Chakwera Apangisa Mkulu Wina Kuzuzula Achewa

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 27. 06. 2024
  • #chilima #chakwera #news ##malawi #trending #viral

Komentáře • 97

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w Před 2 dny +10

    Uku ndiye kulankhula, munthu ozindikila ameneyu. Zoona zokha zokha ❤

  • @IbrahimPhiri-ky5jk
    @IbrahimPhiri-ky5jk Před 2 dny +7

    ❤❤❤ ukuoneka nkhati unayendako pang,ono amwene mchifukwa chake mulungu akusegulako manso mulungu apitilize kukuonensa manso phenya

  • @user-kx3en7hy5j
    @user-kx3en7hy5j Před 2 dny +5

    Thanks for mentioning my Tribe Yao
    Watching from
    Meka Saudi Arabia

  • @JamesOsman-cz9cw
    @JamesOsman-cz9cw Před 2 dny +4

    From south Africa

  • @user-fx2xw2bn4d
    @user-fx2xw2bn4d Před 2 dny +3

    Chakwela bulutu la muthu kkkkk akuti tichotse katundu ameneyu waola akununkha

  • @AlexManuelMisomali-sv1vn

    Mdala iwe ndiwe number one komanso chitsanzo chabwino cha mtundu wako

  • @user-ui4ux5kc8d
    @user-ui4ux5kc8d Před 2 dny +3

    Ambuye akhale nawe mdala iwe waonetsa mtima wachikondi osati anthu adyerawa akungomunamiza presedent kumaombera fiti mmanja mzothekanso presedent kukhala wabwino koma atidye nawowa akumulakwitsa mmauphungu awoo

  • @BENSONRANGWANI
    @BENSONRANGWANI Před 2 dny +2

    Chakwela wamupha chilima zasala zosatila Zach

  • @AlexMthunziChimpeni
    @AlexMthunziChimpeni Před 2 dny +3

    Inuyo mumayitha chilungamo chokhachokha.🎉🎉🎉🎉

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 Před 2 dny +3

    Ine ndine Mchewa, koma Chakwera ayi.

  • @SolomonMbewe
    @SolomonMbewe Před 2 dny +4

    Achewa koma gule wamkulu basi....

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 Před 2 dny +2

    Amalawi MCP yawonongadi dzedi iiii dzomvutsa chitsoni anthu akulila pankhani chuma ndikuphatso chilima inu a MCP agalu kwabasi

  • @MikeMerecah
    @MikeMerecah Před 2 dny +3

    Mwatiimirira Dara ngati mumaganiza choncho ndinumamuna weniweni,

  • @Yungjoe786
    @Yungjoe786 Před 8 minutami

    Muyao to the world#proudlyndinemuyao

  • @HallimaMakwinja
    @HallimaMakwinja Před 2 dny +2

    Zoonadi ife ochewa mvitsirutu kkkk ulemu wanu wakulu

  • @Musa1828-l5d
    @Musa1828-l5d Před 2 dny +2

    Ndipo mchewa ndichitsiru kwambiri mapeto

  • @EllenPhiri-xt8pt
    @EllenPhiri-xt8pt Před 2 dny +1

    Iwe wayankhula zenizeni mwana reality yeniyeni

  • @AmosKalembo
    @AmosKalembo Před dnem +1

    Iweyondiozindikila kwambili mall fire

  • @MarcosDjussa
    @MarcosDjussa Před 7 hodinami

    Koma amalawi akanat azinganiza ngati mndala uyu Malawi 🇲🇼tikusimbalokoma kulakhula chilungamo mulungu akuendele ukhalise

  • @bysongeorge3243
    @bysongeorge3243 Před 2 dny +1

    Uyu weniweni m'Chewa kulankhula chilungamo.. MCP eni wake ndi mizwanya yoganiza bho ya ku Mpoto ya nthawi imeneyo yomwe inayambitsa chipanichi, komabe ndale zathu zinasokonera ndi azitsogoleri ndikubwera kwa matipate..dziko linagawikana patatu ndipo timavotera kuti uyu wakwathu . Zinalakwika kwambiri ndipo tinadzala mbewu yoipa ..

