumkomaTambala-lr9gp Před 4 měsíci

    Ndipo Brian banda ampepese EPM ananyoza koopsa

  • @dumisanimoyo3152
    @dumisanimoyo3152 Před 4 měsíci

    Kkkkkkk kodi munthu modzi nkuzunza amalawi ambiri mbiri malawi army osatenga boma bwa mupaka ti vote

    • @user-jd4oi9lk8l
      @user-jd4oi9lk8l Před 4 měsíci

      amene aja ntchito imaziwa iwo ndikulanda makala basi

  • @mphatsojuliostandy4918
    @mphatsojuliostandy4918 Před 4 měsíci

    Amwene inuso mumaononga zabwino ndi ma comment anu upusawo bwanji osasiya program mene ilili bwanji

  • @user-cf9yz3ei5o
    @user-cf9yz3ei5o Před 4 měsíci

    Martha chizu.ma started very well but it was blessing in disguise

  • @dumisanimoyo3152
    @dumisanimoyo3152 Před 4 měsíci

    Mumene tayambira sizikuyenda sizikuyenda iye akukhuta osatenga action bwanji amalawi