Ndalama zikusowa mmabanki chifukwa cha Chakwera." Dr Dalitso Kabambe, Former Reserve Bank Governor

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 8. 09. 2024

Komentáře • 97

  • @JubulaniRICHARD
    @JubulaniRICHARD Před 5 měsíci +2

    Moto kubuuuu Dr kabambe muliphule dziko lili pa moto god bls u

  • @mercynavaka8489
    @mercynavaka8489 Před 2 lety +5

    Dr Kabambe, is the great man..may God bless him

  • @chippiephiri4505
    @chippiephiri4505 Před 2 lety +9

    I like the way he analysis the issue

  • @mishhillinvestment1672
    @mishhillinvestment1672 Před 2 lety +4

    Nice explanation koma unali konko you did not think this wise..... killing Malawi for your fame, shame to our educated machines.

  • @dreetosh8502
    @dreetosh8502 Před 2 lety +3

    Dr D, freedom fighter, we need best Malawi

  • @wydonmsongole8697
    @wydonmsongole8697 Před rokem +1

    This guy is intelligent...DPP got brilliant economist ❤

  • @marthansaliwa7732
    @marthansaliwa7732 Před 2 lety +5

    Nonsenu mbava zokha zokha palibe wabwino. Musaononge mawu Chauta akuonongani nonse. Inu ngati mumayendetsa bwino Malawiyu bwenzi titaona zabwino zambiri. Enawa ndiye a alowa ndi njala kudzakokotamo zonse. Malawi akufunika mamasulidwe a uzimu wadzadza ndi ziwanda

    • @giftgannet6871
      @giftgannet6871 Před 2 lety +2

      Sikut sangabe ai koma kabedwe kake mpaka anthu kuyenda maliseche panthunda esh mcp ndi mbatata zeni zeni

  • @felaxnambazo1058
    @felaxnambazo1058 Před 2 lety +4

    Chakwela anazolowela kuvina nyau kwao kwa malembo pamene chilima Wakulila tchile kusaka nyama ku tcheu sangakwanitse kuyendetsa Boma

    • @tingo3155
      @tingo3155 Před 2 lety

      We need a town monger to run a state

  • @akilainter10ment
    @akilainter10ment Před 2 lety +1

    Dr Kabambe, come and teach me economics plzzzzz

  • @chelseajackson3200
    @chelseajackson3200 Před 2 lety +3

    I would vote this person into govt but not with DPP!

    • @tingo3155
      @tingo3155 Před 2 lety

      This man has a vision 'cos of his education

  • @nditumenichagunda4192

    U deserve my vote wakumulanjeyu akumachezaso ndi makapewa ndiye ndamutaya

  • @hguytigfjujufigfj2069
    @hguytigfjujufigfj2069 Před 2 lety +1

    Kubambe politician and economic moto kuti buuu chakwera kuti fwaaa

  • @kamwazabonomali825
    @kamwazabonomali825 Před 2 lety +3

    Reminds me of Bingu. This guy knows his story.

  • @ibrahimwaka3916
    @ibrahimwaka3916 Před rokem +1

    Problem with democracy is everyone wants to be leader.Everyone has solutions to the problems but you vote them in they are clueless. They start doing they own ways

  • @princekabvina1718
    @princekabvina1718 Před 2 lety

    The wise man!!!respect...