  • @MustaphaCassim
    @MustaphaCassim Před 2 dny +1

    Odala inu ndi olikonda dziko lanu komaso ndiinu munthu odzindikila ife tabadwila mu mtandile achewa amakonda tea lero sugat ndi 5000 from 500

  • @MphatsoMwale-it4xd
    @MphatsoMwale-it4xd Před dnem +1

    Inu akulu mulungu apitilize kukuoneserani

  • @GraceLimani-zw7dx
    @GraceLimani-zw7dx Před 2 dny +1

    Ndipo chilungamo a chewa ndife zitsiru koipa timangovetsera zopusa kuti ndife a mcp basi ma gofer za zii koma osatukuka mchewa basi mangovina nyau basi tayambitsa nda chewa kusankhana kwa mbiri chitikuko mwangopanga Central Region koma a chewa sitikuona eti toll gate ikapezeka kwathu kwa chatata ndi ku mchezi

  • @kaungabondera892
    @kaungabondera892 Před 2 dny +1

    That's true

  • @FelixBoss-yn9pe
    @FelixBoss-yn9pe Před 2 dny +1

    Oputsa sitonse ochewaa olipo wena Openya nithu ah yayi dala mwatiyankhulila chamuna

  • @user-tb6yh1kx3o
    @user-tb6yh1kx3o Před dnem +1

    Odhala Inu ndi oganiza bhoo

  • @user-mi2xf3sw1i
    @user-mi2xf3sw1i Před 2 dny +1

    Umunthu uwu kumayankhula mmeene zilili

  • @AlexManuelMisomali-sv1vn

    😂😂😂 mkulu iwe achewa anzakowo akuphatu

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y Před 2 dny +1

    Zoona big man

  • @user-zt7hy5lh4r
    @user-zt7hy5lh4r Před 2 dny +1

    😂😂😂😂😂😂😂😂 kkkkk koma abale ai kuli zinthu 😅😅😅😅😅😅

  • @IshmaelJohn-iz1ej
    @IshmaelJohn-iz1ej Před dnem +1

    Chakwela ndi ng'ona ya munthu

  • @louismagongwa
    @louismagongwa Před 2 dny

    kkkkk kk😅😅😅 mavuto alipo ndipo sanat nanga akadzawinas kape ameneyu

  • @ChristopherKabanga
    @ChristopherKabanga Před 2 dny

    ukuyenda osavara chifukwa cha uchitsilu wakowo ukufuna chakwera akupitise kwamereka mchewa wanji galuu lwe

  • @user-bu7ut2gb7o
    @user-bu7ut2gb7o Před 11 hodinami

    Iwe ndiwe mbuzi kwabasi. Utsogoleli sutengela mtundu ayi koma chikhalidwe cha umunthuyo. Iwe ndi mbunde.

  • @zayedmitawa8345
    @zayedmitawa8345 Před 2 dny +1

    Kulankhura tchutchutchu

  • @AufiThera
    @AufiThera Před 2 dny +1

    Live Bola ulamulilo uzipita Ku mpoto or kumwela not agaluwa mmmmm timwat magaz chakachino kusiya tiyi😪😪

  • @fannyzimba149
    @fannyzimba149 Před 2 dny

    😂😂😂😂kalikose tikanva ndi kukaona chaka chino

  • @samchibenene4458
    @samchibenene4458 Před 2 dny +1

    😂😂😂😂😂achewa dzukani wayankhuladi muchewa iwe

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg Před 2 dny

    Ndinudi dzisilu dzokonda kupha anthu machende anu achewa😂😂

  • @user-bu7ut2gb7o
    @user-bu7ut2gb7o Před 11 hodinami

    Mawu awa ndiwodzetsa mpatuko pa mitundu ya anthu. Tiyeni tizinena za ukapolo tilimowu osati za mitunduyi. Galu iwe undinvetse

  • @LastenWesele-wq8jh
    @LastenWesele-wq8jh Před 2 dny +1

    Izi ndizowona achewa ndi mbuzi zimafela ichi Chipani chagogo anthu

  • @StewartGoma
    @StewartGoma Před 2 dny

    Soon malawi will be like kenya
    Malawian are suffering living is so expensive

  • @AufiThera
    @AufiThera Před 2 dny

    Kkkkkkkkkk muchimina zonantoza pa president Aku mwera

  • @user-oc9vl9xz8e
    @user-oc9vl9xz8e Před dnem

    Ndilo zoona muwalangize ochewa anzanuwo kuti akavote moganiza bwino bwino wa nyauyo achoke basi antu apeze mdendele

