Zomwe Zayankhulidwa Za Imfa Ya Saulos Chilima Ku Nsokhano Wa UTM - MVERANI

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 9. 09. 2024
  • Pamene ma report sanapezekebe pa infa ya Vice President wa Malawi Saulos Chilima, Chipani chake UTM chayankhula kuti Tisaope tsogoleli wadziko alipaniyu

Komentáře • 18

  • @paulnyondo7572
    @paulnyondo7572 Před 24 dny

    Uyu ndiye mamuna kukamba chilungamo osaopa yingalure.chakwera mfiti

  • @webstermbewe8395
    @webstermbewe8395 Před 28 dny

    We have been waiting for this continue to give us the best

  • @scoltenroma6240
    @scoltenroma6240 Před 26 dny

    RIP SKC😭😭

  • @elizaBernado
    @elizaBernado Před 26 dny

    achulukadi mafunso osowa mayankho. ngati bodza ndihu

  • @user-io2uw2me9f
    @user-io2uw2me9f Před 26 dny

    Ndipo pokhapo chakwera mmmm anaonetseratu kut ndiwakupha

  • @user-pt8wb4vw6r
    @user-pt8wb4vw6r Před 28 dny +2

    Mfundo mulibe nkhani yikhale yimozi mozi

    • @amoschisisi2070
      @amoschisisi2070 Před 28 dny

      Galu iwe

    • @MaryNyirenda-nq3mh
      @MaryNyirenda-nq3mh Před 28 dny

      Timaziwa azibale ake achakwera ndinu okodwa ndi imfa yachilima komanso anthu 9 aja nde ife musatinyase tisiyen tizilira koma muziwa kut mubweza ngongoli yimeneyi kuli mulungu musawone ngat amalawife tagona dikilan zayambikatu mkwiya zenizen muwuwona nkwiyo wamulungu ndezolesana kulira zithera zinthe

    • @Eric-gb9ms
      @Eric-gb9ms Před 26 dny

      Chifukwa choti anafayo si brother wako wakupha iwe

  • @user-io2uw2me9f
    @user-io2uw2me9f Před 26 dny

    Ndipo ndimkangomva kut mcp ndiyakupha koma ndaziona

  • @MiracleMalichi
    @MiracleMalichi Před 28 dny

    Zooona mafunso osowa mayankho adaferanji achilima😭😭😭😭😭

  • @user-tg3ju1mw9t
    @user-tg3ju1mw9t Před 27 dny

    Ndipo zosamvesetseka ndipo zosaiwalika mmmmmmm koma Malawi hummmm

  • @zorapandor7486
    @zorapandor7486 Před 28 dny

    💪💪💪

  • @EdwardMathuwa
    @EdwardMathuwa Před 28 dny +2

    Chakwela mbuzi ya munthu chitsiru okupha

  • @ErickTym-u2m
    @ErickTym-u2m Před 28 dny +1

    Chalakwe chikangawa sitikumufuna watikwana achoke

  • @user-pt8wb4vw6r
    @user-pt8wb4vw6r Před 28 dny +1

    Zisilu inu mwagulisa chipani kwa adani