I love this guy I like this guy to be a leader of Malawi president I think Malawi.can be changed this guy looks like honest god open the way to him to read us god bless Malawi
Thumbs up the VP and don't end there gwedezani mose ngakhalenso ku ma office a ma civil servants gratuity mmene anawerengerera 2022 kufika lero ndi yomweyo ,,zofunikanso kukambirana
Manganya is sturbon, you can't interfere and influence in the decision making of someones office, the issue here, he is acting on the information which the people are feeding him, koma that is totally wrong, he was supposed to seat on the visitors seat not there, again, he is trying to put pressure on that accountant, I believe he is aware that this man is a professional si mbuli and he is holding a high office so respect is needed asaiwale so kti this guy is a permanent employee and him, his job will end next year
My vice president..... Time is not in his side he just trying to make alot of allowances by creating visits ongowononga ndalama koma sathandiza kalikonse Ku dziko lino iyayi ndi nthawi yanu.masiku tikuchosera away.tikuthothani ndi voti
We to support the vice president he doing we.goverment workers are not helping to develop the country it must stop.Mr Usi can you go and sort out immigration officers as as possible.
The ESCOM guy knows his stuff, u can tell from the confidence and the content presentations,KEEP IT UP
He was very composed
If Usi can be in the office just for two years Malawi will change believe you me my fellow malawian's.
❤❤❤ vp woyeeeeee ineso chimozimozi ndinalipira 2021,pakanapano sanandiyikile , gwilani ntchito bwana wanga mulungu azikuthandiza,
Koma akanabwera kwathu kuno ku mangochi
The accountant is well knowledgeable. I like his confidence 🔥🔥🔥🔥
Mcp take care with this guy if you think u can use this guyz forget about that its a simple guy but taff in mind keep it up Bambo a Sikono
Pena ndikumazimva ngat tidaluza zinthu, boma la chilima ndi abwanawa likadakhara labwino ndithu
This man needs to become president don't look him down
Keep it up Mr VP this is what we need
Dr Usi he deliver, whatever your political party is, but this guy is doing good work for Malawian keep it up Dr Usi
Tikuferanji yabeba 2024😅😅😅😅
😂 😂 😂
Akusankha ma office ophweka, chomwe sakupitira ku immigration ndichani komwe anthu akuzuzika kwambiri?
Akumuwopa ng'oma
Because immigration woes are chakwera’s, his son and Mumba made so he knows
Step by step 🪜 neer worry 😁 kk
Munthu wangoyamba kumene, sangayambire zomwe mukuganiza, ali ndi work plan
Koma ine ndi kuona kuti kwanzeru nkumeneku amationjeza a escom
You can't do everything once
that's greatest work in the country of malawi
I have started liking this guy
I love this guy I like this guy to be a leader of Malawi president I think Malawi.can be changed this guy looks like honest god open the way to him to read us god bless Malawi
The way this guy looks at Manganya eeeh, ngati angomupatsa chi mbamaa.😅
Thumbs up the VP and don't end there gwedezani mose ngakhalenso ku ma office a ma civil servants gratuity mmene anawerengerera 2022 kufika lero ndi yomweyo ,,zofunikanso kukambirana
Anthu akufuna mupite Ku immigration mwachangu makamaka pa Mzuzu.
Anthu aku immigration akalakala kulowa pansi
mfanayo ntchito akugwira mwa chilungamo kkkkkk keep it up bro
Great work Mr president
I like what Mr vice president is doing. Eya agwedezedwe asamaiwale Kuti Ali apo chifukwa chaife.
Nice comments love it.
Uyu Michael Usiyu amafunika adzigwira ntchito ndi boma lilironse lingalowe coz this is stunning
Bwana ntchito mukugwira keep it up
Wow that's fantastic, keep it up don't fear any body you are there for the benefits of Malawian and you make me feel better
Manganya keep up good work do the same to forest,and water sources
We are appreciating your work our VP, that's what we need. Thank you.
Keep it up tsiku Lina mukasuzumireko ku NRB uko kuliso vuto
Inu escom ndimanyaga ine ndinalipila magedzi 2021 paka pano koma anthu akumanga nyumba mwezi umodzi kuwalumikizila magedzi
Nice work vp
Dr michel mumatha tavutika kwatha ndinu mayankho anthu
Bwana muzafikeso ku mzuzu Escom ndinalipira 2019 mpaka pano sanayikile magetsi
Vice State Presedent Dr.Usi, keep it up. Malawi is in a rut professionally.
Izi zokha nduzikonda izi Vp mukugwira mtchito keep it up
Keep it up Usi
Manganya is sturbon, you can't interfere and influence in the decision making of someones office, the issue here, he is acting on the information which the people are feeding him, koma that is totally wrong, he was supposed to seat on the visitors seat not there, again, he is trying to put pressure on that accountant, I believe he is aware that this man is a professional si mbuli and he is holding a high office so respect is needed asaiwale so kti this guy is a permanent employee and him, his job will end next year
Mukanauuza kuti aliyese amene analipila magesi kale kale ayikilidwe magesi pasanathe mwedzi
Vp good development and I like it 👍🔥🔥🔥🔥
Mupitenso ku immigration Mr VP
Good development bwana,I really like you.
