BON KALINDO LERO PA 24 AUGUST 2024 |

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 12. 09. 2024

Komentáře • 124

  • @Blessings-b7h
    @Blessings-b7h Před 19 dny +7

    Tsoka mtunda ndi nyanja poti iopayo watsikira komweko.

  • @TecksonKaima-dr6er
    @TecksonKaima-dr6er Před 19 dny +5

    Mulungu atsogolere dziko lamalawi komanso bushiri ndi chakwera amwalire ndithu.mulungu wachifundo chambiri wachisoni atichotsere anthu awiri amenewa

  • @CharlesPhiri-ds1rk
    @CharlesPhiri-ds1rk Před 19 dny +3

    Jesus, son of living God ,protect Malawi and citizen, what ever planning for Malawi evil,,back to sender in Jesus mighty Name(Aisiah 54:17)(psalm 121:3)

  • @user-wl7xn3or6d
    @user-wl7xn3or6d Před 19 dny +1

    Min bus iyaka bwanji moti ikana yaka inali yama futayo satanic amafuna muli athu ambilimo yama futa kungo gundana ndiina thawi yomweyo imayaka

  • @matiasbenjamim4025
    @matiasbenjamim4025 Před 19 dny +2

    Bon kalindo ndi liwu la a Malawi.
    Abale onse amene Amati ndi ma prophet ndi a satanic ziko la Malawi mwazaza a satanic kwambiri

  • @MoosaChirwa
    @MoosaChirwa Před 19 dny

    Keep fire 🔥🔥🔥🔥 burning Mr kalindo

  • @MlecheFatch
    @MlecheFatch Před 19 dny +15

    Bon kalindo amayakhula ngati wamisala koma there is a sense of truth in whatever he says, May the good Lord have mercy on Us

    • @WorriedNdhlovu
      @WorriedNdhlovu Před 19 dny +2

      Anthu sakuziwa .vuto kumalawi kuno satana anatitseka kumaso

    • @MilacleSankhani
      @MilacleSankhani Před 19 dny

      Hyv bro

    • @SildaKatundu
      @SildaKatundu Před 19 dny +1

      Malawi Chikangawa Party ikugulitsa anthu ku satanic but remember God is watching

    • @leonardmughogho3533
      @leonardmughogho3533 Před 19 dny

      Fact

    • @TimothyMwandila-r9p
      @TimothyMwandila-r9p Před 19 dny +1

      Izi ndie zoona zen-zentu achimwene, ndimaona ngati Inu simkudziwa. Kumalawi kuno zaka zamma mbuyom kunali anthu opemphera kwambiri, koma pano masatanc adziveka uprophet kumangonamiza anthu basi. Ndipo anthu ndfe zitsiru,tsiku nd tsiku anthu tikutha chifukwa cha zingoz zosaziwika bwino. Karelo izi kunalibe. Kungobwera maprophet awa ngoziso mbwe mbwe mbwe bwanji!!! Osazifusa amalawi bwa, zinaz zanyanya mmmmmm ai.

  • @GoodluckVithumbiko
    @GoodluckVithumbiko Před 19 dny

    ndipo munasowadi love you Mr DC

  • @VictorGobede
    @VictorGobede Před 19 dny

    Let us pray hard without cease! To shame the devil 😢

  • @GoodluckVithumbiko
    @GoodluckVithumbiko Před 19 dny

    ndipo zinthu izi zinachitikapo ngati izi ndipo koyamba ndipo buchiri ndichakwera uyu kaya ambuye titsogororeni ndithu ambuye tikurira abare

