LIMPOPO FM 20 JUNE 2024NDI COMRADE NTANYIWA CHIGAWO CHAKU MADZULO

Sdílet
Vložit

Komentáře • 291

  • @MorrisMapiri
    @MorrisMapiri Před 6 dny +1

    God is coming soon to judge this world, this is reminder to everyone who has hunger for power.

  • @daviebrasil4480
    @daviebrasil4480 Před 7 dny +3

    Ntchito ilipo ku malawi ndipo yehovah ana muuza kain kuti ndamva kufuula mwazi pomwe pagwera mwazi wamunthu sipanama

  • @spargomw
    @spargomw Před 7 dny +5

    Ntanyiwa🎉🎉🎉🎉🎉 muzibwera kawiri patsiku mokupemphan😂😂😂😂😂

    • @EllinaBitto
      @EllinaBitto Před 6 dny

      Kawiri patsiku kakuchepa mthanyiwa❣❣❣❣❣❣❣❣❣❣❣❣uzibwera after 2 hours

  • @EllinaBitto
    @EllinaBitto Před 6 dny +2

    Everyday ndizikhala pa limpopo fm😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭

  • @SamukLungu-zg7fl
    @SamukLungu-zg7fl Před 7 dny +6

    Ngati sinina vere program iyi sindimakhara mosangarara chifukwa nimava zenizeni

  • @Happ2y
    @Happ2y Před 7 dny +4

    Kkkk kma guys limpopo fm and bakili muluzi TV and Mr born kalindo ndi MA akulu akulu apa malawi ndinu MA big 😂😂

  • @twavysibale4751
    @twavysibale4751 Před 7 dny +4

    Koma mtanyiwa becaréful,..dnt trust anyone...we value you bro, you're our eyes,..ena akhoza kumatumidwatu...just be careful,..

  • @originalblack100
    @originalblack100 Před 5 dny

    Comrade you are the best. Investigative, informative and truth. Tikuyamika boss.

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b Před 6 dny +2

    Ntanyiwa woyeeeeeeee usadzafe ntanyiwa Mulungu adzangokutengani mlenga mlenga. Ayaluka anthu amenewa. pa dziko lapansi palibe chinsisi Mulungu akukantheni ndithu anthu nonse munapanga chiwembu chimenechi ndipo mizimu ya anthu wonse munawaphawa idzakhala ikukusowetsani mtendere kulikonse mutadzapiteko idzakhala ikukusowetsani mtendere moyo wanu wonse

  • @TonyOkoibedi
    @TonyOkoibedi Před 6 dny +2

    Ndipo live Ntanyiwa tikungodikila kuulutsa mavot tinavota tsiku loikadi chilima M C P inakwililidwadi

  • @BisonJackson
    @BisonJackson Před 6 dny +2

    Mulungu akutetezeleni anthu Ngati inu mutakhalapo angapo mumalawi muja chakwela mukhoza kumuchotsa 2025 isanakwane mmmn galu aneneyi wawonjeza

  • @MebleNgulinga-hi6rg
    @MebleNgulinga-hi6rg Před 6 dny +1

    Apatu Chilungamo chioneke basi çause its painful mene mwachotsera moyo wanzanu ujaaa so sad so painful 😭😭😭😭😭 Mulungu alowererepo

  • @EmmanuelGasiten-fo5dr
    @EmmanuelGasiten-fo5dr Před 6 dny +2

    Kalikonse tikaona. Following from BLK

  • @user-wu4tl2yn9e
    @user-wu4tl2yn9e Před 7 dny +3

    Likangolowa boma Lina likubwelali limpopo fm izakhale yaboma basi

  • @Amgwagwa
    @Amgwagwa Před 7 dny +3

    Kkkkk koma alimpopo umafufuza aiseee😮😮😮

  • @DavidJackson-ox4xm
    @DavidJackson-ox4xm Před 7 dny +1

    The best Radio station in southern Africa.

