DR MICHAEL USI AKUNGOLANKHULA KUMENE ZA MGWIRIZANO MCHIPANI CHA UTM |

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 10. 09. 2024

Komentáře • 99

  • @Thembokatuli
    @Thembokatuli Před 24 dny +13

    Tidya nawo ndalamazo koma palibe vote kwa chikangawa group

  • @JonesChingaya-yf4gg
    @JonesChingaya-yf4gg Před 23 dny +2

    Kodi Dairy kumangoti a President anandisankha, inu ndioyamba kusankhidwako. Kodi imfa ya Chilima ija simakupasa mantha etie????

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b Před 24 dny +4

    Akuwombera m'manja wo ndi akachasu, zikuchita kuwonekera masekedwewo😂

  • @brainsmkumbwa6267
    @brainsmkumbwa6267 Před 24 dny +7

    Masapota oyenda nawo amenewo,mene malawi alili palibe angawombele manja Michael Usi Kumpoto

  • @leonardmalirana7423
    @leonardmalirana7423 Před 24 dny +1

    SKC ANAGWIRIZANA NDI MCP KUTI TERM INO NDI YAKE NANGA INU A USI ZILISO MOTERO KUTI 2025 MUIMA NDINU

  • @user-wb9ji3oe5o
    @user-wb9ji3oe5o Před 24 dny +2

    Landirani ndalamazo muzidye ndipo chisankho charity mumtima mwanu. Adali kuti zaka zonsezi 4? Idyani ndipo voti iri kwa inu.

  • @user-ru1mm7bf4p
    @user-ru1mm7bf4p Před 24 dny +2

    Munanena zonse palibe chomwe mwapangapo mu 4 year ndiye mungapange Chaka chimodzi? Akulu inu dyela mukumva kukoma ndi Chakwela koma nthawi mkachitsilu posachedwapa tikuiwalani

  • @user-hl1jt6eo3d
    @user-hl1jt6eo3d Před 24 dny +4

    ndalama tidya nawo zaulelezo 😂 we gonna accept your gift ..after eating money vote 2 DPP

  • @nelsonnkhambule6292
    @nelsonnkhambule6292 Před 23 dny

    Mukupusika waka wana. Kwali tipeni waka ndrama tilyepo nase ku mzimba kulinje wa mcp

  • @OsmanOsher-sh6gp
    @OsmanOsher-sh6gp Před 23 dny

    Awa akufuna atimangise tiyankhula bwanji mutasema kachanyau ka Ceiba crime

  • @MakabaBauleni-c2i
    @MakabaBauleni-c2i Před 22 dny

    Kma Mr Usi sakutha kuona patali cz udindo uwu ngwa chaka cimodz chabe nde sakudziwa kt president yemwe akuwatuma leroyu pamene convention yacitika ya mcp iwo chawo palibe kmanxo sakudziwikatu pano kt ali cipani chanji mapanga awiri avumbitsa mwacidziwikire apa Mr usi avumbidwa

  • @SolokingChimzy-yt7dj
    @SolokingChimzy-yt7dj Před 23 dny

    Bwinotu koma kumenyela nkhondo ndiolose nkakutafunile pasidya...

  • @bisweckchimphamba8497
    @bisweckchimphamba8497 Před 15 dny

    Kodi ngongolezo umakongoletsa ndi iweyo?ndimayesa kuti kuli bungee laketu!iwe tangopita ku MCP basi usapussise anthu,munthu wachabe chabe iwe

  • @KennedyKanyama-ce8lb
    @KennedyKanyama-ce8lb Před 22 dny

    Palibe mungapange pepani. Kudya katatu athu tikudya katatu pa week. Tikudikira passport yotsika mtengo. Tikudikira univesal subsidy. Tikudikira kuthesa ziphuphu now corruption is mission of this government us u can see. That is no sense. Nde inuo mwaima pamenepo ndikumanena zotsathekazo. Sikufuna kamwa yanuyo ndi chakwera wakoyo zimene tikufuna mungopanga zomwe munalonjeza osati kugawa ndalama sintchito yako imeneo. Za neef zikukukhuzani bwanji? Vice presdent kumanena za neef kkkkkkk. Upite kwa chakwera passport, fertilizer, kudya patsiku katatu, kutheza umbamva omwe a mcp akubazo. Osati zanzii ngati zimenezi sitimadya ndare.

