chifukwa chomwe anthu amamudera Dan Lu

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 9. 09. 2024

Komentáře • 216

  • @sammalvitha
    @sammalvitha  Před 28 dny +16

    Dan lu, amadedwa kwambili ndi anthu amene sankafuna kut DPP ikhale pa mpando ... Popedza kut ambili amene sankafuna DPP anali anyamata ... Dan lu pokhala mnyamata anadana ndi anthu ambuli maka achinyama ....
    Dan lu ndioimba wabwino amene sankayenera kusikidwa ... .
    Zikanakhala kut dan lu ... Ankasapota UTM bwenz zisanachite affect music career yake ... Sindikut career ya Dan inaonongedwa ndi DPP ai koma kut panali kusiyana ndithu ... ..
    I come in peace

    • @tariroJinya
      @tariroJinya Před 28 dny +3

      Palibe amene amamuda Dan lu

    • @GeorgePhiri-ub2of
      @GeorgePhiri-ub2of Před 27 dny

      answer Dan lufan amaimbila chipani choti anthu ambili kuchokwela pasi pa mitima yawo chipanicho amadadanacho mmodzi mwaiwo ndi ineyo basi khani yamala

  • @hannahsitimandau9107
    @hannahsitimandau9107 Před 28 dny +21

    Amamuchitira nsanje nyimbo zake ndi zobeba

  • @AeeshurQuenjie
    @AeeshurQuenjie Před 11 dny +1

    Dan lu u r still my fav artist osadandaula kut ukudedwa ndi anthu worry when God abandon you coz I biliv God loves you more

  • @ShamimuWilliame
    @ShamimuWilliame Před 12 dny +1

    My vote brother Dan lu
    Amamuda shifukwa shachilungamo amayimba saumboni dzoka dzoka love you Dan lu God bless you 🙏 amen

  • @emmanuelkennedy6389
    @emmanuelkennedy6389 Před 6 dny

    Khani nayi amakonda kuyimba nyimbo zoraura atasiya kuyimba nyimbo zaraurazi kubwerera chuni chake chakare zose zitha kubwerera chumake umatha kuyimba iweyo ndiwe number one osagonja ili ndi luso lomwe anakupasa mulungu pitiliza

  • @rainJCMw
    @rainJCMw Před 28 dny +12

    Umangomuda ndiwe ine simamuona vuto ayi

  • @MtolaMbalaso
    @MtolaMbalaso Před 26 dny +4

    Amadele,chifukwa chakuti,Dan luu, amata, OK tangowona nyimbo dzimene anathulusa dzachipanidzo winandan angamakwe, palibe kumalawi kuno km Dan,yemwewo

    • @MussaMbota
      @MussaMbota Před 25 dny

      Man dan luu ndimwana wabwino kwambili amadana nayeyo angokhala ansanje

  • @EuniseMasuku
    @EuniseMasuku Před 28 dny +5

    Dan lu tandiponyeleko kanyimbo ka sanje ndiye mandigwilane imandimvesa🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @FloridaOssy19
    @FloridaOssy19 Před 28 dny +5

    Ine ndimamukonda Dan lu ndip ndazamukondabe mpaka kale ❤❤❤

  • @Randy-er2xo
    @Randy-er2xo Před 28 dny +5

    Ndimfana wabho ndilibe naye bvuto

  • @HypeGallery-ur9xd
    @HypeGallery-ur9xd Před 28 dny +14

    Umamuda ndi inuyo ife timamukonda😊❤

    • @user-px9jd9co3v
      @user-px9jd9co3v Před 28 dny

      Sam Malvitha tikusika akapitiriza kuda Dan Lu

    • @GraciousBayard
      @GraciousBayard Před 28 dny

      Umboni ndi CZcams views ya nyimbo zake

    • @GraciousBayard
      @GraciousBayard Před 28 dny +1

      ​@@user-px9jd9co3vSam mavitha akukamba chilungamo ngati simusata music ndi bwino kukhala chete

  • @LailoguntherElick
    @LailoguntherElick Před 12 dny

    Amamuda kaya chifukwachan nanensosinziwa koma Dan lu ali fantastic 2 mach

  • @ishmaelbrighton9885
    @ishmaelbrighton9885 Před 28 dny +5

    Mumamuda ndiinu asamu mungatiwuze kuti amadedwa bwanji chifukwa ife sitimava athu akukamba zomunyoza mwangosowa zokamba akulu

