Zomwe ayankhura Mai Joyce Banda zokhunza Tonse Alliance kucha kwa Lero

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 13. 07. 2024

Komentáře • 52

  • @PreciousKaliati-l6u
    @PreciousKaliati-l6u Před měsícem +3

    Your excellency,Dr banda, your charitable initiatives are reflection of your remarkable character and dedication to the betterment of society. Keep shining mama , kudana ndi inu ndi thembelero chabe.God bless you

  • @MphatsoMhoney-xn2ft
    @MphatsoMhoney-xn2ft Před měsícem +2

    Malawi leaders are always talk wisely when they are out of gavervent,give them charnceand see there performance

    • @mwale86
      @mwale86 Před měsícem

      This one performed kungoti amalawi mpandila u can't appreciate because she is a woman,when she came in kunalube fuel kunalibe Forex anthu kuchipatala kumwalila because of magetsi after generator zinalibe fuel magetsi akuzima mwanyasi but she did it in just 100 days I feel that's something we need to acknowledge that she did good.

    • @chelseajackson3200
      @chelseajackson3200 Před měsícem +1

      Performed where?? She is full of family politics. Look at her age kukakamila leadership in PP. I bet she was one of those voices calling for Chilima to join MCP! Fully knowing that she will get in through the backoffice.

    • @Lee-lee-w1r
      @Lee-lee-w1r Před měsícem

      @@mwale86why do you want to make women to look like they are the most hated beings for no reason?? Pali zinthu zina zake adachitadi bwino koma anapoilabe ndithu.

  • @chelseajackson3200
    @chelseajackson3200 Před měsícem +2

    Alipo women & girls oti anapindula ndi izi akamba awa?? Atchuleni. She could've mentored a girl or girls for presidency if she was sincere😢😢

  • @SanidaChirwa
    @SanidaChirwa Před měsícem +4

    Our excellent ngat mfuna mbiri yanu izakhale yabwino mkamwalira ,tulukani mu Tonse Alliance,mpakidwa magazi oyipa kwabas

  • @user-uv5rf4zt5q
    @user-uv5rf4zt5q Před měsícem

    The best leader

  • @GilbetaMasamba-te8kp
    @GilbetaMasamba-te8kp Před měsícem +1

    God continue bless you your excellency ma, your such a blessing to malawi

  • @NatashaMakay-k5e
    @NatashaMakay-k5e Před měsícem +1

    Anthu omwe munapanga ngwilizano, mumafunika kutuluka kalekale. Mwaona zisankho zayandikila muzioneka ngati okonda anthu..antku munawatengela kumavuto.

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 Před měsícem +5

    Aaaa awa amayi adyela adzuzitsa malawi kutipatsa MCP yokupha komatsa yankhaza iiiiii tsitidzayiwala mayi banda anatipanga nkhadza dzedi chifukwa chofuna moyo wawo kukhale pabwino otsati amalawi akhala pabwini ayiiiiiiiiiiiiiiiiiiiii mulape mulungu akhululukileni mwanatiyika pa dzuwa

  • @chikondichanza9772
    @chikondichanza9772 Před měsícem +1

    Mayiwa is one of the creams ku Malawi Kuno. Awawa ndi machine enieni. Kudana ndi mayi awa ndikudana ndi chitukuko. aMalawi amzanga alot of known countries are recognizing her as very important trustworthy and helpful woman , why not us . Lord should have mercy on us , so that we can how potential this woman is. aMalawi tinazolowera kutamikira munthu akamwalira.what a shame

    • @juntoiman
      @juntoiman Před měsícem

      Mmmmm Iwe wachibwana Eti Ameney Mesa ndimunthu Modzi adapusisa malawi

  • @user-ry9ql9jv3y
    @user-ry9ql9jv3y Před měsícem +1

    This woman is our Gem. Very good and we love you

  • @MaryMlomba
    @MaryMlomba Před měsícem +1

    Repent before it is late

  • @RuthChilobwe
    @RuthChilobwe Před měsícem +2

    Kkkk Ndàlqma za cash gate zao sadzatenga kumanda.ayi..kumwamba sikufuna cuma..nkhale awawa a mr Sattargate wa a mcp wa ndi zinduna zaozi.kwa Yehovah kuchiweruzo sadzatenga Sattargate chuma chaocho amenYoù honoüable Robbers of our nation just be awaiting to be thrown in ĥll fire by Jesus Cĥrist.for crime of Stealing or Robbing malawi nation.all the same .be blessed as you walk towards jesus christ to be judged

  • @mkajikosya-uq5hs
    @mkajikosya-uq5hs Před měsícem

    God bless her excellence Dr Joyce Banda

  • @dianachabs
    @dianachabs Před měsícem +2

    Ambuye adzikudalitsani masten ntchito zachifundo ndiye mukuzichita

  • @AlexBand-f4p
    @AlexBand-f4p Před měsícem +1

    Mwaganiza bwino kwambirimbiri tulukakoni kumeneko mwaganiza bwino kwambiri mayi zikomo zikomo

  • @vitujames53
    @vitujames53 Před měsícem +1

    Chipanda Dr Joyce Banda sitikanadziwa kuti mu Boma mukunedwa ndalama

    • @mwale86
      @mwale86 Před měsícem

      Ndipo zowona no president has allowed an audit while in office it's only HE Dr Joyce Banda mayi awawa ndikatundu

  • @henryphiri6100
    @henryphiri6100 Před měsícem

    Unakasiya Chilima mkamwa mwa Ng'ona.