❤good job mr vp izizi zomwe amphawife tikufuna chifukwa anthuwa amatailira kwambir
VP mukamatelo anthu aziopa kuchita zinyengo, so Malawi akhuza kusintha kathawi kochepa, well done 👏
I like the guy wogwira ntchito_yo, anali pa easy ..... Nice
So you like what? Can you elaborate 🤏
This is what we need
Go head 💪💪💪💪💪💪
The guys has a magufuli's character
😂manganya is learning how to capture the data kkkkkkk
Better than the president
Chief accountant 🔥. Big man
Keep it up bwana vc.please don't stop this business maybe Malawi can change for the beta
My vice president.....
Time is not in his side he just trying to make alot of allowances by creating visits ongowononga ndalama koma sathandiza kalikonse Ku dziko lino iyayi ndi nthawi yanu.masiku tikuchosera away.tikuthothani ndi voti
Keep the fire burning Mr vp🔥🔥🔥
Izizi zikanayamba 2020 ija malawi bwenzi ali pena
Boma linayamba kugwila nchito. Kwathu kuno zachibwana zedi🇿🇲🇿🇲🇿🇲
Ine ndinalipira mchaka cha 2020 mpaka pano sakudzandimangira.escom ndilibe nayo mawu
Fighting for poor malawians , keep it up chief ,
My fellow accountant ... shaaaa wabvatu
I hope this supervision, will lead to the good management of the company.
Mbambande Mr vp......amationjeza ma guys mma ofesimu...amatitenga ife a Malawi ngat opepera....gwirani ntchito bwana
Zinazo addressing the wrong office
Vp is cleaning Malawi wow what a nice job
Keep it up Dr Usi
Nice job
eish mawa bs ndikupita ku escom kukapanga apply ichichi chitithandiza di amalawi💪
Honestly Michael usi ndamufila heavy,mukuitha bigy
Great job a Vice President
The follow up is a good idea some
civil servants are lazy people.
Good job mr pitilizani
Ntchito ilipo muzingo konzeka m'ma office, good job !😂😅
Muzabwereko kuno ku mzimba enafe nalipira kale sinzikutheka sakutiyikila ma gesi
😂😂😂😂😂
The confidence is just too much bro
3 million yanga mpaka pano magesi ndilibe
Good development VP
Guys ndimaona ngati manganya ndi kape koma pano ndasimikiza kuti ndi dolo
Mumaona ngati Chakwera opusa kusankha Dr Usi aka Manganya.
Wina alakalaka kuthawa ntchito
Bwana VP mukapitiliza kuyendera ma department osiyanasiyana,,i hope mu dziko muno katangale akhonza kutha
Zantchito Machine Katundu Madzi
Go dipper Mr vice president anthuwa akutikwana kwabasi specia nkhatabay nayoso yanyanya kwabasi zisathele kumwela kokha ayi kumapitaso ku mpoto
Athu amenewo mmmh bola mwawayakhula eeshiii kulipila magesi koma nkukhalaso kapolo wowayendera amakonda chinyengo too much
We to support the vice president he doing we.goverment workers are not helping to develop the country it must stop.Mr Usi can you go and sort out immigration officers as as possible.
Keep it up bwana
Good work chief
Kukoza dziko ND komweku uku
Good leader ship Bwana Usi
Please, visit more institutions. They do delay payments of suppliers.
Ali ndi nzeru mkuluyu keep it up mwina ma service ena atha kusinthako
Good job keeping up
Your doing great job mr vp
Pitilizani aUsi zaonjeza chilipilireni kale kale mpaka pano akuwalumikizila wolipira kumene
More to fire ,there taking long to give us magesi
Uyu chief accountant akuyiziwa ntchito ,no pressure poyankha
Well done Mr VP
We need vp like ussi 4ever
Lero manganya sindimunena naga nkhani ya Escom eeee 🙌🙌🙌🙌achita bwino kupitako anthu awa akutinzunza kwambiri Kaye akati magetse azima eeee mavuto samakuthandiza nsanga 😊
That's why I will never trust any politician you do come like God Saint,deep down your heart you hv different plans
Ntchito yabwino boss man
Koma izi xinalikuti thawi yonse
Keep it up Mr usi😅
Odya zake no mlandu
Pitaniso Ku migration Kuma passport uko ziyemde bwana anthu asagone Ku Lilongwe
Bravo Mr Michael Usi
Uyuyu tikuferanji tisiye uko antha kusitha malawi
Umayitha ayaruke 😂😂
zeru zokha zokha❤