Chachititsa kuti banja la Miracle Chinga lithe

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 7. 09. 2024

Komentáře • 354

  • @tesyncamel6758
    @tesyncamel6758 Před 7 měsíci +3

    Uyu wasowa kosewera iyaaah😮😮

  • @pemphokatembe443
    @pemphokatembe443 Před 7 měsíci +6

    Aaah😂😂😂😂 bambo mwakula inu koma !!😂😂nde inuyo chikukukhudzani ndichani?? Zaziiiiiiii basi

  • @ThiananaJustice
    @ThiananaJustice Před 11 dny

    Chinga ndi hulee kuyambira kale😂

  • @BennettNjedza
    @BennettNjedza Před měsícem

    Inuyo man mukuyenera muzibwelesa zinthu zomwe mukuziziwa mukutitaisa nthawi

  • @Jibsan-t2f
    @Jibsan-t2f Před 3 dny

    Iweyoo nde ukukananji program imene pomwe iweso palibechoti utiuze .iwe ngopusa kwambili timaprogram takoti

  • @user-yg6wl1yv7l
    @user-yg6wl1yv7l Před 5 měsíci

    You are doing a great job guys

  • @JackMlenga-j2t
    @JackMlenga-j2t Před měsícem

    Igozisiyan muna eeeeh banja Ra ainiyake mwasowa zochita2 km😮😮😮😮

  • @user-gf7oo9ht4y
    @user-gf7oo9ht4y Před 6 měsíci

    Nde ngati simukuchidziwa mukuyakhuliranji za m'banja mwa eni!!!!!!!!! Ndinu achitsiruuuuuuu!!!!!!

  • @user-fw5cg1yo9f
    @user-fw5cg1yo9f Před 7 měsíci +7

    Palibe chadzelu mwayankhula
    Yamba mwafufudza kaye ngat mufuna kutiudza nkhani

  • @AlieKazembe-md9jl
    @AlieKazembe-md9jl Před měsícem

    Chamba ichi guys maboxa bwanji

  • @user-zw8ns7bk7s
    @user-zw8ns7bk7s Před 7 měsíci +2

    Kape iwe ukufuna ukambe kt chani apa ndiye olo itatha ndi mulongo wako aaaaa chitchende chako ndithu

    • @KettieGwedera
      @KettieGwedera Před 3 měsíci

      😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @user-ti8oj7cm6c
    @user-ti8oj7cm6c Před 7 měsíci +2

    Khati mukusowa zochita kumafotokoza zamabaja aena paneti khati ari maluzi ndi zopusa zimenezo zabaja mwako amakurengezera ndindani sitikuyisiwa khani imeneyo olo titapanda kuiva yandinyasa kwambiri pangani ndarama munjira zina osati zopusazo mbuzi

  • @emosichimphengula8655
    @emosichimphengula8655 Před 7 měsíci +2

    Zopusa ukuti chiyani iwe ndiye kaya aaaa mwatani amwene ntchitoyi siyanu

  • @MarkGonda-qr4vm
    @MarkGonda-qr4vm Před měsícem

    Ndiye nanga chakukhuzani ndi chani

  • @user-hk7fm2hp4d
    @user-hk7fm2hp4d Před 7 měsíci +2

    Mukutinjiiii Inu apa eeee

  • @user-li6so9zl1b
    @user-li6so9zl1b Před 7 měsíci +2

    Asaaaa chilungamo sumukuziwa ingositani kuyakhula iyaaa

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 Před 7 měsíci +1

    Aaaaaa koma iwe chukukhudza mchani aaaaa koma anthu ena ndinu makape bwanji aaaaa

  • @user-pr6qr2tb9c
    @user-pr6qr2tb9c Před 7 měsíci +4

    Nanga poti chooona chenicheni simukuchidziwa mwaudza bwanji anthu zoona musanaponye nkhan zanu mudziyamba mwafufudza zopooira

    • @user-yj2dz5ej7r
      @user-yj2dz5ej7r Před 7 měsíci

      Kufuna kutchukila pa miracle chinga zaziiii kufuna kufana ñdi bakili muluzi CZcams channel
      Wagwa mayo kape peza zina zochita

