APM Sanaluze Zisankho Mu 2019 Ndi Mu 2020 - Innocent Mutholo

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 21. 05. 2024
  • On Nyasa VoiceBox, Innocent Mutholo, says that in his opinion, when he analyses the number of votes cast for APM in 2019 and 2020, APM won the election free and fair.
    Pa Nyasa VoiceBox, Innocent Mutholo, wati malinga ndi maganizo ake, pamene amasanthula mavoti a APM mu 2019 ndi 2020, APM adapambana pachisankhocho mwaufulu.
    #malawi

Komentáře • 100

  • @user-eh1mg3ww6d
    @user-eh1mg3ww6d Před 27 dny +14

    Apapa chofunika tilape mulungu akhululukile Malawi chifukwa chakwela akadapanda kulamulila dziko la Malawi dziko la Malawi kukanakhala khondo yoopya chifukwa athu amafuna chakwela kwambili ndipo mulungu adalola kuti ateteze Malawi kusakhale khondo koma chakwela alamulile kuti athu adziwe kuti sakwela si muthu oyenela kutumikila dziko ndipo amaene amafuna chakwela aona okha kuti chakwela si muthu

  • @user-te3ps3kf2t
    @user-te3ps3kf2t Před 26 dny +2

    Very true,amalawi avutika mokwaila,chifukwa cha adindo anjiru,mwaona zimene amapanga Mulungu, disorganized of Ministers chifukwa mulungu anakwiya,zonsezo Mulungu akuona,tionana 2025 sitilola zopusa zilizonse kudzikolanthu la Malawi

  • @isaaczuze
    @isaaczuze Před 27 dny +5

    Uku ndiye kuyankhula kwenikweni kwas chilungamo .....
    Mr game changer ayi ndithu mumaziwa kuyankhula kwambili

  • @paulbanda9638
    @paulbanda9638 Před 27 dny +2

    I by myself personally I agree with this man, game changer he is 100%right, anaba boma a tonse alliance,

  • @user-is5dl7np9g
    @user-is5dl7np9g Před 27 dny +2

    Zoonad kwambiri Mr. Gama changer💪💪

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 Před 27 dny +3

    Koma chakwera mulungu akuwone Malawi panopa wukuvesa chisoni Kuti wudye mavuto okhaokha

  • @yohanedaudi1740
    @yohanedaudi1740 Před 27 dny +2

    Very true

  • @MorrisMapiri
    @MorrisMapiri Před 25 dny +1

    50+1 must be abolished

  • @PhilipMatolino
    @PhilipMatolino Před 27 dny +2

    Im agree with you game changer

  • @user-mm3es3ph7h
    @user-mm3es3ph7h Před 4 dny

    Come on Brother man game changer.

  • @user-jj7oz4lo9t
    @user-jj7oz4lo9t Před 20 dny

    I agree with you Game changer🎉

  • @JMB804
    @JMB804 Před 27 dny +1

    God remember us🙌🏾

  • @FelixMatebule
    @FelixMatebule Před 27 dny

    Uku ndiye kukamba Mr game changer continue fighting for Malawi, Malawi open your eyes

  • @MikeTheu-ic2dt
    @MikeTheu-ic2dt Před 17 dny

    ❤❤❤❤❤ zowona DPP Vot kujoni Kuno kwatopesa mwina tingabwere kwa2

  • @ivychithyoka1551
    @ivychithyoka1551 Před 16 dny

    And God remains big judge even if earthly judges rule otherwise

  • @spargomw
    @spargomw Před 27 dny +2

    Ma Judge aku Malawi ndi adyera, amagwira ntchito akuyang'ana Umphawi wawo😂😂😂😂😂. Alipo oweluza wa Chilungamo ndiye Mulungu basi.Ma judge nawoso akayankha Milandu pamaso pa Mulungu.Kazilandiran ndithu ma Envelope'wo nd zomwe zikakhale Mboni zanu kumwamba

