This channel has to glow big.... Its wealth watching kuwuza ntundu wa amalawi zomwe ma station ambiri will never broadcast ....... I really support this channel sir salute.... Machiaveli.....2pac shakur
@@ChristinaChimombondayamika ndikuthoza moopsya for advice mwandipatsa for my sister, I really appreciate what you have said and I don't take it light. Thank you so much for your ad and help. P
I like the way you have been articulating this Chilima Tragedy Issue...I'm a Zambian but I'm still Mourning with Malawians the Hero you lost and 8 others 😢😢.. Wish Malawians had a number of People like you who are fearless
And after stealing they make sure that all stolen money is in a format of assets or forgiven exactly the same way late Kamuzu did. Now Malawi I becoming a mafia Elchapo state if not Hushpu in Dubai.
Athu amene akuyikila chakwela kumbuyu ndi wa mcp and ndiwakuba as for me l can't support chakwela why u people u hate the Truth chakwela and his cabinet apha chilima that is truly evidence ok
Fuso langa ndili nalo ndi Ili Black box inali kuti same day Malawi munalowa ndege almost 10 komano ndege ya Chilima yokhayo siinapezeke coz kanthu kaja kamaonetsa or isowe bwanji
Anthu a menewa amwene aziyenda bwino, komanso ndimati ndi pemphe Asirikari aku Malawi asapitirize kumu yang'anira, Chifukwa Ku South Africa a dziwa Kuti ma Israel akumanga misasa Ku Malawi, Kuti achitire Chiwembu Dziko la south Africa,ndiye Africa yonse iku ya ng'ana kumeneko,Ndiye muone m'mene iyenso aphedwere Ndipo zakonzedwa kale.
There will be pressure in MCP, azayamba kuyambana okhaokha ndi kuwululana, mwazi wa a chilima si mwazi wa nkuku, may God cause confusions in the camp of the enemies
Zoona,itakhala radio station,chifukwanso or atakhala nawo ma phone wo,ndi umphawi unabweretsedwa ndi democracy Wu ambiri sangaveko uphungu wina ndi winawu.Koma ine monga nzika yokonda dziko langa ndimadana ndi democracy kwambiri.Inatigawa ndipo ndikuooa kuti tikupitaku ndi nkhondo basi.Malawi itabwera pamodzi ndikukhala ndi chipani chimodzi momwe mudzakhale oyimila dera lililonse kuchoka ku Nsanje mpaka ku Chitipa ingatukuke. Zosintha-sintha zipanizi sizitithandiza,chifukwa ma plan azachuma sangakwanilitsidwe mu zaka four or five,never! chifukwa akaluza ndikulowapo ena,ena aja amabweranso ndi ma policy awo osiyana ndi amene anayambako aja,mwinanso nawo adzaluza kudzabwera ena ndi ma policy awoawonso ndiye kuti palibe kupita patsogolotu pamenepo,oluza ndi a Malawi amene amavotawo,dziko layima.Chitukuko sikumanga kokha,chitukuko cheni-cheni ndichoti moyo usakhale owawa,katundu asamadule,njala ithe koma ndi democracy sizotheka ayi.Bingu akanakhala anali ndi Moyo ndi amene anafunika kupitiliza chifukwa amene aja anali ndi masomphenya komanso okonda dziko lake,koma malamulo a democracy sakanamulora chifukwa democracy ndi,"awo adyako nafenso tikadyeko" rubbish yokha-yokha.
Aga khan is a private hospital, owned by people with so much wealth. Talking of the mess we are in now, abambo ako a Peter Mutharika ndi inu nonse a DPP ndi omwe munasakaza chuma cha boma and left this country in serious debts. Palibeso wa MCP amene angayende mwa mantha, for what?
This channel has to glow big....
Its wealth watching kuwuza ntundu wa amalawi zomwe ma station ambiri will never broadcast .......
I really support this channel sir salute....
Machiaveli.....2pac shakur
Tamangolembeni Chichewa chomwechi mutafuna mutha kumalemba Chi Lhomwe chanu chomwechi.
Kamba kakuti English ndi Chichewa zonse zikukuvutani malembedwe
It's true my brother these is seriously issue. MCP ndi AGalu
Powerful message!!
Chakwera akudziwa kuti waluza kale ndipo omuvotera ndi dzitsilu
Avota afamily bas
Kapena winanso uyu.
Mbuzi yeni yeni iyi
@@user-tk6qh9zs7h wamanyi iwe nyani wachabe DPP inatha achita Kufuna winanso afe akapangenso ndale MCP timalemekeza maliro yense osapota DPP ndiwachilomwe
Ndipo zoona tu mm
Anthu awawa apanga zinthu zowawa mmm
We need people like you in our society to tell citizens the truth
Ma support mcp evil 😈
My brother your the best and genius 💪💪🙌
Following you sir
My sister has been ill for days and went to St Maria Gorretti with mini - stroke and they told her to buy medication in chirani pharmacy
Buy STC 30
@@ChristinaChimombondayamika ndikuthoza moopsya for advice mwandipatsa for my sister, I really appreciate what you have said and I don't take it light. Thank you so much for your ad and help.
