USAUVER S04E09 - TITAPE
Vložit
- čas přidán 6. 09. 2024
- Welcome To My Channel..
Watch My Other Videos 👇
• Piksy Malawi Music Videos
#Langwani #Piksy #Asauver #Sangie #Music #Malawi #Comedy #Africa #Afro #Trending #Usova #hyphen
Subscribe To My Channel 👇
/ piksymalawi
Watch My Play Usauver 👇👇🔥
• Usauver Episodes
PLEASE NOTE: Unauthorized upload of this video unto any CZcams channel is prohibited. (C) 2022. #CCNB. Pastor Ntebede is back at it
Sangie mwatchenatu😂😂💙
Mpaka kutapira Cha khumi koma abusa awa achinyengo in sangies voice
Koma sangie Mani anakonza I Love you keep up mama I fell like ndizapange nawo usauver one dau
Tingopanga za ndalamazo zitayeni zinazo LoL
Kkkkkkkk mpaka kutapa chachikhumi
😂😂😂😂 abusa ayiwona ya yobu
i love this
Kkkkk munakumana kuti ndi abusa angozo 🤣🤣🤣🤣
😂😂😂😂 Koma M, busa uyuyu eeee osalongosoka
A piksy osamasekesa bwanji NGAT mandota or izek
😂😂😂😂😀😀 adakubela ndalama zako ngozo anthu oipa osawapatsa ngongole ai kkkkkk
Kkkkkk koma ndakomoka ngozo kudabwa akuti iiiiiiiiiiii
Watching from Finland with friends please add subtitles am tired of interpreting 😂
Am watching from Russia😂
Akuti iiiiiih, cholinga m'busa asapitirize kukamba za mzimayi😂🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Kuchap kwa akaz amasiku anowa 😂😂😂😂
Timakunyadilani kwambili piksy mumayintha
😂😂😂😂😂😂 Koma abusa inuyo mmmmmm
Kathela panjira😂i wish patie akanabwera after kunvesela nawo
Sugar kumuika mundiwo😋😋😂😂😂
Anamugwilizilitsa 🍷 zachabe 😂 😂 😂 😂
Advance ya chakhumi 😂😂😂😂😂koma abusa ayi zikomo😂😂
Kkkkk titape chakhumi basi
kutapa advance ya tithe 😂😂😂
genedai😂😂😂chakhumi chamwez wamawa
koma ndaseka 😀😀 big up team
Koma ndi abusa di😂😂😂
koma Family iyiyi palibeso
Kkkkkk abusa awa achenjeretsa, ngozo uthesa zako kkkk
😂😂😂😂😂😂 akuti unathana nacho bwanji chimenechija 😂😂😂
eeeeh koma abusa awawa nde kaya hahaha😂😂😂😂
Ngozo sakanapereka ndalama imeneyo popanda kuwuzidwa zoti anamuona kumowa ndichimkazi chazonse mommo.
Hahaha advance ya chakhumi🤣🤣
I like it guys, mumakwana honestly.
Amend sapatoitu ndavula ndine
To be honest you guys ur more mumandimvesa kukoma heavy keep the fire burning 🥰🥰🥰💯💯❣✌
🤣🤣🤣 koma abusa kkkkkkk
Hahahahahaha la 40
😂😂😂😂pre chakhumi
Advance ya Chakhumi
Kkkkkk komatu akanapanda kukuuzan kuti anakuonan ndalama sikanatuluka
Ndafwa😂😂😂😂😂😂
Atape basi chakhumi
Habusaaaa
Ine ndikupanga mafizo kuseriku
Nde mwati za chinzimayi zinayenda bwanji?
kkkkkkkk you guys mumatha honestly
M'busa wanji otapa chakhumi?? Akut "chimene chija wathana nacho bwanji!!!
Achakulugwa
Mumakwana
Titape cha khumi kkkkkkkkkkkkkk
I can't wait for next episode 😹😹#usauver🗣
Tingodikira muwagwire
😂😂
Good comedy guys
I suggest u should make them a little longer than this ..but hey I enjoy every episode keep it up
Cha khumi in advance kkk
Kutapa chakhumi? Koma ya!!
Kumwamba kumafunila
Kkkkkkkkk Kali bho koma kafupka Ngozo waika mavuto busa ameyo akudela chikwa ukmkna kupleka chakhumi azulula za ukomwakumna
Hahaha my ribs....... chakhumi amatapa?
Titape
😂😂😂😂😂😂
😂😂😂
M'bale umamasukatu
❤️Guys
Habusaaaaaa
😂😂😂