Med C - Ndekha (Visualizer)

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 9. 09. 2024
  • ‪@campseenmusic‬
    ‪@Ankolo_Tru‬
    ‪@Malawi-Music_._com‬
    ‪@nyimbozakumalawi‬
    #video #music #Visualizer #art #afrobeat #malawi #hiphop #trap

Komentáře • 30

  • @HaskayKachali
    @HaskayKachali Před 3 měsíci

    Pull up 🔥🔥🔥

  • @Vaps-king
    @Vaps-king Před 6 měsíci +2

    sanakusiye ase vuto makani plus maimvaimva namadingo ndiwabhobho 1:51

  • @daviegamah5370
    @daviegamah5370 Před 7 měsíci +2

    I just want to see you win someday 🔥🔥🔥💯🇲🇼

  • @mphatsomhoney3876
    @mphatsomhoney3876 Před 7 měsíci +1

    Suli mwala massage ziro in this song sitipopa zilizonse Mr ibu

    • @twistermw3544
      @twistermw3544 Před 6 měsíci

      or ine mwanai chomwe amamupopela sindimachiona ndavelapi zingapo koma lyric yake imakhala yosakhwima composition mbola

  • @budalaWillard
    @budalaWillard Před 7 měsíci +1

    Mwanayu ndi shasha

  • @UniquemvulaTv
    @UniquemvulaTv Před 8 měsíci +1

    🔥🔥🔥🔥🔥Med C sikape

  • @user-zy5ck2bz8r
    @user-zy5ck2bz8r Před 7 měsíci +1

    Ndemwati akuti chani

  • @BlessingsNkoloma-kf8rs
    @BlessingsNkoloma-kf8rs Před 7 měsíci +1

    Zimangovuta koma med c umatha kuimba ase

  • @Jesi.T4942
    @Jesi.T4942 Před 7 měsíci

    Fire burn ❤️‍🔥 song

  • @davidnoel599
    @davidnoel599 Před 7 měsíci +1

    this guy got talent

  • @KovaJasper-gd2mr
    @KovaJasper-gd2mr Před 7 měsíci

    Munthu wathu uyu ku mabilinganya 🔥🔥🔥

  • @dalitsomajigamajiga
    @dalitsomajigamajiga Před 7 měsíci

    Positive vibes

  • @user-qt4hj1bl3k
    @user-qt4hj1bl3k Před 7 měsíci +2

    Mfanayu anapanga zaukape kutayana ndi DOCTOR namadingo upempheso ma reback ase kwa DOC apobi utha choncho😂😂😂😂😂

  • @supasta_lilAL
    @supasta_lilAL Před 7 měsíci

    Love this kid🎉

  • @MPHOJACOBTLOU-zp6oq
    @MPHOJACOBTLOU-zp6oq Před 7 měsíci

    Well dlne, keep it up🎉🎉🎉❤

  • @Kannohmw
    @Kannohmw Před 7 měsíci

    Vision🔥

  • @levikamwana9954
    @levikamwana9954 Před 7 měsíci

    Hard

  • @chawezichirwa3322
    @chawezichirwa3322 Před 7 měsíci

    Big things start small 🫵

  • @DopfigureMw1940
    @DopfigureMw1940 Před 6 měsíci

    Talent ilipo km Okakha akuchepa 🧠👀

  • @andymalawi23
    @andymalawi23 Před 7 měsíci

    Nice song bro 🔥🔥

  • @yamikanikotamo9403
    @yamikanikotamo9403 Před 7 měsíci

    nyc

  • @user-zc3fh5yo8m
    @user-zc3fh5yo8m Před 4 měsíci

    Made cee munatha inu ndipo tinakuiwala pano

  • @NgomaRaheem
    @NgomaRaheem Před 7 měsíci

    Tabweleran pa tune ya money maker bro osati zanuzi Mr Ibu

  • @Ankoloslick
    @Ankoloslick Před 7 měsíci

    stop hating...this song is nice...mafuna aziimba zokomela inuyo? lol

  • @jeuzywandasigner4908
    @jeuzywandasigner4908 Před 7 měsíci

    iwe aise next tine ukazalowanso session uzamvele kaye money maker yako ija then uzayambe kulemba nyimbo cz how stupd is dat kuimba nyimbo yonse stle yamunthu ada 6th wakudyanso maten bwanji pammawa azayankhula adakulemberani nyimbo fanzi yako izakumudwa azakutulukanso always member bro be yourself skip if u wnt to but fct bro 😥

    • @BlessingsNkoloma-kf8rs
      @BlessingsNkoloma-kf8rs Před 7 měsíci +1

      Ase sukumama nyimbo ikunveka style ya 6th di

    • @Crae2sixty5
      @Crae2sixty5 Před 7 měsíci

      Mwangosuta zamba zanu uko mwati muchuluke nzeru.
      Muli inuko zanyimbo ndi zero pa teni.
      Keep going Med c, trap yake ndiyomweyi

    • @jeuzywandasigner4908
      @jeuzywandasigner4908 Před 7 měsíci

      @@Crae2sixty5 ndibwino artist akamasokela kumamuthandiza nzeru kupangila pammawa dada zimenezo oimba ambili adakhumudwisa ma audience ao Moti pano saawakonda nso inuyo ndiye mwadya chingambwe bwana 😂🤣