NKHANI YONSE YAKUSOWA KWA DR CHILIMA KWAGWANJI đŸ˜± NDI BRIAN BANDA

SdĂ­let
VloĆŸit
  • čas pƙidĂĄn 9. 06. 2024

Komentáƙe • 19

  • @BenissoneErnesto-eh6zs
    @BenissoneErnesto-eh6zs Pƙed měsĂ­cem +3

    Mcp ija ndimeneyi yabwera kuzatilamulira osati masewera ayı live in Mozambique

  • @abduhrwahmaansilverbanda4908
    @abduhrwahmaansilverbanda4908 Pƙed měsĂ­cem +2

    Kod samadziwa kut nyengo silibwino nde bwanji samagwilotsila ntchito helicopter chakwela anaononga Sadick Mia pano ndi izi

  • @AdoreNgoleka
    @AdoreNgoleka Pƙed měsĂ­cem

    Amalawi tizizinverako chisoni pls osamangotengera kusatira anthu ena tizivota mozindikira taonani sopano izi zidayamba zachitika kumalawi? Otiuza adalipo ochuluka kobasi lero ndiizi 😱😱😱😱

  • @JosephMkandawire-sq7uf
    @JosephMkandawire-sq7uf Pƙed měsĂ­cem +1

    I just think that he wants to coup country or he's on accident please searching must be done so quickly thanks

  • @CollingsJohn
    @CollingsJohn Pƙed měsĂ­cem +1

    2:03 2:04

  • @abduhrwahmaansilverbanda4908
    @abduhrwahmaansilverbanda4908 Pƙed měsĂ­cem +1

    MCP sichipan koma kuononga zithu bas kale zimachitika mu nthawi ya mcp panoso ndi iziiii

  • @JafaliAjusa-zg2xi
    @JafaliAjusa-zg2xi Pƙed měsĂ­cem

    Times radio timakudalilani kwambili, musamadzungulile ngat simukuziwa please, tell us true

  • @NtabaKali
    @NtabaKali Pƙed měsĂ­cem

    Zosayenda iziiiiiii😱

  • @AmiduKachingwe
    @AmiduKachingwe Pƙed měsĂ­cem

    Tangosiyani mukutinyasa kusowa kwa Hani mumufuse bwino chakwera ndi Bshili

  • @ChiukuseIbrahimJNapoloMakungan
    @ChiukuseIbrahimJNapoloMakungan Pƙed měsĂ­cem

    Tell us the true please we are here to be waiting the result

  • @MoreenBanda-mh6el
    @MoreenBanda-mh6el Pƙed měsĂ­cem

    đ‘ș𝒊𝒔𝒌𝒂 𝒂𝒌𝒖𝒐𝒏𝒆𝒌𝒂 𝒘𝒂𝒄𝒉𝒊𝒔𝒐𝒏

  • @KassimmwStevenetc
    @KassimmwStevenetc Pƙed měsĂ­cem

    Apa asatinamize achakwera achitakukoza izi asatinamizepo apa

  • @user-sx7in9vr6b
    @user-sx7in9vr6b Pƙed měsĂ­cem +1

    Koma zitheka bwanji zimenezi

  • @ChiukuseIbrahimJNapoloMakungan
    @ChiukuseIbrahimJNapoloMakungan Pƙed měsĂ­cem

    Tell us the truth please

  • @user-vl8uw8mc3u
    @user-vl8uw8mc3u Pƙed měsĂ­cem

    Chakwela ayamba kupha sidiki miya pano ndi chilima enanu samalani iyi ndi mcp chakwela

  • @innocentmusuli7380
    @innocentmusuli7380 Pƙed měsĂ­cem

    Zosayenda

  • @fostersymon3564
    @fostersymon3564 Pƙed měsĂ­cem +1

    A MALAWI NDIIFE OKONDA MA COMEDY ,,TISAIWALE KAMLEPO KALUWA ,ANAZIPANGE SELF ABDUCTION

  • @ChiukuseIbrahimJNapoloMakungan
    @ChiukuseIbrahimJNapoloMakungan Pƙed měsĂ­cem

    Tell us the truth please