Everyday am coming back to this video to support Granny. Its ablessing to have one alive and enjoying what she loves to do ndi zizukulu zake, enafe athu anapita kale kale😢
Just imagine a grandson kulimba mtima kukatenga agogo ake aakazi kuti aziwasamala,,,,, God had to bless him through her,,,,, very few guys can do that. Pano azidyelela nawo luso laagogo ake, zokoma.
I have watched this video a numerous times...I want Jetu to break the 1 million views record in 12 days!🥳🥳🥳💃💃💃Queen of amapiano! Ndikangolowa mgalimoto ikumakhala pa repeat!nde mulichi beat!
grandma will break the record, like my comment ndibwerenso kachinayi kudzawonera
Ase tabwelan muiwonelenso
Ndipo live. Apweteka ambiri uyu
🖐️
Bweran 😅😅
Bwerani ndithu
We here mpaka atapanga break record... Like my comment, ndibweranso
God bless you
Yes bro until apange new record
Lero mwaonera kale ngati😂
Ine aka nkachiwiri lero 😂🥳
@@CharityChiponda
🤣🤣🤣 Anthu mukuipatsa moto.
Dear grandchildren if you reading this comment in 3000...we had Jetu,she was a vibe and a star in her old age.
U forgot to say ur gone too _&u will miss them😅😅😅
One time❤
Jetu much love from zambia 🇿🇲🇿🇲
Those who watched it more than 5 times, don't be shy, raise your hand🤣🤣🤣🤣🤣
✌️
Ndikubweleza pano 😂😂😂
Ine pano ndikumvera Ka number 10 😂
Iwe 5times yachepaaa pano tikuonera kachihandede😅
10th time now 🤣
Ine nde zundibebera😌 like my comment ndibwerenso
My country people🇲🇼 will make you feel like you can conquer the world once they are with you. Jetu will set a new record. Haters will hate😂😂😂😂
Jetu ndidoro 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Amene amakonda jetu let's gather here more fire😂😂❤
Amakwanatu jetu more fire💥💥
czcams.com/video/w58PDhD105s/video.htmlsi=thlj3RgVa8SNUVDD
Respect to her 👏 ❤
❤here i am
❤❤
Cholakwika Cha nyimboyi ndi kutha msanga please like my comment ndibwereso
Those who watched it more than 20 times don’t be shy raise your hand
I'm trying to watch 3times a day so that enemies for Jetu continue crying
Adani okuda amve kuwawa
Some here 😁😂😂😂😂
🎉🎉🎉🎉 aka kachinamba ten kuonela Agogo muli 🔥 uli Hot
Keep pushing Grandma
Like this comment ndionelatso ka ten leroli🎉🎉
Apa ndikuonera pa 116k. Like my comment ndibwerenso
Ulipo ase?
Ndabwelaso pa 275k views
351k now
Ife tugona pompa 😂
420 now😊
❤❤koma iyiyi munali dance and director wapanga zadongosolo even the outfits its giving the vibe🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉
Olo ine ❤❤❤❤ nyimboyi ili pawiri ndikuuzanibe ndiionere kachikena
Who is here to break the record of 1 million in 12 days🎉🎉🎉❤❤❤let's gather here
12 days yachuluka tufuna within 10 days 🎉
I'm here throughout. Ndisiyileni ntchito imeneyi ndikwanitsa ndekha😅
We are here tirelessly working 😂😂😂😂
10 days bwaa😅
We are here
Amene tili ndi thawi yosaka chakwaza let's gather here..jetu to the world ❤🎉
Felt it when she said "ndinalira, nthawi ndinataya" 😢
I don't care watching it everyday coz I love Jetu🥰🥰🤗
mene tili mu road to million tapangani like ndiziwonera katutatu pa day
Jetu wandipasa chilimbikiso kuti pangatalike munthawi yake ikakwana yakwana kukalamba sukungatilephelese kuchita zokhumba zathu
@@ChristinaSaidi-yf4dm ndipo mzapamwa
Bwerani muzaonerenso
@@clarasibandemdhuli ndipotu akaka ka chi 6 lero sitikutopa
I like the translation
Even president of the republic of malawi aonela nawo nyimbo imenei jetu 🔥🔥🔥
Massive keep up the good work
Go a heard gogo Jet
Ine ndi jetu iwll leave my comment here when ever you like me iwll watch this vedio again❤❤❤
abale ine ngatitu ndigone pompa. Like mine nane ndizibwelabwera
Jetu wabwera 🎉🎉🎉kuonera kachi 10 apa... koma ndibweranso 💃🏻💃🏻💃🏻
Let's support our Grandma for his success 🙏🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Ine ndikungowonela dairy lik my comment 📌💃🏽💃🏽
JETU amapiano queen umatha ulemu upite kwa Mada ambuye azikudalitsa waika agogo ako pa map 🎉😂❤🔥🔥
Yomweyo JETU iweeee😂😂😂 grandma kuzayipasa moto 🎉
Everyday am coming back to this video to support Granny. Its ablessing to have one alive and enjoying what she loves to do ndi zizukulu zake, enafe athu anapita kale kale😢
Gogo JETU tsopano ndizingoonerabee mpaka moyo wanga onse😋😛
jetu yemweyo kuti wawawa 😍😍, like my comment ndionerenso.
