Velikost videa: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Zobrazit ovladače přehrávání
Automatické přehrávání
Přehrát
I’ve loved watching this one with Nep. He has so much respect for others even in his drunk state he kept balancing them…. 👏👏…. And his voice….. 🫡
I see maturity in him, he respected everyone in the industry!!!
He served any artist as his brother and sister,, nice game indeed
Nep ndiwozindikila kusafuna kudana ndi anthu kulibwino azimwa kusiyana nkudana ndi anthu big up my big bro
Zoona
Nepman deserves "One Must Go " 😂😂😂😂
Artist yemwe wazinda bwino mafuso wopoila ndi Nepman...big up
We need to have artist like nep man mafuso onse odanisa watankha bhooo even atayaka❤dolo
This is the best episode of truth or drink currently mumachedwa naye kuti uyu
Its Chitani Chakumwa for me😂😂😂😂😂😂😂
I have liked his behavior even if he was drunk but was calm and controllable.
Fruitful conversations, Nepiala sense amagaya kudos
Our Malawian legend Nepman ,,I feel your song ngona za mumabango❤❤❤❤❤❤
😂😂😂One must GO! Eeh!
i love the maturity thing in Nepman
Nepman is great artist, he has a very unique voice koma amalakwisa zotukwana
This is great 🔥. Keep it up! Tidzicheza nawo chonchi alusowa 🙏
Kkkkkkkk another level, chitani chakumwacho
Thilani chakumwa ndalephela coz ndabwela kuzamwa ine ,respect 🔥 kuyankha mafunso mwanzelu big up mowa uja osazaunamizila ma guy
Best truth or Drink ever
1 must go nde ilibwinotu😂😂😂Artist yekhayo osakakamiza ndi nepman
🤣🤣🤣🤣🤣🤣 nep u r the best 😜😜
Madala Nep ndi anzeru amwene , mayakhidwe abwino heavy💥💥💥💥💥💥💥💥
😂😂😂😂 I am failing even 😂😂😂😂😂😂😂😂
Koma zomaika tinyimbo Tanu kumayambililako sizowaza..anthuwo si akuyenela azikhala ngt akukakamiza zinthuz noo..Anyway tionele
Interview yobebe iyi nepman osanyozapo munthu 🔥
Artist wokhwima pa liwombo uyu
@@user-sk7qh3kd4i kobasi zikakhala bwino kumayamikila ndithu
This guy is genius
Truth or drink iyi ndimachedwa Kuti❤️❤️❤️❤️nepizo eee wabhebhetsa ngat Jetu ndi k banton
nep umatha osanyoka or pangono pokha ngakhale utaledzela umakwana braz salute
Nepman amasunga ulemu yooh
Aaah! Koma guys 🤣🤣! Ine I am confident mkunda wa Brandy I can finish, Any Brandy
Haha Nepman has made history
Akev mumpweteketsa gulu jkkkjj ati ine nsakhale ngati ndukhomelera😂
He's a classified guy. 💥💥
Nepman umakwana......ati kumeneko nde kuthako😂😂😂😂 Koma ndaseka
Drunken master 🔥
Nepman nd German pump ya 6 cylinder ya ma norzal
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣Nepman wadabwa mpaka kufuna kuziwa zakuchipinda wadabwa nanu kkkkkkk
I like Nep akumapanga respect wina aliyesr
Koma sindinanjoyepo Truth or Drink kuposa ya madala awawa, akudziwadi chomwe anabwelera🤣🤣🤣🤣
Aaaaa Ivo waika kkuyamba vach wataya mtu asa😂😂
Nep Man is Authentic
Thilan Fuso ndalephera ili kkkkkk❤ Koma nepia longwe😂😂😂😂😂
one legend at a time..nepia amakwana
Nepman exposing ndirande😂😂😂
Best of the best
ati ndabwelera ma shot...koma mowa wamupha NEPMAN😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
One must go 😂
Chomwe ndabwerera ndi mashot, tachitani😂
sanabwele kuzanyoza muthu km kuzalezela mowa😂😂😂
I chichi China bwerad kuzamwa mowa😂😂😂😂
Program ili hot 🔥 Koma mutisakileso Madala - Maffo
Nepman killed the show.