  • @mariamahamadu8402
    @mariamahamadu8402 Před 7 dny +1

    😭😭😭😭😭 nkhani yo mvesa chisoni kwabasi dzowona kukamvotela chakwela nanga taonani Lero Achakwelatu koma Atha anthu kumalawi chigawenga chakumpa ndichilombo

  • @BenissoneErnesto-eh6zs
    @BenissoneErnesto-eh6zs Před 7 dny +2

    Welcome back Limpopo

  • @user-cv3zw9ic6d
    @user-cv3zw9ic6d Před 6 dny +3

    Komansotu Antanyiwa musamalensotu mwina uyu amutumanso kutiakufufuzeni ngati akufuna kukupatsani imfomationa akufuna kuti akupezeni mosavuta plz brother ife tikudalira inu

    • @cynthiakananji1608
      @cynthiakananji1608 Před 6 dny

      Aaaa uyu sangamupeze akunama awawa amunamiza kanyimbo kakeko angokasunga yekha kapena akapititse Ku zodiac 😂

  • @braveglorymwanzagolah4899

    2 best channels ever nkhanga zaona and bakili muludzi Tv..

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b Před 6 dny +2

    Koma anthu alibe chisoni munthu anawapangila kampeni kumuphanso, sadik miya anapangila kampeni kumuphanso
    Gwenembe ndithu anapha m, bale wake chisoni ndithu shame

  • @user-wi9pe2hz7e
    @user-wi9pe2hz7e Před 6 dny +1

    Wathu wathu comrade more 🤜🤙😍💥

  • @FrancisGama-qb7ze
    @FrancisGama-qb7ze Před 6 dny +2

    MCP zoti nd chpani chokupha ife tikangonvatu pno takhulupilira ndthu

  • @AgnessMatchado
    @AgnessMatchado Před 7 dny +1

    Ntanyiwa usazafe ❤❤❤

  • @user-ob1wx4gf2h
    @user-ob1wx4gf2h Před 6 dny +2

    Dzulo mwatiudza za Malunga...lero Manganya...

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 Před 6 dny +1

    Kafukufuku wamaliro achilima sitikufuna nyau kuti zigwire ntchito imeneyi, tufuna mabungwe oziyimira pawokha komanso mabungwe akunja agwire ntchitoyi, asatana nonse muwonekera ng'amba chaka chake ndichino cha 2024

  • @user-er7ub4ug7y
    @user-er7ub4ug7y Před 6 dny +1

    Comrade ing'aluliren afiti amenewa ayaluke akakhala chakwelawo diso ngat makilere afune asafune 2025 APM bomaaaa munyanafe agalu inu

  • @nellikkmwenda7087
    @nellikkmwenda7087 Před 7 dny +3

    Ulemowanu a limpopo

  • @user-ku2fe8nb3j
    @user-ku2fe8nb3j Před 7 dny +2

    Welcome my brother ife chete kuno, ,from south africa De deur

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y Před 7 dny +2

    Chakwela gwenembe you mast go

  • @sheila5812
    @sheila5812 Před 7 dny +2

    Ntanyiwa usakhale wapereka number kwa Soldier yo,akumangitsa atha kukumanga mwina watumidwa ameneyo.

  • @IsaacMusa-py2jm
    @IsaacMusa-py2jm Před 7 dny +1

    Loud n clear here Mpumalanga,, big up💪

  • @HopesonMkomaula
    @HopesonMkomaula Před 7 dny

    Limpompo fm you are the great radio master
    I salute you my people

  • @lazarusluciano6916
    @lazarusluciano6916 Před 6 dny +1

    We've been waiting for it❤️🌹

  • @user-vl5on2lj8b
    @user-vl5on2lj8b Před 7 dny +2

    Ndipo mizimu ya anthu 9 amenewa ifinye chakwera

  • @MuhajirAnusa
    @MuhajirAnusa Před 7 dny

    Chilungamo chinenedwe basi Limpopo Radio station number one the whole Malawi more fire ❤❤❤

