Velikost videa: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Zobrazit ovladače přehrávání
Automatické přehrávání
Přehrát
😂 😂 😂 Akhoza kusanduka mbatatesi eti
Ndikamuonetsabe kwa ankolo 🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Keep it up mbambande
Homie apa ndiye mwaitha🤣🤣🤣🤣 ati pulofeti makhamani 😂😂😂 so funny
Hahahahaha mulamu uyuyu wealthy kumuponda zedo.... Kunte you killed it again😂😂😂😂😂😂
Kkkkkkk kma kunte sazatheka
😂😂😂🤣Ichi amwene
Aaah koma kwa Prophet Makhamani kumapezeka zinthu😂😅😂😂...eeish Fiyonse ameneo anapeza chimamuna amwene😂😅😂😂
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣koma yaaaa
Asogoleli mkwati uyu ayi🤣🤣
Akuti kudzasolora tape meja kkkkķkkkk
Auze neba kkkkkkk😂😂😂😂😂😂😂
Aaah koma Kunte pilizi😂😂😂😂😂
Kunte usiye kumwa mowa😂😂
Nswala akaike mkabati😂😂😂
The best of what I have seen so far
Kkkkkkkk nnadziwa zoti siitha bhoo mbobawa ndi ama scandal kkk umatha big up
Koma kunte kususuka 😂😂
Nice comedy
Koma alendu ake alibe ulendu kuyamba kufika pankhoma koyamba paka. Kumasusa chocho zamanyazi kwambiri
Chapati chija andipatsabe 😅😅😅😆
Osamakonda kuiwala zinthu amwene hahahahah
Komano ndisaname muzipangako zoti ziligwirizane ndi dzikoli osati zopusa mwapangazi zimenezi kulibe usinthe kt ukhare ndiwokuwolnerera ambili malangizoanga ndamenewo zikomo
Ase Kunte iwe ndi Machine ase 🔥🔥🔥🔥
Kunte amathaa,n I like d guy more
kunte is the guy who would miss his doctor session cause he is sick😂🤣
🤣🤣🤣🤣🤣
@@kennedyKuntKunteKomedy yu are my malawian favourite
🤣🤣🤣🤣🤣🤣
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣 ati chapati chija andipasabe
😂😂😂😂😂😂 Komatu kunte azakuphatu mkulu uyoyo
😂 😂 😂 😂 😂 Koma iwe Kunte eeeish undipha ndithu
Kunte adhaa kumasuka kwabwanji kumeneko 😂😂😂😂😂
Kunte your Drama is one of the best in malawi bro keep it up and we will keep supporting you watching in SA umatha aise
Kunte udzathela mmanja mwa anthu aise 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
🤣🤣🤣🤣Wise Man wa Prophet Makhamani wasezedwa🤣🤣🤣
Hahahahaha komatu uzikhalika kusekelerako for me Lol
Hahaha iweyo ndidolo ase kungokuona before usanawonele umayamba kuseka wekha
big aseh😂😂😂😂 moto wambiri ankolo
Kunte inuyo mumatha ❤😂
Komatu bae, ndaiwalatu baibulo ndi chipewa kkkkk
Koma kunte iweo anakonza njala yonse kuthera kuwonekera
Kunte aaaaah iweyo ndi dolo eeeeh
Kkkkkk kamwini wamisara chapate njumbo
Komatu kunte, Akuti swala ameneyo
Ati ndikamuonetsanso Kwa ankolo koma azimayi🤣
I enjoyed watching this comedy...ur the best kunte
Uyu azakumanenazo ndee azantibure🤣🤣
Nice content
Man unuyo palibe winaso mumatha💪👊
I like the Guy mulamu Ali nyatwa kkkk
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 akulu inuo aaaaaa
Kudwala uku
Keep it 🆙 km next time mudzawineko piliz osangokhalila kuluza
😂😂😂😂😂this man
The best Comedian in Malawi
Hahaha umakwana Akita😅😅😅
Umakwanitsa comedy aise
Mulendo ameneyu waonjeza kumasukatu kkkkkk
Kunte uli kuseka kwabodza😂😂😂😂
Koma Kuntee kkkkkkk
Kkkkkkkkk my rich friend kkkkkkkkk don't kill me ooo
Phuma😂
Fiyonse😂😂😂😂😂😂😂😂😂
good job
Koma you guy😂😂😂 Umakwana🔥
Number one ulemuwanu
kkkkkk kuntelanji
Mwezi ukumatalika koma atleast weeks abraz . Musamakhalitse chonchii
😂 😂 kunte u are the best ase
Ndikusandutsani mbatatesi nonse 😂
My guy kunte 🔥💯
You the best comedy
Sunachenjele bwno kunte😁😁
Kikikikiki koma!!! He can make someone lose his cool
Millage nsapato yachita kutuwa 25 imeneyi 🤣🤣
Mmmmhhh koma iweyo kkkkkk
Fiyonseeeeee
My favourite comedian on the land 🇲🇼🔥❤️
Umakwanaa ase
Iwe kuntey banja lakuvuta basi
The gift aaah😅🙌
Iwe ndi dolo😂😂
Kkkkkk koma kunte sazatheka
Malawi 🇲🇼..... Kunte u represent
Nice
Respect kunte unafika
Bola wamumwelabe fanta 😂😂😂😂
Wiseman kukonda kupalamula 😂💔
😂😂😂😂😂😂 koma kunte
Nice one Kunteeeee
😂😂😂koma adha inuo m'matha
Koma ase penapake
Mofaya🔥
Kunte umatha bro🔥🔥
Ati fiyonse 😂😂
😂😂🤣🤣🤣🤣 koma kunte
Kunte ndi dolo 🤣🤣
Koma kunte eeersh
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Komatu atate.🤣🤣🤣
😂😂
Komatu kunte🤣🤣