HOT CURRENT YA LERO ACHINA BRIAN BANDA ASAMBWANZA MCP NDI DPP YOMWE OPANDA OSALA ONSE KUWATOKOTERA

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 11. 09. 2024

Komentáře • 192

  • @hastingsmdindo627
    @hastingsmdindo627 Před 24 dny +28

    Brian please read my comment; In one of the coming programs, mudzapange program special:
    1. Santhulani zifukwa zonse zimene a Malawi anaitopela DPP.. amve ndithu
    2. Santhulani zifukwa zomwe a Malawi aitopela MCP, nayo MCP imve

  • @chesterphiri7523
    @chesterphiri7523 Před 24 dny +9

    The fact that there was no mass exodus of members of parliament after DPP lost the election is a sign that MCP is not good.
    DPP is still intact with almost all MPs in place that must give MCP sleepless nights.
    The demise of Chilima has made things very awkward for MCP, they thought that they were clearing their way BUT it seems that it has backfired.

  • @WaNDEVUSeventeen
    @WaNDEVUSeventeen Před 24 dny +17

    DPP ndi chipani chikuonekako kuti chikhoza kutitsogolera pamene tikuyembekezera kubwera kwa mfumu yachilungamo yemwe ndi YESU CHRISTU

  • @MusaManati-ho4zf
    @MusaManati-ho4zf Před 24 dny +5

    Koma a Bishop wa ndie eeeee akuphaphalisa heavy ameneyu ndi mamuna,,,,,,,,,sakunyengelera😢

  • @BenjaminPhiri-n2r
    @BenjaminPhiri-n2r Před 24 dny +8

    Well arranged and organized

  • @GrecianHaward
    @GrecianHaward Před 24 dny +3

    APM MY VOTE, CHIKANGAWA AKAGWERE UKO

  • @PatrickSomanje
    @PatrickSomanje Před 23 dny +2

    But chakwela don't deserve anything to people of malawi

  • @wadsoncontinue3017
    @wadsoncontinue3017 Před 24 dny +5

    The best hot current programme I've ever watched

  • @FredLiwonde
    @FredLiwonde Před 24 dny +13

    Chilunga ndichakuti Mcp ina wina chifukwa cha ma vote a Dr chilima osamayiwa kupanda kuphatikiza mavote sakana wina remember this DPP is true party

    • @chesterphiri7523
      @chesterphiri7523 Před 24 dny +3

      There is no two way about it.
      Without Chilima there was no Boma for MCP ayi.

    • @williammandhlopa
      @williammandhlopa Před 24 dny

      Sure sure

    • @williammandhlopa
      @williammandhlopa Před 24 dny

      ​@@chesterphiri7523zoona

    • @Musa1828-l5d
      @Musa1828-l5d Před 23 dny

      @@chesterphiri7523Zoona koma why anaganiza zomupha Chilima eishiii zimene zija ndikhaza zoposa ufiti

    • @henryphiri6100
      @henryphiri6100 Před 23 dny

      Greedy.dyera​@@Musa1828-l5d

  • @KembastaSll
    @KembastaSll Před 24 dny +3

    Kkkkkk iiiiii kma abusa musamatiseketse mwava
    Manyazi agwira mchembers?

  • @UchizieFMtemela
    @UchizieFMtemela Před 24 dny +3

    MCP payokha siyikanawina pachilungamo and inawina coz of UTM koma DPP ndiye imawina olo payokha koma panopa ndiye ndi bomba la nyooooo coz ndikaona AFORD, UTM, ndi UDF❤❤❤❤❤

  • @elishamael-shadai
    @elishamael-shadai Před 23 dny +1

    Bola Peter ,uyu Chakwera nde wanyapo heavy,what has he done in his term.

  • @petersinga3114
    @petersinga3114 Před 23 dny +1

    Tidziyamika Yehova tikadali ndi moyo chifukwa wakufa sangathe kuyamika. Nice program keep it up guys.

