ZIPANI ZOTSUTSA DPP ,,AFORD ,,UTM,,PDP KOMANSO UDF CHENJELANI.

Sdílet
Vložit

Komentáře • 57

  • @sylvesteralfred8355
    @sylvesteralfred8355 Před 2 dny +10

    Ndikanakonda DPP, UDF, AFFORD akanabwera pamodzi ndikuyankhula za ma ID maka zomwe NRB ikupanga

    • @harrisbanda5891
      @harrisbanda5891 Před 2 dny

      Akuluu, asogoleli osusawa chomwe ndachiona ine ndichoti akuwopa kumangidwa ndikuphedwa nda mcp crocodile party 😂😂😂😂, funso mkumati akamawopa chomchi, amene awasogolele amalawi achokela kuti?, poti omwe timawatenga ngati m'busayu ndiuyu anayamba kutipha komanso kutikhamzikaka ndikutigoneka ndinjalayu.

    • @GospelSoldiers-sr7np
      @GospelSoldiers-sr7np Před 2 dny

      Ndipo kwambili akuyenera kusamala

  • @sylvesteralfred8355
    @sylvesteralfred8355 Před 2 dny +9

    Chakwera kudzangowina basi ngakhale otiyankhulira alerowa sadzapezekaponso ndithu chifukwa ma warning ndiye tikulandiliratu koma no any action is taken

  • @sylvesteralfred8355
    @sylvesteralfred8355 Před 2 dny +6

    Action ndiyomwe imafunika koma aMalawi ife ndizitsilu timangoyang'anira zinthu zikuonongeka

  • @user-un6qv6sj3h
    @user-un6qv6sj3h Před 2 dny +1

    Ma opposition party mukumumva mzimaiyu kkkkkk Kodi mukukhalangati akuikani mmbotolo bwanji

  • @kurhikhoza8298
    @kurhikhoza8298 Před 2 dny +1

    Zoonadi wakuva akuva monga otsutsa

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 Před 2 dny +2

    Nkhani ndiyoti tisazagwilise mavoti pokavota, tizangovota ngati momwe tinavotera 1994 opanda chawumzika , ndipo izi kuti zitheke zikufunika asogoleli osusawa kupita ku court akasume komanso a law society apangepo kanthu pankhaniyi, koma vuto ndiloti mabungwe onse omwe amayenera kumaima pawokha pano alimunkhwapa mwa crocodile party

  • @user-jw5rx9ze8k
    @user-jw5rx9ze8k Před 2 dny +3

    PDP ichotseni ndi ya Ku tonse alliance.

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 Před 2 dny +1

    A law society komanso a mec onse angokhala pheee , kumangowonelela zinthu zikulakwika mudziko lathu , nkhani ndiyoti anadya ndalama zamisonkho yathu akafucheche amenewa

  • @user-jb5yb9wq3y
    @user-jb5yb9wq3y Před 2 dny +1

    We are ready here in Lilongwe, mademo ayende basi

  • @MaxwellMbesa
    @MaxwellMbesa Před 2 dny +1

    Zoona ma leaders a opposition wake up from the your deep slumber start preparing for the election coming soon nonse otsutsa kharani pamodzi nthawi yatha mcp sikugona🎉

  • @hamiltonsolomon3756
    @hamiltonsolomon3756 Před 2 dny +1

    Mau Mau Mayi.....Ndikhulupira kuti Opposition yathu inva.zimenezi

  • @JohnJohn-og8rt
    @JohnJohn-og8rt Před 2 dny +1

    Kkkkkk zoona achakwela ndi muthu woyipha kwambili zavura zamuthu ayi

  • @Extratremendouszeus
    @Extratremendouszeus Před 2 dny +1

    Ma opposition a Ku malawi ndi ogona...ndi MCP yokha imene inali ya jack up...Ali Ku opposition...zachamba basi

  • @joebrown1158
    @joebrown1158 Před 2 dny +1

    Kodi kumalawiko kunayamba kwa khala opposition? Kodi a Tupele muluziyo kuti adzipezeka m'boma zinakhala bwanji? Chifukwa kunena zowona malankhulidwe pena pake amafotokoza m'mene munthu aliri.

