Palibe Chamuyaya Pa Dziko La Pansi - Hon Kamlepo Kalua

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 10. 07. 2024
  • On Nyasa VoiceBox, Hon Kamlepo Kalua says nothing is forever. Especially Political Power and Politicians.
    Pa Nyasa VoiceBox, Olemekezeka a Kamlepo Kalua akuti pa Dziko La Pansi Palibe Chamuyaya. Makamaka Mphamvu za Ndale Komanso anthu andale.
    #malawi

Komentáře • 37

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y Před 23 dny +6

    Good Messnge Mr Kamulepo kaluwa, Chakwela you mast go

  • @user-be5fc3ed1i
    @user-be5fc3ed1i Před 23 dny +3

    Amene kamulepo kalua ndimamziwa ndi ameneyo nthawi yamakezanayo ankayimba nyimbo zamatikitikii tiki tiki zamatikitiki so samalani amcp ndi chakwera wanuyo

  • @CHARLESMASINA-xx5kt
    @CHARLESMASINA-xx5kt Před 22 dny +1

    A great speech sir ...so wise and mature

  • @user-qq3ip1od6i
    @user-qq3ip1od6i Před 23 dny

    We are wit you sir, all the way.... God be wit u n the whole family

  • @user-mh7cc8up4i
    @user-mh7cc8up4i Před 22 dny

    Ulemu wanu Mr kamulepo ambuye akutetezeni Ku khwandwe za MCP we love you ❤

  • @user-eh1mg3ww6d
    @user-eh1mg3ww6d Před 22 dny +1

    Ndipo ndizoonadi apolice akumalawi ziwani kuti mawa limafika ine ndikupepha kuti ualamulilo wakuphau ukazangochoka apolice ose azawachotse tchito mmm ayi

  • @beakab2378
    @beakab2378 Před 23 dny

    Viva KK, great message 👍

  • @PrincepreciousMwasangwale

    Wise man 😊

  • @princedetbozsmallboy1749

    Listen is better than beautiful sacrifice, palibe chamuyaya

  • @MadalitsoTamayenda-ez5pj
    @MadalitsoTamayenda-ez5pj Před 23 dny +1

    Yex thus fact becareful ma fon amene anaranda apolice akufune ayikemo ma poison at the end aperekeno what kind of this government am be shame😢😢😢

  • @user-fi7ko7bl6f
    @user-fi7ko7bl6f Před 23 dny

    I salute you Mr K K

  • @SteveAngaMuwellah
    @SteveAngaMuwellah Před 22 dny +1

    Mwaputa olakwika....

  • @Raph-kayRaph-kay-g5v
    @Raph-kayRaph-kay-g5v Před 23 dny

    Respect to you Mr kamulepo

  • @frankiechasokoneza5802

    Bravo Mr kamlepi kaluwa

  • @aubrygrasten1441
    @aubrygrasten1441 Před 23 dny

    Great voice sir

  • @AdoptedNaijaBoy
    @AdoptedNaijaBoy Před 22 dny

    Patiently waiting for the day to see cctv footage of the fools mumu police

  • @user-db3mh9wr9v
    @user-db3mh9wr9v Před 22 dny

    This Chakwera must go they take people like fools

  • @lovenesskampira
    @lovenesskampira Před 23 dny

    Ku Malawi si kulilongwe kapena kukasungu hiyaaaa!!!!

  • @frankjolijo
    @frankjolijo Před 23 dny

    Kamulepo Kaluwa🙏🔥👊🔥

  • @user-fi7ko7bl6f
    @user-fi7ko7bl6f Před 23 dny +1

    Tell them the liyaliya😅😅😅

  • @LumbaniNeba-d9n
    @LumbaniNeba-d9n Před 23 dny

    Mawu amphavu Mr Kalua

  • @cacksygustarf6260
    @cacksygustarf6260 Před 23 dny

    Tell dem sir agalu amenewa hiyaaa

  • @user-fi7ko7bl6f
    @user-fi7ko7bl6f Před 23 dny

    Hiyaa! Mwanyanya a MCP kwatola amalawi lero mwakumana nazo,muyesa Malawi yu ndi wamanu agalu okupha

  • @MadalitsoTamayenda-ez5pj

    Respect

  • @iamandypandy
    @iamandypandy Před 23 dny

    Mwalasa honourable Kaluwa you should stand for presidency you will get support from Malawians

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 Před 22 dny

    Aaaa MCP anadzolowela kupha ndi kudzuza anthu mistake tinapanga poyibwedzelatso boma iiii

  • @StevenGoodson-kn7ug
    @StevenGoodson-kn7ug Před 23 dny

    😂😂😂😂 kwachema

  • @juliusnjerengo2610
    @juliusnjerengo2610 Před 22 dny +1

    We worn you guys about Chakwera and MCP you didn't listen. Chakwera ndi munthu oipa mtima and he has never been a pastor.

  • @Cathy-oc7vd
    @Cathy-oc7vd Před 22 dny

    You always chase money... thumba mukauma (dry) you make noise.. it has been ur tricks.. you have been always following the party that is ruling kusaka ndalama... ine simungandipusise nawo Mr Kalua...

  • @IsabelMvula-xn8po
    @IsabelMvula-xn8po Před 22 dny

    Kukula kumeneko kkkkkk

  • @finchiadriano
    @finchiadriano Před 23 dny

    Bwanawa alindi umboni kapena akungolumbwalubwa

  • @phillipstamaley7901
    @phillipstamaley7901 Před 22 dny

    🤣🤣🤣🤣🤣

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 Před 23 dny

    Zoona munthu uyu anathana kale ndi kamuzu ku one party system panonso aszuzinke mmmmmm koma chakwera bwenzi utakhala ndi umuthu pena

  • @user-hm9nc7lz6e
    @user-hm9nc7lz6e Před 22 dny

    Ambuye mutetedzereni penjani kalua mmanja mwa satanic awa chakwera ndi mcp akufuna aononge moyo wace but ladzalo cakwera why moyo wako umakondwa ukamapha anthu popanda kukhetsa mwazi thupi lako kukapwanya tulo silibwera mmaso mwako bwanji osamupha nick chakwera bwanji

  • @johnarushamasese108
    @johnarushamasese108 Před 23 dny

    ❤awudzeni chilungamo 🔥

  • @user-kk4uj8ko8k
    @user-kk4uj8ko8k Před 23 dny

    Awuzeni dppppppppppp

  • @crosbyphiri1745
    @crosbyphiri1745 Před 23 dny

    Please do not abandon the Lord Jesus Christ for the sake of politics. Please be a true Christian. It's surprising that the former man of God has gone satanic.