  • @UmaliTama
    @UmaliTama Před 5 měsíci

    Ndikufuna ndidziwe nkhani yeni yeni yokhuza za grace chinga

  • @AleksaWilliams-qc6cn
    @AleksaWilliams-qc6cn Před 7 měsíci +3

    Amalawife tili ndi kuchikamwa eti,mulengezeso la mwana wanga lathaso

  • @user-ty3dm4is3c
    @user-ty3dm4is3c Před 7 měsíci +2

    Ndiwe galu kwambasi cz sukamba zoveka komaso sudziwa kufotokoza nkhani.ndiwe galu kwambasi utaitsa nthawi anthu

  • @DanMhone-iw6xg
    @DanMhone-iw6xg Před 7 měsíci +4

    Kod mukufotokozela amalawi chan kweni kweni chifukwa palibe chomwe mukufotokoza please

  • @kelvindickson
    @kelvindickson Před 7 měsíci +1

    Komatu simunanene chomwe chathela banjali mogwizana ndi mutu wankhani aaaa madala tafufuzani Kaye mutiuze bwino

  • @user-ho5nb2kx7b
    @user-ho5nb2kx7b Před 7 měsíci +1

    Km inu mulibe zelu pa dziko lapasi lotse 😊

  • @user-tt7eh6bm2j
    @user-tt7eh6bm2j Před 7 měsíci +1

    Next time mukadzafuna kuposta nkhani yamunthu mudzafufuze bwinobwino coz palibe chanzelu chomwe mwapangapo

  • @AnnieJackson-b5g
    @AnnieJackson-b5g Před 25 dny

    Akuziwa okha iya😢

  • @samuelbrian3409
    @samuelbrian3409 Před 7 měsíci +1

    Mutu wa nkhani?????? 😮😮😮😮😮 Waisting my data and my time yoooo 😢😢😢

  • @VanessahIsaac
    @VanessahIsaac Před měsícem

    Inu cakuvutani mcian mulibe zocita?

  • @SurprisedBubbles-dr5rt
    @SurprisedBubbles-dr5rt Před 7 měsíci

    Uku NDE kupusaa.......uchitsiiru weniweni wa amene akulankhulayi.. mauwo akunvekaso Kuti ndinu bamboo aakulu ndithu... Amakamba zabanja lanu ndani? Mwangokula ...leave miracle and the husband alone... Ali ndi ankhoswe awo ...kupanda nzeru

  • @ianjohnson3364
    @ianjohnson3364 Před 7 měsíci

    Aaaaaaa inunso nde ma report anu ali poor tu palibe chanzeru mwakambapo apa kambani zanu ndi akazi anu 😂

  • @user-vc7bk2ut6b
    @user-vc7bk2ut6b Před 7 měsíci +2

    Aaaaah ndimaona ngatitu akulankhura ndi mamunayo
    Umboni weniweni tikanaumva kuchokera kwa mwiniwake

  • @user-si7po9sd5i
    @user-si7po9sd5i Před 7 měsíci +6

    Mukamalankhula muzikhala mutakonzeka bwinobwino

  • @leahnyirenda3836
    @leahnyirenda3836 Před 7 měsíci +4

    Koma please guys be serious,find something tangible to do than waste your time and our data on useless things,ayambitsa yekha ndiye akuwuzani kut post that, everyone has issues mmabanja no marriage is perfect and they are neither saints, stop minding other people's businesses this is 2024

  • @chiluzbandah
    @chiluzbandah Před 7 měsíci

    Aaah lilime lanu likunveka chilomwe kwambir 😂 ndie zikunveka mopanda dongosolo

  • @user-si7po9sd5i
    @user-si7po9sd5i Před 7 měsíci +6

    Banja was meant for well matured people,not makanda,if you are not well matured enough,don't force yourself into marriage.

  • @TessMjuma
    @TessMjuma Před 7 měsíci

    Adah simumaziwa kulongosola mukumveka ngati mukutafuna pena ngati akuchita kukukakamidzani kuyankhula

  • @user-jb6rq4mh2d
    @user-jb6rq4mh2d Před 7 měsíci +1

    Nde ife titani umatha moyo wamunthu banjaso ndikachan end bro mokupepha uzipanga khan zoti tikamva tizitolamo kanthu ine sindimakudziwa ndipo ndilibe nawe vutoo bro end timakufilani coz mumatiziwitsa zambiri koma kumabwela mdi khan zokupsa

  • @user-um9yw9yl4w
    @user-um9yw9yl4w Před 5 měsíci

    Kkkk zina umangoona waziyamba kaya kuiyamba yot sungaimalize

  • @user-gf7oo9ht4y
    @user-gf7oo9ht4y Před 6 měsíci

    M'kamwa mwa chilomwe ngati m'menemo ungatiuze chani galu iweeeee!!!!!!!