  • @stephenmondlane7844
    @stephenmondlane7844 Před 2 lety +1

    A chakwela walephela kuyendetsa bom. Steven from mozambique

  • @mulanjehydro6684
    @mulanjehydro6684 Před 9 měsíci

    Thats true mr Kabambe zinazi ndi mbudzi zawononga dziko lokoma lija

  • @wisdomchilanga723
    @wisdomchilanga723 Před měsícem

    No fear tell them truth how the dragon 🐲 swallow all the money

  • @RaymondKaumba
    @RaymondKaumba Před 4 měsíci

    Just like Monday coaches
    What did you do when you were in govt

  • @roychirombo1081
    @roychirombo1081 Před 2 lety

    Wise and great munthu oganiza boh amanenedwa uyuyu osati apuludzuwa

  • @HendersonGonnessph-px1rb
    @HendersonGonnessph-px1rb Před 3 měsíci

    Am waiting your book about your experience and economics please

  • @ryankabambe3298
    @ryankabambe3298 Před 2 lety +1

    👏🏽👏🏽👏🏽👏🏽

  • @AminAbbasi-xc4qk
    @AminAbbasi-xc4qk Před 29 dny

    🎉🎉🎉🎉🎉🎉✊✊✊

  • @charlessulumba2521
    @charlessulumba2521 Před 2 lety

    Great wisdom and speech, but trust ya aMalawi inathawa on politicians, becoz you change within seconds. Kukuvoteran basi ma adviser mbwee opanda nzeru, without economic backbone and expected services to poor Malawians. But anyway, may God intervene pa zochitika pa mpando umeneu.

  • @johnstonechipeta8277
    @johnstonechipeta8277 Před 2 lety +3

    This guy is brilliant " l wish kuti anthu amupase mpata wolamula zikoli🙏

    • @ibrahimwaka3916
      @ibrahimwaka3916 Před 3 měsíci

      Zapakamwa.Kungo peza mpando zimayiwarika.Amangofuna podyerera

  • @user-yi4oc4xz4v
    @user-yi4oc4xz4v Před 11 měsíci

    This is best

  • @user-zn5xh1ki5e
    @user-zn5xh1ki5e Před měsícem

    Making sense

  • @bobkenneth2947
    @bobkenneth2947 Před 2 lety +2

    Chakwera ndi Chilima please stop playing games please

  • @jbchidothi7166
    @jbchidothi7166 Před 2 lety +3

    That's voice of the failures just accept

  • @JuvenileDebwe-bv8ow
    @JuvenileDebwe-bv8ow Před měsícem

    kuti mavuto athe amafunika yemwe akudziwa vutolo this man may be capable sure

  • @leonardjika2100
    @leonardjika2100 Před 2 lety

    A NEW VERSION WILL GOVERN OUR LAND DON'T TELL ME WHAT TO DO I KNOW MYSELF HOW TO GOVERN A MY PEOPLE I KNOW HOW A SUCCESSFUL NATION SHOULD BE AND I WILL BE SUCCESSFUL SO HELP ME GOD

  • @MonicaThocco
    @MonicaThocco Před 9 měsíci

    Akulu akulu musamvutike zomalira kuti ndalama zikuchotsedwa ku bank ,komanso ndalama yagwa,nkhani yake ndi yakuti pali chinsinsi ndi ichi, akufuna ibwere ndalama yomwe imanenedwa ija ,kuti we are going to use one money,ziyambira ku Malawiko, ndalama zomwe zikubwera ku chokera kuja zikupita kuti ? 1, 2 achotsa ndalama ku bank ,cholinga chawo ndi chiyani? Pali chinsinsi chowopsya pamenepo chomwe chikuchitika

  • @samuelsergio5343
    @samuelsergio5343 Před rokem

    Mwalakhula zovekatu

  • @ramseychozale9526
    @ramseychozale9526 Před 10 měsíci

    True economy can't develop

  • @abisalomchunga6695
    @abisalomchunga6695 Před 2 lety

    I like u Mrs man

  • @maxwellchikwanjembaya4596

    Malawi 🇲🇼,,,,,,,,.....,,,,,,,,,

  • @EmanuelMwanza-ko7tm
    @EmanuelMwanza-ko7tm Před 2 měsíci

    President wakhala wovina nyau angakhale ndi nzeru that's why boma likumuvuta

  • @osamabinraden9391
    @osamabinraden9391 Před 2 lety

    👏👏👏👍

  • @aubreywallo1987
    @aubreywallo1987 Před 2 lety +1

    Kodi momwe munali pa mpando ku Bank kuja zonse zimayenda bwino?