  • @TerryNac
    @TerryNac Před 2 dny

    Chitsilu ndi chimodzi osati a chewa onse Loma chitsilu chikuoneka

  • @user-rg4du4vu9r
    @user-rg4du4vu9r Před 2 dny

    Ndizowonadi km inetu ndinkadabwa kt ku marawiko kukangot kwagwa njara achewa onse amakazaza kwathu kumpoto chaka ndicha nde kumazifusa kt kodi osayesako njira zina bwanji pot akat chakudya sikut ndi nsima yokha ayi kkkkkkk wandiwaza aise mitu izigwira ntchito osamango swana ayi achewa mwanva

  • @user-kr1tf2tu7s
    @user-kr1tf2tu7s Před 2 dny

    Kodi iwe pulezident wake uti mbuzi yamuthu iwe.akumwera kwake kuti anakupNgira chiyani

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b Před 2 dny

    Inu ndi munthu woganiza bwino kwambiri ndipo muli ndi nzeru auzeni ndithu

  • @martinnyirongo2892
    @martinnyirongo2892 Před 13 hodinami

    Mchewa ntchito yake ndikuba bas, not kuyendetsa dziko ai koma amalawi ee mistake tinaipanga Kaya tiyikoza bwanji

  • @BillySimkonda
    @BillySimkonda Před 2 dny

    Kachilungamo kabwanji aka??????

  • @user-rd4ft9nd8t
    @user-rd4ft9nd8t Před 2 dny

    GOD HAVE MERCY ON US

  • @EmmanuelKaziyenda
    @EmmanuelKaziyenda Před 2 dny

    Ukunana iwe ndekuti umangokhala manja kotsa iwe udikira za ulele ubwere kuno kumponela udzawone mmmene anthu akugulira fertilizer wa cash iweyo ndiwe chitsiru not chakwera

  • @WilliamBandaWili
    @WilliamBandaWili Před 13 hodinami

    Koma mchewa wanzeru ngati uyuyu sindinamuone walankhulatu wakumva wamva

  • @user-rf4br1fv2z
    @user-rf4br1fv2z Před 2 dny

    Iweyo anthu aku mwela akulamulila tanena chomwe chinachitika ku lilongwe iweyo za kwanu osati zopusazo nyawu zo nvuto ndichiyani zoti amakuyuzani anthu sumadziwa kodi anthu akukugulani mala nfi anthu akut mbuzi yamuthu

  • @TawongaGSMwale-cc2vm
    @TawongaGSMwale-cc2vm Před 2 dny

    Apo mwayakhuladi Baba katundu uyu Kut alowe mu boma adalowa ndima demo kuzatulusaso katundu ameneyu pakufunikiraso pazakhale ma demo

  • @ChifundoChiwanda-ru3pg
    @ChifundoChiwanda-ru3pg Před 2 dny +1

    Zosayenda

  • @user-ww9rj2wx8d
    @user-ww9rj2wx8d Před 2 dny

    Zikomo poti mwazindikila nokha achewa

  • @user-it5zv2nz7f
    @user-it5zv2nz7f Před 2 dny +1

    Mchewa wakuzindikila uyuyu ulemu wanu

  • @samdiverson9733
    @samdiverson9733 Před 2 dny

    Mposo kobasi 😢

  • @henryhenry6632
    @henryhenry6632 Před 2 dny

    Panyini pamako iwe wava kapolo wachabe chabe

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 Před 2 dny

    Paja chakwela ndi nyau 😂😂😂

  • @user-tm3zh5zk4t
    @user-tm3zh5zk4t Před 2 dny

    Iwe si chewa ayi iwe ukayelekeze ndianthu akumwela samalima ndiye apa akuwona kuti boma lapana alibe mweya

  • @JohnNdau-bl4op
    @JohnNdau-bl4op Před 2 dny

    Kkkk

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy Před 2 dny

    Ndipo live sekulan maso Achewa thaw yatha

  • @omaligeorge4296
    @omaligeorge4296 Před 2 dny

    Koma he is fact guys mnthuyi inu data mukutsitsayo ipindura chani kwa mnthu waku mudxi tamaganizani please

  • @jamesgama5489
    @jamesgama5489 Před 2 dny

    Koma iwe nde mchewa weni weni wapa phata mchewa koma ufumu kuvina gule ndipo sazatheka kusintha

  • @user-tb9ib4mu7c
    @user-tb9ib4mu7c Před 2 dny

    Mmanyang'watu 😂😂before

  • @EdisonNakulenga
    @EdisonNakulenga Před dnem

    Kkkkkkkkkk

  • @chitanibenito1109
    @chitanibenito1109 Před 2 dny

    Ka mtundu kopusa!!!

