Zomwe Apanga A UTM Kuchoka Ku Tonse Alliance Zandisangalatsa - Manza Wa Kwa Chinsapo

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 11. 07. 2024
  • On Nyasa VoiceBox, a Malawian named Manze from Chisanpo in Lilongwe shares his thoughts on UTM's decision to exit from the Tonse Alliance.
    Pa Nyasa Voicebox, M'Malawi wina dzina lake Manze wa ku Chisanpo ku Lilongwe akufotokoza maganizo ake pa ganizo la UTM lotuluka mu Tonse Alliance.

Komentáře • 20

  • @user-hm9nc7lz6e
    @user-hm9nc7lz6e Před 24 dny +5

    Kumuikapo manganya chifukwa manganya ndiyemwe anapeteka chilima mmanja mwa cakwera kuti amuphe ndimkona anamuika pampando at avice president akunama manganya wangoona kutenga sambi chabe

  • @Hamzamabvuto
    @Hamzamabvuto Před 24 dny +4

    I'm the first person to comment here I love UTM but I'm not the member of UTM

  • @MerryWayson
    @MerryWayson Před 24 dny +3

    Achita bwino kuthesa ❤❤

  • @JairoseManuel-p5p
    @JairoseManuel-p5p Před 24 dny +3

    Sanalakwise kuchoka

  • @SHEREEFKanthochi-ft3dm
    @SHEREEFKanthochi-ft3dm Před 24 dny +3

    inenso ndikunva kukoma zedi

  • @AugustineTheu-of6nv
    @AugustineTheu-of6nv Před 24 dny +1

    Zikomo kwambiri nkulu wanga kwa mawu ako ogwira mtima. Inenso m'bale ndikanakhala mwana wa chilima mbuzi imene ija Chakwera ndikanamuthamangitsa pa maliro kuti asowepo. Amene uja si president ayi

  • @VeronicaChirwa-ct4os
    @VeronicaChirwa-ct4os Před 24 dny +1

    Manze ndagwirizana nawe kwambiri pa zomwe wanenazi. Inenso Chilima akanakhala m'mbale wanga sindikanalora kuti abwere pa maliro a Chilima. Ndipo ndikanachita zoti amalawi sanaziwonepo. Kaya ndikufa nanenso ndikanafera pompo. Chakwera ndi munthu oyipa kwambiri.

  • @susantembo2076
    @susantembo2076 Před 24 dny +1

    UTM please forge ahead. Don’t listen to any other distractive noises

  • @DannielOnions-fy3dc
    @DannielOnions-fy3dc Před 24 dny

    Nice one thanks U.T.M MORE

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 Před 24 dny +1

    Mumakwana inuyo more fire 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @raffickaffick
    @raffickaffick Před 24 dny +1

    Bravo fada

  • @stevenfrancism3638
    @stevenfrancism3638 Před 24 dny

    ❤❤❤❤❤❤

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 Před 24 dny

    Ineyo ndinakakhala m'bale wanga ndinakati Maliro sikuika tiyeni tikamutulire chakwera akadye sured pakanavuta komanso sinakalora wina aliyense wachipani cha MCP kupedzeke pa Maliro ndithu kunakachema

  • @Felista-m4q
    @Felista-m4q Před 24 dny

    Inenso ndanyadira kwambiri

  • @ErnestChansa
    @ErnestChansa Před 24 dny

    Mwalakhula fundo zabwino big chakwela ndi galu yambuzi fiti

  • @MacleanKwacha
    @MacleanKwacha Před 24 dny

    Ndipo ine ndizafunisisa anthu amenewa asazaikidwe,tizadyere nsima

  • @user-ui4ux5kc8d
    @user-ui4ux5kc8d Před 24 dny

    Ngakhale kufa kwake kwachakwera anthu tidzavina kusangalala ndipo kaya imfa imeneyi kwaiyeyu ikuchedwa patii munthu oipa uyuu akanafa koma ndithu ambuye timenyereni mkhondo afee ndithu presedent ameneyi

  • @user-hm9nc7lz6e
    @user-hm9nc7lz6e Před 24 dny

    Kuga mwacakwera anthu tidzakondwa komanso kuvina kuti chokupha chija chafa

  • @gracemkandawire8769
    @gracemkandawire8769 Před 24 dny

    Tiyeni tizavotele UTM. Kuti mzimu wachilima uzause mu mtendele