Video není dostupné.
Omlouváme se.

Umboni wa a Twaibu pa 8 July 2023 ku Blantyre - "Zinthu zomwe satana samafuna anthu adziwe"

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 8. 07. 2023
  • Mverani zinthu zodabwitsa ndi zobisika zomwe satana samafuna anthu atadziwa. Nthawi yatsala pang'ono. Tiyeni tikonzekere kubwera kwa Ambuye wathu Yesu Khristu mu mkwatulo womwe watsala pang'ono kuchitika.

Komentáře • 65

  • @tintophiri2312
    @tintophiri2312 Před 8 měsíci +1

    God of Mercy save my life.😭😭 Thank you for sending salvation for my life tthrough this great man of God. 🇿🇲

  • @user-vl5go3nr2v
    @user-vl5go3nr2v Před rokem +3

    Yehova awadalise mr twaibu nthawi zonse...koma otumizanu chonde musaiwale kutitumizilaso zinthu tenizo tiziwekoso nafe

  • @ArnoldKamanga-wm7gc
    @ArnoldKamanga-wm7gc Před měsícem

    Mulungu akudalitseni brother Twaibu

  • @user-wb5vp7km4z
    @user-wb5vp7km4z Před 9 měsíci

    Amen amen abuye akupatseni mavumbulutso ochuluka mwandichotsa Pena mwandika Pena kumwaba kulemekezeke kwambili 🙏🙏🙏👏

  • @mikebernabechimundi3472
    @mikebernabechimundi3472 Před rokem +4

    Amen Christ,,following all the way from Mozambique,Atamandike mu nthawi zonse

  • @EmilyManase-fz6cv
    @EmilyManase-fz6cv Před rokem

    Amen, Mulungu ndi okoma mtima ndi anthu ake Ndipo amawawululira zi nsisi zake kudzera mwa atumiki ake. Mulungu akudalitseni mtumiki.

  • @husseinmoffatt
    @husseinmoffatt Před rokem +3

    Zoona Mr twaibu

  • @PetroKachingwe-jf7dh
    @PetroKachingwe-jf7dh Před rokem +1

    Amen mtumiki
    Tikudikira zithu ten
    Mutidziwitse please

  • @RyleChole
    @RyleChole Před 20 dny

    Satana amalamulira dziko lonse lapansi koma Mulungu amalamulira oyera mtima onse Masalimo 23 amati odala omwe Yehova akhala m'busa wao, amatero malemba

  • @user-if1kd3kh4d
    @user-if1kd3kh4d Před 6 měsíci

    Amen

  • @KeffasSimion
    @KeffasSimion Před 9 měsíci

    Amen ndikuvetsera mwachidwii

  • @tonyinocent1770
    @tonyinocent1770 Před 10 měsíci +1

    Blessings

  • @user-cc4dz5rw3i
    @user-cc4dz5rw3i Před 9 měsíci

    amen amen

  • @user-mo3rz4zp8e
    @user-mo3rz4zp8e Před 7 měsíci

    Thank you for exposing the devil, may God protect you

  • @user-cv1ob9uo1t
    @user-cv1ob9uo1t Před 11 měsíci

    Ndife amwayi tingompempha mulungu apitilize kukutetezani mtumiki wa mulungu Mr twibu

  • @MaryRasmussen-mr4zo
    @MaryRasmussen-mr4zo Před 10 měsíci

    Amen
    May God help us all Sir
    God nless you for what your doing thank you for the truth
    Amen

  • @fapsonbanda3453
    @fapsonbanda3453 Před 11 měsíci +1

    Amen God help us in Jesus name 🙏🙏🙏

  • @samuelnyirongo8965
    @samuelnyirongo8965 Před rokem +1

    KEPT UP MR TWAAIB

  • @DanielMbuzu-sf4ey
    @DanielMbuzu-sf4ey Před rokem +2

    Atsogoleri uthenga wanu umandizindikilitsa za ntchito ya ikulu kwambili yomwe okhulupilira ambuye Ali nayo pa dziko lapansi lino

  • @KeffasSimion
    @KeffasSimion Před 9 měsíci

    Pepani ndava mokwana ndithu kom 10 zija mwina ngati ndikotheka ndiziveko kuti ndiyendere limodzi nanu pepani thandizani atsogoleri ndine mmodzi wotayika

  • @richardchirwa7030
    @richardchirwa7030 Před 9 měsíci

    Please continue assisting and teaching us of Gods groly

  • @jamesphiri9930
    @jamesphiri9930 Před 7 měsíci

    Go deeper man of God

  • @user-nx8gy8lq4q
    @user-nx8gy8lq4q Před rokem +2

    Palibe chobisika pamaso pa mulungu ambuye adzikutsogolelan thawi zonse atsogoleri kuti tiphunzile zambili

  • @alexjeremanuel2541
    @alexjeremanuel2541 Před rokem

    Ulaliki wanu Mr Twaibu siulaliki okha ai komanso ndi chiphunzitso, chenjezo, chidziwitso, ulangizo ndi chitsitsimutso

  • @user-bh2uk7ls5e
    @user-bh2uk7ls5e Před 8 měsíci

    Hossana ! Hossana! To God Almighty. I would like to beg the WhatsApps link for God teaching through Mr Twaibu Ali, if any.

