BON KALINDO NDI MALAWI FIRST APANGITSA NSONKHANO NDIPO AOPSYEZA BOMA KUTI APANGA MA DEMO PA 8 AUGUST

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 7. 09. 2024

Komentáře • 131

  • @adamhassan7451
    @adamhassan7451 Před měsícem

    You guys you are the best. Malawi needs people like you for the change ,Mr DC more 🔥🔥🔥

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h Před měsícem +6

    Timakiyimilirani Ife amalawi ulemu wanu a Malawi first ❤

  • @JuniorHala-vf9ov
    @JuniorHala-vf9ov Před měsícem +1

    Koma bon kalindo ulemu wanu watching from Pretoria

  • @ndauzamtonga6719
    @ndauzamtonga6719 Před měsícem

    Watching from Zambia

  • @ThokohPrescotKalonga
    @ThokohPrescotKalonga Před měsícem +7

    Kodi munati pa 31 ndimawatu pano mwayambaso kutchula zapa 8 August mm ndidaziwa ndithu kuti sizingatheke kupanga mademo ayi. Komaso mungosiya kutchula za mademo osati muzidalilitsa anthu then ndikumalepheresa😡

  • @SoundmasterElectronics
    @SoundmasterElectronics Před měsícem +2

    Ma demo akumalawi saphula kanthu timakayenda mu nsewu pomwe yemwe tikumunayo Ali ku state house what's that samamva kuwawa kulikonse that's why sitipindula kanthu komanso anthuwo sapangapo kanthu ngat mukufuna zinthu zosinthe go straight kwa amene akupangitsa not munsewu nkumasokonezanso bizness zovuta kalezi

  • @emmanuelchirwa3420
    @emmanuelchirwa3420 Před měsícem +1

    Thank you brother more 🔥🔥🔥 well done ✅ malawi first to save poor Malawian
    We all love you
    , more 🔥🔥❤❤❤❤

  • @user-ul1fb4yn5o
    @user-ul1fb4yn5o Před měsícem

    I love bon kalindo and malawi First live from ntcheu

  • @lyiemax
    @lyiemax Před měsícem +5

    Beautiful press conference but the problem is the weaknesses of opposition parties of this country , it seems our opposition parties are not ready to rescue it's citizens.

  • @MrThomas-j9d
    @MrThomas-j9d Před měsícem

    Thank you B k & your support your freedom fight god protect you each & everytime ( from port Erazabeth kostern South Africa

  • @EmmanuelNgambi-y6h
    @EmmanuelNgambi-y6h Před měsícem

    Mbambande mr DC

  • @user-tn2qg1vs9j
    @user-tn2qg1vs9j Před měsícem

    Malawi first ❤

  • @user-ky4ce9gb6j
    @user-ky4ce9gb6j Před měsícem +2

    Watching live from Mangochi mmbaluku

  • @getbusy7173
    @getbusy7173 Před měsícem +1

    bma lake liiiiitiiii zakumachende eti mcp izitixuxa aaaaaaaaaaaaaaa

  • @vivianmkwate8536
    @vivianmkwate8536 Před měsícem

    we love you Malawi first Chonde malawi tiyeni tituluke zinthu zisinthe tatopa Amalawi

  • @GiftMwaungulu
    @GiftMwaungulu Před měsícem +2

    mwasinthaso date aaah😅

  • @Dysonkhofi
    @Dysonkhofi Před měsícem

    Go! Malawi First, we are supporting you!

  • @user-fg1me1un8p
    @user-fg1me1un8p Před měsícem +1

    Alunta continua Bon your indeed pangolin

  • @NeverBeforeMnesa
    @NeverBeforeMnesa Před měsícem +1

    Mwayiwala road traffic ndi immigration ( driving license & passports )bravo malawi first

  • @gannkazembe1746
    @gannkazembe1746 Před měsícem

    Bon Kalindo simunthu waba.

  • @user-ff9xq5ss8d
    @user-ff9xq5ss8d Před měsícem

    Watching from msundwe

  • @JonathanMsiska
    @JonathanMsiska Před měsícem +3

    Mademo mwachulusa boza masiku muñgosintha.

