Fredokis has no level, The guy is a genius, i like the way he answered the giving in front of a camera allegation. Oooooh Men..Fredo to the kiss kiss, fredo to the mwaaah!
Brilliant interview non bias. Komano mudziika ma caption achizungu kuti Africa idimbvanawo zantchito zanu zabwinozi, kuthetsa neocolonialism and injustice.
The fact is we are not leaving in those old days,if the community needs his help he must do it,they have tried to reach out to those who call themselves mps but at the end of a day they are ignoring so,please let the boy shine,this thing you call respect,respect goes to people who deserve it,especially to those who hear thier people crying
Mafuso anu salibwino inu muli ngati ma doctor ena amene amadikira munthu akadwalika mkumati tidikile report la kupolisi afredo siokula mtima chifukwa nayeso ali ndiufilu ofusa ndipo muli udindo omuyankha chifukwa mene mukunenela kuti he can't ask you any questions where did get for example munthu wina asikumenya ine ndiye ndibwele mkumakuuza inuyo kuti musamabwezele kwayinuyo mungave bwanji wina azimenya inu kungo imakkkkkkkk😃interview yanu pamenepo siyikuyenda
Ndipo program imeneyi sindikuyimaliza how can be honest fredo to be not ask any questions how fix your system get me well what imeans all those tifayisa mabomba fire mabomba fire mabomba 👆
How many of us are watching this episode in 2024?😊😊😊
Frodokiss is genius and I love him so much Big up 👆 Big😅
Very powerful Freddo,,showing the wisdom of God,,all the best Son
My favorite artist
I will vote for u aise from Lilongwe will go ku BT malume
Fredo is genius
Wow Fredo !!! I like this 100%
Fredokis has no level, The guy is a genius, i like the way he answered the giving in front of a camera allegation. Oooooh Men..Fredo to the kiss kiss, fredo to the mwaaah!
Uku ndi kuyankhula vomveka kwambiri. Nchana ndamuva bwino kwambiri ndi woganidza mwanzelu ndiyambaso kumutsata mma programme ake❤❤❤
Ma nigga your mind set is on point and let your endeavors come to manifestation
Keep it up dear
Your future is brighter 🎉🎉
Brilliant interview non bias. Komano mudziika ma caption achizungu kuti Africa idimbvanawo zantchito zanu zabwinozi, kuthetsa neocolonialism and injustice.
Great job
🔥🔥🔥🔥🔥🔥umakwan fredo
you are good fredokis
Keep up fredo ❤❤
Fredo 🔥
I like you bro and love your advice
Keep it up Mr Kalua
Respect
Fredo ❤
The fact is we are not leaving in those old days,if the community needs his help he must do it,they have tried to reach out to those who call themselves mps but at the end of a day they are ignoring so,please let the boy shine,this thing you call respect,respect goes to people who deserve it,especially to those who hear thier people crying
Oky Fredokiss Ndi ginius pa yekha
Fredo iweyo ndi mbambande ulemu wako I salute 👏👏👏👏👏👏👏👏👏👏👏👏👏
IT IS MUST TO LET YOUNG TO GROW AND LET THEIR VOICE TO BE HREARD
Well spoken 😂
Ntchana ndiwe katundud zoyamwila ka Mr Kamlepo. Iwe ku utm kukukhaladi big up
Mikozi hahahahaha! Fredo ndiwovutitsa eti kkkkk
Genius Fredokiss
ilike it fredo morefire
Fredo iwe ndi ntchana aixe👏🏿👏🏿👏🏿👏🏿
i like Fredo and Black Nina😍
Plato said, "If you don't participate in politics, you let fools rule you"
elderman represent, anyamata ake nde ifeo
Big up man fezo kuyankha mwachimuna
Sitimaganiza ndi tsitsi timaganiza ndiubongo 🔥🔥🎉🎉
😂😂😂 tell him the brain in not hair 😂
Inspired
Good boy
Just take leader of president of UTM yachinyamata
Fredo nd dolo
Fredo is a genius seriously. I have learned a lot from this interview.
🤣🤣🤣 Koma fredo ulindi mbalume muthu modzi omweyo kukhala father, brother uncle komaso utha kukhala bank manager........umatha iweyo uli bho kwambili fredo
Ndimvele timamafira Fredo apa😂 salute
Mn wa amandiyimbira bwino nsaname kma musamaphwekese pa Dstv mumatiyimilira ndipo timamva kukoma tikamaonera nyimbo zanu zosachititsa manyazi
Kuyankha mwa nzeru, komanso mwautsogoleri
Nice dada
RIP CHILIMA
Umatha iweyo fredo
Fredo ndi Katswili guys
Mafuso anu salibwino inu muli ngati ma doctor ena amene amadikira munthu akadwalika mkumati tidikile report la kupolisi afredo siokula mtima chifukwa nayeso ali ndiufilu ofusa ndipo muli udindo omuyankha chifukwa mene mukunenela kuti he can't ask you any questions where did get for example munthu wina asikumenya ine ndiye ndibwele mkumakuuza inuyo kuti musamabwezele kwayinuyo mungave bwanji wina azimenya inu kungo imakkkkkkkk😃interview yanu pamenepo siyikuyenda
Ndipo program imeneyi sindikuyimaliza how can be honest fredo to be not ask any questions how fix your system get me well what imeans all those tifayisa mabomba fire mabomba fire mabomba 👆
Presenter wopusa ameneyu
Team Fredo basi mtchana
Kusapetsa tsitsi ndi ndale zikugwirizana bwanji nawe funso lakolo lakale kale kwabasi 🙈🙈🙈🙈🙈🙈🙈🙈
"anthu onse okuba amameta momwe mwametela inuyo mo" lol
Osamatero dolo iwe maonekedwe apusitsa sorry
Mumakwana fredo
Kuno ku cape town 💥💥
Kwatani
Fredo tili nawenawe ntchana mpaka zitheke zofuna zanu
interviewer umalemba chani?
Ntchana ndimakufirani
Fredo akukuyenda mmbali mpka kukufusani nkhani yometa mmbali
Timafila freddo
Ur talking sense boy
ntchanaaaaa!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!
Choka evil inakupweteka iwe iyah
Simuma ganiza ndi tsitsi 🇲🇼kkkkkkkkkk
Kkkkkkkkkkkkkk giant
Osadikila matenda akule ndikumapititsa ku chipatala fire nchana
Umakwana big
Umakwana tchana
Ntchana ndimakufirani 11:00
Ntchana
Umandibowa bwanji mxiiieee 😠😠😠
Koma presenter wantundu wanji uyu🤣🤣🤣🤣
Kkkk ndiwokula mtimatu
He is not proffessional at all
Ambuye musalole chipan Cha evil kt chiwine in mighty name of Jesus Amen 🙏🙏🙏
next time find a proper interviewer not chour master ameneyu
Nonsense, kulankhula mopusa kwambiri iweyo udzakhalapo 2063?
Ntchana ndimakufirani
Ntchana
Koma ofusa mafusoyo ndimbuzi yamunthu
Ntchana ndimakufirani
Ntchana ndimakufirani