Timawonera ma show onse ife kunena zooona mparibe angafikepo wamwa mmowaa adaa bro...nep man ndiwachabe😂😂😂😂
Uyu nde ntonga weniweni chakumwa timwe 🍺
Nkhani yamunyasa ndiyakuchipindayo Nanuso muzioa ndiathu ake owafusa zimenezo apo munaonjeza kwambili Nep mani ndiwankulu sumunayenera kumufunsa zimenezo
Mafuso ena ndi wopoila bas dziko lonse liziwe zaku chipinda kwako
Tili pa one must goo😂😂😂
Umakeana nep number one palibeso mowa simadzi
NEPMAN 🔥🔥
Episode iyiyi 🔥🔥🔥 Nepman ndidolo
Patseni coca wadabwa nazo😂😂😂😂
Kma Nepman ndidolo pakhan yamowa
Truth or drink yothamangira nthawi 😂😂😂
Anabweladi kudzamwa mowa uyu 🙌🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Uyu azatiphera ma artist uyu shaaa..Nep akati thiran chakumwa ine ndat aaaaah😢
kkkk koma nep ndi dolotu 🔥🔥🔥😂😂😂
madhala inu ndi one zikanakhala ziwili🤣🤣🤣
Wabwela Ku amwa mowa😂😂😂😂
One must go yemweyo😂😂😂😂😂
Ati uwu ndithile ndekha😂
at ine2 musandinvele chison ndabwela kuzamwa thilan
Nice 👍
madhala anaabwela kuzautunga eeeeh hahaha ndi zitsulo
Inuyo mwafunisitsa kudziwa za kuchipinda kwanga😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 mwandionjeza
Mowa ukanatha show ikanali mkati
Koma pangani zoti anthu azidya nsima anthuwo azimaliza botolo lonse akankhuta 😂😂😂 defiya wadandaula anakangwetsa botolo anakankhuta 😂😂
Mwalowa mkati a jaa kev😂😂
ati kodi mwayamba kujambula😂😂😂😂😂
Koma anazuka bwino uyu 😂😂😂
Umakwanila nep Ndirande sisunga kape
koma mowa si madzi akulu akulundimawona ngat nepia saledzera😂😂😂😂😂😂
Mupweteka anthu ndimowa.....
This show belongs to Madness Entertainment. How come it's not on their channel? Kapena mwachita kuba
My question too
ineso ndikudabwatu
Exactly my question
Aba kumene. They must be reported
@@andrewmazunda3846Sanabe even ku channel yawo kulibe
Nepman anafika ndimatukutuku . Wayakilatu apa 😂😂😂
Kom akundivesa cisoni kwambili 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Nepman ndi akatundu koma muli respect
Achimwene Anga.....Anakonza safuna ..kudanisa Anthu ife Ana Amu ghetto.....timatha.......Anakakhala mugapo Jemson....yo umatha Kelvin❤.....iweyo ndi 1😂😂
Home boy😂😂😂
Imeneyo yokha chitan chakumwa🔥🔥🎯
Big up🎉 nepizo😍😍😍😍
Ma Philadelphia umakwana nep
Koma Nepia wayankhako funso?🤣🤣🤣🤣🤣
Mwachiongolero momweMo basi😂😂😂
Kma adaaaaah 😂😂😂😂😂
Kkkkkkkk ase umayesa 😂😂😂
kunamwedwa ukuku eeeeh eeeh............ ankolo nkhope mpana kunyezimila ndithu
Komano nyimbo yojamayo ikutanipo kev 🤔
Munakati Jetu ndi Najere😂
NEP adzilephera dala,cholinga aumalize,,,,big up nep
Osamazasewera ndzidakwa ndthu 😂😅
😂😂😂😂mu ndilande ma corn flakes otapitsa???😂😩😩 I'm relocating iiiih😩😩😩😂😂😂
Ndirande anakonza😂
Wangopitil mow aaà
I’ve loved watching this one with Nep. He has so much respect for others even in his drunk state he kept balancing them…. 👏👏…. And his voice….. 🫡
I see maturity in him, he respected everyone in the industry!!!
He served any artist as his brother and sister,, nice game indeed
Nep ndiwozindikila kusafuna kudana ndi anthu kulibwino azimwa kusiyana nkudana ndi anthu big up my big bro
Zoona
Nepman deserves "One Must Go " 😂😂😂😂
Artist yemwe wazinda bwino mafuso wopoila ndi Nepman...big up
We need to have artist like nep man mafuso onse odanisa watankha bhooo even atayaka❤dolo
This is the best episode of truth or drink currently mumachedwa naye kuti uyu
Its Chitani Chakumwa for me😂😂😂😂😂😂😂
I have liked his behavior even if he was drunk but was calm and controllable.
Fruitful conversations, Nepiala sense amagaya kudos
Our Malawian legend Nepman ,,
I feel your song ngona za mumabango❤❤❤❤❤❤
😂😂😂
One must GO!