  • @MosesMkandawi-e2v
    @MosesMkandawi-e2v Před 22 dny

    Kno 1000000 job's kno vote mfundo mulibe munawanamiza 1 000000 job's
    Pano mwapeza mfundo yonamizila anthu
    Pakuti munawalonjeza feterizes 4500
    Zonse munalemphera no job's no vote

  • @ConfusedAstronaut-qv6wq

    Manganya becareful where is cheap feteleza,iwe wapakamwa kwabasi,thawi ya mcp yatha,don't bring excuses pls

  • @user-ev6bi7jr7g
    @user-ev6bi7jr7g Před 23 dny

    Ndalama tengani ndizomwe zija amaba zija koma osawavoteranso

  • @MadalitsoIbrahim
    @MadalitsoIbrahim Před 24 dny +4

    Masapota oyendanawo mpaka kuwapasa mic kuti azimveka kkkkkkkkkkkkk

  • @ELLENZAPS
    @ELLENZAPS Před 22 dny

    Alibe manyazi manganya kuwimbera mfiti mmanja chakweya anzako athawa Koma iwe Uli maso pyu komko unya uwona galu

  • @ConfusedAstronaut-qv6wq

    Kodi ameneyi akuyendayenda ngati ndani,ndi kapeni kapena vichi

  • @user-ww9rj2wx8d
    @user-ww9rj2wx8d Před 23 dny

    Za ziiiii zamanyi nthawi yonseyi munali kt monse tavutikila muzaka 4 panopa muziti nyu nyo nyo ukawawuze ana ako wamva unamagulisa chilima ukufuna utiguliseso Kwa chakwela wakoyo

  • @user-sh5wq4uf6r
    @user-sh5wq4uf6r Před 24 dny

    Kamunthu aka akuti ka kamanganya aka ndikopenga

  • @connexlita2846
    @connexlita2846 Před 23 dny

    Zimene akupanga Micheal Usi , nchimodzimodzi kusongozera mawungu ovunda ....

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy Před 24 dny +3

    Kod daily uzingot chakwera anandisakha Ine vice president kod zachilendo et sudaonepo

  • @user-cb5gh9md4i
    @user-cb5gh9md4i Před 23 dny

    Awa angoyambitsa mpingo

  • @AllanWyson
    @AllanWyson Před 24 dny

    Nawo bambo a sikono 😮😮😮 daily kumangokhalila a Chakwera pondisankha ine,,, 🤣 🤣🤣🤣

  • @lingsonmitunda293
    @lingsonmitunda293 Před 23 dny

    Koma dziko la Malawi lapepetulidwa ndithu 😅

  • @georgengwira3152
    @georgengwira3152 Před 23 dny

    Mbuzi yamunthu gwape

  • @user-je8jm5uy1q
    @user-je8jm5uy1q Před 24 dny

    Za ziiiiiiiiii asasokoneze anthu uyu ali nchipani chake osangopita kumene ko bwanji???

  • @INNOCENTMOFOLO-io8tg
    @INNOCENTMOFOLO-io8tg Před 23 dny

    ukachimwa dziwa nyimbo

  • @SaidDayton
    @SaidDayton Před 24 dny +1

    Kkkkkk sakuziwa chomwe akuyakgula aaata

  • @FrancisMazamba
    @FrancisMazamba Před 23 dny

    Ngongole anthu amasauka nayo kapena mukufuna muwapatse zaulele ndalamazo

  • @user-kt5bq2wg6v
    @user-kt5bq2wg6v Před 24 dny

    Komatu munthuyu akamba chilungamo.

  • @INNOCENTMOFOLO-io8tg
    @INNOCENTMOFOLO-io8tg Před 23 dny

    wina wabuka kale kachaso wake uko kut apatsidwa ndalama

  • @AdamKay-q1l
    @AdamKay-q1l Před 24 dny

    Shipisani katunthu basi osati zogawa ndalama ai mwagawila anthu angati?

  • @Joe-vf1ym
    @Joe-vf1ym Před 24 dny

    Iwe chitsiru akutuma galu

  • @petertaulo8014
    @petertaulo8014 Před 24 dny

    Manganya ndi bulutu amangobweleza speech 😅😅😅

  • @paulmanyamba5437
    @paulmanyamba5437 Před 24 dny

    Zopanda mutu idziii mwaziwa liti dzimenezo kapena ndi tikufelanji eeeti

  • @user-rk3gq7gd8f
    @user-rk3gq7gd8f Před 24 dny

    Unya uwona ulibe chipani

  • @RaphaelAniva
    @RaphaelAniva Před 24 dny

    Za ziii bas, koma awa

  • @JasonMailos
    @JasonMailos Před 24 dny

    Opeleka chilima uyu galu wamundu

  • @RaphaelKweve-u5s
    @RaphaelKweve-u5s Před 24 dny

    Bwanawa sakudziwa chomwetu akuyankhula ,,,,nanga akayamba fundo sakuyimaliza ,,mkuyamba ina osamayimaliza ,,mkubweleraso mbuyo palibe chimwemwe ndavapo ine