    • @user-ui6vh1ld4f
      @user-ui6vh1ld4f Před měsícem

      Mwina mademowo akuwagulitsanso chifukwa akungosinthasintha matsiku

  • @HalimaDamiano
    @HalimaDamiano Před měsícem +1

    Bravo the Dc

  • @user-gj4li2gc8o
    @user-gj4li2gc8o Před měsícem

    Mumapangila kuti mademowo ku thyolo kapena ku mulnje

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh Před měsícem +1

    Ine sinatuluke ID should I say ndine wa ku southern region sizikutengela mbali Koma that delays is everywhere so osamatigawanitsa please

  • @PhillspicJere
    @PhillspicJere Před měsícem +1

    Koma munthu mukuti kalindoyu kwao ndi kumalawi komwe kuno? Eeeeeh chifukwa kuda kokhako akuoneka ngati ndiwaku Malli

    • @Yahiya-wm8nd
      @Yahiya-wm8nd Před měsícem

      wabodza iwe ndakuona kale pamtundapo

  • @YangMaku-x8w
    @YangMaku-x8w Před měsícem

    Sekwanele, aluta continue Mr kalindo

  • @DavidJackson-ox4xm
    @DavidJackson-ox4xm Před měsícem +2

    The DC'S mwana woooopsa kwambiri

  • @MphatsoMhoney-xn2ft
    @MphatsoMhoney-xn2ft Před měsícem +1

    Malawi first, people first with Boooooon kalindo and the Malawi first tiyeni pansewu on 8th of August

  • @YasinAdam-pn4bh
    @YasinAdam-pn4bh Před měsícem

    God bless you Bon Kalindo

  • @DavidAugustine-y5v
    @DavidAugustine-y5v Před měsícem +3

    Zikomo kwambili abon😮 kalindo ambuye azikudalisani

  • @Brianchisi
    @Brianchisi Před měsícem +1

    pangani zazeru kalindo musana mize anthu khondo siyimanga muzi ndikatindiku yangameni mupando momwe mwakhala izachisoni ine siwachipani koma kulila kwa amalawi tinayambaliti kusintha kufike ndi inu takhalandi asogoleri angati anasitha ziko kalindo ngatikuli kusauka tangowa pephani achakwera akuthandizani zione selo munayamba ndinu ngati kopazioneselo zosetapanga tapindulachani nangakatangale anayambaliti mungophesa ana aeni

    • @KumbukaniKafatia-cd2hq
      @KumbukaniKafatia-cd2hq Před měsícem +1

      Mumatsata zimene zikuchitika maiko ena monga Kenya? Kapena mungoyankhula nchimbulimbuli?

    • @SamKaposa-i5c
      @SamKaposa-i5c Před měsícem +1

      Ameneyu simmalawi ntayeni 😂😂 ndiudindo ngati ndimmalawi kulankhula chomwe chikulakwikacho

    • @PhillspicJere
      @PhillspicJere Před měsícem

      ​@@SamKaposa-i5cInu Kalindo ndichitsiru sakuimira amalawi mumuuze, akakonze Kaye banja lake hule ameneyu munthu okhalira kuthamangisidwa mma rent koma anali MP

  • @user-vh9uk1jy7w
    @user-vh9uk1jy7w Před měsícem

    More fire Booooon kalindoooo

  • @MonijaKataika
    @MonijaKataika Před měsícem

    Am loosing trust on the demos aaaa.. zithera kumabanzi iziii panayambira paja...aaaa😢

  • @JosephKuyeli-rc9on
    @JosephKuyeli-rc9on Před měsícem

    Tigulenso ma plasma motchipa🤸🤸🤸

  • @isabelmartin7567
    @isabelmartin7567 Před měsícem

    More fire 🔥🔥🔥

  • @MonijaKataika
    @MonijaKataika Před měsícem

    Poyamba u said the reason is to let the president to step down..now zina aaaaaa

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh Před měsícem +1

    Kalindo akugwilitsidwa tchito ndi chipani cha DPP osamuvela akulemeletsa family yake

    • @Vascomw
      @Vascomw Před měsícem

      Km mene anthu akuvutikira iweyo kumayakhura chochi ulimbe umuthu

    • @HalisonSolomon
      @HalisonSolomon Před měsícem

      INUNSO MUSANAMIZE WANTHU APA KALINDO IZI SANAYAMBE LERO NGAKHALE NTHAWI YA DPP ANALI AKUPANGA ZOMWEZI, INU NDAMENE MUSAKUFUNIRA DZIKO ZABWINO

    • @HalisonSolomon
      @HalisonSolomon Před měsícem

      KOMATU INU ANZATHU A MALAWI FIRST LIJA NDI KALE MUNAYAMBA KUKAMBA KUTI KWAKWANA KOMA PALIBE CHIKUCHITIKA ENOUGH IS ENOUGH MUNAYAMBA KUYANKHULA NDI KALE KUKONZA MADEMO KUMAPANGA CANCEL MUMATI PA 31 LERO MUKUTI PA 8 CHIKUCHITIKA NCHIYANI

  • @user-mh7cc8up4i
    @user-mh7cc8up4i Před měsícem

    Moto 🔥🔥🔥🔥🔥🔥💯

  • @JafaliChiwimbi
    @JafaliChiwimbi Před měsícem

    Boooon kalindo

  • @DavieChinkwaso
    @DavieChinkwaso Před měsícem

    Viva Malawi first, the people first. Pliz keep on voicing for us, we indeed suffering and struggling in our own country.

