Komentáře •

  • @eunicesaiti
    @eunicesaiti Před 5 dny +3

    Amen, God is still sitting on the throne 🙏

  • @spargomw
    @spargomw Před 5 dny +2

    Glory be to God Almighty. Chakwera akumatenga Tembelero nd zozizira.

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b Před 5 dny +2

    Kusowa zochita eti? Kukamanga mtumiki wamulungu iye mmayesa amanena chilungamo shame Malawi government

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y Před 5 dny +2

    Chakwela you mast go

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 Před 5 dny +2

    Chakwera komwe wuliko zeru wulibe bwanji wukuwazuza anthu pomwe wukuziwa Kuti ndiwe wakupha

  • @StellaChizombo
    @StellaChizombo Před 4 dny

    Amen 🙏

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon Před 5 dny +2

    Aaaaaaa mukunamatu inu mukati sintchito yake ndi azibusa angati akambapo pa zineneza chitikazija mutakhaka pheee zikanakhala kuti zachitika kwa achibale anu mukanamva bwanji, alipo yemwe suzinamuwawe zimenezija osamayankhula musefukira

  • @ChimmsRichardOrden
    @ChimmsRichardOrden Před 5 dny

    Our God is real, He never fails. And He is not a man.

  • @AbitiFinala
    @AbitiFinala Před 5 dny +1

    Thank you God

  • @user-db3mh9wr9v
    @user-db3mh9wr9v Před 4 dny

    Mwayambanso kumanga azibusa mukuzichosera mavoti nokha mwina simukuziwa

  • @user-cp4qt9hs8w
    @user-cp4qt9hs8w Před 5 dny

    Km chakwera zot umkachita kufuna kulila asakulowa m,boma waiwala mwai mchilima kukukozela tsogolo apa uli fiti mchewa iwe chadzunda oonela mkamwa mpake anthu angokuba

  • @user-dn3gp6yi4y
    @user-dn3gp6yi4y Před 5 dny

    Not za bodza koma zenizeni anthu atopa ndi chilungamo ndi chomwe anthu amafuna

  • @RhodneyBwa3
    @RhodneyBwa3 Před 5 dny

    Chakwera ndi Nooka muwudzu.

  • @sweeneykamwendo6251
    @sweeneykamwendo6251 Před 5 dny +1

    Boma likuona nyekhweee

  • @KennethMpininga-iz2ie
    @KennethMpininga-iz2ie Před 5 dny +1

    Umuuze chakwerarayo chaka chamawa akuluza

  • @AbuOsman-ts6ef
    @AbuOsman-ts6ef Před 5 dny

    Amen

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of Před 5 dny

    Olakhula zopanda umboni chonde amangidwe osawasiya ai please dziko limayendela malamulo ndipo lamulolo ligwile tchito azibusa ena ndizisilu

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 Před 5 dny +1

    Koma MCP NYASI ZACHIPANI

  • @JamayakoJamayako-rv2he

    Praise God

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg Před 4 dny

    M'busa uwanenedza kwamulungu awakanthe

  • @RomeoPrecious
    @RomeoPrecious Před 5 dny

    Ndifuse ma comment athuwa amawafikq ngati amawafikw muwauze ose akulamulilq Malawi
    Kuti Malawi siwamake

  • @user-eh1mg3ww6d
    @user-eh1mg3ww6d Před 5 dny

    Muyezo omwe ukumuyeza m,zako iweso uzatezedwa omweo vindikilani chilungamo koma mulungu alipo akusiyani poyela tsiku ndi li modzi

  • @AndrewMagombo
    @AndrewMagombo Před 4 dny

    Wapenga nalo boma chakwera

  • @Musa1828-l5d
    @Musa1828-l5d Před 5 dny +1

    Chakwera achoke

  • @Alliechamolie
    @Alliechamolie Před 5 dny +1

    Achoke chakwela

  • @ChriKezi
    @ChriKezi Před 5 dny

    kkkkk koma boma

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika6784 Před 5 dny

    Zipwisi zawo achina gwenembe

  • @user-sk3ld2ss7s
    @user-sk3ld2ss7s Před 5 dny

    Atsogoleri adzipembedzo ( azibusa), muzipewa kulowelera ndale, simunalumbire kupanga zandale...