  • @user-ve2ts3yr2n
    @user-ve2ts3yr2n Před 19 dny +1

    Everything he speaks is 💯 true.... Amalawi kugona too much

  • @user-up2vb8kb5e
    @user-up2vb8kb5e Před 19 dny

    Big up the DC

  • @collennyadile8179
    @collennyadile8179 Před 19 dny +1

    dziko lili mumanja mwa satana tizilipemphelera dziko lathu labwino la Malawi

  • @PempheroAlli-v8y
    @PempheroAlli-v8y Před 19 dny

    Ziziwika zonse ndi thawi mulungu atiyang'anire plz

  • @EvelynKhalani-p5v
    @EvelynKhalani-p5v Před 19 dny

    Ambuye atithandize atipulumutse kuzowawazi

  • @GoodluckVithumbiko
    @GoodluckVithumbiko Před 19 dny

    koma anthu awa ngozi paripose anthu achipongwe kwambili kumpha anthu ngati nkhuku Mastanic ndipo yes ufiti uri ko mukunena zowona

  • @lyiemax
    @lyiemax Před 19 dny

    Powerful speech from our beloved president, the Dddddd Cccccc!!!!❤❤❤

  • @moseskavalo3304
    @moseskavalo3304 Před 19 dny +2

    Ufiti uliko even ku azunguko ufiti ulikoso,

  • @GeorgeBanda-x6l
    @GeorgeBanda-x6l Před 19 dny +1

    iweyo wa pasi pa nyanja amene ukupeleka ma coment ako auchitsiluwo chikumbu mtima chikugwire iwe wa mcp

  • @annamazingashaibuh6276

    The D C naked truth 🔥🔥🔥🔥🔥

  • @dalitson3558
    @dalitson3558 Před 19 dny

    Mafumu ndi anthu oipa kwambiri we need to get rid all of them

  • @ShamidaMatola
    @ShamidaMatola Před 19 dny +2

    Wamisala anawona nkhondo zoona

  • @MavutoMbiri-q8x
    @MavutoMbiri-q8x Před 19 dny

    Zoona DC tipephere kwambiri zoona ndithu

  • @user-mp4oz3fz3h
    @user-mp4oz3fz3h Před 19 dny

    Mulungu tifungatilen ife ana Anu

  • @MaxwellMilanzi
    @MaxwellMilanzi Před 19 dny +1

    The DC number one......

  • @EuritaDeric-fz3ds
    @EuritaDeric-fz3ds Před 19 dny +1

    Ambuye atetedze dziko lathu tili pachiopsyezo

  • @Lazarus-qo1sl
    @Lazarus-qo1sl Před 19 dny

    we need your mercy our father 🙏 🙏

  • @dondamissonchdziwe3958
    @dondamissonchdziwe3958 Před 19 dny +1

    Pamene Chakwerayo wapha Chilima pamodzi NDI wanthu ena bwanji sama ngidwa, wanthu wonse avotere Dpp, Chakwera NDI amzake a MCP amangidwe,mbuzi zimenezi za watola a Malawi

  • @AlasonPaulo-ht7zb
    @AlasonPaulo-ht7zb Před 19 dny +3

    Osamasowa chonchi koma

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b Před 19 dny +1

    Yes prayer is needed❤❤

  • @RuthChilobwe
    @RuthChilobwe Před 19 dny +1

    Zoonadi Atsogoleri ambiriwa a dzikowa onse ndi afiti.ciffukwa amaipa mitima. Ndikumapha anthu.Mulungu yekha basi ndiye wa chikondi .saapha wosalakwa .ayi.Amfumu a kwathu..chief mwangata wa kuzomba t/ a Mulumbe .anandiuza kuti @ AZUNGU ONSE AKUNJA AJA NDI AFITI.NDIPO MAFUMU ONSÈNSO AMAKHALA AFITI CIFUKWA IWO AMAYANG'ANIRANSO AFITI ONSE; OSAUKA ONSE;AMISALA ONSE.OYERA MITIMA ONSE ;AKUBA ONSE.ETC.@NDIPONSO MABWANA ONSE AMMAOFESIWA NDI AFITINSO.SAMALANI NAWO NGANGA WATHU..INENSO PANO NDIINE MFITI MMUDZI MWANU MUNO.KOMA SINDIMAPHA ANTHU AYI.CIFUKWA KUKHALA MFUMU NDI KUKHALA NDI ANTHU MMUDZI ..EETU NGANGA WANGA ABITI CHAONA ANJAONA CHEMWALI.WANGU

