UTM YAGANGALAMA, DR MICHAEL USI ZAKE ZIKUONEKA ZIKUMANA NDI KHOMA |

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 13. 09. 2024

Komentáře • 26

  • @user-ml4bl2ll2g
    @user-ml4bl2ll2g Před 17 dny +6

    The spirit of SKC is at work in Fredokiss Kaluwa,,he is the future leader of this country.we love you young man

  • @falliotphiri688
    @falliotphiri688 Před 17 dny +1

    Patricia Kaliati is the best leader ever to lead UTM and Malawi

  • @GodfreyMajamanda
    @GodfreyMajamanda Před 17 dny +1

    Koma mphekesera zomwe zikumveka zopanga alliance with dpp , that's a wrong decision,please to my suggestion I don't want this to happen, chidzakhala chibwana cha mchombo lende,musazayerekeze

  • @JohnfosterNkusengwa
    @JohnfosterNkusengwa Před 17 dny

    Guys am happy to hear what you have discussed and l wish if l was there to give support with my vote ❤❤❤❤❤ utm more fire all the from cape Town pa boma moto kuti buuuuu

  • @ChifundoDuncan-t9t
    @ChifundoDuncan-t9t Před 12 dny

    😢

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz Před 17 dny +2

    Now utm is well matured 100 percent and will see new Malawi indeed, nkhwangwara aoneka tikamawoloka tsinje kuti sikakowa

  • @Chikumbuso-l5m
    @Chikumbuso-l5m Před 16 dny

    Voti yanga yili ku UTM ndikanakhala ndindalama ndikanavota ngati ndinavota 2019 ndilikumalawi

  • @JohnfosterNkusengwa
    @JohnfosterNkusengwa Před 17 dny +1

    In Jesus power l swear this government is going and mr chakwera will see pepeya

  • @BatumeyoChikopa
    @BatumeyoChikopa Před 16 dny

    UTM my party forever, SKC mhsrip 😭

  • @user-ml4bl2ll2g
    @user-ml4bl2ll2g Před 17 dny +1

    Fredokiss is very wise indeed he has bright future In politics

  • @RABSONSIKELO
    @RABSONSIKELO Před 17 dny

    Fredo ...wise wise

  • @CharlesPhiri-ds1rk
    @CharlesPhiri-ds1rk Před 17 dny +1

    Aaaaaaa lero mwatembenukaso,,dzanja munkanyoza usi muli ku mzuzu,,,,mwachedwatu apa

    • @AlihIbrahim-s7v
      @AlihIbrahim-s7v Před 17 dny +1

      Mwachedwa ndinu a mcp musomva kodi zikunyasanipati

  • @henryphiri6100
    @henryphiri6100 Před 17 dny +1

    Abwana athuwo akafuna kupita kumeneko apite okha akamulandire bwana wawoyo.kkkkkkkkkkķķkkkkk

  • @YusufMapata
    @YusufMapata Před 17 dny

    akakhala vice president michael usi samavala utm uniform amavala uniform ya flames

  • @Chikumbuso-l5m
    @Chikumbuso-l5m Před 16 dny

    Manganya ndi wa mcp

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz Před 17 dny

    Ngati mumawelenga ma comments nanga zovuta za network ya chiphaso zja bwanji? Ife we are fight for future koma chiphaso

  • @alomuddin8801
    @alomuddin8801 Před 17 dny

    Okondedwa nose abale a utm, chonde khalani maso ndi manganya akufuna kukumangani mmaso, manganya ndi chintu mbewa mapiko mmbalame samalani,

  • @jameskadete2196
    @jameskadete2196 Před 17 dny

    Ndibweraso ndiphere kae

  • @CharlesPhiri-ds1rk
    @CharlesPhiri-ds1rk Před 17 dny

    Kaliate i goyankha funso

  • @MsondaBanda
    @MsondaBanda Před 17 dny

    Njawala ndiwe mwanalume, wa ntchindi , Utm yinganangika na kaliyati chifukwa ngwakujitemwa mukayowoyero ngwambula kujipepula,

  • @VictoriaKumwenda-k6o
    @VictoriaKumwenda-k6o Před 17 dny

    Akaliyati sangakhale .lida ndi apamwa kuzikonda

  • @GodfreyMajamanda
    @GodfreyMajamanda Před 17 dny

    Chonde musazapange mgwirizano ndi dpp