  • @AtupakisyeMwakasengo
    @AtupakisyeMwakasengo Před měsícem +1

    Mademo nde angosintha sintha bwanji,mutitchosa appertite

  • @AustinChiyembekezo-cx4mz
    @AustinChiyembekezo-cx4mz Před měsícem

    Viva malawi fist❤

  • @ChiukuseIbrahimJNapoloMakungan

    Power💪🤝🙏👍✅

  • @KasCarter-k8q
    @KasCarter-k8q Před měsícem

    Umakwana boooon!

  • @Okalekale
    @Okalekale Před měsícem

    Kabungwe ak8a alipo akukapatsa ndalama kugawa ntundu wa a Malawi,Bon Kalindo and his gang are sell outs.Who'ever is sponsoring them has an agenda to divide Malawi.Uyu Kalindoyi ndi owononga.

  • @RhodneyBwa3
    @RhodneyBwa3 Před měsícem

    Thanks to Malawi first❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @user-dn3gp6yi4y
    @user-dn3gp6yi4y Před měsícem

    Ngati sakuyankha mafutso anu mesa ndiye Mademo koma inu musindatso ma tsiku zinduzi osamatizilowesa mantha anthuwa ine akunyasa ndikufuna a choke bs

  • @ZebronTembo-u6p
    @ZebronTembo-u6p Před měsícem

    Congratulations kalindo these senseless people must learn something from stric

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 Před měsícem

    Nkhani yatikulu yayikulu yoti opanda ma ID salembetsa vote ipa ndipane pagona nkhani idzi ya mitsonkho ngati amalawi titavota mwaufulu MCP ichoke nde kuti kumankhidwa kukwela mitsonkho kuwononga ndalama za boma kuchoka chakwela ndi MCP boma ndimayankho ADZOTSE AMALAWI AKULILA SIKU NDI SIKU KOMA NDI TILOLE KUTI OPANDA MA ID ASAMVOTE MCP YAWINA BASI NOETSE OSUTSA BOMA PALIBE CHANU INU MUDADWE ID NDICHITSANKHO ZIYENDA LIMODZI BWANI AKUDZIWA ANTHU AKUMWELA AMBILI SAKAVOTA CHIFUKWA ALIBE MA ID OSUTSA CHONDE CHONDE LOWELELANI MA ID ASAKUNAMIDZENI KUTI ALEMBA KACHIWILI AYI BIDZA CHIDULE NDIKUCHOTSA NJILA YA MA ID BASI NDE MWAYI OWINA OTSUTSA UKHALAPA KUPANDA APA BASI OSUTSA IWALANI ZOWINA VOTE 2025 ANYETSA MANYI OMWEWA A MCP

  • @neemahkapatamoyo9563
    @neemahkapatamoyo9563 Před měsícem

    Tsono mademo achitika iweyo atabwerako komwe akupita kapena mupanga iye kulibe?
    Chifukwatu ngt mupanga iye kulibe palibe chomwe mungapindule

  • @user-xd1cm7tm7t
    @user-xd1cm7tm7t Před měsícem

    King d c malawi

  • @WilliamGuyJonathan
    @WilliamGuyJonathan Před měsícem

    Pangolin ❤❤

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh Před měsícem

    Akalindo akumwa tea wakaka kwawo a malawi ake oti akuyimilira kalindo ayime uphungu kwawo azizayimilira athu akwawo

    • @EliasApofu
      @EliasApofu Před měsícem +1

      Pasana pako garu iwe

    • @SamKaposa-i5c
      @SamKaposa-i5c Před měsícem

      Kodi iwe chikangawa team eti mmene wayambila kudandaula muja😂😂😂

    • @MaryNyirenda-nq3mh
      @MaryNyirenda-nq3mh Před měsícem +2

      komatu anthu ananu pabwino mudabasa galu zoona munthu akukumenyelan ufulu kut mukhale pabwino bas mukumunyoza komatu kalindo yu sakupanga zakunyumba kwake koma kwa Malawi ovutika enanu ndinu abale ake achakwera komanso mkudaya nawo aboma koma Pali ena kunjaku akuvutika kwambiri nde enanu uzimu wamulungu unakuchokelan chifukwa chaziphuphu mukudyazo kuma muziwe kut palitsiku limozi muzawona polekera kulimulungu kumwanbaku

