Ena mwa anthu ofuna kwabwino, ali okhudzidwa ndi kuvutika kwa ana.

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 9. 09. 2024

Komentáře • 28

  • @HurryBeston
    @HurryBeston Před 7 měsíci +1

    Ntchito yabwino anyamata pitilizani,
    Kuchokera Ku phalombe Malawi🇲🇼🇲🇼

  • @pioireneuvictorpio1391
    @pioireneuvictorpio1391 Před 7 měsíci +1

    Ulemu wanu ndasangalara pakuva za khani ya bungwe la Mr moyo.chifukwa tidayamba nawo limodzi momwe limayamba koma timasokhetsa katundu wothandizira athu akutari.apa ndakodwa powona akuthandiza athu apa vilapo

  • @alicehananiya
    @alicehananiya Před 7 měsíci +1

    Maganizo abwino kwambili mama pitilizan kusamala anawo mulungu akuenjezelen masiku amoyo

  • @user-wt1hf7hd5t
    @user-wt1hf7hd5t Před 7 měsíci +1

    Mulungu azipitiliza kukupatsa mzeru mwana iwe a Govart tikuyamikila ntchito yanuyi ndi Akadewere nomwe

  • @ODGENZUNGA
    @ODGENZUNGA Před 7 měsíci +1

    Mulungu alemekeze kwa anthu amene atengapo gawo lothandiza anawo

  • @HurryBeston
    @HurryBeston Před 7 měsíci +1

    Mayi wanzeru ameneyo kwaabasi wayankhula bwino, ndizoona kuti anawo akhale kosiya mhh ayi sizikhala bwino koma apitilize kukhala limodzi

  • @Mariana-vo5nu
    @Mariana-vo5nu Před 6 měsíci +1

    Mulungu dalisani onse amene azipele kuthandiza ana awa

  • @CatherineManda-j2v
    @CatherineManda-j2v Před 7 měsíci +1

    so painfull

  • @AleksaWilliams-qc6cn
    @AleksaWilliams-qc6cn Před 7 měsíci +1

    Pachipwitikizipo muzimasulira mchichewa pepani mongopepha

  • @joyceellis9045
    @joyceellis9045 Před 7 měsíci +1

    Viva anyamata athu.
    Inuyo ndi apululutsi.
    Kuchokera komwe kwa Kafere mmbalimbali mwa phiri la chiumbo, ndakunyadirani.

  • @user-bp5po7rt8e
    @user-bp5po7rt8e Před 7 měsíci +1

    Ndadandaula😢

  • @FrynessMoyo-to2du
    @FrynessMoyo-to2du Před 7 měsíci +1

    Mulungu apitilize kukundalisani agovat pantchito yomwe mukugwira

  • @user-ip6pt3rw7f
    @user-ip6pt3rw7f Před 7 měsíci +1

    zikomo mayi pitilizan chifundo chimenecho

  • @horaciofranciscofrancisco1535
    @horaciofranciscofrancisco1535 Před 7 měsíci +1

    Mphavu azibambo ulemu wanu basi

  • @user-zi7lt4gg5e
    @user-zi7lt4gg5e Před 7 měsíci +1

    Pitilizani nkhani zabwinozo God bless you

  • @AlasonPaulo-ht7zb
    @AlasonPaulo-ht7zb Před 3 měsíci +1

    Mulungu alemekeze agovat tchito mumatha

  • @NaduMbewe-zz6iw
    @NaduMbewe-zz6iw Před 7 měsíci +1

    Mulungu alemekezeke

  • @AleksaWilliams-qc6cn
    @AleksaWilliams-qc6cn Před 7 měsíci +1

    Keep it up BS,osamangotipasira zophana Zija eeeee

  • @Maklanalfredo
    @Maklanalfredo Před 7 měsíci +1

    Mwaitha anyamata happy new year

  • @meganabigail-ye7fw
    @meganabigail-ye7fw Před 7 měsíci +1

    Gova n kadewele be blessed guys

  • @meganabigail-ye7fw
    @meganabigail-ye7fw Před 7 měsíci +1

    Koma mwanayi wa zaka 16 ali ndi nzelu yaumunthu koma bambo wa anawa mulungu amukanthe kumene aliko nkuzuzisa ana osalakwa kumeneku

  • @user-us3hx4mv1n
    @user-us3hx4mv1n Před 7 měsíci +1

    Mumakwana ndipo timakunyadilani

  • @ziyamikanmakowa5981
    @ziyamikanmakowa5981 Před 7 měsíci +1

    God bless u govati

  • @MisheckAselo
    @MisheckAselo Před 7 měsíci +1

    Mau anga ndi amodzi, Agovate ulemu wanu pamodzi ndi team yanu🙏🙏

  • @pioireneuvictorpio1391
    @pioireneuvictorpio1391 Před 7 měsíci +1

    Ulemu wanu ndasangalara pakuva za khani ya bungwe la Mr moyo.chifukwa tidayamba nawo limodzi momwe limayamba koma timasokhetsa katundu wothandizira athu akutari.apa ndakodwa powona akuthandiza athu apa vilapo