P
I like the way you have been articulating this Chilima Tragedy Issue...I'm a Zambian but I'm still Mourning with Malawians the Hero you lost and 8 others 😢😢.. Wish Malawians had a number of People like you who are fearless
we here to support us. big up my brother
Exactly brother mwadzi.wa munthu simasewela apenga misala onse a mcp
Amp my vote
Mumafotokoza zondisangalasa zonveka kwambiri
MCP and Chakwera time yawo yatha.
Zosatheka kuvotera chakwera mm no🤔
Yes zeni zen zimenezo
Big Up 🔥🔥
Zophana zinari zakare pano nithawi yoti nizigwira chito tizipanga mabizinesi tizipeza ndarama.osati kuphana ayi chakwera ni sataniki
Ndipo ife tinadziwa kale kuti dpp ndiyonyasa ndipo sizidzathekaso kutenga boma ili
Who will arrest CHAKWERA poti he has killed chili and Ralph kasambala?
Unamatu iwe😅😂
Kulankhula kopanda umunthu ,am a chewa too koma akupanga zopusa ndipo sindingapange zopusa ngat akupanga chakwera nda nzakezi ai
@@Tenjklvtcy ndanama pati kuti mundiweluze bwino bwino kuti ndisadzalakwenso?
@@raytavares2256 osamaperekera umboni wonama iweyo unamuona chakwera akupha anthuwo zoverazo
Zoona big mumakwana koma keep it up
Zitsilu kuyamikirana pa Zopusa
Iweyo khala ndi udolo wakowo ukuyankha comment ya chitsilu bwanji?
@@user-pn7cj9hb3t kagwere uko Munthu okhulupilira zonama iwe
genius
Big up brada
Yes , read it as well he was a great diplomat he discovered about people,land and authority
Mumatipatsa hope.... God bless you
Big up Bravo keep it up
The real citizen
Keep it up tithane ndimakapa a mcp malawi poison party
I support you bro
And after stealing they make sure that all stolen money is in a format of assets or forgiven exactly the same way late Kamuzu did. Now Malawi I becoming a mafia Elchapo state if not Hushpu in Dubai.
Yes that's true sadzapeza mtendere chifukwa mizimu ya anthu onse amene aphedwa pangoziyi idzakhala ikufuula mpaka kalekale
Thats true bro
Our own Snoop Dog ,I love your sense of humor
Athu amene akuyikila chakwela kumbuyu ndi wa mcp and ndiwakuba as for me l can't support chakwela why u people u hate the Truth chakwela and his cabinet apha chilima that is truly evidence ok
Good work brother
Brother ukunena zoona anthu ochitabwino sakonda ziko lawo ati mmene anadusa iwo enaso aduse momwemo zoti Mulungu waika pamenepo kuti ena apulumukilepo alibe nazo kungomulora satana akule mmiyoyo yao bsi zosaenda.
Never thought 💭 this he gonna win again never
Imvaaa!!!!
Good one
❤❤❤
Ndipo
Bwana
Fuso langa ndili nalo ndi Ili Black box inali kuti same day Malawi munalowa ndege almost 10 komano ndege ya Chilima yokhayo siinapezeke coz kanthu kaja kamaonetsa or isowe bwanji
Anthh omwe tikuwafuna ndi awa osati Ben longwe kubakira chigawenga chakwera
Mibado yawo yonse idzaona zowawa 😢 mcp chipani chotembeleredwa
Biggy mmakwana malawi vutolidakalipo coz mmene mwanenela atsogoleri amafuna azioneka iwowokha osati ena komatso ambili Ali ndintima woti ndiziyitanidwa ndekha ma milionea
Your crazy just leav it
Anthu a menewa amwene aziyenda bwino, komanso ndimati ndi pemphe Asirikari aku Malawi asapitirize kumu yang'anira, Chifukwa Ku South Africa a dziwa Kuti ma Israel akumanga misasa Ku Malawi, Kuti achitire Chiwembu Dziko la south Africa,ndiye Africa yonse iku ya ng'ana kumeneko,Ndiye muone m'mene iyenso aphedwere Ndipo zakonzedwa kale.
There will be pressure in MCP, azayamba kuyambana okhaokha ndi kuwululana, mwazi wa a chilima si mwazi wa nkuku, may God cause confusions in the camp of the enemies
Never vote MCP 2025
Olo councilor or Mp ayi
My vote my choice MCP woyeee🎉
You don't know how to talk to people,
Azipita kwao uyu kuzimbabwe nyani tilibe ntundu umeneu Kuno Omani mphonozo guys
Ovotera chakwera ndiopusa opandanzerunso
Dpp ikulowanso m'boma 2025❤❤
Akafula akanatha kutipatsa governance yabwino. #monarchy
Akamuna😂
zoona achakwera amaona ngat awina osaziwa kut akuononga, osaziwa kut akuzionongera zinthu ekha apa ndipomwe azaziwe kut pokoza zina zinaso zimaonongeka, 2025 ndipomwe azaziwe kut khobwe sinyemba no vote awo magazi a chilima akumuyenda pa mphumi pake uyo
The problem is omwe azavote next year alibe ma phone oti atha kumanvela kapena kuwelenga za pa social media
Zoona,itakhala radio station,chifukwanso or atakhala nawo ma phone wo,ndi umphawi unabweretsedwa ndi democracy Wu ambiri sangaveko uphungu wina ndi winawu.Koma ine monga nzika yokonda dziko langa ndimadana ndi democracy kwambiri.Inatigawa ndipo ndikuooa kuti tikupitaku ndi nkhondo basi.Malawi itabwera pamodzi ndikukhala ndi chipani chimodzi momwe mudzakhale oyimila dera lililonse kuchoka ku Nsanje mpaka ku Chitipa ingatukuke.