    • @user-px9jd9co3v
      @user-px9jd9co3v Před 28 dny

      Sam Malvitha has a problem with Dan Lu

    • @user-ol1hf7ru1v
      @user-ol1hf7ru1v Před 28 dny

      Ndipo ine kuyamba Kumva zoti Dan amadedwa mmmm

    • @GraciousBayard
      @GraciousBayard Před 28 dny

      Kaoneni CZcams views ya nyimbo zake mupeza kuti Sam akukamba zoona muziitsata music paliponse not m'ma benning centre koma pa social media

  • @OnwellDzuwa
    @OnwellDzuwa Před 27 dny

    Vuto anaimba nyimbo yotukwana ya nyere anthu zinawabowa

  • @MaupoMhango
    @MaupoMhango Před 21 dnem

    Koma enafe Dan lu sitikumuda ayi. Komaso nyimbo zake zimatisangalasa koopya akamati kuyamba nyimbo zake nkumati Malawian music Dan lu❤❤❤❤❤❤

  • @CASSIMDinala-z7e
    @CASSIMDinala-z7e Před 28 dny +4

    Amatha nfanayu broskie

  • @DeodataKachapira
    @DeodataKachapira Před 13 dny

    Mnyamatuyu amaimba bwino asavutike ndi anthu all days are not Sundays. Komanso akati mpikisano ndi umenewo. Ajetuwo alibe nthawi, go ahead vuto achinyamata ambiri ngakhale aziimba zoimbidwazo samamva

  • @RICHARDMAGWIRA
    @RICHARDMAGWIRA Před 6 hodinami

    Iwe nawe Muthu sakondedwa ndi onse osangonena kt umamuda iwe bwanji

  • @MalitaKapesi
    @MalitaKapesi Před 20 dny

    Nkhani yakula ndinjilu imene imavuta kwa ena mwa amalawi fe

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy Před 28 dny +3

    Dan Lu amaswa koopsa athu amachita .naye nsanje ali ngt mfumu payekha ... nyimbo zake Za chipan anaswa

  • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
    @HappyAbyssinianCat-xt2bm Před 24 dny +1

    Dan luuuu amamuda chifukwa ndi munthu ozindkira kunena zoona dpp ndi boma labwno alibe zambiri ngat mcp chipan chamagazi manja nde Dan luuu ndi nyamata oganiza bho❤

  • @hanffyamizy2706
    @hanffyamizy2706 Před 28 dny +4

    Unayamba wapitako ku sho yake ngat

  • @KelvinChitwanga
    @KelvinChitwanga Před 27 dny +2

    Umamuda ndiweyo nde ukanati ndichifukwa chan munthu amamuda dan lu osat anthu! Wamva iwe

  • @TheresaKuluwemba
    @TheresaKuluwemba Před 21 dnem

    Inetu ndye I love him kwambiri enawo ndizawonso!

  • @sharifujoe7633
    @sharifujoe7633 Před 27 dny +1

    All most amakhala oyimba amnzizawo ife kwatu kuyamikira any one amapanga bwino pa music industry

  • @BunayaSalanje
    @BunayaSalanje Před 28 dny +2

    ine ndimakhonda kwambili ❤kupoza winaaliyese oyimba ku malawi ko 🇲🇼 achalume wachiyao wangalusa brother

  • @user-si7po9sd5i
    @user-si7po9sd5i Před 28 dny +2

    How about malemu Lucius Banda poti nayeso wakhala akuimba nyimbo zandale

  • @YusufDyton
    @YusufDyton Před 28 dny

    Ngani ndiyakuti dan lu amawada anthu chifukwa choti ndi muyawoo ukaunika ku malawi ndi zikho losalana mituthu kuli monga D20, Dan lu,Bandera,ndi ayaoo ena km zakhondedwa ndi anthu akumalawi ayi

  • @MikeAlabi-w2g
    @MikeAlabi-w2g Před 22 dny

    Iweyo Sam nddi amene umamuda Dan lu osati anthu enawo enafe timamukonda kwambiri ndiye siya uchitsilu wakowo