  • @LeonardKantondo-fu9tf
    @LeonardKantondo-fu9tf Před 11 měsíci

    Amen
    May God help us and protect Mr Twaibu in Jesus Christ

  • @alicephiri3706
    @alicephiri3706 Před rokem

    Amen amen following Mr Twaibu

  • @user-xg9lq3pj8h
    @user-xg9lq3pj8h Před 9 měsíci

    Ambuye akudalitseni

  • @alexchipanda1669
    @alexchipanda1669 Před 8 měsíci

    We love u Mr twaibu mulungu akudaliseni

  • @user-cb8sp9ip3r
    @user-cb8sp9ip3r Před rokem

    Amen powerful uthenga

  • @papelariareis.e.
    @papelariareis.e. Před rokem +1

    This guy he knows more about devils future plans

  • @mauricetayali8041
    @mauricetayali8041 Před rokem

    Ambuye mulungu akusungeni a twaibu

  • @RyleChole
    @RyleChole Před 20 dny

    Palibe chipembezo chili mmanja mwa Mulungu

  • @user-nz7lj3qk4g
    @user-nz7lj3qk4g Před rokem

    Amen ndasunthika nfimawu anu

  • @user-ko8qd9wh6f
    @user-ko8qd9wh6f Před 9 měsíci

    Amen and Amen

  • @husseinmoffatt
    @husseinmoffatt Před rokem +1

    Zoonadi Mr

  • @jeffmalizan9878
    @jeffmalizan9878 Před rokem +1

    Kodi bwanji nthawi zambiri mmakonda kuduliza nkhani mukatero simudzanenaso zathera pomwepa ,tilindi ma lonjezo ambiri ochokera kutinihani Tanu tomwe tumangothera panjira mkudzati mufzapitilizabe nthawi ina yake koma mpaka lero kuliziii

  • @jeffmalizan9878
    @jeffmalizan9878 Před rokem +1

    Mudzaipituliza liti nanga

  • @frankkaipa8925
    @frankkaipa8925 Před rokem +1

    Ameeen

  • @nyanguoipa6996
    @nyanguoipa6996 Před rokem +1

    Amen 🙏

  • @user-cv1ob9uo1t
    @user-cv1ob9uo1t Před 11 měsíci

    Mwayi umenewu maiko ena alibe woti Ave zisisi za satana koma ife lero ndi Feb

  • @yolandamasaiti-mf8gu
    @yolandamasaiti-mf8gu Před rokem +1

    Pitilizani kuti dziwitsa ambuye azikudalitsani..

  • @ChikondiKaliza
    @ChikondiKaliza Před rokem +1

    Kufutukula zobisika munthu wamulungu

  • @ClementDkamwendo
    @ClementDkamwendo Před 11 měsíci

    Amen🙏🙏🙏

  • @user-xx7xj8br3x
    @user-xx7xj8br3x Před rokem

    Thanks mr

  • @preciousmkute4041
    @preciousmkute4041 Před rokem

    Following

  • @user-mc6tz2yb8s
    @user-mc6tz2yb8s Před rokem

    Kp going Mr Twaibu but with the truth

  • @KeffasSimion
    @KeffasSimion Před 9 měsíci

    Koma zasitha moyo wanga ngati pari njila ina chonde tapangani motero

  • @alexjeremanuel2541
    @alexjeremanuel2541 Před rokem

    Monga mwa funso lanu Mr Twaibu kuti : kodi mungasiye chuma chanu ndikutumikira Mulungu ?? Yankho ndikukhulupilira kuti palibe munthu angatero

  • @agnes7675
    @agnes7675 Před 6 měsíci

    AMEN

  • @yusufsadic2930
    @yusufsadic2930 Před rokem +1

    Nkhan zopand tsogl
    Komanso zabodz zokh zokha

  • @user-bf1px4nv8d
    @user-bf1px4nv8d Před 10 měsíci

    The devil is always liar

  • @AfunikaTembo-ty1qy
    @AfunikaTembo-ty1qy Před rokem

    CZcams

  • @user-ro1yw7op1c
    @user-ro1yw7op1c Před 7 měsíci

    Ndisaname mtumiku off ndikhala ndikusatira maumboni anu kuyambira kale ndimakusatani bwino bwino mukufotokoza kwanu in brief munafotokokoza kut before you was a Muslim mpaka munafika pa udindo wa mufut munafotokozanso za makorona angapo oophsya ku chipembezo chomwe munali mzaka zapitazi mukufotokoza kwanu munaphatikizapo za korona wa asilamu mkati kati mommu ndikumamva mukumavomerezanso kut machitidwe ena asilam alibwino kusiyana ndi akhirisitu eg kupempera akachoka kapena akachita chimbudzi malingana ndi ziwanda Zina zonse zimakonda fungo lakuchimbudzi pepani mungafotokozenso paichi kuopa kut ndingataike

  • @user-it1kn8ux9g
    @user-it1kn8ux9g Před 9 měsíci

    Amen

  • @user-cv1ob9uo1t
    @user-cv1ob9uo1t Před 11 měsíci

    Mwayi umenewu maiko ena alibe woti Ave zisisi za satana koma ife lero ndi Feb

  • @user-lf5ou9lc4e
    @user-lf5ou9lc4e Před 10 měsíci

    Amen

  • @Samyohane
    @Samyohane Před rokem +2

    Amen

  • @thirdgenerationmovies710

    Amen

  • @muyabasamson
    @muyabasamson Před rokem

    Amen

  • @user-pm2bo8vb2z
    @user-pm2bo8vb2z Před rokem

    Amen

  • @leonwisikesmwkbyowner

    Amen

  • @user-ds9sx4rt4j
    @user-ds9sx4rt4j Před rokem

    Amen