Alick Ponje engages musician Limbani Banda also known as Lambani Dube on his musical career, religion, and why he changed his name, in this edition of Tikudziweni.
Chilungamo Ndi chowawadi Lambani Dube Uli boooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooniiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiii osanyengelera munthu anthu aku Malawi Ndi anakafumbwe
JB wanu uja ndi times 3
The song is good I did like it, the interview no comment.
Matamatu
Munthu wamatama ngati uyu ndisanamuone
He is a good artist and I cherish his music
Awa kuimba kunawagaya kunangotsala nkuzipopa
fact ndiyoti amatha kuimba akuluwa
Mkulu uyu ndiwachonchi,sakudziwa pomwe ali#matukutuku
Wofwayila awa akuzithenga ngati mzungu kupusa basi
Nyimbo yodziwika ndi modzi basi awa nyimbo zake ziti reggae yake it. 😂😂😂
Just want to know what he's doing for a living
Katana thoo ndalamaso za mkazi ngati izo
Chilungamo Ndi chowawadi Lambani Dube Uli boooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooniiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiii osanyengelera munthu anthu aku Malawi Ndi anakafumbwe
Adha awa ndi king 👑
Dada Tosh 🎉
Ndiye mwati chamba munasiya inuyo
Way up, way down 😊
Ndiopoila uyu , matama azamupweteka ,
Don Dada ❤
😂😂😂 mayina opoyira 🙏🙏🙏🙏
Kkkkkk! Awa ndi machine
KOMATU KHANUNDU
Fodya wachamba
Awawa ndi king. My favorite kkkkkk
Don't make sense
Ulkumalawi ukunyoza Malawi
Samayimba reggae uyu 😅
Limbani Banda He doesn't sing this reggae
Akut nyimbo zake amamvera anthu a class, simbatata iyai😂😂😂, koma aLambani mundikomola ine 🤣🤣🤣
Koma Limbani ada
Awa akufunika 1hr😅😅
Lambani is a Zulu word which means hungry person 😅
Baths
koma eish
😅😅😅
Iiiish..... Too sensitive
Very pompus 🚮
Kkkkkkkkkkkkkkkkk
😂😂😂
😂😂😂😂😂