Amene taonera more than ka 5 like this comment
Ndibwerenso
Road to 1m views
Ine pano story of my life eeeeee anandisiya manja alinkosi 😅😅😅
My support Jetu mpaka utakweza flag✌️
Where is One Million Views SADC and Africa at Large, 🇳🇦🇳🇦🇳🇦🇳🇦🇳🇦💐
Moyo wanga umkalinda kuteloku, amalawi tsiku lina lake, dziko la pansi lizatidziwa zeni zeni, jetu keep the fire burning
iyi ifike one million fuse.. Like my comment ndibwerenso kuzaonera kachikena ❤
Lyk de confidence mwabwera kuzakhala jetu❤❤❤❤
We all have one goal, people make people ,
Making Jetu record holder,
Raise your hands if you watching for the same reason ❤
Haha amwene jetu nd vibe the whole malawi grandmo💥💥💥🥰🙏
Malawi celeb wankulu wayakhula kuseliku akuthokoza 200 kgs , 1 MILLION VIEWS yatsala pang'oma . Let's make it 1 MILLION VIEWS guyz
Watching this from SA 🇿🇦 This is a masterpiece let's reach 1M fam I'll come back after every single like on my comment
IWE NDINDANI INE NDI JETU I LOVE YOU WATCHING FROM CAPETOWN ❤❤❤❤❤❤❤❤
Ndizoonadi,,,ena kukutayisa nthawi,amazakufuna zikakawavuta.nkumawawuza kuti munapoyira game ili yanu...umakwana Gogo Jetu❤
We are here mpaka Jetu apange break record.. Jetu to the world 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Ine ndikumangoonera Daily pakundiwaza ndipaja akuti iwe ndinda ine ndi Jetu!!
Me I don't know how many times I watched this super star 🌠 music video for selebu wankulu JETU🔥🔥🔥🔥
🇿🇲🇲🇼Malawi let's gather here for the support of our grand mother 🔥🔥🔥🔥🥇🥇
Ndpo uyuyu
Eee plibenso,🔥🔥🔥
Mukamati grand ma muyambana naye jetu
Omwe timamva ngat JOHN UKUFUNA CHANI mmalo mwa TELL ME UKUFUNA CHANI lets gather here😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Let me leave this here, whenever you give me a like will come see Jetu again❤❤❤❤❤🔥🔥🔥🔥🔥
Great 💯
Iyi tivela mpaka 2080 sizatha fasho ,,, Jetu akazat Ai pitan tulukan 😂😂 ❤❤
yafuka 1M views yokha😆
Watching more than 30 times now💥💥
Project 1million 🎉 wozaaaaaa jetu iwe basi 10 days basi guys tiyeni tiyeni
We are here mpaka jetu a break record 🎉🎉🎉 like my comments ndibweraso🥰
Leaving this now in order to come back once like it🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Am so happy for you jetu,keep fire burning🔥
Ma gunners let’s gather here tatchulidwa uyu ngwa arsenal ndithu 🎉❤
Mpaka tikaponde million KGs ❤❤❤ tapanga like ndibweleso nsaiwale please ❤❤🔥
A Jetu tsopano❤❤❤❤, tiyeni tiyeni tikwane militoni viyuzi
Jetu to de world🔥🔥3 stop,,, road to 1 million fuse
Cosoma get ready for The 10 Million Kwacha Jetu needs to receive 2024.......
Mnali nsanayimvele koma ayi ndithu gogoyi ndi celebrity weniweni 💥💥💥
Ndipo ndapeza chochita watching from South Africa Capetown
It's day 10 lero.....
1 million views in 10 days has a good ring to it....