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 Před 7 dny +3

    Sikisinja anapha mu bale wake chifukwa cha dyera ng' ona iwe

  • @user-vl5on2lj8b
    @user-vl5on2lj8b Před 7 dny +2

    Pansi pathambo palibe chobisika chakwera ndiumbuli wakowo kufuna kukakamira pomwe usakudziwa chilichonse

  • @MichaelJannah-hn9qv
    @MichaelJannah-hn9qv Před 7 dny +2

    Ndipo 2025 yo ikuchedwatu tiwachose anyani amenewa

  • @CharlesmakveliNyirenda

    Comrade ntanyiwa yhe best always am washing limpompo fm

  • @amoschataika7440
    @amoschataika7440 Před 7 dny

    May God protect you all the time Mr Ntanyiwa. Thanks for all your info, big up.

  • @mirriamwilliam-nq9wg
    @mirriamwilliam-nq9wg Před 7 dny +2

    Bodza akupanga trace akupeza usapereke #

  • @HalimaShafie
    @HalimaShafie Před 7 dny +2

    Yomweyo galu iwe chakwera kukonda ndalama

  • @user-wp9js5vu6s
    @user-wp9js5vu6s Před 6 dny +1

    Padziko lapasi palibe chitsisi chilungamo chiwoneke ayaluka agaluwo

  • @GospelSoldiers-sr7np
    @GospelSoldiers-sr7np Před 7 dny +1

    Kkkkk more fire palibe chobitsika pansi pa thambo,kuli Yehova kumwamba sagona kapena kuwodzera

  • @WinfordGondwe
    @WinfordGondwe Před 7 dny

    Keep it up please 🙏 you are opening the eyes of the Malawians

  • @STARLIGHTGSM-cd8uv
    @STARLIGHTGSM-cd8uv Před 6 dny +2

    Komaditu zoona

  • @ZungeniBanet
    @ZungeniBanet Před 7 dny +3

    Yipase Moto ntanyiwa

  • @MPHATSOKALUWA-lm2uy
    @MPHATSOKALUWA-lm2uy Před 6 dny

    Zina zmne amanena mind you zmakhla estimated zina Nd zoti zachtka km zina amanena kut tiyembekezere zmnezozo but to say the truth LIMPOPO FM si ya masewera🔥🔥🔥🔥

  • @user-be5fc3ed1i
    @user-be5fc3ed1i Před 7 dny +1

    Chilungamo chiyende ngati madzi amalawi koma comrade ntanyiwa Inu ndi akatundu ndikamavera programuyi ndimasiya zonse kuchita kwanga kumakhala kumvesera .ndiye ndizoona magalimoto a army alowadi muziko lathu 9😞

  • @LeonardMhone-cg1tk
    @LeonardMhone-cg1tk Před 7 dny +1

    May God guide you Ntanyiwa

  • @FredlillianMbuba-sx3dd
    @FredlillianMbuba-sx3dd Před 6 dny +2

    Pitirizani kutipasila malipoti a imfa ya Chilima 😂

  • @JafaliAkimu-ll1bf
    @JafaliAkimu-ll1bf Před 7 dny +2

    chakwera ndichigawenga pamtumbo pa make ndithu

  • @PatrickSamu-kp2xf
    @PatrickSamu-kp2xf Před 7 dny

    Mumatha comrade Mthanyiwa, yomweyo galuiwe,

  • @user-lk8kj9zv6x
    @user-lk8kj9zv6x Před 7 dny

    Kuyenda ndi Limpopo simudzasowanso kumva bodza Lili lonse ikakhile kwa kuyaaaa Comrade Ntanyiwa

  • @Imraanjafali
    @Imraanjafali Před 6 dny +2

    Koma Malawi aaaa lelo Vice president ndi Michael usi akifuna tilitso or Uyu a Ali ku mcp

  • @EllinaBitto
    @EllinaBitto Před 6 dny

    More fireeeeeeeeeeeeèeeee waiting comrade ❤❤❤❤❤❤❤

  • @augustinechibbalazi8897

    Where there is lack of philanthropy and patriotism, cupidity prevails.