    • @GiftJulius-gx2kb
      @GiftJulius-gx2kb Před 9 měsíci

      Understand akuti anali just gorvener of reserv bank.nayenso amayendela malamulo a presdent

  • @thondoyaenterprise3795

    Naked truth

  • @user-bs1bw7yz5u
    @user-bs1bw7yz5u Před rokem

    Àw😢

  • @dondamissonchdziwe3958

    Mukango khuta madeya mukuganiiza kuyamba za ndale cholinga mukakhala pampando muziba mulemere Mapwara ambwiyanu agalu osauka inu,mitu ngati zitanga sala zosungiramo anamapingo ndikazango bwerera ku malawiko tisaza kumane pazalewa iyai wina ndiza Mu ponda

  • @isaaczuze
    @isaaczuze Před 23 dny

    Awa ndi amunawa kwambili

  • @Benty_Pro
    @Benty_Pro Před rokem

    Dolo Kwambiri

  • @susantembo2076
    @susantembo2076 Před rokem

    Inde limbikirani blaming the president for everything so you can win in 2025.

  • @ibrahimjackson-cg6tc
    @ibrahimjackson-cg6tc Před 10 měsíci

    Mumatha abwana

  • @xevierharrykamiza3577

    Then why u didn't put this energy when u were within the system

  • @lifnetmakoka2175
    @lifnetmakoka2175 Před rokem

    nzeru izi mukalowa mboma zimapita kuti? politicians please please mumalamulira anthu osati nyama consider the welfare of poor malawians, muzikhalako ndi umuthu.

  • @RabsonMatope
    @RabsonMatope Před 17 dny

    Anthu anzeru alipo

  • @meesailikeyougirlmoosa9801

    Mmakwana boss posaeopa kutulutsa mau owonawa

  • @amosnyirenda5712
    @amosnyirenda5712 Před 2 lety

    for this reason my interest is to know you Dr kabambe

  • @anoldkapolo4493
    @anoldkapolo4493 Před rokem

    AKabambe mudalikuti apamukunamiza anthu lero? Osangonena kt mwayamba kubwebweta popeza pam'phika adakusamutsaponi? Ife ndi Chakwera 2030 wooolh

  • @rabsterkamoto8953
    @rabsterkamoto8953 Před 2 lety +2

    Yah ichi nde chilungamo

  • @johanessphili-ano788
    @johanessphili-ano788 Před 2 lety

    Mwazidziwa liti izi a Kabambe

  • @abdulullahkhamiss1236
    @abdulullahkhamiss1236 Před 2 lety

    Akuba awa

  • @susantembo2076
    @susantembo2076 Před rokem

    Ratios nazo

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 Před 2 lety

    Gbu

  • @jafarisani
    @jafarisani Před rokem

    Zinthu zinali bwino bwino koma tinagomera ndale, umbuli plus kupupuluma lero ndizi

  • @frstyhavoc6678
    @frstyhavoc6678 Před 2 lety

    Umatha ntchito yako ayise udangobadwira banja lolakwika 😀😀😀😀😀😀

  • @user-ky4ce9gb6j
    @user-ky4ce9gb6j Před měsícem

    Dolo kwambiri uyu

  • @alexnyirenda123
    @alexnyirenda123 Před 2 lety +4

    Just keep quiet my friend,,,

  • @innocentmanyera1861
    @innocentmanyera1861 Před 11 měsíci

    Machende

  • @harrisonmwanga9812
    @harrisonmwanga9812 Před 2 lety

    Munthu ofunika koma ku DPP ndiye mbola bola angoyambisa chake chifukwa ngati ali wa DPP angofana ndi chilima kapena Peter ku dpp

  • @paulvimbamvula9508
    @paulvimbamvula9508 Před 2 lety

    Uyuso a Malawi tinakuziwa kale mbiri yako...iyaaaah

  • @dennischikunkhuzeni5805
    @dennischikunkhuzeni5805 Před 2 lety +1

    Double speak....

