6:57 good song and powerful even the voice is so good Thom keeping on singing for the Lord
nyimbo yabwino kobasi ngati kuti yatuluka dzulo ndimadalitsika nayo kwambiri, Ambuye akudalitseni.
One of my favorite songs, azatipasa nyimbo Yehova❤
Yehova wandipasa nyimbo 🙏🙏
Amen
Honestry may the good Lord bless u indeed
This guy is blessed !!!
Just asmile😊
You are so talented bro
Mukuyimba bwino amwene keep it up!
Powerful
Wahoo bro,pitilizani ku mulambira Yahweh powerful
Mbambande
powerful song keep it up broo
Amen Atsogo 🙏
Uli bho Thom
Yes wosakhulupilira munthu yesu yekha adzadze mu mtima basi
Zamphamvu uzi bro,musazimitse motowo.keep it up bro.
Amen Amen 🙏🙏🙏
Nyimbo ya mphamvu
Mulungu azikudalitsani ndi nymbo zanu zabwino komaso zachilimbikitso
It is a touching song.
Nice song 🙏🙏🙏
Very talented
Wandipasa nyimbo❤
nyimbo yambavu yopereka chiyembekezo
Yes
Zikungondilimbikitsa mulungu azikudalitsani
❤❤❤❤❤
Mukuimba mbwino ,, jst go to good Cameras
Amen
Powerful
Powerful
Amen
God bless your music 🎶 you have come from far