KWAGWANJI LELO PA 10 JULY ON TIMES 🙌 MALAWI!!

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 9. 07. 2024

Komentáře • 8

  • @MustaphaCassim
    @MustaphaCassim Před 20 dny +2

    Ayi palibe utsogoleri

  • @FlorenceNgomba
    @FlorenceNgomba Před 20 dny

    God have mercy

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w Před 20 dny +1

    Malawi yatha, kaya adzachila , mmmmmmm kuli umphawi ku Malawi, President kumangowononga ndalama maulendo.

  • @CatherineChidothe
    @CatherineChidothe Před 20 dny

    Eee our own country

  • @user-jj7oz4lo9t
    @user-jj7oz4lo9t Před 20 dny +2

    Too bad Zosayenda

  • @user-xc2zm9bu1i
    @user-xc2zm9bu1i Před 20 dny +1

    Leadership plays a big role in development wawa
    Chakwera and his cabinet how much are they receiving,their salaries and allowances
    Cabinet anthu onsewo, bwanjii osachepetsa
    Chakwera wayenda kangati,ma allowance akungopita
    How can cabinet ministers kulemela chonchi?
    Ndichiyani chimene wapanga in this last 4 years
    Kuntcheu kuno misewu kumangotinamiza
    Next year azibwera kuti ndivoteleni
    Are you sure a chakwera?
    Tidakupatsani mavote kuno ,ndithu tionana mu 2025

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w Před 20 dny +1

    Vuto ndi utsogoleri basi akulu akulu, imagine Boma ililo , 4 years yomwei wakongola kuposa boma lilironse kumbuyoku.

  • @MsondaBanda
    @MsondaBanda Před 20 dny +1

    From Udf , dpp, all money stolen by these parties, so don't say all money taken now