If only we can deliberate over our national teasers philanthropically and patrioticallly other than provocative demonstrations,Malawi will achieve her blissful vision and missions for prosperity
Mau mau audzeni Big boy ndipo ndakodwa Nanu kwambiri tiyeni tipange zomwedzo Indeeeee opusa anaimba Ng'oma ochenjera navina azaziona ndithu Bola kuotcha nyumba yawo akuona ngati Malawi ndi amao ndi achagogo awo Big boy Moto kuti Buuuuuu🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Guys let stand for the truth ,chakwela must step down before 10 if not fire every timaoffce topusa ta mcp anthu amagazi mumanja nfiti kumampha anthu ofunilila anthu zambino
Zamaphunzirozi ndiku Malawi konkuno maiko ena amasankha munthu ngakhale osapita ku sukulu chifukwa utsogoleri si maphunziro ayi koma luntha kuchokera kwa Yehova. Za maphunziro izi ndi dyera komanso kuponderedza anthu anzeru za chilengedwe
Muwoneseni kenya kenya bas kkkkkkk anzanutu anaikidwa ku mzuzu ku zorozoro uko nthawi ya bingu marawi itakungana mpaka masiku atatu asirikari nkat kuchoka nthawi imene ija sindina woneposo mademo anzeru
Ine sindikupanga comment Koma boma likadzasintha,ngat anyani amenenewa simudzawamanga...tidzapanganso mademo kutanthauza kut it is a must kumanga aliyense anene akutizunza lero.....
Malawi muno mukukhala ngati tilibe zipani zotsusa angokhala phwiiiii kudikira kuti Born kalindo aziwamenyera campain thats not true this is time for you to rise takumbukirani momwe ankachitira a mcp ma demo amapanga daily.
Inu assemblies tabwerani muliwuze zoona dziko, kodi uyu mwati analidi m'busa? 😭😭😭😭😭😭😭😭Malawi waliratu
Basi mr bon kalindo ankhale president wa ziko ndipo ndizomwe ndikuona aaaaa❤❤❤❤
Apapa mene mcp yafikapa ofunika tonse tidzuke tikaduduze chakwela ku state house kumweko azipita kwawo kukasiya mbuzi imeneyi isatitenge ngati ife a Malawi ndife anthu opusa ai
Palibeso zoendetsa bwino kuno , achoke basi awa palibe chilimo awa
Kuyankhula zanzeru aise ndipo chakwala sindikuonela kukondwa ndipo ufe ndithu pasana pamako
Watiphela chilima pano ma radio angokhala chete kuwopa ikukamba zowona ndi social media basi museke ma radio anuwo😊
Tell them my brother listen from Zambia
Well spoken my brother amene akukhalilabe kumbuyo chakwera ndi boma lakeli ndimfiti yothelathu
Tatopa ndithu ndachakwera achoke
Amwene nthawi yomulangiza chakwera inali kale pano anytime is teatime osakhalanso za tsikulina mapeto ake atiphatonse galu amaneu akuenera kuchoka lero olo m'mawa pano
Mu m c p muli mbudzi zokhazokha za wathu
Enough is Enough we're tired, on 10 July something is going to happen , Malawi viva let's unite together
If only we can deliberate over our national teasers philanthropically and patrioticallly other than provocative demonstrations,Malawi will achieve her blissful vision and missions for prosperity
🎉🎉🎉🎉 ndipo kwambili zikwanje pa 10 komo ku pramet
Big up phalombe boy, dziko la Malawi is for every one, Chakwera akutidzolowera heavy,akuona Ngati Ali Ku church what he knows is stealing and killing
Azakhumudwa tsiku Lina chakwera Born Kalindo Ali President Tidzabwedza
Go malawi Goo!!achoke and analowela mademo mbavazi anaoipa chakwela
Apolisi opusa samalani. Musiya ana Anu chifukwa chofuna tuteteza chigawenga komanso mbava yanuyo.
Muli busy asilikali komanso apolisi kuteteza mbavazi.