  • @MustafaAbdullah-pb5zv

    Mtanyiwa more fire LiLiLimpopo

  • @BacklinebwanaliBwanali
    @BacklinebwanaliBwanali Před 7 dny +1

    Zooonad zokhazokha ndipo tikufuna chilungamo chidziwike

  • @SymonZemben-gd3ne
    @SymonZemben-gd3ne Před 6 dny

    More ffffffffiiiiiiiirrrrrrrrreeeeeee🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥 I m behind you Limpopo FM akanganyawa aziwona sanati ana achepa😂😂😂😂😂🤸🤸🤸🤸🐐

  • @AnimalproductionandVeterinarys

    Aaaaa wabodza uyu akumatiphulitsa nalo bodza. Dzulo watipatsa dzina lina la vice president

  • @HedgensChisale
    @HedgensChisale Před 7 dny +1

    Mulungu akupase moyo wawutali

  • @ChimwemweKondowe-nj4lx

    May God protect you Ntanyiwa together with all good and sound activists

  • @user-xm3zl5cg6x
    @user-xm3zl5cg6x Před 7 dny +1

    Ngati chakwela amaziwa kumanga anthu abwele ku Mangochi timugawe awone ifetu ndi ana oyipa kuzindikila kwambili

  • @DoreenEmmanuelj
    @DoreenEmmanuelj Před 6 dny

    Ndikamavera waires iyi ndimakhala ndichiyembekezo Kuti Malawi asitha Zikomo ❤

  • @user-on2me8ek5w
    @user-on2me8ek5w Před 7 dny

    Ipondeni fada inuyo mum antha Abro mtanyiwa more fire❤❤❤❤❤

  • @LeonardMhone-cg1tk
    @LeonardMhone-cg1tk Před 7 dny +2

    Nkhanga lero zinasowa😂

  • @YasinMusa-ym8lp
    @YasinMusa-ym8lp Před 5 dny

    Umakwana bwan😊😊

  • @StechelectronicsRepair-qh5jl

    ❤❤❤we just waiting for the truth

  • @user-uc1pd1tc2x
    @user-uc1pd1tc2x Před 7 dny +1

    Limpopo FM NDI Bakili Muluzi tv alibeyi zibwana muyaluka nonse a MCP dziwani amalawife siopeperayi

  • @ChristinaLigomeka
    @ChristinaLigomeka Před 7 dny +1

    Choona chidziwika ife tikulila pamaso Pa Mulungu kt choona chioneke misozi yachuluka masomu, nkhalamba zikulila owagwila dzanja ndamene apitawa kuphuzitsa mwana simasewera

  • @MosesSolomoni
    @MosesSolomoni Před 6 dny +1

    Ine ndinagona palimpopo kunyumba kwa kalundo and muluzi TV bas

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 Před 6 dny +1

    Please comrades mtanyiwa, usamale ndi awa akumati alindi nyimbo yolilira chilimawa, enawa nda mthirakuwiri ngati malata, munlo, ben longwe, layitoni mangochi, agape, ana opusa kwambiri amenewa

  • @CharlesmakveliNyirenda
    @CharlesmakveliNyirenda Před 6 dny +1

    Chakwela mix apengeso ndi nyini ya monica wache yopanda kumeta mavudzi agalu awa ayaluka

  • @dumisanihara
    @dumisanihara Před 7 dny

    Mutanyiwa umakwana, more fire

  • @futurekanjanga1290
    @futurekanjanga1290 Před 6 dny

    Nyimboyi ndaifira hvy

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz Před 7 dny +1

    Abakili tidavapo zamilandu yawo koma apa wina azafera ndende ndithu plz akulu akulu ingoziphani kusiyana ndi ukaidi basi😂😂😂😂😅😅😅😅

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg Před 7 dny

    Mr Ntanyiwa ineyo sinditukwana Koma ndi mkwiyo Mr chilima RIP😢😢😢 chakwera chakwera chakwera sikulina udzaona ngelo USANA 12:30😢😢