  • @user-pj3qi7gb3s
    @user-pj3qi7gb3s Před 23 dny

    Keep it up brother

  • @user-op3nx5qt4q
    @user-op3nx5qt4q Před 23 dny

    Chulungamo ukuyenda ngati madzi okumva wamva osamva asamve ndipo tikumvutika kwambiri kuno ku malawi chifukwa cha MCP Chakwera Chakwera ndi Chilima UTM 😢😢😢 Abuye chitanawoni anthu amenewa

  • @chifundocharles2348
    @chifundocharles2348 Před 26 dny

    That judgement was not fair indeed

  • @ibrahmdoka7486
    @ibrahmdoka7486 Před 27 dny +1

    Manyaka aboma...mbuli zenizeni zankhanza

  • @user-pt5wn7nu1d
    @user-pt5wn7nu1d Před 27 dny +2

    Tikufuna anthu ngati inu

  • @FranklinNdovi
    @FranklinNdovi Před 10 dny

    Two blind persons can not lead each other properly for both of them are unable see what is ahead of them.

  • @juliochiwalo
    @juliochiwalo Před 25 dny

    Ngakhale mayi Jane Ansah anenanso kuti APM ndi amene anawina ndipo chisankho chinayenda bwino

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 Před 27 dny

    God bless you malawi wafika pa Zimbabwe lelo 2025 kumvota no ID ngati akufuna dzimenedzo polembetsa mamvoti popo pakakhale elembetsa ma ID chilinga aleyetse atsalephele kumvota chifukwa cha alibe ID dzikalepheka apo bolani vote ilepheleke adzilamula popanda kumvota kutsiyana kuti atibele tikuwona Maso anthu alephela chimene akufuna adzilamulilbe chiyani kuwopa mulandu bwanji

  • @ChifundoNinje
    @ChifundoNinje Před 20 dny

    💪💪💪🔥🔥🔥

  • @user-gn4mx2es3k
    @user-gn4mx2es3k Před 4 dny

    Totally true

  • @user-xh1ve5ym3l
    @user-xh1ve5ym3l Před 27 dny

    Zowona big brother 🙏💕♥️

  • @WitnessMaulidi
    @WitnessMaulidi Před 18 dny

    Osawopa Bwana tili nanu

  • @chrischiwere7279
    @chrischiwere7279 Před 27 dny +2

    Zoonadi zolanda

  • @ivychithyoka1551
    @ivychithyoka1551 Před 16 dny

    Gooooio !!!!!

  • @user-gn4mx2es3k
    @user-gn4mx2es3k Před 4 dny

    Alekeni athana okhaokha a tonse alliance wo. Ayamba kale.

  • @user-cy7gd1go6y
    @user-cy7gd1go6y Před 27 dny

    Fire 🔥🔥 plus 💪💪

  • @YasinMusa-ym8lp
    @YasinMusa-ym8lp Před 27 dny

    Kunena soona malawi wata boma lamalawi rochimtisa manyasi chivukwachani kumalawi kukukanika 🇱🇾😭

  • @MonicaChunga-wg6xz
    @MonicaChunga-wg6xz Před 15 dny

    Mutichitire chifundo mulungu pautsogoleri uwu

  • @GanieAlidih-gu7no
    @GanieAlidih-gu7no Před 27 dny

    💪🏼💪🏼💪🏼💪🏼💪🏼

  • @user-st6bt5vv9c
    @user-st6bt5vv9c Před 25 dny

    Achule awa achoka basi tizikavota ngati amalawi zoona ndithu

  • @LovemoreSalima
    @LovemoreSalima Před 24 dny

    Ndizoona. Anaberadi

  • @user-oq7hi3hd4p
    @user-oq7hi3hd4p Před 27 dny

    Amen

  • @user-te3ps3kf2t
    @user-te3ps3kf2t Před 26 dny

    True,

  • @TracyZiyaya-nz4pd
    @TracyZiyaya-nz4pd Před 25 dny

    Maka maka chilima mulungu athane nawe ndipo unapanga zonyasa kwambiri ku dziko lino lamalawi

  • @IssaKapalamula
    @IssaKapalamula Před 14 dny

    Munthuyo ndi sapota wa dpp, ndiye mukuona ngati anganene za nzelu?

  • @EmmanuelGasiten-fo5dr
    @EmmanuelGasiten-fo5dr Před 23 dny

    Mulungu awalange ma Judge amenewa.