  • @allanchawanda1889
    @allanchawanda1889 Před 7 měsíci

    Iwe ada ndi nyasa hit yakoyi ukafuna kuti anthu apange like zakozi uzibwera ndinkhani zoti ulinazo umboni komanso zizikhala ndi mutu weni weni nkhani zotyakuka bwino bwino , ngati nkhaniyo simukuidziwa sibwino kubwera pa media choncho nkumazatithela madata. Cause inuyo mukamayamba kufotokoza ife timaona ngati odziwawo ndinuyo, koma mmm ata, nde munthu upangapo like nkhani yake itiyo apapa?

  • @user-eh4zb2kj8x
    @user-eh4zb2kj8x Před 6 měsíci

    Nde mukufuna athu apange subscribe izizi😂😂😂

  • @user-uv1ub3xz7l
    @user-uv1ub3xz7l Před 7 měsíci

    Nde iweyo ngat choona chake sukichidziwa nde ukubwelelanji apa mkumayankhula fundoles zakoz zaziiiii

  • @user-cy5ko2qw5d
    @user-cy5ko2qw5d Před 7 měsíci

    Man vomerezani simukuziwa chomwemukuchita tonse sitingakhale atolankhani inu ofunika mupeze chochita china

  • @ThomasKawowa
    @ThomasKawowa Před 6 měsíci

    nde chakumvuta iwe ndi chani kutha kwabanja paziko pano wayambisa ndi Miracle yekha or kwaiwe akwanu palibe mabanja anathapo uli ndi topola amva

  • @littealbanda2404
    @littealbanda2404 Před 7 měsíci

    😂😂😂😂😂aaaahhh man inuyo simuli serious

  • @user-iv9vs3lf8u
    @user-iv9vs3lf8u Před 7 měsíci

    Kusowa zochita palibe ndamvapo apaaa busy ndi banja laeni basi lanulo ndiye likuyenda😅😂

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 Před 7 měsíci +2

    Banja sichiñthu chamasewela uli ngati usogoleli umafuna nzeru zakuya poyendesa banja Ndichifukwa chake muzaona zose mu banja zilimo koma limathabe chasowa baja ndi nzeru

  • @omarlux3434
    @omarlux3434 Před 7 měsíci +2

    iwe sukukwanisa ndikuza chilungamo sam mavita unja amatha

  • @DavidMontford
    @DavidMontford Před 7 měsíci

    Koma mwakhonzeka koma sizikunvekatu apa aaah mesa mukuti mwafufuza bwino bwino kuti mutiuze

  • @wonderfulkatsekela6210
    @wonderfulkatsekela6210 Před 7 měsíci

    Find something to do rather than giving us nosence here, go and meet one of them they'll tell you exactly what happened, stop fooling us 😂

  • @CliffitonSatema
    @CliffitonSatema Před 3 měsíci

    Banja ndilovuta ndepafunikakupilila

  • @alicembetewa5151
    @alicembetewa5151 Před 7 měsíci +5

    My data data 😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭

  • @user-bw8zb2wf8r
    @user-bw8zb2wf8r Před 6 měsíci

    Zazi nanu mwasowa khan ,

  • @OleTaika-xl1tg
    @OleTaika-xl1tg Před 6 měsíci

    Aaa nkuyankhula komwe mukanika zopanda mfuno nkomwe 😂😂😂

  • @denissegabriel2752
    @denissegabriel2752 Před 5 měsíci

    Sitikuv zomwe mukunen ankol mulibe nkhan

  • @dianna3577
    @dianna3577 Před 7 měsíci

    Nanga inuyo chukukhudzani nchiyani inuyo mulibe manyazi mmmmmm inuso ndinu Malawi

  • @MuhammadTennes-tx5ti
    @MuhammadTennes-tx5ti Před 7 měsíci +1

    Awatu tifika momangodutsa ma post awo aaa,kungotioningera bundle.

  • @user-cv7ow3vb4w
    @user-cv7ow3vb4w Před 7 měsíci

    Ukamaika ma headlines uzifotokoza zokhuza mutuwo osat zamkutu ukuyakhulaz zikugwiliza ndimutuwo

  • @BiquitoniNsandamila
    @BiquitoniNsandamila Před 7 měsíci

    Koma mwafufuza zotinamiza Ife ayi abambo inu ndi amabodza muli ndi mtima ngati wachure loko loko aaaaaa hhhhhhhhahhhh.