  • @user-un8yq1gg2i
    @user-un8yq1gg2i Před 24 dny

    Musawanamizire anthuwa mwene, palibe amene wapempha apa inuyo ndiamene mukuwalonjeza, komansotu a utm wo avala dzanyuwanitu kkkkk anyway nyimbo ikamatha or ukweze volume imatsikabe

  • @YNOTGEORGE8
    @YNOTGEORGE8 Před 23 dny

    Nonses

  • @JeanBetha
    @JeanBetha Před 23 dny

    Mbuz

  • @StevenBanda-f5g
    @StevenBanda-f5g Před 24 dny

    Ulibe nzeru komanso ndiwe garu

  • @Kiyamachilipa
    @Kiyamachilipa Před 24 dny +1

    Mwadziwa liti?

  • @kondwanichiwanda
    @kondwanichiwanda Před 24 dny

    Zaziiii kape uyuu

  • @CassimMbalaka
    @CassimMbalaka Před 23 dny

    Mulungu salakwitsa kalikose akuwoneni pokuyikani nose wokhudxiwa pa ifa ya chilima

  • @CharlesPhiri-ds1rk
    @CharlesPhiri-ds1rk Před 24 dny

    Chokhachi usi,,,ndimakudyadira...akumbutse ndare kumwamba kulibe....

  • @JosterNgalawa
    @JosterNgalawa Před 24 dny

    Opanda dzeru iwe mr chikangawa

  • @user-eh1mg3ww6d
    @user-eh1mg3ww6d Před 24 dny

    Chitsilu iwe eti uyu amandinyasa

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 Před 24 dny

    Nifi yo tiyeni tilandire tidye koma osavotera chikangawa. Komaso akunamayo akuti akupereka nifi ku nkhota koto limenero ndi boza vp lamukunkuniza

  • @dennisbanda4751
    @dennisbanda4751 Před 24 dny

    Bwana usi mulungu azikutsogolerani mulindi umunthu

  • @CobratwaibYusuf
    @CobratwaibYusuf Před 24 dny

    Chemanganya azanu ali ku convention inu simudapite bwanji kodi utm imene muli inuyo ndiiti ??????

  • @felixjoseph8161
    @felixjoseph8161 Před 24 dny

    Chitsiru uyu alibe nfundo anapha nzake kufuna mpando panyini pamake akuona ngati ndife ofoira ngati iye

  • @EmmanuelGasiten-fo5dr
    @EmmanuelGasiten-fo5dr Před 24 dny

    Kodi akuyimbira m'manjawa anawagulira aMbuye ntengeni?

  • @INNOCENTMOFOLO-io8tg
    @INNOCENTMOFOLO-io8tg Před 23 dny

    komatu guys anthu ndiye Ali ziiiii 😂😂😂😂 akungodziwa kut bodza lawo lachepa anthu akungodziwa komwe akupita kkkk

  • @AREFRIEDNELSON
    @AREFRIEDNELSON Před 24 dny

    😂😂kusangalarila mr yudasi yoooooo 😂😂😂😂😂😂😂😂 koma njara ili thoooo osamanama usiiiii iweeeee ukukakamira achakera ukugula mavoti kwawathu

  • @jazielbenford5881
    @jazielbenford5881 Před 23 dny

    Panja penipeni

  • @user-rz8qp8tj8e
    @user-rz8qp8tj8e Před 24 dny +1

    Go and sleep mbuzi iweyo

  • @AleksaWilliams-qc6cn
    @AleksaWilliams-qc6cn Před 24 dny

    Akuyakhawo ndie mawu ngat Isaac ndi Jakob

  • @alexandermwandira2376
    @alexandermwandira2376 Před 24 dny

    No sense, u r not a public speaker

  • @user-tb6yh1kx3o
    @user-tb6yh1kx3o Před 24 dny

    Galu iwe ife a UTM sitimakuwelengela wamva

  • @MabvutoMichaelPanagona

    Pelekani ndalamazo koma udzasowa mavoti ndi chipani cha MCP.