10 July ndilo tsiku mulisunge apolisi komanso asilikali.
Palibe zopempha chilolezo
Go konko pa 10 pano tikaonesana konko
Koma MCP nyasi zachipani agalu kwabasi
Kodii inuu ma big boy pa 10 sipanatalike pa 29 bwanji oloo pa 30 tikhozatu oloo lero lomwe tatopa nazo ifee
Kalu ameneyu analibe chilicose koma amalawi matha kukondamoyo tatiyeni tichangamuke ngat pa Mozambique
Ndipo masoohenya abwino boni kalindo adzakhale plesdent wazuzika kwambili ndipo chakwela tikukhala ngati ku Malawi si kwathu njenje mulungu atithandize 😢😢
Amade...Amade...yakukenya ichitike kumalawi kwathu kuno phaka chakwera anyere kaya kuzipha aziphe tilimbe naye tchinto azaluza kwaoko
Amalawi tiyeni tisaope apolice nawotso apolice wo sizikuwasangalatsa tiyeni tipange ngati kenya
Mitimayathu ili Mwamba asiyeni pamene titachile mademopo opolisi tizaphana, kunkuyu zikhale ng'oma tizathana naye
I support u to put someone who is suffering now to be our future President like bon kalindo
Ukuneneska razarus must fall , Ine Kuno nanozgeka pa 10 July ,Lazarus gwenembe achoke
Ndipo mwalakhula moveka bwino president ndiomwe akuononga maiko ndithuditu tikuvuti kusauka chifukwa chama president wa
Zamveka we are tired I miss chilima for good analakwa chani?
Akutamika kumanga anzawo nthawi yawo ikubwera nawonso amagidwa kuba kupha agalu
Mau mau audzeni Big boy ndipo ndakodwa Nanu kwambiri tiyeni tipange zomwedzo Indeeeee opusa anaimba Ng'oma ochenjera navina azaziona ndithu Bola kuotcha nyumba yawo akuona ngati Malawi ndi amao ndi achagogo awo Big boy Moto kuti Buuuuuu🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Guys let stand for the truth ,chakwela must step down before 10 if not fire every timaoffce topusa ta mcp anthu amagazi mumanja nfiti kumampha anthu ofunilila anthu zambino
Zamaphunzirozi ndiku Malawi konkuno maiko ena amasankha munthu ngakhale osapita ku sukulu chifukwa utsogoleri si maphunziro ayi koma luntha kuchokera kwa Yehova. Za maphunziro izi ndi dyera komanso kuponderedza anthu anzeru za chilengedwe
Muwoneseni kenya kenya bas kkkkkkk anzanutu anaikidwa ku mzuzu ku zorozoro uko nthawi ya bingu marawi itakungana mpaka masiku atatu asirikari nkat kuchoka nthawi imene ija sindina woneposo mademo anzeru
Chakwera achoke walephera, tili kusewu koko more fire
Guys chakwela timuonese mwaziona ruto chimodzimodzi ndi chakwela akuziona ndi madolo chimunthu banda usamale
Wopha chilima aphedwesonaye,busa Wang,nombeyo
NO PAIN NO GAIN AWUZE BIG BOY BON KALINDO ONE DAY ITS ONE DAY AZAKALA PHULUMUS INSHA ALLAH
Tilikonko ku ma demo ko anthu amenewa atilowa Mchala kwabasi
Amenewo ndiye mau chakwela ndimbuzi yamuthu
Zoonadi chakwela waonjeza akupanga zamanyi ngati akuzuza buys a mkaziwake
Pa 10 gokoko more fire
Gwenembe anapha m, bale wake Chilima zachisoni ndithu😭😭😭
Sikusinja ndi yemwe adapha gwenembe. Komabe nzachisoni kuti Chilima azitchedwa kuti malemu 😢😢😢
ndipo mzoopsa guys
nsitingapange chifukwa manda kwambili tiyegalasi kuyamba kuthawa
Tatopa tatopa chakwera out ndi gululanu muchoke
Go ahead my boss I love you so much
Ine sindikupanga comment
Koma boma likadzasintha,ngat anyani amenenewa simudzawamanga...tidzapanganso mademo kutanthauza kut it is a must kumanga aliyense anene akutizunza lero.....
We coming from deference country we are ready to do!!!!!! Mr chakwela please step down we are tried with u!!!!!!!