  • @GerardFelixDyson-tp1sp
    @GerardFelixDyson-tp1sp Před 7 měsíci +3

    Guys uyuyu nde amafuna chani? Kusatha kuyankhula, zopanda umboni nkumabwera nazo apa? Mxieww

  • @user-zf9mj4jj9w
    @user-zf9mj4jj9w Před 7 měsíci +1

    Kweni kweni ukufuna kutiuza kt chan ndangoononga bundle yanga ine

  • @user-es8pz3ie3v
    @user-es8pz3ie3v Před 5 měsíci +1

    So what's the issue of bringing nkhani yoti u don't have evidence

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 Před 7 měsíci +1

    Nde ngati choona sukuchidziwa ukudzatani apa apatu amzanu akufuna kutvhukisitsa umufumse zomwe amapanga namadingu akafuna ki akita

  • @FYAHMANNINETENINE-ty4jc
    @FYAHMANNINETENINE-ty4jc Před 7 měsíci +1

    Keep Up The Good Work 💪♥️🔥

  • @user-nb7bv6zy8c
    @user-nb7bv6zy8c Před 7 měsíci

    Palibe chomwe mukudziwa kafufuzeniso bwino bwino

  • @phillipstamaley7901
    @phillipstamaley7901 Před 7 měsíci +2

    Ndiye ife chikutikhudza ndi chani za zimenezi

  • @ReginaSiment
    @ReginaSiment Před 7 měsíci +1

    Fundoless .... Zaziiiiii

  • @ratkillermusic8482
    @ratkillermusic8482 Před 7 měsíci

    Osamabwera ndikhani Yopanda umboni

  • @dicksonphili3466
    @dicksonphili3466 Před měsícem

    Ine ndiye palibe ndavapo zokha mbwelela..mutu wankhani ndizomwe akulankhula sizikugwilizana mwina azanganu mwavapo kanthu timasulileni😂😂😂.

  • @user-nw6om5sc2n
    @user-nw6om5sc2n Před 7 měsíci

    Waweso nde maphwara anu aise bwanj kundithera bundle Yanga mukudziwa kuti zilibe umboni weniweni ndikuyifuna Pompano data Yanga

  • @user-marrie784
    @user-marrie784 Před 6 měsíci

    Osapeza Zina Zokambilanaxo bwanj.
    Zachani zimenezo

  • @user-mr7mx8sg5f
    @user-mr7mx8sg5f Před 7 měsíci

    kkkkkk tsono inuyo ngati simu ku dziwa choona cheni cheni chomwe mwa bweletsela nkhaniyi pa bwalo ndi chani

  • @GiftJulius-gx2kb
    @GiftJulius-gx2kb Před 7 měsíci +1

    Kusowa doing.chikwamkhuza mchani anthuwo.ngati loyamba kutha ndiilili mmmmmm

  • @johnmatola9374
    @johnmatola9374 Před 7 měsíci +4

    Chamba musizuta bwino Galu iwe Pesa dzina zocheta

  • @KenChitete-pg3ws
    @KenChitete-pg3ws Před měsícem

    Otsatithela ma data ndidzoputsa pano ngati banja latha kodi inu ndikoyamba kunva kuti banja latha,,chofufudzila mabanja athu ndi chiyani kusiya anu,,pitani mukakhodze ma banja anu ku makhaya kwanuko pano dzoputsa ayi foseki foseki kwanu kunuko shit

  • @user-wu8kp7ui5j
    @user-wu8kp7ui5j Před 7 měsíci +1

    Kufotokoza kukuvuta ankolo muzipanga Kaye training musanayambe program yanu.

  • @user-qh5jo5qh3b
    @user-qh5jo5qh3b Před 7 měsíci +1

    Yamban kae mwapeza official information yokwanila then kumabwera pa podium
    Cos palibe chanzeru mwakamba koma kungobwera ndi maboza chabe😂

  • @StevenJanuary-nm9bl
    @StevenJanuary-nm9bl Před 6 měsíci

    Ndipo zomwe ulankhulazi sizikupatsa chidwi chomvela....
    Uzikhala serious ukafuna kupanga zinthu zakozi

  • @phillipstamaley7901
    @phillipstamaley7901 Před 7 měsíci +2

    Zaziiiiii zaziiiiii!!!!