  • @DoresChisale
    @DoresChisale Před 28 dny +1

    Ine nde ndmakonda mpaka Pano ndpo nyimbo zake ndmazikondaso Maka Maka ija ya Tulani pasi udindo ija eeee anapha 😊😊

  • @falliotphiri688
    @falliotphiri688 Před 21 dnem

    Dan Lufani Ali ndi Magazi a Blue, ndipo palibe oyimba amene Ali wa DPP. Kuposa Dan. Choncho amene amadana naye ndi adaninso a DPP

  • @SamsonNyoma
    @SamsonNyoma Před 28 dny +2

    Amamuda coz ol yandareyo Imakhala hit

  • @muhammadisaid3968
    @muhammadisaid3968 Před 22 dny

    Komaso oyimba ambiri monga Billy , Banda bwanji samawaba , ndiye kuti anthuwo ndidzsilu

  • @user-qe2lz7mx7u
    @user-qe2lz7mx7u Před 27 dny

    Malawi amadana ndichilungamo komanso jealous chifukwa Dan lu amatha komanso ndiokongola samaoneka ngati mbuli za kumalawi

  • @VeronicaSekobi-is6dk
    @VeronicaSekobi-is6dk Před 28 dny +2

    Nice one 🎉❤

  • @stevietungama9775
    @stevietungama9775 Před 28 dny +2

    Amamudela Zina ameneyo bwanji nkasa samadedwa

  • @ChikuMega
    @ChikuMega Před 26 dny

    Samamuda dan lu umamuda ndiweyo

  • @IshumeilHaroon
    @IshumeilHaroon Před 26 dny +2

    Dan lu is the best

  • @tamandanimaliro7519
    @tamandanimaliro7519 Před 26 dny

    Umafotokoza zosaveka iwe ungosiya bola bakili tv

  • @SmartMasauli
    @SmartMasauli Před 14 dny

    Ife timafila Dan Lu🔥🔥🔥

  • @InnocentMaganga-gd6kn
    @InnocentMaganga-gd6kn Před 22 dny

    Anthu amamuda chfkw nd oimba amene anaimba za ndale ndkupindula nawo pamene oimba ena onse mwanenewo palibe chomwe anapindula kuposa Dan lu😢😢😂😂

  • @andrewchirwa2193
    @andrewchirwa2193 Před 26 dny

    Dan Lu ndiwoyimba wakulu so sakuyenela kuyamika andale aziyimba nyimbo zake woyimba akwathu ndale zikuwabwezelesambuyo🤷

  • @blessingkamanga1781
    @blessingkamanga1781 Před 28 dny +7

    I don't know that people hate Dan Lu myself I love him.

  • @KingDavedNkhata
    @KingDavedNkhata Před 18 dny

    Omudawo ali ndi zawo zomudera kkk

  • @user-pi2gf5tp2k
    @user-pi2gf5tp2k Před 22 dny

    Ilove danlufani and his music

  • @MillyKachepa
    @MillyKachepa Před 27 dny

    Anthu akamakuda akuona zabwno za iwe kumangoyamika osamazitengera amakhala akukubersa madalitso ako

  • @HappyBotha
    @HappyBotha Před 28 dny +1

    Dan luu ndimunyamata oyimba bwino,,,that's y amamuda

  • @AsimaAndiwochi
    @AsimaAndiwochi Před 27 dny +1

    Ine ndimamukonda dan ru

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 Před 12 dny

    Oimba ena sadedwa ndi anthu chifukwa alibe mbali ya chipan pomwe Dan lu akuwonesela kuti ndiwa dpp

  • @MosesPinto
    @MosesPinto Před 27 dny

    Anthu amachita mantha ndi dpp nde kuwawidwa ntima kwake mchifukwa amadana ndi dan lu

  • @AdamsIssa-p3j
    @AdamsIssa-p3j Před 27 dny

    Vuto ndiloti anali pa payroll ya boma pa chifukwa chongoimba nyimbo za dpp

  • @user-cn3bp1cr6r
    @user-cn3bp1cr6r Před 17 dny

    Mbambande 🎉

  • @billymhoni9527
    @billymhoni9527 Před 27 dny

    Zimene zikuooneseni kuti ambirife sitikuikonda DPP.