  • @PatrickSomanje
    @PatrickSomanje Před 23 dny +1

    I love u guys for gd job u done for people of malawi well done

  • @StanleyChabwera
    @StanleyChabwera Před 24 dny +1

    Dpp. Please 🙏 anyamata amikono asakhale ndi phamvu zochuluka kupotsa boma. Asakwele magalimoto nambala plant...isakhale ngati. Ana Adad. Asamuwophyeze wapolice

  • @JamesDaud-jz7uq
    @JamesDaud-jz7uq Před 24 dny

    Guys you are very wonderful, may the almighty Allah give you and give you more wisdom

  • @Sedicmuzammil
    @Sedicmuzammil Před 24 dny +1

    I love the program... This is hard talk😊😊

  • @user-dy7oo5uy8l
    @user-dy7oo5uy8l Před 24 dny +4

    Eeeee guys mumatha. This is great.

  • @user-mh7cc8up4i
    @user-mh7cc8up4i Před 24 dny +1

    APM yemweyo tchitozawo ndizabwinoko kusiyana ndi Mr chikangawa DPP 2025 boma

  • @user-ix4yv4rn1f
    @user-ix4yv4rn1f Před 24 dny +2

    koma abusa mumayankhula keep it up

  • @genesismbewe
    @genesismbewe Před 22 dny

    pankuku , a bishop and brain a very good combination...mmakwana mabwana

  • @JonesMatthews-p6p
    @JonesMatthews-p6p Před 24 dny +1

    To be honest Mr BB this is incredible program.
    But I would like you to talk openly where these people they missed as on there last government so that they must fixe it and have new and changed people that can change malawi.
    Please please we need the party that will lead us in right way without selecting

    • @justinmaonga738
      @justinmaonga738 Před 24 dny

      Only God can lead us to the right path as a nation

    • @JonesMatthews-p6p
      @JonesMatthews-p6p Před 24 dny

      @@justinmaonga738 but God can fulfill our wishes if we ask him to do so.

    • @EndisonKamanga
      @EndisonKamanga Před 23 dny

      MCP kuba it's too much naumo Analowela mmboma kuwona ma billion Amene Ana koma Akuti maiko ena zikuvutaso chimodza modzi koma ndalama Anthu Awo Amangoba zinthu zambiri Anangolonjeza nthawi ya complain palibepo zimene Anakwanilisa.zinthu zawo zimangokhala Zosemphana ndimalonjezo

  • @grittersuzy7294
    @grittersuzy7294 Před 24 dny +1

    That man sounds like Wonder. If not watching you can think it's ndevu za mwayi talking

  • @wynkatengakaunda2275
    @wynkatengakaunda2275 Před 23 dny +1

    Dpp can not change, umphawi chabe uwu

  • @CleverChiumia
    @CleverChiumia Před 18 dny

    A APM adzawina ndipo osakaika. Ife anthu osauka nfi amerene tikavitere DPP. Kuukaslamba sichifukwa koma nzeru ndi zomwe anthu akufuna

  • @patrickmuronya7486
    @patrickmuronya7486 Před 24 dny +3

    Yea. Dpp moves on.

  • @user-eq8hr8li8h
    @user-eq8hr8li8h Před 24 dny +2

    Ndipo ndizoona ine ndinamuimbilapo phone Dr kondwani Nakhumwa ndikulembaso pa wap koma sanandiyankhe mpaka lero koma akuyembekedzera vote yanga

  • @SydneyNyasuli
    @SydneyNyasuli Před 24 dny +1

    When you are hangry you can eat even madeya this is great hot current

  • @HajjAmadu-e1u
    @HajjAmadu-e1u Před 24 dny +2

    Timakunyaadiran simuyangana mbali pitilizani kuyankhula chilungamo or chimapweteka wandisokosera kulinga utamva

  • @williammandhlopa
    @williammandhlopa Před 24 dny

    The death of Chilima represents a significant issue in Malawi. It is imperative for the government to disclose the circumstances surrounding this event in order to mitigate speculation. There should be accountability for the plane crash. In the United States, we have witnessed authorities being held accountable and questioned in the aftermath of incidents such as the shooting involving Trump; however, in Malawi, there appears to be a lack of responsibility regarding the plane crash, which is a serious concern.