Paja arsenal ndikumadzulo?? Top fan💃💃💃
Amene tumati tikagwira fon kumakumbukira kut tikawonereso like my comment nzibwera bwera kuzawonera apa #Jetu🎉😂❤
Tikumabwerabe
Hahaha ife pano
Kkkkkk
🤣🤣🤣🤣 ndipo nde tilipo ambilitu
Ife pano😂
Eishiiiiiii sindimadziwa kuti zilitelo... Mulungu Anasitha nyengo za Hannah uja pano wasitha Za Jetu mulungu wanthawi mulandile ulemu 🙏🙏
Road to 1 million kgs fuse🔥🔥🔥
This is my tenth time watching it.... Wanna help Jetu break the record
Heart break mpaka kulowesa fisi kuti akapolese Jetu? AAAH ayyii munamulakwira Ching'axy.
Just imagine a grandson kulimba mtima kukatenga agogo ake aakazi kuti aziwasamala,,,,, God had to bless him through her,,,,, very few guys can do that. Pano azidyelela nawo luso laagogo ake, zokoma.
Mpakana ndafika pomaonela ngati dosage,kawiri mamawa, kawiri masana kawiri pogona 🥳🔥Iwe nde ndani💜
Watching over and over again 💥💥
For me, it will be on repeat until it reaches 1mili in 5 days. #Breaking the record🔥🔥. Like my comment ndibweretso 🔥🔥🔥
Zomwe ali yese akufuna
Those of us who are watching this mamawa masana madzulo everyday let's gather around😅
Kkk am here again 😂
@@AnnDNaluso 😹 mwandipangitsa nane ndibwere
❤
Ine mpaka ikwane 1 million views
@@evancesteven9755olo nane ndisiya kubwera ikakwana 1M😂😂😂
Granny got vibes and the song is a hit 🔥 let's take to a million views one love from Zambia 🇿🇲✊
This is so dope gogo watching straight from South Africa
Kaya ku CZcams azindnena kuti mwandilipira koma kabhoweka nd jetu emweyu akundsekesa❤
I have watched this video a numerous times...I want Jetu to break the 1 million views record in 12 days!🥳🥳🥳💃💃💃Queen of amapiano! Ndikangolowa mgalimoto ikumakhala pa repeat!nde mulichi beat!
Ine ndiye ndumaonera 5 times a day since day 1...big up Jetu..wapha
It is certainly true that Jetu is trying on her behalf but she has good dancers, This is Jehovah's grace 🫡
Ndabweranso kachikena, Jetu taking over at such old age💯✅
Kwacha bwerani tiwonele mpaka 1 million vuwuzi
Jetu to the world🙅💃💃
Am from Zimbabwe 🇿🇼 but you guys i really enjoy zinyimbo zakumalawi ❤❤❤❤❤
Ameneyu akufunika plot basi,Congratulation Jet lee,Oyimba ose apamalawi wakhalira misana,ine ndawonela almost 7times
Ndipo anyamata mumavinanso bwino ,nyimbo zanu zonse mumavina zogwilizana ndi nyimbo.Go deeper guys our granny to the world .Thanks Em D
Age is nothing but just a number. Love you grandma and your music 🎶🎶🎉❤❤
Am here liking your comments so that you should come again and watch this masterpiece, team Jetu all the way🔥🔥🔥
365k viewers in just 2 days kuposa artist winawake ozipopa kwambr ozimva kutchuka mu music industry
Jetu to the world ❤❤💪💪🔥🔥
Kwabeba kuno like my comment ndibweretso😍❤️
🥰🔥
I speak on behalf of all Malawian ...we had a meeting and we all agreed this song is more valuable than gifts of GOLD
When I grow up, I wanna be Jetu🔥🔥
Ndionera mobwerezabwereza mpaka ikwane 1 million views as soon as possible.
Please, like my comment ndibwerenso.
Ineso cndkupuma😂
Ulibe jerasi🙏
yomweyo garu iwe
I'll leave my comment here so that when someone likes it I'll come to watch it again.🔥🔥Much love from Zed🇿🇲
🔥🔥🔥
Come watch it again😂
7 time's abii😊❤❤
@@hendrixchingambeni2221Here I am for the 200 time
In love with this woman ❤she vibing her old age
I will be here until this video hits 1 million views ❤🎉 JETU to the world 😊
Let's Give it a Million guys😂😂 ... All zambians let's gather here😂😂😂
Let's watch it again and again
Will leave this comment here kuti even aftr ten years this shall be regarded as a hit and a record breaking song 🔥🔥🔥
any Zambia's here🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲
Congratulations JETU nthawi yotamba alibe🎉🎉🎉🎉