  • @ivychithyoka1551
    @ivychithyoka1551 Před 16 dny

    Speak Game changer!!!!!?

  • @user-oc9vl9xz8e
    @user-oc9vl9xz8e Před 27 dny

    Kodi monse munayambila muja kuti mupita pa mseu muzapitapo liti pomwe zinthu zikupitilila kuwonongeka???

  • @user-st6bt5vv9c
    @user-st6bt5vv9c Před 25 dny

    TIZALOWA AMBIRI PAMSEU

  • @NicholasJames-cb7du
    @NicholasJames-cb7du Před 27 dny

    Big man bwanji simutumiza ma audio a dj munyanane pepani ngat ndalakwisa kufusa

    • @nyasavoicebox
      @nyasavoicebox  Před 27 dny

      Simukulakwitsa tiyesela tiziponya mungoti tipatsa ka mpata pang’ono

  • @MasiyeDayton
    @MasiyeDayton Před 27 dny

    Kkkkkkk game change ❤

  • @BistonNjobvu
    @BistonNjobvu Před 27 dny +1

    Koma antnhu amaziwa kutsata nkhani

  • @ivychithyoka1551
    @ivychithyoka1551 Před 16 dny

    Eeeeeeee Apm anaberedwa

  • @BensonMalaulo
    @BensonMalaulo Před 27 dny

    Mumakwana Mr game changer

  • @user-qm1ri6cr6w
    @user-qm1ri6cr6w Před 26 dny

    Zen zen

  • @JosephMwambe-rz2oy
    @JosephMwambe-rz2oy Před 17 dny

    Zoona zimezo

  • @uchizJoelMumba
    @uchizJoelMumba Před 27 dny

    Ndiye ngati ukulimbana ndi majaji mbale wanga ndi dpp yakowo mulipamabvuto ndithu amene akutumawo akupweteketsa mbale wanga

  • @user-mm3es3ph7h
    @user-mm3es3ph7h Před 4 dny

    MCP, yawonga zambiri.

  • @user-nj5vu8cd5l
    @user-nj5vu8cd5l Před 25 dny

    Kodi APM , mukunena galu wakupha ma albinos ndi kuba ndi chisale

    • @DIRECTORJARVMACK
      @DIRECTORJARVMACK Před 16 dny

      Mukuganiza ngati mwanatu mesa achakwera amamufufuza sanamupedze ndi mulandu uliwose

  • @amiduclement2142
    @amiduclement2142 Před 19 dny

    Kodi ku mcp kuribe wina wazeru

  • @SolokingChimzy-yt7dj
    @SolokingChimzy-yt7dj Před 27 dny

    Chakwela Ali ngat Hule wa pa saloon yemwe amazazionesa ngt munthu wabwino koma Ali ooopsa kuposa hule yemwe Ali ku Bar

  • @homeremedys3748
    @homeremedys3748 Před 27 dny

    Panopa MCP yayamba kuchotsela masiku, DPP yayamba kuwengela masiku

  • @BertharrySecurity
    @BertharrySecurity Před 27 dny

    Chilungamo chimawawa,Koma mnthu wayankhula chilungamo uyu.

  • @paulbanda9638
    @paulbanda9638 Před 27 dny

    Chi christu nthawi zina sichiri bwino, a chakwera ndi a khristu, zikuchitikazi ndi panichimeti kwa amalawi onse, chakwera ndi tonse alliance ndiakuba anaba boma kuli ndalama kukhala bwanji

