Video není dostupné.
Omlouváme se.

Timumva Kuwawa Chilima Mu 2025?

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 28. 02. 2023
  • Fans of UTM and Right Honorable Dr. Saulos Klaus Chilima Vice President of Malawi this is for you. Enjoy! For the anyone else do you think SKC is a force to reckon with in 2025?
    #nyimbozachimalawi #malawimusic

Komentáře • 47

  • @ndabaningichisiza9574
    @ndabaningichisiza9574 Před 2 měsíci +2

    Rest easy my Guy, for once i had hope for real change. Thank you for your service

  • @ephraimphiri8919
    @ephraimphiri8919 Před rokem +4

    Supporting mbava Malawi style. Choncho katangale angathe ku Malawi. Nkomwenkomwe Chilima sangayime pa president as thye law forbids him.

  • @msaiwaleumandi6077
    @msaiwaleumandi6077 Před rokem +6

    Chilima akachoka ku Mcp , chipani chowina ndi Dpp

  • @moses372
    @moses372 Před rokem +4

    Chilima ndi machine

  • @msaiwaleumandi6077
    @msaiwaleumandi6077 Před rokem +4

    Afuna kumunamiza Chilima anthu

  • @manasemaposa
    @manasemaposa Před 3 měsíci

    Bhazuka machine Dr SKC

  • @RofinoJastenJasten
    @RofinoJastenJasten Před měsícem

    Chilima

  • @sgemshane3645
    @sgemshane3645 Před rokem +3

    Ayise Ngati ukufunya gayiwa bola usikafuna maganyu kuchomerera mbamva amwene😱😱😱😱

  • @user-le9su3mt7r
    @user-le9su3mt7r Před 4 měsíci +1

    Chilima mashine

  • @aleksawilliams710
    @aleksawilliams710 Před rokem +2

    Aaaaaaa koma umbuli ndikhani zina,,,kumbera mfiti m'manja

  • @gladysbonongwe1038
    @gladysbonongwe1038 Před rokem +2

    Wasowa choimba kodi, kodi chimakhala chili chain kumasapota mbavazi

  • @shadreckphiri1799
    @shadreckphiri1799 Před 5 měsíci +1

    Chilima is not a thief, it was just a move by MCP to turnish his name So that he doesn't stand in 2025. It was well calculated by Chakwera.

  • @mustafailanga2585
    @mustafailanga2585 Před rokem +1

    Zachamba chilima mwanva!!!

  • @FrynessMoyo-to2du
    @FrynessMoyo-to2du Před rokem +1

    Kuombera fiti manja mbava yeniyeni

  • @danielzitande5231
    @danielzitande5231 Před 8 měsíci

    Kkkk mmmm koma mudziyimba kuti Chima wakubayeeeeee! Komanso wabodzasaaa, mukadzamuvotela Chilimayeee, adzabayeeee.

  • @clementmahoka6287
    @clementmahoka6287 Před 5 měsíci

    Chilima machine

  • @user-gd7xm7xr9v
    @user-gd7xm7xr9v Před 6 měsíci

    Mmmmm
    Mbava

  • @NgomaRaheem
    @NgomaRaheem Před 5 měsíci

    Mukufuna apitilize kuononga zakeso et gwape ameneyu angakhulupilire ndan

  • @EmercianahKasiku-en6hl
    @EmercianahKasiku-en6hl Před 6 měsíci +1

    Tapelekani ma comment mukusowa chonena because the guy muli nzeru osati sewero and titamupanga kukhala president wa dziko lino ndikuuzani munthawi yochepa chabe Malawi atha kusitha tikuyenera kusiya mndale za zipani monga tinachitira muja ndikusakha omwe Ali ndi kuthekera not poti ndi wakwathu ai mkulu analakhula uja wapelekako example Chilima ali bwino ndi Pitala zinthu zimayenda bwino koma atangochoka chipwilikiti mpakana DPP inaluza boma nayoso MCP pomwe inalu ndi ubale wabwino ndi Chilima mesa tinagula fertilizer wa 4.9.99 muno pano bwanji? NDE the guy muli nzeru bad zotukukira dzikoli..abale azanga zoona mukufuna Gogo lotha ntchito LA zaka 82 litilamulire?azikangogona achina Norman Chisale azikaba ndalama, mpakana kutayilita kutisakhira munthu osadziwa chilichose Chimulirenji as vice president abale munthu ukafika zaka zimenezo umapuma orso mwiniwake ananena osakakamiza magogo kukugwilirani ntchito inuyoso munthati kuima ngati president kulibe school ya upresi 6:35 dent lamuro la age limit lija limayeneraso kupanda pass imagine the candidate Ali ndi zaka 80 nde alamulire 2 terms azakhala ndi 90 yrs are we serious ndi dziko lathuli a malawi, mavuto omwe boma iliri ladutsamo agogo aja sakanakwanitsa or pang'ono, Chilima ndi machine akatundu or kuti amene kut apanga press conference mawa ma battery awailesi mumashop amatha malo oonetsa film kudzadza meaning the guy has something special let's try him malawias