  • @JosephyGetala
    @JosephyGetala Před 19 dny

    Mulungu achitepo kanthu

  • @MikeArthur-jd2ij
    @MikeArthur-jd2ij Před 19 dny

    The DC 🔥

  • @MaxwellMilanzi
    @MaxwellMilanzi Před 19 dny

    Chilungamo ndi chipongwe

  • @user-wq3cg9nc6b
    @user-wq3cg9nc6b Před 19 dny

    Mmmm osachulusa zambiri nayeso anali limozi kut tengera kumeneko koma pano iye akunena ngat simumozi mwaiwo zithu zikuvuta km titan sikut ndizose tingathandizidwe ndi president 17:44

  • @MaxWell-d7o
    @MaxWell-d7o Před 19 dny

    Kuchikweza The Dccc

  • @WysonAnton
    @WysonAnton Před 19 dny +1

    Ndp live ngoz zafka pawese mmm 😢😢

  • @user-js6xn9qj1r
    @user-js6xn9qj1r Před 19 dny

    The DC mwana oopsa kwambiri President of the poor people ❤❤❤❤❤❤❤

  • @victormbewe7462
    @victormbewe7462 Před 19 dny +1

    Guys ndili okhumudwa kuti tilimudziko lokonda social media mmalo mokonda wina ndinzake
    How come timakonda kujambula pamene anzathu akuthatha ndi imfa instead kupulumutsa myoyo ya nzathu?

  • @Moses51
    @Moses51 Před 19 dny +1

    The DC bon kalindo 🎉

  • @FelixKachera-je4yk
    @FelixKachera-je4yk Před 19 dny +1

    🤗🤗🤗 ALIYESE PA MALO AKE 😅😅😅

  • @KondwaniMamveka
    @KondwaniMamveka Před 19 dny +1

    Speech yako tinaisowa Dc

  • @EmmanuelNgambi-y6h
    @EmmanuelNgambi-y6h Před 19 dny

    Mulungu alowelelepo😢

  • @MartinNyirenda-wf5oz
    @MartinNyirenda-wf5oz Před 19 dny

    Bon kalindoooo
    Pitilizani kung'alula mmativetsa kukoma,🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

    • @TimothyMwandila-r9p
      @TimothyMwandila-r9p Před 19 dny

      Yes apitilize amene amadana ndzoonaz mdziwe nchito zake ndzomwezo moto kt buuu umupeza wa MLUNGU patsogoropa

  • @happymumba2261
    @happymumba2261 Před 19 dny +1

    Munasowa Mr dc

  • @ShadreckMtepuka-sj8ue
    @ShadreckMtepuka-sj8ue Před 17 dny

    Koma mkulu uyuyu amayankhulatu

  • @AfakiMussa
    @AfakiMussa Před 19 dny +1

    Abushiri ndi achakwera ndi asataniki anthu akupha

  • @RosebyChiromo-x5u
    @RosebyChiromo-x5u Před 19 dny

    Zonse mwakambazi ndizoona tikupezeleledwa cause voice yathu siipita patali andalewa sakutimva

  • @PaulineHassan
    @PaulineHassan Před 19 dny

    Powerful msg mr

  • @limbanikamanga7514
    @limbanikamanga7514 Před 19 dny

    Zoti ngozi zikuchitikazi zili ndi a supernatural cause n'zoduka mutu.
    Mayiko onsewa pa dziko lapansi satana, if at all he exists, azikalimbana ndi Malawi??? Khalani serious akuluakulu