Kodi titakhala five million angatikwanise
Uku ndiye kuswa kwenikweni😂😂
Tili konko tipange zomwe zachitika ku Kenya a malawi tisapuse anthuwa atitola!!
Chakwera walephela komaso kupha kwa Chilima anapanga zolakwika and I hurt Chakwera with passion because of the death of Chilima.
Powerful speech Big Boy
Kutelokotu chilungamo chimapweteka akuyendela iweso akumange 😂😂😂😂😂
Tikuona ndi maso athu zonse zomwe zikuchitika. Kuteroko akutitseka pakamwa by kumangana
Kenya yayambitsa kutiphunzitsa kulimba mtima
Malawi ndikumuziwa ine sangapange mademo ngat a ku Kenya
Awuzeni zowona Antalya again amenewa
Truth have spoken
Truth have spoken😂😂😂
RAZARO wadzilonda tamuuzeni watizolowera kwambiri tiyeni ku nseu basi
Yes🤞🤞🤞🇿🇦💪🏾💪🏾💪🏾💪🏾
😂😂😂 siku lina pa mpando wa u presedent pa zakhala muthu wamisa ,,,
This is only the action!
Malawi muno mukukhala ngati tilibe zipani zotsusa angokhala phwiiiii kudikira kuti Born kalindo aziwamenyera campain thats not true this is time for you to rise takumbukirani momwe ankachitira a mcp ma demo amapanga daily.
Iwe u president ungakukhale tayimilani tikuvotereni
5:43 mantha to much a Malawi,kkkkkkk......simukwanisa anzanu amachita mademo mowirikisa inuyo mungathe?aaaaaa......koma pakamwa basi
Makape a mcp 🚮🚮🚮
Chakusuzga ntchivichi iwe ?
Game on 😢😢😢😢
Iwe galubwako mpaka pampando born kalindoyo chitsilu iwe wava
Tiyeni nafe tilionese bomali amalawi maiko anzanthu zinthu zikumasitha chifukwa satsekelera boma boma liziopa anthu not anthu aziopa boma ndichifukwa chake amatizuza
Akulu akulu ndidziko lonse Izi dzikoli lingotha
Koma nde anthu mwatopadi tsopano ndakuwonan ee koma zinthu sizili bwino mkomwe ayi kkkkk😂😂😂😂😂
What are we waiting for here let's go guys
Mwa chakwera mulibemo usongoleli ,kupha ,kuba ,
Tikwapulanamo mmenemo soon
Muzikapangira kupariyametiko
Komaso wamisarayodi ankhaledi mpampando aramuliledi
Tiyen Tiyen tonse bas ulemu watha!!!!..
Thyolo mulaje phalombe zomba chikwawa sanje blatantly chilazulo usakapagiseko sokhano chakwela uziwezimenezo uzafa uli ndi achitetezo tili pano ku school timaliza pomwepano
Ndipo live kuno ku chikwawa sitimamufuna kuyambra kare
My malawi
Anthu mumafika potopa kkkkkkkkkkkkkkkkk
Enough is Enough we're tired
Chakwela fiti went weni achoke bac watibela mokwana
😅😅😅😅😅😂😂😂🎉yomweyo galu iwe Gwenembe out go go go go
Chakwera ndiwakupha kutumbu kwake
Yomweyo galu iwe😂😂😂😂😂😂
✌✌
💪💪💪💪💪
Facts
Zoona brother
💪💪💪
Komadi tikugonadi bwanji tiyeni tidzuke guyz
Ndilibe loya ine
Boma lathapo kale ili president angokhala chifukwa cha mphavu ya constitution uyu, pa 10 Pano timuyendera
Amalawi tiyen tizuke pamene Kenya yatizindikilisa kupanga zinthu nkulimba mtima. freedom is coming ... Koma mmaso mwanga ndikuona nkhondo kumalawi. 😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
ndili pambuyopo tiyeni
Chitsiru chen Chen za zii tikuziwa ndiwe ntumiki wa dpp koma enafe sitilola zautsiru uzipangira kwako komweko ku lomwe belt
Okay
Khani koma imeneyo tili limozii inu
Enough is enough now we don't want shit
Ulendo ulikodi konko.
Komanso aonadi
Auzen ❤