CRUISE 5 WITH RASTA GALAWANDA KAWALE NYABHINGHI PART 2
Vložit
- čas přidán 10. 07. 2023
- Elder Ras Galawanda of Kawale Nyabhinghi continues to share insights into the Rasta community in Malawi. He explains why rastas smoke marijuana, why they keep dreadlocks and how excited they were when the Government of Malawi passed a directive that rastafarian children can go to school with dreadlocks.
- Zábava
I always proud of you joab frank
What I like most about Joab, kudziwa nyimbo eeeh
Koma zoti Yesu anabwera kale kachiwiri through Haile Selasie nde nzachambadi
Mmmm rastar uyu akukamba zachamba
This is nice Joab
bwana could you do a cruize 5 with DR KEN ZIKHALE NG'OMA, it woul dbe epic i suppose
Joab umatha kucheza
Damn..I paused the video to verify about Marcus Mosiah Garvey...Ras Gwalawanda chimene akunena achikudziwa...the man is on point!SALUTE
92
2h6ju6udd😢
programme ya Cruise ndimayikonda kwambiri,imandisangalasa kwambiri kuno ku Zambia
Uyuyu ndi wa chambadi , mpaka mtumiki wao ndi mulungu.
What is the quencequence of uchimo if there is no Gehenna?
Imfa
Ndie mukuti tizilima chamba mulimbe.
I think mu pange more research on Bobo Ashanti.
Eeeeh zithu zake
Komanso banja ndichilengedwe kuti mwamuna amayenera kuzitengera mkazi wa iye yekha
raster iponden fada
Mumativesa kukoma achakhaza
Rasta
Rasta akunama tsikulinalake adzakumana naye mulungu maso ndi maso
Oiv
Joab akut sungasambire ku toilet bath lilipo... watero galawanda 😂😂😂😂😂
A Chakhaza panopo tili mu stage of Kingdom, we have three stages, stage of Law, stage of Grace and stage of Kingdom. Ma Raster akunama the second incarnation God now is in China not what what he is talking. Jahena is there, the new Jarusalem is there
May the lord open your eyes rastamen.......am touched
Mmm..Funso kwa Ras GALAWANDA ..Mwati Yesu ndiye Mulungo yo: Ndiyeno nchifukwa chiyani 'Yesu ku Munda wa Getseman kuja adadzapemphera pemphero yili".
ILAHI ILAHI LAMASABA KATANI ,, MULUNGU WANGA MULUNGU WANGA MWANDISIYIRANJI..Apapano Yesu yo ankapephera kwa Mulungu wake wutiyo.
Komanso pomwe ankanyamuka Yesu kukwera kumwamba iye adawatsanzika wophunzira ake ponena kuti ; NDIKUPITA KWA ATATE WANGA NDIKUKAKUKONZERANI MALO ...kodi atate wake wa yesu yemwe ankamunena apayu anali ndani.?
Inu khulupulirani yomwe mukumudziwayo osati za ma arguiment ambwelera apa
Misala ndi nthenda ya ku makololo ngati asima, bpp ndi matenda ena ambili
Koma Joab ndiwe dolo, nyimbo iliyose umaidziwa
Munthu sungaziwe nyimbo iliyonse..iwee😂
Ndimbambande mamunayu ❤❤
Bwanji zimene iwo anakana azungu mubaibulo ndizomwe akupanga..kumalemela,,ifeyo osatira baibulo nkumagwirila ntchito..
Anati sokoneza mutu
Chifukwa ngati akuti chiweluzo nkumwamba bwanji tikulangana pansi pompano??😂😂😂😂
Nde yesu anasutapo chamba ?? 🙄🙄🙄 inu ndachambadi heet. 😂😂😂
Koma penapake aChakhaza zoona mungalephere kufufa zamatathauzo a makaka owowo omwe akuzungulira I mean red, black, green and yellow, inu basi busy kufusa have u killed chicken before?
🤣🤣🤣🤣
Munthu sukumbuka kapena kuganuza zonse atleast watiimilira 😊
Mu chamba muli ntchitooo
This is stupid to be honest they praise Ethiopian president
Koma MA Rast eeeeeeee zamba zimapweteka hvy 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Christianity is a propaganda
*nde mukufuna kundiwuza kuti nthaw ija Yesu anali m'manda for 3 days Dziko linakhara lopanda Mulungu??*
*Chambadi sichabwino🤣🤣🙌*
Bible ndi nsete...