  • @mathewsmbaluko8522
    @mathewsmbaluko8522 Před rokem +1

    Zopusa mwaponya apanu mukusowa chochita😲

  • @user-ee6be5kl5o
    @user-ee6be5kl5o Před 4 měsíci

    sitikufuna anthu otibera misonkho yathu onse atonse alliance alibe CHOTI angatiuze ife amalawi zotinamidza ife tatopa Nanu nonse mbava zokha zokha

  • @dicksonilimbani3443
    @dicksonilimbani3443 Před rokem +2

    Akuba ngati ameneyi

  • @bernaddickson
    @bernaddickson Před rokem +2

    Km zowona zonsezi tikumvadi ukuwawatu ndi ATONSE ALLANCE

  • @abdulrafiquekalembo469
    @abdulrafiquekalembo469 Před 6 měsíci

    Inatimvetsa kale kuwawa ameneyu tilibe naye mau.wabodza, ofowoka.

  • @AminaPhiri-pp9tw
    @AminaPhiri-pp9tw Před 4 měsíci

    Munatinamiza kale inu sima yodya katu ija ilikuti munataya geme
    Nokha basi

  • @idris6597
    @idris6597 Před 11 měsíci

    Mboli zanu

  • @juniornaphazi4852
    @juniornaphazi4852 Před 9 měsíci

    Awandiopusa inu

  • @yahiyajonse
    @yahiyajonse Před rokem +1

    Koma satana ndi oopsa guys eerr

  • @user-xe1so5xj2w
    @user-xe1so5xj2w Před 6 měsíci

    Chilima ndiwakuba mupaka nyimbo guys

    • @user-le9su3mt7r
      @user-le9su3mt7r Před 4 měsíci

      Wakuba mambo wako chakwera na pitala chilima bomaa

  • @abdulrafiquekalembo469
    @abdulrafiquekalembo469 Před 6 měsíci

    Kujoinana ndi MCP kuja pakokha it was a very big mistake and nkhanza that he did to Malawians.Ndiye poti aMalawi ambirife tinalodzedwa/opepela zinthu ngati zimenezi samaganizira kuti tikuvutika ku Malawi chifukwa cha decision imene iye anapanga yolibwezeretsa boma la nkhanza m'boma.Atleast akanayima payekha Kapena kujoinana ndi chipani China chake olo Aford.Koma MCP!????.Ayi ndithu people uyu mngwaphuma kwambiri uyu ndipo wa dyera musadzayelekeze kuononga vote yanunso pa uyu.God forbid

  • @abduljafari7387
    @abduljafari7387 Před rokem +1

    Koma ndiye mwalawilila chitukuko tinasachione ko iwe ndi mbuzi ndi thu

  • @EmercianahKasiku-en6hl
    @EmercianahKasiku-en6hl Před 6 měsíci

    Chilima ndi 1 palibeso make pandale mdziko mino

  • @user-wd7lk7nx7m
    @user-wd7lk7nx7m Před 10 měsíci

    Koma misala ina iyi

  • @dingim1234
    @dingim1234 Před rokem +1

    Chilima si mbamva zili ku MCP. The most effective way to destroy people is to deny and obliterate their own understanding of their history. Thats propaganda.

  • @abdulrafiquekalembo469
    @abdulrafiquekalembo469 Před 6 měsíci

    Munthu wa dyera uyu.Anatenga kuwachotsetsa achinyama ku ulamuliro wabwino wa DPP umene zinthu zinali bwino kuwapititsa ku Ng'ona za MCP.Zonsezi anapanga chifukwa cha dyera ndi Phuma ndi upresident.Only anthu akhungu mosaona patali amagomera Chilima

  • @salimmkumakumakitombi-yc7pw
    @salimmkumakumakitombi-yc7pw Před 6 měsíci

    Amakumbukira ADAD uyu kuti anali .munthu wabwino... pano manyadxi okha okha ... ADAD ananyodxedwa kutukwanidwa kusemeredwa nyatsi koma ADAD anali pheee kumvesera .lero chilima wangoyetsa kupanga matukutuku mmmmm mcp yati aaaaa mwanayu sakuidziwa mcp ndiyesa anali mwana 1987 koma timuonese anaona Muwaro ndi Gwede .lero uyo

  • @mussahcassim4963
    @mussahcassim4963 Před rokem +1

    Zaziiiiii

  • @mandamandamanda2208
    @mandamandamanda2208 Před rokem +2

    Amene ukuyimba nyimbo yako yopusa naweso ulimugulu lambava zoopsya m.malawi muno muhanya uno munthu wanzeru zake angavotereso chilima mbava ya zuneth satar iweso ndiwe garu umanamiza dziko kuti anthu adzadya katatu azagura fertilizer 50kgs pa mtengo wa k4950 zikutheka Lero chilima ndiye munthu woyipa kwambiri 50kgs fertilizer mpaka na k90. 000 stupid foseki akagwere uko

  • @usumanimusa411
    @usumanimusa411 Před měsícem

    Kuchenjres akulu awa apit nazooo kumanda