  • @MacDonaldkachala-cm5gc
    @MacDonaldkachala-cm5gc Před 2 měsíci

    You start the news without story

  • @victorauwana7258
    @victorauwana7258 Před 7 měsíci +2

    Mamuna waulula? inu nomweso mukutiso chathesa banja simukuchiziwa?

  • @user-xx5dc5wl7g
    @user-xx5dc5wl7g Před 7 měsíci

    Finally my brother machende ako may you please get out from CZcams chilungamo inuyo simukwanis solo ndi bakili Tv

  • @timothykayesa1143
    @timothykayesa1143 Před 7 měsíci

    Aseee improve, ukusewelesa mu Gold bwanj aaaaaa

  • @fabbyncube8900
    @fabbyncube8900 Před 7 měsíci

    Mmmm ndiwe wabodza iwe eeeeee 😂😂😂😂

  • @user-zt1kk1gb4n
    @user-zt1kk1gb4n Před 7 měsíci

    Chimene mukuyankhula simukuchidziwa ingosiyani

  • @WonganiSakala
    @WonganiSakala Před 7 měsíci

    Aaaaa kod mufuna mukhale nd ma aubscriber ambili et

  • @ConfusedAtv-bs4gc
    @ConfusedAtv-bs4gc Před 7 měsíci +3

    Nonse mboliyambambo anu nyini Zamanu musamatinyanse APA anthu Ngati ndookongolanso amene mukutithela madata apawa banja limakhala nyumba osati mafoni zauhule basi iwenso Ngati umamufuna huleyo kapeze wako Ngati sumatha kufunsila olo mbuzi ziliko utheka kumakagonanazo kuyambila lelo me siye kumabwekesa nkhani zamabanja aweni APA nanunso anthu amene muli ndimabanja pasani ulemu banja lanu polisunga nyumba osati pafoni

    • @GanizaniBalon-ie2oq
      @GanizaniBalon-ie2oq Před 7 měsíci

      Nanuso kahweleni uko zochitsilu

    • @user-bs7mi3td3f
      @user-bs7mi3td3f Před 6 měsíci

      Komatu mau a Mulungu anakaniza zopereka umboni wa bodza...if you don't know what happened lean to be chete cos mudzayankha nazo mlandu ku mpando wa chifumu wa Mulungu mwini kuweruzaaaaaa ohoooo

  • @masanjalaor247
    @masanjalaor247 Před 7 měsíci +1

    Inuso ndie ndi denje bwanj mukuyakhula zot mulibe information y can't u keep qyt

  • @ChipiliroLeadson
    @ChipiliroLeadson Před 7 měsíci

    Ndiwe omvesa chisoni kwambiri

  • @MakhangajIssah
    @MakhangajIssah Před měsícem

    Opusa ndi iweyo😂😂😂😂

  • @EmmanuelHiggaPhiri
    @EmmanuelHiggaPhiri Před 7 měsíci

    zose mwafotokodza Apa tikuxiziwa kale chomwe tabwelera apa ndikutha kwa banja ma reasons not mbolazo

  • @WzdomChipeta-xc6ic
    @WzdomChipeta-xc6ic Před 2 měsíci

    More💥💥

  • @nelsonchiyandikashaba4404
    @nelsonchiyandikashaba4404 Před 7 měsíci

    Topic ikukhala ngati ukudziwa chomwe chathetsa chonsecho palibepo chomwe ukudziwa

  • @FrankBrazioPhiri-bp8gh
    @FrankBrazioPhiri-bp8gh Před 7 měsíci

    Big up boss

  • @MadalitsoMaungu
    @MadalitsoMaungu Před 5 měsíci

    Palibe chimene chikuvekapo pamenepo

  • @user-eb3jv9zr8i
    @user-eb3jv9zr8i Před 7 měsíci +1

    Aaaaaa koma madala inu sizikumvekapo apa musatinyase

  • @wedumaulidi1199
    @wedumaulidi1199 Před 7 měsíci

    U dont know what ur tolking bro😮😮

  • @hopembendela
    @hopembendela Před 7 měsíci

    Ndiye ndiye chamba chimenechi kusowa zochitaaaa chani iwe ada pedza Zina zochita izi zakukanika palibe chimene ndatolapo apa sorry my dear

  • @ShaiHende-up7nf
    @ShaiHende-up7nf Před 6 měsíci

    Ndinu a chitsilu chabe chomwe muyqkhulq simuchixiwa

  • @emosichimphengula8655
    @emosichimphengula8655 Před 7 měsíci +1

    Ndiye ukuti chiyani palibe chomwe walankhula