  • @WilliamLeo-w5q
    @WilliamLeo-w5q Před 19 dny

    Asiyeni amenewo ndi makape

  • @Pangolinimw
    @Pangolinimw Před 28 dny +3

    Imakhala jelasi anthuwo

  • @TmdCurtains
    @TmdCurtains Před 28 dny

    Munthu ochita bwino mwanthawi zonze amadedwa

  • @BenardMuhammad
    @BenardMuhammad Před 24 dny

    Penapaket osamachukira pa munthu osamanamiza anthu apa

  • @user-jm6xv5kb5n
    @user-jm6xv5kb5n Před 23 dny

    Ife timamukonda❤❤❤❤❤❤

  • @JoevsJohn-fg6wz
    @JoevsJohn-fg6wz Před 26 dny

    Athu amaziwa Kut iweyo umamuda Dan Lu ndikuziwa munamufananidza ndi Dala wanu uja jetu iwe ndikaphe

  • @AgnesMwale
    @AgnesMwale Před 24 dny

    Mungoti chili chose chili ndi season... Nanga rashly wakhala zii apa???

  • @user-si2dx2ww2y
    @user-si2dx2ww2y Před 28 dny

    Tachoka naye patali Koma zomudazo mukuziwa ndinu kapena anakuuzani yekha

  • @OsmanRatbu
    @OsmanRatbu Před 23 dny

    Yathu ija amalawi munthu zikamamuyendera sitisangarara imakura nd sanje dan lu amatha man ndpo kwambliiiso

  • @nkosikhonasiphiwemdlalose227

    Palibe amamuda alomwe mwapanga bwanji

  • @GeraldPeter-m6y
    @GeraldPeter-m6y Před 28 dny

    Tidalek kumufila coz adayamba bho vuto zipani

  • @user-rz4ks4ie5h
    @user-rz4ks4ie5h Před 20 dny

    Anamuda chifukwa mumati ndi wasatanic kumuonongera mbili

  • @PatrickJemus-x7s
    @PatrickJemus-x7s Před 27 dny

    Anthu amama nd jars chabe ban lu amayimba bho komaso amaziwa kumvara bwino

  • @MangulenjeTwangu
    @MangulenjeTwangu Před 24 dny

    Kumuda munthu kumakhala kumpasa mwai

  • @yotamumahomed1313
    @yotamumahomed1313 Před 20 dny

    Chomwe ndimadziwa ndichot moyo was aliyense uli mmaja mwa mulungu bas that's all

  • @AlexBanda-p1k
    @AlexBanda-p1k Před 21 dnem

    Ine danieli Joe kuno kwangabu Dani lu amafuna mtendele ngati mene adadi Ali wamtendele

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete Před 21 dnem

    Ineyo ndimamukonda dan lu ❤❤❤ APM uja osazamuphwekesa

  • @JacksonNamalumbe
    @JacksonNamalumbe Před 26 dny

    Alipo wakutuma kuti uziyakhula zopusazi ? Ife ukuziwa mene timakondela Dan Lu ( lozani zanu ife tiwone)❤

  • @shukurajaaffarie-cr2nm

    Iweyo samu ndiamene ulindi vuto

  • @AquimodinisbilioteBiliote

    Dan lu ndi big,ochita zabwino amachuluka ndi adani even jesu christu ankachita bwino koma yuda adangulisa kwa adani mpaka kuchosa moyo wake.

  • @Alexkalonga-t9s
    @Alexkalonga-t9s Před 28 dny +3

    Iyi wapala mavita

  • @user-kl1vk1gx2q
    @user-kl1vk1gx2q Před 18 dny

    Ngati dziko la malawi emwe anayimba nyimbo zabwi nzachipani ndi Dan lu bs nde tingamudele nji ife ma citizens iwe umamuda siife ayi

  • @MatridaChikaphonya
    @MatridaChikaphonya Před 22 dny

    Mtengo womwe ulindidzipatso ndumene umagendedwa don't worry Dan luu

  • @GraceMaida
    @GraceMaida Před 27 dny

    Done ndimfana oti amatha ndiye timuda bwanji iweyo ndiye usamamuwonela kukondwa koma Done ndimbambande moooo fire Done we love you so much ❤❤❤❤❤❤

  • @FRANKMUSSA-u8h
    @FRANKMUSSA-u8h Před 27 dny

    Umamuda ndi iweo osat ife

  • @MussaMalon
    @MussaMalon Před 27 dny

    Kwayineyo dan lu ndi super power osamutuluka.

