ATUPERE MULUZI WAKONZEKA

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 9. 07. 2024

Komentáře • 18

  • @AREFRIEDNELSON
    @AREFRIEDNELSON Před 18 dny +1

    Kamwani gamora yooooo muchira akufuna kuti akhale ndi athu ambili azidwalabe HiV gorvinment likufuna kuti azidya Ndalama zochera kumayiko akunja ziti sizingawafikile athu odwara matenda waaaa ndikulimbikitsa kuti athu amwe akugulitsa mamkhwara wo kuti Azigulitsabe osawanvera athu achakwera woooooo 😮😮😮😮😮

  • @MarriamBakalie
    @MarriamBakalie Před 17 dny +2

    Aliyese ali ndi choice asiyeni anthu azimwa inu vuto lanu ndichani? Zausilu basi agalu inu mumaziwa mankhwala ndiinu nokha basi ? Osanena kuti business ilowa pansi bwanji machende anu nonse

  • @MisheckAselo
    @MisheckAselo Před 14 dny

    Aaaaa chakwera pa ulimi okhao ndiye mukunama fertilizer saoda ku butchery

  • @PempheroAlufandika
    @PempheroAlufandika Před 15 dny

    Boma ioro

  • @wysonmpatama4393
    @wysonmpatama4393 Před 17 dny

    Mulungu chonde akanatipatsa uyu abale chonde kumwambakooo😊

  • @KenChitete-pg3ws
    @KenChitete-pg3ws Před 15 dny

    Mankhwala amene akhodza kukhala ochidza koma,tsangavomele chifukwa amadyela momo.

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 Před 17 dny +1

    Ena Ku MDF, Ndiku MCP Mupemphele Musaluze Zisankho 2025 Imfa Ya chilima Ija Ena Muzamangidwa,
    Sindikukuopsezani ichi Ndilungamo ndithu

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu Před 17 dny

    Yaaa zoona arv is powerful

  • @user-co3wr3rn4h
    @user-co3wr3rn4h Před 17 dny

    In fact tose angoni tikanakhala pamoz mzimba ntcheu tiyeni tigwilane manja kumuzimbaso akanazisiya kaye tilimunyengo yolila

  • @KenChitete-pg3ws
    @KenChitete-pg3ws Před 15 dny

    Ndani angavotele atupule,,olo atakhala opambana ku convention mwina Bambo wake ngati akulephela kuwina pawu mp kudela lakwawo adzawina u president????

    • @EamonChikanda
      @EamonChikanda Před 15 dny

      Kodi a Chakwera adakhalapo nduna or mp asadakhale president? Its better Atupele coz anakhalapo muma unduna ambiri komanso he has had been served in different government parastetals.
      So he is eligible to serve the sit

    • @user-dv6rt6vb6e
      @user-dv6rt6vb6e Před 14 dny

      Mbuli munaivotela ija nde imaziwa chani?anthu kuyesa kukuuza kuti mbuli ziikuziwa chilichotse iyi koma inu kakaka laro ndi izi Malawi wasanduka Zimbabwe

  • @user-un6qv6sj3h
    @user-un6qv6sj3h Před 18 dny

    Kupusa kwa chakwera kumatumiza anthu ku Israel kukalima pamene mukulephera kumawalimitsa kwao shame on you MCP

    • @kingsleyhopematchaya5184
      @kingsleyhopematchaya5184 Před 17 dny

      Ndiwe mbuli ndipo sukudziwa chomwe ukuchita iweyo kulima kumudzinkwanu akuletsa ndani ulesi wako usapake chakwera

    • @Eric-gb9ms
      @Eric-gb9ms Před 17 dny

      Imagine to bring those mega farm in our country is better than to go work outside the country that's not good

    • @Eric-gb9ms
      @Eric-gb9ms Před 17 dny

      ​@@kingsleyhopematchaya5184mbuli ndiwe you don't know nothing about economy

    • @kingsleyhopematchaya5184
      @kingsleyhopematchaya5184 Před 17 dny

      @@Eric-gb9ms my brother send 2million this month from Israel ndipo taona kusitha kwa m bale wathu komaso sakakamiza mukhala ngati anakakamiza muthu bwanji

  • @OssmanAbubaker-l5s
    @OssmanAbubaker-l5s Před 17 dny

    Ayi mankhwala alipo a HIV