  • @JosephMwambe-rz2oy
    @JosephMwambe-rz2oy Před 2 dny +2

    Kuyambilakalekale sitimavotela chaunzika ayi ndipozimenezo sizizathekaayi tizavota mmenetimavotela zakazonse

  • @user-em1qi8kj9h
    @user-em1qi8kj9h Před dnem

    Vuto ya zipani zotsutsa zikuyakhulira nyumba....sizikufuna kubwela poyera mkuima pa mbalambanda mkuyakhula angoti ziii sopano anchinyamata akufuna mtendele atulukila bwanji poyera....opposition rising up

  • @JumaKachala
    @JumaKachala Před 2 dny

    Kodi ndee inu a opposition zinthu zimene zimakambidwaziii simavera ?

  • @user-mo5od8cy3n
    @user-mo5od8cy3n Před dnem

    Munthu amene anali osaopa ndi kusunsa anali malemu Mr chilima

  • @user-dp7bc7yy6s
    @user-dp7bc7yy6s Před 2 dny

    Amwene mwalankhulana zomveka ndipo ine ndagwirizan nazo,zoti povota tisazagwiritse ntchito ID

  • @user-nr1xo1nw3z
    @user-nr1xo1nw3z Před 2 dny

    Kuyankhula kwabwino ndithu munthu wankazi

  • @MosesTangwe
    @MosesTangwe Před 2 dny

    Ndipo izi ndie zoonadi

  • @anifoiuene6301
    @anifoiuene6301 Před 2 dny

    ,Amayi dzikomo kwambiri chifukwa cholikonda dziko lathu ndiponso powadzutsa azipani zotsutsa a Malawi tichenjere chifukwatu chakwera ndi kathyali

  • @user-un6qv6sj3h
    @user-un6qv6sj3h Před 2 dny

    Komanso kodi a kalindo ndianzanu simungangoyambitsa chipani chanu mudzitsutsa bwino

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika6784 Před 2 dny

    Tafika bwana

  • @DavidJackson-ox4xm
    @DavidJackson-ox4xm Před 2 dny

    Ma ID akhasulidwe tikavote basi.

  • @John-to8gl
    @John-to8gl Před 2 dny

    ID Isagwilitsidwe Ntchito povota ambiri ife tilibe ID, koma tikufuna kuzavota ndiye ichosedwe system yovotera ma ID aliyense azizangovota basi

  • @EDGARKADZAKUMANJA
    @EDGARKADZAKUMANJA Před 2 dny

    Palibe kuvota nd id

  • @user-ul1fb4yn5o
    @user-ul1fb4yn5o Před 2 dny

    Ngati amtsogoleri a DPP, Aford, utm ndi zipan zina sayakhulapo zimenezi,, adziwe kuti ife timuika mokakamiza boooooooon kalindo

  • @user-hx6ly3cl8m
    @user-hx6ly3cl8m Před 2 dny

    Nzimenezo ndidzoona kupanda kusamala chakwela kungolowa Boma tiziwe Kuti tidzankhala muukapolo

  • @Leo-fj6gz
    @Leo-fj6gz Před 2 dny

    Where are the fuckin opposition in Malawi, mulikuti makapenu zinthu azikuyankhulilani anthu zoona??? Like seriously???

  • @JohnJohn-og8rt
    @JohnJohn-og8rt Před 2 dny

    Chakwera akuchepera kaba zisiteka kuwinaso ayi athu aganisazoso mwachangu zoona madam

  • @eliaskhofielias8152
    @eliaskhofielias8152 Před 11 hodinami

    Tikudabwa anthu angati chetee sakuyankhula azipaniwa ndi mabungwe tinganene kut akuopa?amenewadi asadzatinyanse otsutsawa akadzawa bela kut tiyeni pansewu.akugona okha otsutsawa even wachiwili otsutsa boma aliphee kupaliuament osayankhula adzalira amenewa mwina sakufuna u president.