  • @LatifBeni-e6z
    @LatifBeni-e6z Před 19 dny

    ❤❤❤

  • @EmilyKanyika
    @EmilyKanyika Před 19 dny +1

    Amen 🙏

  • @user-fy3yo5xy1v
    @user-fy3yo5xy1v Před 19 dny

    You are saying truth

  • @GeorgeBanda-x6l
    @GeorgeBanda-x6l Před 19 dny +1

    iweyo amene wapeleka coment yot vuto ndi miseu iwe ukukana kut ku malawiko ngozi zimene zikuchitikazo ndiye kuti iweyo uli mumgulu la anzako asatanic wo iweyo. ndiye osa mapeleka ma coment opusa apa anthu akutha ndiy ife tiziti imeneyo si satanic munamuphelanji chilima

    • @TimothyMwandila-r9p
      @TimothyMwandila-r9p Před 19 dny +1

      Fuso ndrakut Kodi kumbuyoku miseu yoipa kunalibeko yaipa lero!!?

    • @SteveKanongwa
      @SteveKanongwa Před 19 dny +1

      ​@@TimothyMwandila-r9p eti amwene miseu yaipa lero

    • @Lee-lee-w1r
      @Lee-lee-w1r Před 18 dny

      @@TimothyMwandila-r9pkoma ndipo.

  • @ThokozaniElesoni
    @ThokozaniElesoni Před 19 dny

    Zoonad big

  • @HawardKalipande
    @HawardKalipande Před 19 dny

    The people's first!

  • @MaxwellMilanzi
    @MaxwellMilanzi Před 19 dny

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 Před 19 dny

    Kodi ma audio amenewa akalindo muli pa payroll?

  • @MosesDicostar
    @MosesDicostar Před 19 dny

    Dziko lilipamoto tiyeni tipephere molimba amalawi

  • @ChikoEthopia
    @ChikoEthopia Před 19 dny

    Big op the DC stanic iliku Goshen city

  • @Johnwiam-pq8lq
    @Johnwiam-pq8lq Před 19 dny

    Aliyese payekha azipemphelera malawi ,zochitika masiku otsili(2timoteyo 2vs3))

  • @MaryMary-dz2th
    @MaryMary-dz2th Před 19 dny

    Yiponde fada 😅 munthu umatopa basi kung'alura

  • @HondaFredzoG
    @HondaFredzoG Před 19 dny

    Ooo ambuye tetezelan malawi

  • @Sadi6123
    @Sadi6123 Před 19 dny

    Amezing

  • @user-po9yj6io3c
    @user-po9yj6io3c Před 19 dny

    The DC number one

    • @TiongeKaonga
      @TiongeKaonga Před 19 dny

      Amen mau achimbikitso ndizoonadi amalawi tipephere akhalitse bonikalindo amatiyakhulila

  • @JeremiahKapundu-j1p
    @JeremiahKapundu-j1p Před 19 dny

    Kom mu2yo wanena chilungamo akubweza sembe

  • @user-eh1mg3ww6d
    @user-eh1mg3ww6d Před 19 dny

    Makamaka tsoka liyenda chakwela mulungu amukathe ndithu ndichifukwa Chake akati ndikapanda kuwina ndisakhetsa mwazi wanga