  • @HanifaTabia
    @HanifaTabia Před 2 dny

    Kkkk bola mukuziwa

  • @ExcitedBreakingWaves-oh3zb

    Anyamata aku danbwe amenewo .

  • @user-ke7ii6ip4s
    @user-ke7ii6ip4s Před 2 hodinami

    😂😂😂😂❤❤

  • @omaligeorge4296
    @omaligeorge4296 Před 2 dny

    Koma guys eeeh

  • @FelixBoss-yn9pe
    @FelixBoss-yn9pe Před 2 dny

    Nakondwa nawe nzedi

  • @user-ln3zx6wo4w
    @user-ln3zx6wo4w Před 2 dny

    Exatly

  • @DavidMtambo-zm8ne
    @DavidMtambo-zm8ne Před 9 hodinami

    Zoona atiranga

  • @alicehananiya
    @alicehananiya Před 2 dny

    😂😂😂😂😂 katundu ameneyi achokedi

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl Před 2 dny

    Ndi mbusi zachabe chabe mcp

  • @user-un6qv6sj3h
    @user-un6qv6sj3h Před 2 dny

    Kuyanhula monga mmalawi weweni

  • @oscarnamirecah5386
    @oscarnamirecah5386 Před 2 dny

    😂😂😂😂😂😂😂😅😅😅

  • @user-uc1pd1tc2x
    @user-uc1pd1tc2x Před 2 dny

    Chilungamo koopsa zedi apapa ndikoyambadi ndikomaliza 2025 kwanu kwatha guys.

    • @user-eh1mg3ww6d
      @user-eh1mg3ww6d Před 2 dny +1

      Achewa ndi athu oipa ndipo ndi athu ozikindikila achewa ndi wadziwa ndichifukwa ineyo sinamuvotele chakwela mulungu atithandize ku Malawi

    • @user-uc1pd1tc2x
      @user-uc1pd1tc2x Před 2 dny +1

      @@user-eh1mg3ww6d Ndipo ndi anthu achabechabe, umadziwa Nyau ineee kuvotatu sindinavoterepo chipani china chilichonse kuposa DPP Ndipo family yakwathu yonse ndiife a DPP Mpakana kale Tri

    • @user-eh1mg3ww6d
      @user-eh1mg3ww6d Před 2 dny

      @@user-uc1pd1tc2x koma tiphele kwambili kuti m,busa ameneu mulungu atichitile mmm ayi ndithu athu tazuzika kwambili

  • @chitchohistorical1036

    😂😂😂😂😂😂😂

  • @giftdavie240
    @giftdavie240 Před 2 dny

    What is democracy important for if it incourages tribalism. We're the people of the same nation but we're being divided because of democracy. Someone who's brain function properly will realize that the route cause of these all sources of drama is democracy

  • @LidasoniManual
    @LidasoniManual Před 2 dny

    🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣

  • @JIMMYWATSON-ph5jg
    @JIMMYWATSON-ph5jg Před 2 dny

    Mandenga wako iwe bulutu siwe mchewa chakwera sanakulakwire adakulakwila ndi abambo ndi amako kukhala osauka iwe galu kwa basi

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of Před 2 dny

    Ndiwe galu chitsilu mbuzi yamunthu choka usatinyase

    • @MikeMerecah
      @MikeMerecah Před 2 dny +1

      Manyazi bwa ifeso ndi achewa koma munthuyi wanena zoona mpaka kuphana chifukwa Cha mipando nafe zikutiwawa,

    • @Aisha-db6ds
      @Aisha-db6ds Před 2 dny

      Chakwela wationesatu zinthu

    • @NovassTambala
      @NovassTambala Před 2 dny

      Koma mr mwalankhulatu ndi gonthi lamuthu chakwela mbudzi akulu hmmmm inuyo mwayedadi ndipo

  • @ClaudiaarmandoMafunga

    Zoona ife achewa tili ndi vuto

    • @user-bu7ut2gb7o
      @user-bu7ut2gb7o Před 11 hodinami

      Vuto lanji? Mukuona ngati vuto limadza kamba ka mtundu wa munthu? Musapuse gayezi ufiti wa chakwela usakhudze achewa tonseyi