Zosintha-sintha zipanizi sizitithandiza,chifukwa ma plan azachuma sangakwanilitsidwe mu zaka four or five,never! chifukwa akaluza ndikulowapo ena,ena aja amabweranso ndi ma policy awo osiyana ndi amene anayambako aja,mwinanso nawo adzaluza kudzabwera ena ndi ma policy awoawonso ndiye kuti palibe kupita patsogolotu pamenepo,oluza ndi a Malawi amene amavotawo,dziko layima.Chitukuko sikumanga kokha,chitukuko cheni-cheni ndichoti moyo usakhale owawa,katundu asamadule,njala ithe koma ndi democracy sizotheka ayi.Bingu akanakhala anali ndi Moyo ndi amene anafunika kupitiliza chifukwa amene aja anali ndi masomphenya komanso okonda dziko lake,koma malamulo a democracy sakanamulora chifukwa democracy ndi,"awo adyako nafenso tikadyeko" rubbish yokha-yokha.
Big up brother
Mxiiii Lord have mercy
It's a curse for selling fellow black people in South Africa and they do it today with Israel.
Mcp is the party full of blood from the beginning
Even mutachita sanje bwanji koma chakwela adzamwalila akudya money ,kukamwa kopotokako galu
😭😭😭😭😭
Amalawi akuti ukuwawuza iwe kape osakawuza kazi wako zopusazo bwanji
Sizikumvekatu walemba za chibwibwi
That's true brada
Uzinamiza mbuli zinzako zomwezi if you have evidence come and provide it ndiwe kape kwambili ndi macadet anzako onse akupanga support
🔥
Thus pro found bro..keep up a good work
Tiwakwapula akamapanga misokhano
Walankhula ngamo bro zophana nzakale
Guide book yawo ndi zitsamba mwa aSing'anga
Zoonadi man mumakwana ndipo mukulitsegula maso dziko komanso Malawi wa lero siwakale uja
fotsek apa, kumene kuja pali kutukua ,bcz ose amene mmapanga ndale ndiovutika ngt ine.Mulibe zochita zina zotsatira zake mmaba ma tax athu.
Aga khan is a private hospital, owned by people with so much wealth. Talking of the mess we are in now, abambo ako a Peter Mutharika ndi inu nonse a DPP ndi omwe munasakaza chuma cha boma and left this country in serious debts. Palibeso wa MCP amene angayende mwa mantha, for what?
Hahahahaha sawina lazalas
mmmm mukuona ngati dpp ikhoza kuwinaso? kkkk ngati kulioimira kumeneko kkkk
Sitivota kwa munthu wàmagàzi
Nchimo kuzunza😢
Kkkk wasowa zofotokoza iwe wayamba kupenga kkk
Mbiri ya ndionyasa
Zona chakwera Ndi nfiti, a Muluzi ankanena zoona
Chakwera plan yomwe anayipanga kupha Chilima basi azichosera mavoti okha agalu amenewa
Mbambande big ulemu wanu
Which evidence you looking for
Anthu amapenga misala ndi ma drug .kumayenda maliseche
Simukunama boss
Mumativesa kukoma inuyo
Chilungamo chikwabayatu a mcp
❤❤❤❤❤❤❤❤DPP
Musanamunamizile Chakwera ndipo Mulungu akukhululukileni mukunena zinthu zomwe mulibe nazo umboni .....nomwenu ndamene mwapha Chilima Kuti muononge mgwirizano wathu
Iwenso mulungu akukhululukire coz you dont know what you're talking about
Iwe opusa kwambiri
Wanzeru ndiwe ukukonda anthu okuphawe
Ifeyo kuno ku Ntcheu Central BAWI pankhumba tagwilizana zodzavotera APM 2025 ndipo MCP ndi Chipani chakumpha
Don't bother only God knows the truth
MCP , never never again watikwana,
Adani aku UK 😂😂
Adzabera mavoti ndi zomwe akundalira
Iwe ndi kape unakakhala uli ndi zochita sibwenzi ukumayankhula kunyela Kodi ukuyankhulila kuchiphisi kapena kuti ngati uli ndinzeru usandiyankhulenso
MCP will never change 😢
Ndipo sindiziwa kt kapen azapanga bwaji? Koman ifa sithawik pano thawi yamuthera
Zazi bwerani pa ground
Muli nd I vuto