  • @veronicamustafa305
    @veronicamustafa305 Před 23 dny

    Eeeeeh Brian is Bae🤣🤣🤣🤣😆🥳🥳🥳💃💃💃💃nde alinkuseka mwamwano mopweteketsa mtimatu kkkk

  • @BenjaminPhiri-n2r
    @BenjaminPhiri-n2r Před 24 dny +3

    Well organized DDP

  • @LauterioJoséPadeiraSabonete

    Inde paribe wabwino koma Adad timadya pasiku katatu koma chikangawa eeeeeeee paribe chabwino choti tinganene bola adad omwewo basi

  • @RuthKaunda-tc5qd
    @RuthKaunda-tc5qd Před 24 dny +1

    Koma Moto wayaka kuti buuuuuuuuuu mumatha atsukuludzi. Tiyimbe mng"omaaaaaaa

  • @williammandhlopa
    @williammandhlopa Před 24 dny +1

    Powerful program

  • @Lingstone-r3z
    @Lingstone-r3z Před 24 dny

    And one thing that I hear from our excellence Peter he said ,to go every week to outside country for nothing just west our money that is not good

  • @DatsanChickwekwe
    @DatsanChickwekwe Před 24 dny +1

    Very good question or assignment to both mcp and dpp why should we vote for u again??????
    Dpp in 2020 was voted out now wants to came back have learn the mistakes which u did to fail??
    Mcp u promised good thi gs to malawian to canani have fulfilled ure promises or u have failed?
    To both of u chakwela and mutalika ure weakness are on corruption ure not strong enough to end up corruption that's why ure failing to forfill ure promises

  • @felixMhone
    @felixMhone Před 24 dny +1

    Dpp is agood party

  • @Lingstone-r3z
    @Lingstone-r3z Před 24 dny +1

    And even he choose the people to give some chairs he make balancing from north south and east you see it what he did ,my length looks like to win that ,,,, I hopefully get well

  • @AdamAhamad-k2i
    @AdamAhamad-k2i Před 23 dny

    MCP siyingawine mzimu wachilima wakwiwa ngakhale atabera bwanji ndimwana wa John tembo

  • @MarthaMtonga-qt6tc
    @MarthaMtonga-qt6tc Před 24 dny

    Anthu abwino inu mwaunikila zenizen ❤❤❤ but APM my Vote🔥🔥🔥

  • @simuwisick-it2yc
    @simuwisick-it2yc Před 24 dny +1

    Manyazi agwira ntchembere😅😅

  • @johnpeterchikagwa
    @johnpeterchikagwa Před 23 dny

    A Chakwela kodi alibe wowauza kuti a chepetse msulendo a kunja ndi mdziko lino kuti ndalama zisamaonongeke?

  • @PatrickSomanje
    @PatrickSomanje Před 23 dny

    Koma mcp itipha ndi njala boza amalawi tikuvutika koma uyu chikangawa ayi boza wawazuza amalawi

  • @MayamikoYMsusa
    @MayamikoYMsusa Před 24 dny +1

    Jona lero wayaka,moti kuphatikizapi ambuye Bishop,,kwatenthadi

  • @JudithClement-vj9ds
    @JudithClement-vj9ds Před 24 dny +1

    MCP ndichipani chokhacho cha masophenya abwino wadziko. MCP my vote

    • @shadreckphiri1799
      @shadreckphiri1799 Před 23 dny

      Abale, till you feel bad that MCP killed your fellow Malawians.Come on guys

  • @IssaJohn-cb8vn
    @IssaJohn-cb8vn Před 22 dny

    Ndipo for sure a bishop sakunama mcp payokha siyingawine

  • @PettyMadondo
    @PettyMadondo Před 19 dny

    Kuyakhula kwanu mumayakhula chilungamo koma mmmm kusava azitsogoleliwa koma pano pake bolani DPP chifukwa msuzi okha timanyambitako