  • @GiftManuel-er7yh
    @GiftManuel-er7yh Před 6 dny

    Salute Limpopo fm

  • @user-vl5on2lj8b
    @user-vl5on2lj8b Před 7 dny +1

    Pansi pathambo palibe chobisika chakwera wabisala m'mbatata nsana ukuoneka

  • @LiamTennessee
    @LiamTennessee Před 6 dny +2

    Comrade could you please hit my inbox your song is ready

    • @clubjunta
      @clubjunta  Před 6 dny

      +27822885847 tumiza pa WhatsApp

  • @dysonfysonchifundo2284
    @dysonfysonchifundo2284 Před 6 dny +1

    More 🔥🔥🔥🔥

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz Před 7 dny +1

    Kkkkk yomweyo garu iwe, iponde fadah wina asathawe😂😂😂😂

  • @user-tk6wf2eg4z
    @user-tk6wf2eg4z Před 7 dny +2

    Achakwelawa atopesa koma dairy ma programs sapuma kd ndikumacheza ndi banja lawo😂😂

  • @LeonardMhone-cg1tk
    @LeonardMhone-cg1tk Před 7 dny +2

    Ayaluka awaa ntanyiwa gwira ntchito

  • @AuspiciousKalambula-hp7gj

    Best fm ever🔥🥳

  • @SangwaniThika
    @SangwaniThika Před 5 dny

    Comrade wabwera

  • @timothyphiri2895
    @timothyphiri2895 Před 6 dny +1

    Koma apapa ineyo ndadabwa america soldiers kupita ku Zambia adakanirapo kalapotu

  • @user-vl5on2lj8b
    @user-vl5on2lj8b Před 7 dny +1

    N'chewa weni weni ndiye munthu wina nkumati chakwera boma misala

  • @KhonzoBlose-wq7zm
    @KhonzoBlose-wq7zm Před 7 dny

    Mumayitha brother Ntanyiwa timakunyadilani

  • @Carolynmzonde
    @Carolynmzonde Před 7 dny +2

    😂😂 Afiti amenewa nawonso aphedwe basi opha mzake naye so aphedwe

  • @wayafrank2405
    @wayafrank2405 Před 7 dny +1

    More than BBC ❤

  • @mirriamwilliam-nq9wg
    @mirriamwilliam-nq9wg Před 7 dny +1

    Akunama osampasa nambala uyu watumidwa akuphani ndithu be careful

  • @user-hl3vl9nt1b
    @user-hl3vl9nt1b Před 6 dny +1

    Timakunyadilani big

  • @user-ww4ei5fb7d
    @user-ww4ei5fb7d Před 6 dny +1

    Anthu ena ndi opusa kwabasi, zoona kulandira ndlama kukafera Chakwera? Kumadziwa kuti uku tikukafa, ana anga ndi mkazi wanga akhala pa umasiye, cholinga ndiike Chakwera pampando? 😢 nde adzaluzenso omuferayo 😅😅😅😅😅😅 mmmmm anthu a Mulungu, Yesu adatifera kale, osamapusa a Malawi. Mmmmmmm ameneyo ndithu adapanga chisankho chopusa. Ndiri ine ndithawa ndi banja langa ndlama andipatsanzo mkumuuza akukonzetseredwa chiwembuyo amusumire wakuphayo. Mulungu atithandize abale anzanga, moyo uwu sitikalowa nawo kumwamba

  • @IgnatiousFote
    @IgnatiousFote Před 7 dny +2

    kkkkkkkk akut ngt vitsilu padzko lonse lapansi nd ochewa

  • @KelvinJpchimphepo-sh6nc

    More fire

  • @dontreybanda278
    @dontreybanda278 Před 7 dny +1

    More fire ntanyiwa 😂 ndipo ayalukatu

  • @mustafailanga2585
    @mustafailanga2585 Před 7 dny

    Mkulu mmakwanila ndipo mmatimvesa kukoma kwambili ❤❤❤❤❤❤❤❤