  • @phillipstamaley7901
    @phillipstamaley7901 Před 21 dnem

    Chakwela woyeeee mcp m'paka 2063

  • @SALIMASSAN-vr8ld
    @SALIMASSAN-vr8ld Před 27 dny

    Ndip iwey ulem wak srs chilungam chikuveka bwin kwambir

  • @RaymondKaumba
    @RaymondKaumba Před 10 dny

    Galu iwe

  • @user-xy9vz6jj4u
    @user-xy9vz6jj4u Před 27 dny

    MA judge pawo pawo ndthu

  • @MonicaChunga-wg6xz
    @MonicaChunga-wg6xz Před 15 dny

    Chitsime chakudya chimaoneka chikaphwa

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b Před 27 dny

    Mulungu akuwona zonsezi tsiku la 40 lidzawakwanila anthu amenewa

  • @IsaacMusa-py2jm
    @IsaacMusa-py2jm Před 27 dny

    Mau amphanvu 👊 👊

  • @gladysbonongwe1038
    @gladysbonongwe1038 Před 27 dny

    Dzuka Malawi dzuka

  • @Chiso2019
    @Chiso2019 Před 27 dny +1

    A munthalika amagona kwambili that's why analandidwa dziko....nanuso mukuyankhula kwambili koma action zilo

    • @ShabaniKuswere
      @ShabaniKuswere Před 27 dny

      Kupewa sikupusa anapewa nkhondo

    • @user-eh1mg3ww6d
      @user-eh1mg3ww6d Před 27 dny

      Ndipo ndizoonadi mulungu samalakwitsa amafuna athu amuone chakwela kuti si muthu oyenela kutumikila Malawi

    • @ibrahmdoka7486
      @ibrahmdoka7486 Před 27 dny

      Umafuna Peter apange nkhondo mbuziwe

    • @ibrahmdoka7486
      @ibrahmdoka7486 Před 27 dny

      A judge amenewo tidzawamanga

    • @SolomonNjolomole
      @SolomonNjolomole Před 27 dny

      Kuyankhula kwabwanj uku mumafuna ayambitse nkhondo?

  • @gladysbonongwe1038
    @gladysbonongwe1038 Před 27 dny

    Majaji ndi amene ayika amalawi pamoto

  • @IssakeMateyo
    @IssakeMateyo Před 27 dny

    Kkkkkkk

  • @user-ky8eq5ek1p
    @user-ky8eq5ek1p Před 27 dny

    Zoonadi munthu wamkulu

  • @uchizJoelMumba
    @uchizJoelMumba Před 27 dny

    Galu wa dpp kulila mobangula ndiye sunati ukanalila mcp 2025 boma kale

    • @mafukenimasangwi5487
      @mafukenimasangwi5487 Před 27 dny

      Dzinazi osamatengela kut bambo anu anali a mcp kapena a dpp koma kumaona kut nziko mwathu zinthu zikuyenda? kapena ayi ngati mumamwa tea sikuti ndi azibale anu nso onse akumwa tea ayi akuvutika mukatengala ku muziti simunaati muziwe kut azibale anunso ali mugulu lomwelo lomva zowawa

    • @FelleCasim
      @FelleCasim Před 26 dny

      Zitsilu za nyau inu wamzelu angavotele mcp panomso?

    • @DIRECTORJARVMACK
      @DIRECTORJARVMACK Před 16 dny

      Kumalikonda dziko lako osati umoyo wako ayi anthu akumva kuwawa

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 Před 27 dny +1

    Malawi panopa akuvesa chisoni machine opanga mapassport sakugwira ntchito panopa machine wopangira ma ID akuvutaso Koma chakwera wuziwe komwe wuliko Kuti wulamuliro wako ndi mulungu yemwe ndiwokwiya ndi iwe

  • @Littlefair7
    @Littlefair7 Před 27 dny

    Mutholo ndi anzako achina Ben Longwe mupeze zochita, what you're doing is not activism, this is stupidity of its highest order, mwasanduka oyankhukira zipani, zopusazi tasiyani, ngati mukufuna u activist pitani ku school mukaphunzire osati kumasokosa ndi zopusa zanuzi.

    • @EvanceEdson-fz1vn
      @EvanceEdson-fz1vn Před 21 dnem +1

      Akunena chilungamo, chilungamo chimawawa. Why 50+1, why alliance yet anakana a mec fresh vote registration? Don't you see kut the same rules of 2019, could apply for the fresh 2020 election

  • @user-mf7hf7we2u
    @user-mf7hf7we2u Před 27 dny

    Simungavumeleze

  • @LilianKachala-yz2xf
    @LilianKachala-yz2xf Před 27 dny

    Mau Amphamvu ngati amenewa tamva ndithu