  • @CharlesChipwere
    @CharlesChipwere Před 23 dny

    Boma tikuupatsaninso koma sitikufuna galimoto zolembedwa ana adadi regionalism muzintchitomu muike policy yokweza anthu pantchito morivation

  • @VizalonaRichard
    @VizalonaRichard Před 23 dny

    Dpp iwina ndithu ndipo tikuyembezera kuti izasintha zinthu , koma ndikanakonda kuti boma ngati silinakwanilitse zomwe imalonjeza wanthu pakhale lamulo loti izitula udindo pasanathe 5 years

  • @MexcoJepter-p5f
    @MexcoJepter-p5f Před 24 dny +1

    Brian Banda and Jona pamkuku ulemu wanu

  • @johnpeterchikagwa
    @johnpeterchikagwa Před 23 dny

    Bwanji A chakwela akulola kuti mwana wao ayendetse za immigration mpaka kuononga printing of passports? Katangale wachuluka ku Road Traffic ndi ku police .Tikuchita nazo manyazi zimenezi.Boma lipereke report pa imfa ya Vice President kuti achite clear suspicion .Sitonse tikudyelera muboma koma maboma ochepa mu central region akunamiza President ndani?

  • @BlessingsMakalani
    @BlessingsMakalani Před 23 dny

    Mr Bishop Mukutimirila

  • @samuelsergio5343
    @samuelsergio5343 Před 24 dny +2

    Dpp panopa ndi 🔥

  • @DanJohn-ws5gl
    @DanJohn-ws5gl Před 23 dny

    Tiye nazon mr Brian b✅✅✅

  • @pacharokoloviko1694
    @pacharokoloviko1694 Před 23 dny

    Eh! Koma iyiyi madolo mwaibayatu okumva wamva

  • @LingstoneLing
    @LingstoneLing Před 18 dny

    DPP is innocent people

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 Před 24 dny

    Ndipo Dpp ❤❤❤❤ yanyamuka iyi basi palibe kuyima iyi

  • @ThatcherNdhlovu
    @ThatcherNdhlovu Před 22 dny

    Nkhalamba ndiimene imadziwa kusamala ana bwino adad omwewo

  • @CydrickBandah
    @CydrickBandah Před 23 dny

    Kodi mukuti Dpp inapanga chani kuti inkhoza kubwelelaso mbo'ma ???

    • @AbdulsharifulKalipinde-m6u
      @AbdulsharifulKalipinde-m6u Před 23 dny

      Timadya katatu
      Sopano chikangawa yapanga chani
      Chimanga mbola
      Fertilizer mbolo yako
      Kupha mbolo yako
      Kumanga anthu osalakwa mbolo yako
      Katangale mbolo yako
      Boma likuvutika koma iyeyo kumawononga ndalama zakhani khani

  • @DanielKaombe-im3pr
    @DanielKaombe-im3pr Před 23 dny

    APM my vote

  • @hamiltonsolomon3756
    @hamiltonsolomon3756 Před 23 dny

    The best Hot Current More Fire 🔥 Guys❤❤❤❤❤❤

  • @mcsydenynsinga7610
    @mcsydenynsinga7610 Před 24 dny

    Malangizo, kapena kuti maeso mumawuziladi ndithu makosana, anthuwa koma kusamva kapena mwina muziatumizilanso program imeneyi Ku ma email awo kuti mwina adzumva ndithu as a result tizakhale ndi Malawi wabwino

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 Před 23 dny

    Zoonadi ineso ndi kuwona chocho Kuti MCP izipakira because time is over takhara tikudandawura nthawi yayitari Koma MCP kuzikonda panopa siting abwerere tawona kale choipa ndi chabwino

  • @danielmagwaya1074
    @danielmagwaya1074 Před 23 dny

    Is true simukunama

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy Před 24 dny +1

    This is true hot current big up guys

  • @IssaJohn-cb8vn
    @IssaJohn-cb8vn Před 20 dny

    Abrain mukuyiwala feteleza bwanji???????