  • @EmmanuelFinias
    @EmmanuelFinias Před 24 dny

    bwana august akutha ngongole anthi sanayambebe kutenga

  • @JohnJohn-og8rt
    @JohnJohn-og8rt Před 24 dny

    Kom mene ukuyanguliramo ziteka poti thawi yata kare dpp ikulowe boma koma mene chakwera afomerese bs areperela

  • @jamiajafali6619
    @jamiajafali6619 Před 24 dny

    Uwawuze aMCP kuti asiye kukapa antu..naweso

  • @brainsmkumbwa6267
    @brainsmkumbwa6267 Před 24 dny

    Galu wa chabe chabe iwe Michael Usi

  • @MarthaMbewe-uk5nn
    @MarthaMbewe-uk5nn Před 24 dny

    YUDASI KUMVETSA CHISONI KWAMBIRI

  • @JoycieMbaya
    @JoycieMbaya Před 24 dny

    Koma ndiye sewero Leni leni

  • @KondwaniBanda-ul8sj
    @KondwaniBanda-ul8sj Před 24 dny

    Aaaa zazi munayiwala kuti chilima anakuchitilani wabwino mumangokamba zachakwela basi kuyiwala kuti pali wina amene anakufikitsani pamaso pachakwelayo tiwona ngati ukhalepo paka 2026

  • @Kiyamachilipa
    @Kiyamachilipa Před 24 dny

    Kulibe chulungamo, mwaluwa

  • @JoycieMbaya
    @JoycieMbaya Před 24 dny

    Ka speech aka katikwanano. Kodi akuchemelerawo akuchita sewero?

  • @wisdomchilanga723
    @wisdomchilanga723 Před 24 dny

    Bwanji mukanaseva Biyen inu ausi

  • @user-kq6rp6hn7y
    @user-kq6rp6hn7y Před 24 dny

    Business iyenda bwanji anthu alimbe ndalama

  • @PhillipHendre
    @PhillipHendre Před 24 dny

    Anthu omvekawo kaya angati kkkkkk usi kwako kwatha tachita manyazi anthu angati akukululutira manyazi bwanji kale lonse zaka 4 za neef munali kuti 😊

  • @IsmaelBilal-lh1pi
    @IsmaelBilal-lh1pi Před 24 dny

    Zidakwa zalezela zaulele 😅😅😅

  • @user-wl7xn3or6d
    @user-wl7xn3or6d Před 24 dny

    Ndalama mosemuja simunayambebe kugawa mungowapusitsa Athu kkkkkk dzinenakuti tili busy tikupanga ndalama kkkkk ndalama zakeziti

  • @HanifaAdam-tm9yv
    @HanifaAdam-tm9yv Před 24 dny

    Kma ma comnent wa mmakhala ndi nthawi yowerenga mr nthiko? anthu akukuitanani bambo a sikonooooo... anthuwatu ali ndi njala

  • @BlessingsMikeyasi
    @BlessingsMikeyasi Před 24 dny

    Zamakommedy ine ai Keanu konko Pusey

  • @thulambale2836
    @thulambale2836 Před 24 dny

    Owina wina

  • @isaacimmantambala5294
    @isaacimmantambala5294 Před 24 dny

    Anyamata ama two sawu akutinyasa ma backing opoila...zilizose avekele eyaaaaaaaaaa bwanaaaaaa eyaaaaaaaaaaaaa kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk

  • @Martha-m6e
    @Martha-m6e Před 24 dny

    Chikangawa

  • @Kiyamachilipa
    @Kiyamachilipa Před 24 dny

    Pepani chepetsani bodza bwana mthiko

  • @user-wl7xn3or6d
    @user-wl7xn3or6d Před 24 dny

    Athu ake aka chasutu kkkk angofuna ndalama

  • @HappyBirchForest-zy8nq

    A utsi ulemu sumakuyenelanitu muziona ma comments awanthu 😢

  • @GeraldMkwewu-gd5eb
    @GeraldMkwewu-gd5eb Před 24 dny

    Galu lwe palibe chadzeru pa lwe galu manganya nonsense

  • @ShadreckAustin
    @ShadreckAustin Před 24 dny

    Kape

  • @user-nt9go2fz3k
    @user-nt9go2fz3k Před 24 dny

    Nyopakeee

  • @EmmanuelFinias
    @EmmanuelFinias Před 24 dny

    zazii awa apenga

  • @MikeKanyaza-bm5tp
    @MikeKanyaza-bm5tp Před 24 dny

    Mbuzi

  • @Kiyamachilipa
    @Kiyamachilipa Před 24 dny

    Wabodza mthiko

  • @EmmanuelMoyo-hy5ni
    @EmmanuelMoyo-hy5ni Před 24 dny

    Useless comedy man

  • @user-nt9go2fz3k
    @user-nt9go2fz3k Před 24 dny

    Fusek