  • @BenardPhili-wp5jt
    @BenardPhili-wp5jt Před měsícem +1

    Amayi anthu timakukondani komanso Inu Mai mumatikonda amalawi munawamangira yumba anthu osauka ambirimbiri kuno kunkhamenya, anthu atavutika ndi ngozi za madzi munawathandiza powamangiranso nyumba kumwera

  • @FosterChakanga
    @FosterChakanga Před měsícem +1

    Tulukakoni masten,,asakupakeni nawo manyiwa pliz.Inu ndi mbambande

  • @gladysbonongwe1038
    @gladysbonongwe1038 Před měsícem +6

    Makhuluku akumalawi

    • @vitujames53
      @vitujames53 Před měsícem

      Ukhuluku wakuti anasintha dzikoli with 100 days ukhuluku anapangila kuti

  • @PreciousJames-fh1xs
    @PreciousJames-fh1xs Před měsícem +1

    Amai mumakwanila palipose zitukuko muno mudziko lamalawi mwapanga m, boma ririrose
    Tikanena zothandiza osowa nde ndikudya kwanu ndipo simuona khope kana mtundu
    Amai Banda Mulungu azikudaritsan thawi zonseeee eee

  • @DevisonHala
    @DevisonHala Před měsícem

    Inu mayi chilima mumanena kuti ndi mwana wanu ndiye munachilandila bwanji chipongwe chimenechi

  • @vitujames53
    @vitujames53 Před měsícem

    Anamanga nyumba Kameme , Chisenga in Chitipa District..
    Chilumba and Khwawa in Karonga
    Chintheche, Bandawe, Vizara, Chisala in Nkhata Bay
    Mzimba Boma, Njuyu, Thunduwike, Nkhamenya in Mzimba
    Lula and Ng'onga in Rumphi list endless under Mudzi Transformation

  • @BlessingsBanda-nh7ur
    @BlessingsBanda-nh7ur Před měsícem

    Zilibwino koma zomayika background music instrumental ndizopoyila pama serious massages

  • @isaihmagani5697
    @isaihmagani5697 Před měsícem

    Lankhurani chabe chichewa

  • @vitujames53
    @vitujames53 Před měsícem

    Anthu amalandila nkhuku kumaweta mabanja kumapeza ndalama ndikumadya bwino panyumba pawo..
    Mbuzi, N'gombe

  • @SaeedHurzrut
    @SaeedHurzrut Před měsícem +1

    hule wachabe chabe

  • @vitujames53
    @vitujames53 Před měsícem

    Nthawi yawo mankhwala mzipatala samasowa..kunalibe basi kaguleni ku pharmacy

  • @Shelifibraheem
    @Shelifibraheem Před měsícem

    Mmmmmm m'mai otapa tapa uyu uliboh mudzapita ndindalama amzathu

  • @vitujames53
    @vitujames53 Před měsícem

    Nzeru zawo ndizopititsa patsogolo dziko maka maka anthu ovutika ammamidzi

  • @vitujames53
    @vitujames53 Před měsícem

    Ambuye azikudalitsani ndikukupatsani moyo wautali

  • @rightlombe380
    @rightlombe380 Před měsícem +2

    Which youths do you assist?

    • @mwale86
      @mwale86 Před měsícem

      Ambilimbili through her community Development initiative project people mainly youths benefitted kupeza chakudya in kasungu isn't that helping youths??

    • @mkajikosya-uq5hs
      @mkajikosya-uq5hs Před měsícem +1

      Ambiri anapindula anagawa njinga zamoto pano akulipilira ana ma school fees through Joyce Banda foundation

    • @mwale86
      @mwale86 Před měsícem

      Ndipo zowona zake even she feeds over 15,000 children through her Joyce Banda foundation pajatu Amati mmela poyamba hence ana akakula bwino azakhala ma youth othandiza dziko lawo​@@mkajikosya-uq5hs

    • @vitujames53
      @vitujames53 Před měsícem

      Kodi kabaza ku Malawi kuno anabwera ndindani

    • @vitujames53
      @vitujames53 Před měsícem

      Tapitani ku ma secondary a Boma mdziko muno atsikana akupelekedwa ma fees..

  • @vitujames53
    @vitujames53 Před měsícem

    Mzimayi wachikondi uyu

  • @JusticeMpondaphili
    @JusticeMpondaphili Před měsícem +1

    Awa ndi mai amzelu sangakakamile ku mcp acokako