  • @FracksonAskanSoko
    @FracksonAskanSoko Před 24 dny

    MCP yili mumaji

  • @BerthaMisanjo
    @BerthaMisanjo Před 23 dny

    DPP my vote

  • @KembastaSll
    @KembastaSll Před 24 dny

    Achina brain kdi ndinzeru nzanji muli nazozi?
    Zochokera kwamulungutu lzi

  • @KeraMkandawire-pn5lx
    @KeraMkandawire-pn5lx Před 24 dny +1

    Mau a Jessie kabwira "Chakwera WA muyaya" Sanalankhule bwino, Mau okhawo it's a threat kwaopanga nawo mgwirizano. Kuthamanga kuyankhula

  • @user-gk6bf7xe9g
    @user-gk6bf7xe9g Před 24 dny

    MCP ❤❤❤

  • @LovenessKamzimbi
    @LovenessKamzimbi Před 21 dnem

    Zoona iyi Ili bho

  • @beinhardkausiwa7107
    @beinhardkausiwa7107 Před 24 dny +1

    Bishop ❤

    • @WesleyKalimwayi
      @WesleyKalimwayi Před 23 dny +1

      Bishop ndi anyamata awili awa chilungamo chikuveka

  • @user-cv5ef4hb6e
    @user-cv5ef4hb6e Před 24 dny

    Zoona ngati DPP izalowe mboma chinyengo chomanga misewu yosalimba muzasithe kumamanga zithu zokhalisa

  • @NoelChimkango
    @NoelChimkango Před 23 dny

    Mkulu wa arsenal ali bho😂😂😂

  • @mathewsmakina7845
    @mathewsmakina7845 Před 24 dny

    Program yowunika dzipaniyo ndiyoona komano anthu akumudzi muwathandiza bwanji mwachitsanzo Kuno kunsanje north times simamveka tithandizeni Ife Bwana Brian Banda chonde

  • @PeaceElias-z4b
    @PeaceElias-z4b Před 24 dny

    Arfod nayo ngati sagwizana pachibale Inock ndi Elmira angalamule bwanji

  • @AmoniCVwalika
    @AmoniCVwalika Před 24 dny

    Zikomo inu a hot currency mwatilakhula bwino ife amalawi wakubva ava

  • @CharlesChipwere
    @CharlesChipwere Před 23 dny

    😂Nthawi yatha kuti mcp itipange convince zinthu adaononga kale ndanena izi kutengera zomwe zachitika pa10june mpobvuta kwambiro kuti tiwakhuulupilirenso cyber crime tatopa nayo tione zina ndikunenane ndiwachinyamata yemwe adayamba kutsatira ndale chifukwa Cha mbiyeni

  • @DaudMbumba
    @DaudMbumba Před 24 dny +2

    Dpp yavinidwa sizachitanso lets give them vote

  • @ManganiStanley
    @ManganiStanley Před 24 dny

    Ndipo kwambiri abweele ndi list zomwe anatiuza kt akwanisa cani kukwera Kwa zinthu komanso ndalama yathu kucepesedwa mphavu Kodi ndizomwe anatilonjeza?