  • @MussaLenard-k4l
    @MussaLenard-k4l Před 19 dny

    Mr presdent❤❤

  • @HamzaMkwanda-bh8dc
    @HamzaMkwanda-bh8dc Před 19 dny

    Legend

  • @ChrispinEdward
    @ChrispinEdward Před 19 dny

    Khaniyi A DC akunena zoona

  • @Alexkalonga-t9s
    @Alexkalonga-t9s Před 19 dny

    Km nyoo akunena zoona❤❤

  • @TemwaKabisa
    @TemwaKabisa Před 19 dny

    Amen 🙏❤❤

  • @MaxwellMilanzi
    @MaxwellMilanzi Před 19 dny

    Zoonad km

  • @MathewsMajiya
    @MathewsMajiya Před 19 dny

    Ambuye atithandize please

  • @FrancisGama-qb7ze
    @FrancisGama-qb7ze Před 19 dny

    Ngozi yimene ija ndya satanic ndthu oasakayikaso ayi

  • @YahayaKondwan-mo8hu
    @YahayaKondwan-mo8hu Před 19 dny

    Abale sizikuyenda Mulungu atichitile chifundo

  • @MathewsMajiya
    @MathewsMajiya Před 19 dny

    11:48 Ambuye atichitire chifundo

  • @DanMhone-iw6xg
    @DanMhone-iw6xg Před 19 dny

    Zona zake the DC

  • @MathewsMajiya
    @MathewsMajiya Před 19 dny

    11:48 Ambuye atichitire chifundo 12:23

  • @HendrickBanda
    @HendrickBanda Před 19 dny

    🔥🔥🔥

  • @MarleyMchenga
    @MarleyMchenga Před 19 dny

    The DC ulemu wanu

  • @CathrineKumwenda
    @CathrineKumwenda Před 19 dny

    Focus pray

  • @malawigeneralguide1646

    More fair mumatiyimila

  • @JunaKananji
    @JunaKananji Před 19 dny

    ❤❤❤❤lovekarido

  • @MonicaChanza
    @MonicaChanza Před 19 dny +1

    Mulungu atitetenzere....choipa chibwerere kowochipanga...DC mumatimvetsa kukoma

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 Před 19 dny

    Nkhani ndimisewu yoipa si satanic osalozana zala umenewu ndi umbuli, dziko lilonse kumachitika ngozi

    • @ndalamaandrew
      @ndalamaandrew Před 19 dny +2

      Ndiwe Mbuzi omvesa chisoni kwambili, ndipo ulibe nzimu wachiziwitso. Akazakuphera abale ako moaned uziwe Kuti Chakwera ndiwa sanic. He is evil than devil himself.

    • @ChikoAlicky
      @ChikoAlicky Před 19 dny

      Ndipo zowona mulungu amuthandize azake akulila ataya moyo wabare awo iye kumarakhura atankhuta deyayo osangopita kumakanyera bwanji

    • @Lee-lee-w1r
      @Lee-lee-w1r Před 19 dny

      Vuto lake sinu anthu otseguka mmaso. They hide it in the plain sight and you still can’t see it

  • @user-zg9se4rw6v
    @user-zg9se4rw6v Před 19 dny

    Zinu izo,

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of Před 19 dny

    aboni kalundo anatha akalindo anali kale

    • @MarkMapondo
      @MarkMapondo Před 19 dny +1

      Inu kale lanu mwapanga chani?

    • @ChikoAlicky
      @ChikoAlicky Před 19 dny +2

      Kaya tamufuse bare wake wachakwerayo

  • @NelsonSambo-e2s
    @NelsonSambo-e2s Před 19 dny

    The DC

  • @HoseKatsekera
    @HoseKatsekera Před 19 dny

    chilungamot chimenecho

  • @PempheroMoleni
    @PempheroMoleni Před 19 dny

    Live DC

  • @user-xj9uy6wz7b
    @user-xj9uy6wz7b Před 19 dny

    Exodus 14vs14😢😢😢

  • @graciouszgambo560
    @graciouszgambo560 Před 19 dny

    Pita ukawathandize iweyo umakonda kulalata deyile chisilu

    • @HappyMunthari
      @HappyMunthari Před 19 dny +1

      Chitsiru ndiweo moti iweo suva chisoni mene zililimu garu wamkulu mbuzi ya munthu mutuluka m boma dikira

    • @BLESSINGSSTOLO-lt9di
      @BLESSINGSSTOLO-lt9di Před 19 dny +1

      Iwe ndiyed ndi galud wamva!!! Moti kufa kwa anthu ena ukumakondwa eeet???

    • @HawardKalipande
      @HawardKalipande Před 19 dny +1

      Iwe usatipalamulitse ndye mmodzi mwa afitiwo et??

    • @ChikoAlicky
      @ChikoAlicky Před 19 dny +1

      Iwe mutu wawukuluwo wava ? Ulibe zelu et

  • @MauriceMukona
    @MauriceMukona Před 19 dny

    Bushiri Chakwera promised mwazi 2019 pa compaign