  • @MCLoudZeka
    @MCLoudZeka Před měsícem

    Booooon Kalindo

  • @FelixGambiza-fp7tn
    @FelixGambiza-fp7tn Před měsícem

    Pa 8 ndi zagwesa mvura mpaka pa 15

  • @juliochiwalo
    @juliochiwalo Před měsícem

    Dpp sikukhuzidwa nkhani ndi mavuto ochuluka omwe bona chakwera ndi MCP alibe nazo ntchito

  • @PhillspicJere
    @PhillspicJere Před měsícem

    Tiyeni tingoswana yamanja akulu

  • @ernestnyirongo3962
    @ernestnyirongo3962 Před měsícem

    Zaziiii

  • @victorbanda9039
    @victorbanda9039 Před měsícem

    Atonkhàni mukusowa zochitatu mpaka kukapezeka ukuku aaa

  • @yotamumahomed1313
    @yotamumahomed1313 Před měsícem

    Tilikomweko osaopa osafoka

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh Před měsícem

    Komaso issue ya ma ID even central region ambiri alibe ma ID even ine yanga sinatuluke since last year

  • @GospelSoldiers-sr7np
    @GospelSoldiers-sr7np Před měsícem

    Ndipo tisindike pamenepo pa chiphaso chaunzika ena sakulembesa

  • @user-nn7ys7fu5u
    @user-nn7ys7fu5u Před měsícem

    Tiyenazo kachamba😂

  • @JohnEliyas-j9j
    @JohnEliyas-j9j Před měsícem

    Our country has gone

  • @user-kr1tf2tu7s
    @user-kr1tf2tu7s Před měsícem

    Zika zake ziti zakumudzi kwanu mwauponda, kwanukomweko

  • @user-ce9yj9ln4z
    @user-ce9yj9ln4z Před měsícem

    Pangan zomwedzo bas andikwana kwabas anthu amenewa

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh Před měsícem

    Lilongwe ndiwakulu moti simumadziwa zimenezo mukulimbana ndi Lilongwe bwanji

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh Před měsícem +1

    Lilongwe wake up kalindo akudana ndi Lilongwe and central region

  • @user-ri5qm8qo7g
    @user-ri5qm8qo7g Před měsícem

    Atingulitsa

  • @Standwell78
    @Standwell78 Před měsícem

    Apule 😂😂

  • @OweniMolokooweni
    @OweniMolokooweni Před měsícem

    😂😂😂😂😂❤❤❤ 31 mandemo

  • @DavidAugustine-y5v
    @DavidAugustine-y5v Před měsícem

    Abon kalindo timawanyadila kwambili

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh Před měsícem

    Kodi ku ma demoko nkazi wa kalindo ndi ana ake akakhalako mesa nawoso nda Malawi asamatitenge zitsilu ife anyani amenewa atengeko akunyumba kwake akayende

    • @HarlodMbalati
      @HarlodMbalati Před měsícem

      The DC bon kalindo mwana oooo🔥

    • @Dysonkhofi
      @Dysonkhofi Před měsícem

      Ulibe nzeru mboli yako wakongeresi

    • @SamKaposa-i5c
      @SamKaposa-i5c Před měsícem

      Iwe watumidwa ndikama jekete😂😂

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon Před měsícem

    ACHOKA PA 31 JULY PAJA AFIKA PA 8 AUGUST

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh Před měsícem

    Usamale ndiwe ife chimanga tilandila

  • @TimothyDamiano
    @TimothyDamiano Před měsícem

    Tiyeni konko,osaiwala kunyamula ma bucket a madzi paja kumakhala tear gas

  • @alnordtembo8930
    @alnordtembo8930 Před měsícem

    The DC

  • @dysontasowana7429
    @dysontasowana7429 Před měsícem

    Wachepa iwe

  • @user-ky4ce9gb6j
    @user-ky4ce9gb6j Před měsícem

    Kuchema

  • @user-lj7lm6ly7z
    @user-lj7lm6ly7z Před měsícem

    Mwasiyaso paja mmati mupanga mawa mademo?