    • @JacquelineKanjedza
      @JacquelineKanjedza Před 24 dny

      Izi ndizachuma simungalankhule chonchi apo bii ndinu mbuli pazachuma coz enafe fanta tagulapo k3 lero ndi k700 onani kusiyanako

  • @BaulenPatison
    @BaulenPatison Před 24 dny +2

    Namodzi onani mipunoyo athu oipa yawa

  • @DanMhone-iw6xg
    @DanMhone-iw6xg Před 24 dny +1

    Ayipa lelo pazana paja anali achilungamo zikuvutanibe anyamatawa amangoyima pa chilungamo

  • @PaulBeyad
    @PaulBeyad Před 24 dny

    Yes this is true story

  • @WesleyKalimwayi
    @WesleyKalimwayi Před 23 dny

    Choyamba tibweletseleni zimu wa chilima omwe mukusunga achakwela chifukwa ngati mukukanika kubweletsa report ndiye kuti mukusunga zimu yake

  • @robietadeyo9205
    @robietadeyo9205 Před 24 dny

    🔥🔥🔥

  • @DanielKaombe-im3pr
    @DanielKaombe-im3pr Před 23 dny

    Powerful

  • @WesleyKalimwayi
    @WesleyKalimwayi Před 23 dny

    Akuti achakwela mudzafuna voti mmmm

  • @IssaJohn-cb8vn
    @IssaJohn-cb8vn Před 22 dny

    Anthu inu ndimafumu ndipo bwaloli mukuziwa kulitambasula

  • @WesleyKalimwayi
    @WesleyKalimwayi Před 23 dny

    My DPP

  • @OnceMwawembe-x7c
    @OnceMwawembe-x7c Před 24 dny

    Fantastic polical analysis Brian and your friends

    • @rodglae6657
      @rodglae6657 Před 22 dny

      Actually it was a journalistic analysis without good research. They forgot kuti APM and Bingu ankakwera ma mini bus komanso kugula usipa mumsika wa Lilongwe and getting involved in so many commonly organized activities; only to grow wings when they were in power. In addition, zikwanje ku MCP zidakonso nthawi ya Gwanda ndi JZU, and there was a time they ran 2 parallel conventions on the same dates, ina ku Lilongwe and ina ku Blantyre. Politicians won't learn from their mistakes and assume that they may be asking too much from them. Speaking with confidence kuti awina is a political language imene sufunika kuyankhula ngati ndiwe failure. Do a good research before coming on air.

    • @rodglae6657
      @rodglae6657 Před 22 dny

      Actually it was a journalistic analysis without good research. They forgot kuti APM and Bingu ankakwera ma mini bus komanso kugula usipa mumsika wa Lilongwe and getting involved in so many commonly organized activities; only to grow wings when they were in power. In addition, zikwanje ku MCP zidakonso nthawi ya Gwanda ndi JZU, and there was a time they ran 2 parallel conventions on the same dates, ina ku Lilongwe and ina ku Blantyre. Politicians won't learn from their mistakes and assume that they may be asking too much from them. Speaking with confidence kuti awina is a political language imene sufunika kuyankhula ngati ndiwe failure. Do a good research before coming on air.

  • @PaulMwachande
    @PaulMwachande Před 24 dny

    MWALANKHULA ZONVEKA OSANVA NDI AMCP BAS

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs Před 24 dny

    Iyiiii munali miyambi 😂😂😂❤❤❤❤❤❤

  • @AustinBottoman-x1y
    @AustinBottoman-x1y Před 21 dnem

    Koma ma comment ali apa eish ndiokweza bp

  • @williammandhlopa
    @williammandhlopa Před 24 dny

    Donot underate the leaving of UTM and the death of chilima

  • @BlessingsSeleman
    @BlessingsSeleman Před 24 dny

    Mcp ikukula mtima chifukwa akudalira mpika oyang'anila zisakho uli mbali Yao koma popanda izo sangawine

  • @LouisBanda-j2m
    @LouisBanda-j2m Před 24 dny

    Nkhani ndi mazi

  • @YusufAjiruh-c5q
    @YusufAjiruh-c5q Před 24 dny +1

    🎉🎉

  • @VikingsMalawi
    @VikingsMalawi Před 24 dny

    Mcp ndimakaphe ndianthu akupa