    • @user-uc1pd1tc2x
      @user-uc1pd1tc2x Před 4 dny

      Chakwera mesa naye Ndi m'busa Kodi, ukufuna unene chani iweyo?

    • @user-uc1pd1tc2x
      @user-uc1pd1tc2x Před 4 dny

      Uzisiyanitsa mawu oti Ndale ndi Chilungamo then uzalinvesetsa dziko mmene limakhalira

    • @viennasamuel2976
      @viennasamuel2976 Před 3 dny

      Ndiponso

    • @user-uc1pd1tc2x
      @user-uc1pd1tc2x Před 3 dny

      @@viennasamuel2976 Chakwera Kodi sibusa?? Mukamanena muziganiza guys Chakwera wanuyo bwanji ankayamba zandale munaleka kumuuza??

  • @ZungeniBanet
    @ZungeniBanet Před 5 dny

    Kkk Malawi so pano

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon Před 5 dny

    CHAKWERA ndi nduna zake ndi manyi enienk

  • @jonathanmbewe4246
    @jonathanmbewe4246 Před 5 dny

    Mulungu amakonda aliyense

  • @AaronMautanga
    @AaronMautanga Před 4 dny

    Koma agalu inu mukapangira campaign kuti

  • @CassimMbalaka
    @CassimMbalaka Před 5 dny

    Uremu wanu nose akhoti

  • @SteveriaZimba-qs1id
    @SteveriaZimba-qs1id Před 5 dny

    Anachita bwino kumumanga iye sintchito yake yonena zadziko iye ntchito yake ndikupereka uthenga wachipulumuso kundare amakatiko

    • @YankhoGuza
      @YankhoGuza Před 5 dny

      Nde mukumuikira malire kuti sim'malawi or ngakhale Ali m'busa?
      Nanga bwanji azibusa amatenga nawo gawo kuvota ngati zochitika za mdziko siziwakhudza?

    • @inessmsiyambiri8517
      @inessmsiyambiri8517 Před 5 dny

      Nde ndiwe omvetsa chisoni sudziwa kuti munthu amayenera kukula muudlzimu ndi nu umunthu omwe

  • @EagerChicken-qj6xu
    @EagerChicken-qj6xu Před 5 dny

    Mpaka kumanga m'busa? Ndinu anthu otembeleledwa zedi.

  • @YasinMusa-ym8lp
    @YasinMusa-ym8lp Před 5 dny

    Chakwera machende ake fokof

  • @user-pt8wb4vw6r
    @user-pt8wb4vw6r Před 5 dny

    Azibusa nanuso mmalo mofalisa uthenga nanuso mwalowa mchisawawa zaziiii

    • @Zelinakhisswell
      @Zelinakhisswell Před 5 dny

      Iwoso ndi anthu 😅😅

    • @inessmsiyambiri8517
      @inessmsiyambiri8517 Před 5 dny

      Sukudziwa chomwe ukulemba

    • @user-nv3rf7bl7r
      @user-nv3rf7bl7r Před 5 dny

      Ndipo that's y ku church kwawo kuja anayambisa ndewu zeru alibe abusawa mumalo mulalikila kulipemphelela ziko lathu iwo akupasula

    • @Zelinakhisswell
      @Zelinakhisswell Před 5 dny

      @@user-nv3rf7bl7r mmafuna azikubakirani zokupha mkumachitirana nkhaza? Iwoso ndi anthu Ali ndi ma feelings amava kupweteka poti ndi m'busa nde asalankhure tilitu mu democracy aliyese alindi ufulu kaya ndi m'busa, sheikh , activist, politician everyone has got freedom of expression

    • @user-nv3rf7bl7r
      @user-nv3rf7bl7r Před 4 dny

      @@Zelinakhisswell iwe usandichimwise ndinapha ambuyako kupusa bwanji osaweluza amako amawuluka