  • @DestinyKasiya-j5p
    @DestinyKasiya-j5p Před 25 dny

    Ndekuti maimbidwe amasiyanaka

  • @IssaLazack-ij1gf
    @IssaLazack-ij1gf Před 18 dny

    Amaphangila jerazi amayimba momveka bwino Dani yoo❤❤❤

  • @KennedyMitochi-nz8fp
    @KennedyMitochi-nz8fp Před 24 dny

    Dan lu amadedwa chifukwa amaima pachilungamo pajatu chilungamo chimawawa Dan lu kumenya kugwesa

  • @danielChisal
    @danielChisal Před 26 dny

    Amwene Sam mukutimasula maso

  • @user-ju9lg5pg5g
    @user-ju9lg5pg5g Před 21 dnem

    Guys Moyo ndichoncho munthu amankhala ndi anthu omukonda komaso odana naye sizingantheke kukondedwa ndi anthu onse olo utankhala wabwino

  • @user-pf5vj4em4f
    @user-pf5vj4em4f Před 28 dny

    Ine ndimamukonda Dan ngati mumadana naye kwanuko mwina

  • @sylvesterkapusa8781
    @sylvesterkapusa8781 Před 27 dny

    Amakonda mbali imodzi ngati chipani Cha DPP

  • @DIMZYRECORDS
    @DIMZYRECORDS Před 28 dny +1

    Amavita boza sanachite kuwawoda achina psquare

  • @JusticeFriday-q1j
    @JusticeFriday-q1j Před 28 dny +1

    Muthu sakondedwaandi athu ose kom kwaenafe tiribe naye murandu amatisangarasq kuno

  • @AsimaAndiwochi
    @AsimaAndiwochi Před 27 dny

    Inu ruziyasi banda timamuda dan ru sitimamuda musatinamize ine

  • @VultureVoice95
    @VultureVoice95 Před 26 dny

    Sanje chabe dan lu ndi mbambande ka aaaah!!

  • @Chiwaya-v6h
    @Chiwaya-v6h Před 18 dny

    lne ndimakonda Dan lu ndip ndazamukondabe mpaka khale😊😊😊

  • @EusébioLucianoGaiondo

    Muli ndibodza bg dan lu ndi bg

  • @shukurajaaffarie-cr2nm

    Umamuda ndi iweyo osati ifeyo iwe sudziwa kut Dan ndi mu yao ? Ndie sundiwaso kut mchewa ndiwa sankho?

  • @CuthbertMughogho-u1b
    @CuthbertMughogho-u1b Před 26 dny

    Uja anaimba yoti tiyende pamodzi ndi mtima umodzi timayikonda mpaka lero. Kuna koipa kuimba nyimbo ya Peter panthawi yoti dzithu zikubvuta iye kumanjoya. Iyeyo amasapota Muthu amene amaszunza anthu ndipo anthu amamuda Peter amapanga mademo kusamfuna Peter munthalika.

  • @owenmaseya6936
    @owenmaseya6936 Před 28 dny

    Ndinu zitsiru kwambiri zifukwazo nde mwanena?

  • @lacksonmanyewu3615
    @lacksonmanyewu3615 Před 27 dny

    Zoti Dan lu anthu amamuda ndi bodza lankunkhunidza

  • @user-ww9rj2wx8d
    @user-ww9rj2wx8d Před 28 dny +2

    Vuto muli ndi msanje mmmmm

  • @DavieLosani
    @DavieLosani Před 27 dny

    Iweyo udzinvela kwambili nyimbo ya Dan ,msanje.

  • @Jermah51kennias
    @Jermah51kennias Před 25 dny

    Umamuda wekha ife ayi

  • @blessingsnyalo-rp9ko
    @blessingsnyalo-rp9ko Před 28 dny

    Akulu inu kumuda kwanu Dan lu sitonse amene timamuda ayi