Eeh!
i love the maturity thing in Nepman
Nepman is great artist, he has a very unique voice koma amalakwisa zotukwana
This is great 🔥. Keep it up! Tidzicheza nawo chonchi alusowa 🙏
Kkkkkkkk another level, chitani chakumwacho
Thilani chakumwa ndalephela coz ndabwela kuzamwa ine ,respect 🔥 kuyankha mafunso mwanzelu big up mowa uja osazaunamizila ma guy
Best truth or Drink ever
1 must go nde ilibwinotu😂😂😂
Artist yekhayo osakakamiza ndi nepman
🤣🤣🤣🤣🤣🤣 nep u r the best 😜😜
Madala Nep ndi anzeru amwene , mayakhidwe abwino heavy💥💥💥💥💥💥💥💥
😂😂😂😂 I am failing even 😂😂😂😂😂😂😂😂
Koma zomaika tinyimbo Tanu kumayambililako sizowaza..anthuwo si akuyenela azikhala ngt akukakamiza zinthuz noo..Anyway tionele
Interview yobebe iyi nepman osanyozapo munthu 🔥
Artist wokhwima pa liwombo uyu
@@user-sk7qh3kd4i kobasi zikakhala bwino kumayamikila ndithu
This guy is genius
Truth or drink iyi ndimachedwa Kuti❤️❤️❤️❤️nepizo eee wabhebhetsa ngat Jetu ndi k banton
nep umatha osanyoka or pangono pokha ngakhale utaledzela umakwana braz salute
Nepman amasunga ulemu yooh
Aaah! Koma guys 🤣🤣! Ine I am confident mkunda wa Brandy I can finish, Any Brandy
Haha Nepman has made history
Akev mumpweteketsa gulu jkkkjj ati ine nsakhale ngati ndukhomelera😂
He's a classified guy. 💥💥
Nepman umakwana......ati kumeneko nde kuthako😂😂😂😂 Koma ndaseka
Drunken master 🔥
Nepman nd German pump ya 6 cylinder ya ma norzal
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣Nepman wadabwa mpaka kufuna kuziwa zakuchipinda wadabwa nanu kkkkkkk
I like Nep akumapanga respect wina aliyesr
Koma sindinanjoyepo Truth or Drink kuposa ya madala awawa, akudziwadi chomwe anabwelera🤣🤣🤣🤣
Aaaaa Ivo waika kkuyamba vach wataya mtu asa😂😂
Nep Man is Authentic
Thilan Fuso ndalephera ili kkkkkk❤ Koma nepia longwe😂😂😂😂😂
one legend at a time..nepia amakwana
Nepman exposing ndirande😂😂😂
Best of the best
ati ndabwelera ma shot...koma mowa wamupha NEPMAN😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
One must go 😂
Chomwe ndabwerera ndi mashot, tachitani😂
sanabwele kuzanyoza muthu km kuzalezela mowa😂😂😂
I chichi China bwerad kuzamwa mowa😂😂😂😂
Program ili hot 🔥
Koma mutisakileso Madala - Maffo
Nepman killed the show.
Timawonera ma show onse ife kunena zooona mparibe angafikepo wamwa mmowaa adaa bro...nep man ndiwachabe😂😂😂😂
Uyu nde ntonga weniweni chakumwa timwe 🍺
Nkhani yamunyasa ndiyakuchipindayo Nanuso muzioa ndiathu ake owafusa zimenezo apo munaonjeza kwambili Nep mani ndiwankulu sumunayenera kumufunsa zimenezo
Mafuso ena ndi wopoila bas dziko lonse liziwe zaku chipinda kwako
Tili pa one must goo😂😂😂
Umakeana nep number one palibeso mowa simadzi
NEPMAN 🔥🔥
Episode iyiyi 🔥🔥🔥 Nepman ndidolo
Patseni coca wadabwa nazo😂😂😂😂
Kma Nepman ndidolo pakhan yamowa
Truth or drink yothamangira nthawi 😂😂😂
Anabweladi kudzamwa mowa uyu 🙌🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Uyu azatiphera ma artist uyu shaaa..
Nep akati thiran chakumwa ine ndat aaaaah😢
kkkk koma nep ndi dolotu 🔥🔥🔥😂😂😂
madhala inu ndi one zikanakhala ziwili🤣🤣🤣
Wabwela Ku amwa mowa😂😂😂😂
One must go yemweyo😂😂😂😂😂
Ati uwu ndithile ndekha😂
at ine2 musandinvele chison ndabwela kuzamwa thilan
Nice 👍
madhala anaabwela kuzautunga eeeeh hahaha ndi zitsulo
Inuyo mwafunisitsa kudziwa za kuchipinda kwanga😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 mwandionjeza
Mowa ukanatha show ikanali mkati
Koma pangani zoti anthu azidya nsima anthuwo azimaliza botolo lonse akankhuta 😂😂😂 defiya wadandaula anakangwetsa botolo anakankhuta 😂😂
Mwalowa mkati a jaa kev😂😂
ati kodi mwayamba kujambula😂😂😂😂😂
Koma anazuka bwino uyu 😂😂😂
Umakwanila nep Ndirande sisunga kape
koma mowa si madzi
akulu akulu
ndimawona ngat nepia saledzera😂😂😂😂😂😂
Mupweteka anthu ndimowa.....
This show belongs to Madness Entertainment. How come it's not on their channel? Kapena mwachita kuba
My question too
ineso ndikudabwatu
Exactly my question
Aba kumene. They must be reported
@@andrewmazunda3846
Sanabe even ku channel yawo kulibe