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 Před 2 dny

    Mai mukunena zoona ineyo ndinanena kale kuti ngati mcp izawine 2025 amalawi ambiri adzavutika. Ndipo mazuzo aka adzaposa amene tikuganiza akubaga moyo

  • @FunnyKalimwayi
    @FunnyKalimwayi Před 2 dny

    tivota opanda chazika

  • @LukaAron-el5qh
    @LukaAron-el5qh Před 2 dny

    Ndizoona ndithu okuva ave chonde dzuka malawi

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 Před 2 dny

    Muone kuti osusa ndiogona ndi izi ku mzuzu blantyre mangochi ma ID ma passport anasiya kupanga zose zikupangidwa ku lilongwe komwe kuli mcp please sekulani maso osusa.

  • @DavidJackson-ox4xm
    @DavidJackson-ox4xm Před 2 dny

    Zoonad zimenezo

  • @user-gj4li2gc8o
    @user-gj4li2gc8o Před 2 dny

    Tivotera chakwera yemweyo ndi mcp chifukwa ndi chipani ziko osat za kubanja zija,olo kut afe peter leloli nde kut akatengaso mwana wa bingu ,kukanfunafuna kut mpaka nayeso azakhale president

  • @user-hg8zy8pt5b
    @user-hg8zy8pt5b Před 2 dny

    Mukunena zoona amayi

  • @user-ji5gq4cf6r
    @user-ji5gq4cf6r Před 2 dny

    Zazii. Vuto ndi lakuti ma boma ambuyo akhala akubwera mavoti

  • @user-uc1pd1tc2x
    @user-uc1pd1tc2x Před 2 dny

    Mbambande zedi ndithu ❤❤❤❤ guys lamuro la ID tisazaloreyi, aliyense azizangovota basi

    • @isaacchiwaula731
      @isaacchiwaula731 Před 2 dny

      Simudzalora motani? Muuzeni amene watumiza audio-yi kah kut ndiye tizatanii osati azingoyankhula without solution

    • @user-uc1pd1tc2x
      @user-uc1pd1tc2x Před 2 dny

      @@isaacchiwaula731 Tati sitizalora coz ndiufulu wathu ovota ndipo tizavota osagwiritsa ntchito ma ID coz tonse ndi mdzika

  • @ThomasHandson
    @ThomasHandson Před 2 dny

    Zoonadi izi

  • @LilianKachala-yz2xf
    @LilianKachala-yz2xf Před 2 dny

    Zoonadi Ma lD yavutadi .Tisadzagwilitse ntchito ma id Chonde eeeeeeeee

  • @Rose-wu5ef
    @Rose-wu5ef Před 2 dny

    Zoona dzuka malawi

  • @user-gx3xc9lk8x
    @user-gx3xc9lk8x Před 2 dny

    Amalawi tiyen tidzuke tisalore kut chakwera 2025 alowenso m'boma

  • @ChimwemweKondowe-nj4lx

    Chilungamo kwambiri chemwali.
    Opposition parties wake up and go to courts seek for justice.
    Stop this ID protocol while it's too early

  • @GospelSoldiers-sr7np
    @GospelSoldiers-sr7np Před 2 dny

    Kuyankhula ndiye anthu akulankhura ndipo zowona zokhazokha koma zipani zosusa zangoti ziiii basi kaya chifukwa chani mmadera ambili anthu sanalembese

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of Před 2 dny

    Osati tsoka akulu dziko muziyenda nalo atsutsa akuno Ku Malawi sangawine musabvuti ai ndiokulilana mtima

  • @DavidJackson-ox4xm
    @DavidJackson-ox4xm Před 2 dny

    Ma ID akhasulidwe tikavote basi.

  • @EagerChicken-qj6xu
    @EagerChicken-qj6xu Před 2 dny

    Mukunena zoona mayi.