  • @isilagmaulana9425
    @isilagmaulana9425 Před rokem

    Tausani

  • @chiefmalindi4070
    @chiefmalindi4070 Před 2 lety +2

    Zofunika okumwa ink izi osati chifukwa amalima bwino fodya kumunda kwanga

  • @jameskadete2196
    @jameskadete2196 Před rokem

    Dr ndi ma equasation awo

  • @kondwamlungu8384
    @kondwamlungu8384 Před rokem

    Chiuta akutumbike nasetamanya apo pafuma suzyo

  • @BonfacePhiri
    @BonfacePhiri Před 8 měsíci

    Mukunena zoona bwana

  • @moseselia6582
    @moseselia6582 Před 2 lety

    Iweyo unali koko thawi ya peter koma umalandila 20 billion ndiye apa ufuna unene chiyani

  • @moseselia6582
    @moseselia6582 Před 2 lety

    Oyamba kuononga dziko ndi ddp ndiye musatisokosele tionana 2025 takudziwa

  • @user-pn7ek7wb7n
    @user-pn7ek7wb7n Před rokem

    Wakuba iwe galu kwanasi

  • @abduljafari6577
    @abduljafari6577 Před 2 lety +2

    Agalu amkaona ngati kuyendesa boma kobwheka

  • @jkfodya9997
    @jkfodya9997 Před rokem

    Tidaonga vote ndithu

  • @kensonmbewe6692
    @kensonmbewe6692 Před 2 lety

    MUMANAMIZA AZUNGU INU KUTI MULI NDI MAKOBIDI AMBIRI

  • @gilbertmategula5613
    @gilbertmategula5613 Před 2 lety +1

    Chitsilu cha munthu

  • @henlyyassin1718
    @henlyyassin1718 Před 2 lety +1

    Mukanika kupanga produce ma companies ndalama mugula ma expensive houses and cars for your own. Ndalama mukuba Malawi is wise now, useless

  • @frankkamunde4575
    @frankkamunde4575 Před 2 lety

    mbava zikuluzikulu kunamizano mtundu wamalawi kufuna mavoti 2025 anthuwa zawo ndizimodzi tinatopa ndimodza ife

  • @peterkasema9948
    @peterkasema9948 Před rokem

    Kodi satta alikuti

  • @yaowking4609
    @yaowking4609 Před rokem

    Boma.ili ndi laziiiiii

  • @princedetbozsmallboy1749
    @princedetbozsmallboy1749 Před 2 lety +1

    Fuso labwino kwambili kuti kodi ma doller wose anawapeza mu boma alikuti?

  • @gabrieljulius6151
    @gabrieljulius6151 Před 2 lety

    Sono akafusidwa akuyankha
    Akut ayi umboni ndi uyu

  • @isaacthomas4005
    @isaacthomas4005 Před 2 lety

    Khala chete iwe Dalitso suja unatibela ndalama nthawi yako ija ku Reserve Bank pamene unkadzilandiritsa K30 000 000 pamwezi. Sitinaiwale. Komaso unachita manufacture accounting yako kuti upeze ngongole kuIMF kuchitira kuti iwe ndizitsiru zinzako zakuDPP mupezeko kangachepe. Iweyo uli part of Malawi's problems sungatipatse ansala

  • @victorchikuse9837
    @victorchikuse9837 Před 2 lety

    Useless voice you were there kmano nothing you did ndie apa mukuoneka ngati wanzeru poti uli kunja kwa office, mnthawi ya Peter muthalika kwacha inagwa kangati? Kod chi nyengo chimene zonnet sattar amapanga ndi boma anayamba liti?