  • @user-fd1tu6ku1r
    @user-fd1tu6ku1r Před měsícem

    The DC ndi Mfumu

  • @user-ri5qm8qo7g
    @user-ri5qm8qo7g Před měsícem

    Bola asakupatseni kenakake

  • @AngolanChinga
    @AngolanChinga Před měsícem

    Yes mr bon kalindo we are in democracy now but we stay like we are not in democracy what is that chakwela machende ake with zikhali ng'oma and all of there

  • @HusseinRashid-m4l
    @HusseinRashid-m4l Před měsícem

    2

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh Před měsícem +1

    Kalindo akufuna kugawanitsa a Malawi

    • @SamKaposa-i5c
      @SamKaposa-i5c Před měsícem

      Amthu anagawikana after ngozi yakuchikangawa ija man

    • @Okalekale
      @Okalekale Před měsícem

      ​@@SamKaposa-i5cNgozi inawagawa bwanji?,mwina atati Chakwera anapha anthu aja,pali umboni yah pangakhale ponveka pang'ono komanso zingatanthauze kuti pa Malawi umbuli ukadalipo.
      Peter ndi amene amapanga ndale zogawa aMalawi and kabungwe aka ndikuonamo dzanja lake.Anakapanga ndicholinga chofuna kulepheretsa Tonse Alliance chifukwa zinamuwawa kuti umbava wake unaululika.Ndi mdala osadziwa ndale or kuyendetsa dziko,kwake ndi kuononga,maphunziro sanamuchotse umbuli.

  • @Vascomw
    @Vascomw Před měsícem

    Kwvta

  • @jomochirwa
    @jomochirwa Před měsícem +1

    Mademo adatha mphavu palibeso boma limene lidzawopaso mademo.mademo adapita ndi mtambo kazikalimani chaje.

  • @dysontasowana7429
    @dysontasowana7429 Před měsícem

    Can government respond to you munthu osuta chamba ndi mkwidzi? Inutu mukadakhala ngati munali nduna sibwezi mukulankhula chamba chanucho

    • @Dysonkhofi
      @Dysonkhofi Před měsícem +1

      Akulu vomerezani zinthu zinasokonekera,Kalindo sakulakwitsa vuto lili ndi iweyo

    • @MaryNyirenda-nq3mh
      @MaryNyirenda-nq3mh Před měsícem

      Awawa ndi abale achakwera komanso ndiwomwewo azibale awo akuba ndalama za Boma chifukwa chake akupanga makan koma mziwona musatitenge opusa amalawife iya

    • @Okalekale
      @Okalekale Před měsícem

      Anasokoneza zinthu ndi ndani ku Malawi?,tonse Alliance kapena MCP zalowa liti m'boma?,Chakwera walowa liti m'boma?.
      Mbava zimene zinaononga dziko inu simukuzidziwa?,okay kuyambira 1994 ndi ndani amene wakhala akulamulira?,ndi zipani ziti zimene zakhala zikulamulira?.
      Bakili UDF,Peter DPP,Joyce PP,izi ndiye mbava ndi zipani zimene zaononga chuma cha Malawi,Kamuzu anasiya chuma chikuyenda bwino.
      Ngati mukungonena zinthu chifukwa choti ndi inu akumwera ndinu nzika yosafunila dziko lanu zabwino,ndalenza umbuli.Chilungamo mukuchithawa dala pamene mukudziwa anthu ndi zipani zimene zaononga dziko.Kuyambira 94 ndi Bingu yekha amene anapangakonzooneka ena onse ndi useless okha-okha maka maka Joyce ndi uyu akumuti adad a Lomweyi.Peter ndiye muntu oyipa kwambiri chifukwa ndi osadziwa ndale,iye amangodalira kugawa anthu.nfundo alibe anangokhala professor.

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh Před měsícem

    Kalindo akufuna unduna DPP ikazalowa boma chonde chonde anali azanga musavele kalindo

  • @PhillspicJere
    @PhillspicJere Před měsícem

    Chosani Malawi yo muyikepo muhlakho first, dzina la malawi osamngopasapo ndizisiru zomwe,

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj Před měsícem

    Mademo pangani koma boma iziyendabe chomwecho ngati a opposition sakulakhula iweyo ndiye boma lingakuvere pitani pàsewupo tikumana komweko

  • @jeanbotomani9081
    @jeanbotomani9081 Před měsícem

    Kawawa kalindo osaopa osatopa

  • @MarkinaJohn
    @MarkinaJohn Před měsícem

    Tili ready PA 8ogasiti

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh Před měsícem

    Awa kalindo akudya ndalama za DPP mutuluka nonkha kumwelako

    • @SamKaposa-i5c
      @SamKaposa-i5c Před měsícem +1

      Nanu inu sizachigaozo malawi first kaya iwe mngwakuti mavuto mngatonse

  • @YasinAdam-pn4bh
    @YasinAdam-pn4bh Před měsícem

    God bless you Bon Kalindo