Kayo Withu - Mandede ( official visualizer )

Sdílet
Vložit
  • čas přidán 15. 05. 2024
  • Kayo Withu - Mandede ( official visualizer )
    #trending #hiphop #music
    song by kayo withu
    it's just for vibing when your bored .
    lyrics
    Verse 1
    Ine ndi mfana otisindilola kukhala m'maluzi
    Ndimapanga dollar zanga mboni yanga muluzi
    Life yanga ili bo ndeye usatifuse
    Ndimadana ndimaluzi ndeye usandipute
    Ndimadzuka too five kukameenya mahasoo
    Nde ndalama ulibe mawa tikupezasooo
    Inde tikusaka beib koma Ross chiwambo
    osamanga meshh koma owoneka booh
    Hook
    💰
    taona mandade ase eeee!!!!!
    Taona mandede adah iweeee!!!! X2
    Verse 2
    Iphone 15 alipo (many voices) Bola zi dollar
    Pic ndimakani makani, pocha ndiya bohh
    Tisataye thawi tangotengani broo
    Ndangotsitsa mtengo umaziwa am block
    Ndimadzuka too five kukameenya mahasoo
    Nde ndalama ulibe mawa tikupezasooo
    Inde tikusaka beib koma Ross chiwambo
    osamanga meshh koma owoneka booh
    Hook
    💰
    taona mandade ase eeee!!!!!
    Taona mandede adah iweeee!!!! X2
    @Malawi-Music_._com
    @nyimbozakumalawi
    @westarmoney

Komentáře • 13